ZOOPSA ZAULURIKA MZIMU WA SKC UKUMUBWELERA PRESIDENT ANATHAWILA KU ITALY KUTI AKALAPE MACHIMO

  Рет қаралды 90,895

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 259
@domminicchikalenda
@domminicchikalenda 2 ай бұрын
He is more knowledgeable in spiritual matters more than many of us writing the nonsense here. An iron sharpenes an iron, he wanted to learn from someone who has the same Moto of servant leadership at heart
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 ай бұрын
Ndipo kudziwike kuti kuli mulungu ku dziko la Malawi 😢😢
@DKMWALE-ew3lp
@DKMWALE-ew3lp 2 ай бұрын
Comrade za report zo musazengelezetu mutiponyele timadalila pompa apapa
@AndrewZimba-m3j
@AndrewZimba-m3j 2 ай бұрын
Ndiye kolapako mpaka anthu 385 bodza ilo❤❤
@AnnahMpamati
@AnnahMpamati 2 ай бұрын
Ndipo mulungu amukathe motheratu chakwerayu popeza iiiii ndi muthu woipa kwambiri kumupha mnzake zaziii , chikungoyenda yenda ngati chigalu tsono mumayiko amnzake ,chikapange ngozi kumeneko bac asaaa
@FeliaNgunga
@FeliaNgunga Ай бұрын
So we have no God in malawi😂? God is alive 💪
@CharityChirwa-t1e
@CharityChirwa-t1e 2 ай бұрын
SKC ndiathu ose omwe anamphadwa mopanda chifukwa ambuye chitaninawo athu oyipawo misozi sikutha pakhope zaathu olila tikulemphela kuvomeleza zakuti chilima ndimalemu ndichithu chosayuwalika Bola inu achikangawa munakangomuchosa nkono kapena kumusowesa kwamasiku chabe kuti mukawina muzamutuluse koma kufika size yakupha 😭😭😭😭😭 ambuye achitenanu ndithu inu Mr chikangawa
@UngweruGausi
@UngweruGausi 2 ай бұрын
Okumba zenje agwelemo yekha misozi yosatha mumaso
@jicakadewere40
@jicakadewere40 2 ай бұрын
Momwe amapanga zimenezoo samadziwa kt akuchimwaa? Eeeish.
@yamikanitagoneke9215
@yamikanitagoneke9215 2 ай бұрын
Mmmhhh muzonse tiyamike mulungu iye salakwitsa
@misoMoyo
@misoMoyo 2 ай бұрын
Tsono mukamati bodza bodza anthu sindikumakumvetsani ena kuti munaganiza chani likhala bodza bwanji munthudi wapita Ku Italy kma zinthu zinazi ai ndithu ngati mulibe zoikira comment kungoona za nzanuzo anatiphera anthu ambiri osalakwai mizimu Yao iwasowetse ndithu mtendere Ambuye mutimenyere nkhondo ndinu
@MustafaIbraimo
@MustafaIbraimo 2 ай бұрын
@ChippieNkhwali
@ChippieNkhwali 2 ай бұрын
Winawu ndi umbuli,,kuli mulungu ku italy?
@BarwickSalanje
@BarwickSalanje 2 ай бұрын
Akalapa bwanji pamaso pamunthu kusiya mulungu...akuluwa zinthu zawavuta basi
@CassimuKasaka
@CassimuKasaka 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 kayaa
@ubs7030
@ubs7030 2 ай бұрын
Iwe ndiwe Satanist ndi DPP yakoyo, mukunama boma simungatenge.
@ubs7030
@ubs7030 2 ай бұрын
Sanje yakuvutani
@clesheinvestments
@clesheinvestments 2 ай бұрын
Nsanje yawakuta mpaka ku Matako a dpp ndiye palibe Cha nzeru chomwe angalankhule. Agalu a dpp kusankha Munthu okodzedwa kukhala Mtsogoleri wawo. Pano dpp tasintha dzina tsopano ndi Mikodzo Party
@ColiousLevinson
@ColiousLevinson 2 ай бұрын
Mwachebwetsa anthu sangadye kunyumba kwako komaso sangadye kwachakwela awuzeni anthu adzingwila nchito ife SITI ngasinthe
@Paul-q2p
@Paul-q2p 2 ай бұрын
Kkkk ndiye kuononga ndalama kukalapa ku Italy kuno church kulibe 😂😂
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 2 ай бұрын
Kaya kkkkkkkkkk
@AlcidiaMacario
@AlcidiaMacario 2 ай бұрын
Kkkkkkkk
@CHAKAKACHAKA-MANMW
@CHAKAKACHAKA-MANMW 2 ай бұрын
MULUNGU ALANGA YEKHA AMENEWA
@DavidKanyemba-n2s
@DavidKanyemba-n2s 2 ай бұрын
Mukundipheranji😢kolona ali pakhosi
@patrickscott9086
@patrickscott9086 2 ай бұрын
I remember imfa ya Chilima Chakwela anabisa km uyu ananena kut amalawi Chilima kulibe wafa ndi2 Km boma limabisa
@RebeccaWalusa-lb5yi
@RebeccaWalusa-lb5yi 2 ай бұрын
Choipa chimasata mwini oyenda ndilupanga
@OwenNthala
@OwenNthala 2 ай бұрын
Munthu oyipa uyu kwambili 🤔 But anyway 🙄 mzumu wa a Chilima & other 8 innocent people 😭😭 May their souls continue rest in peace in the name of Jesus 🙏🏼
@DKMWALE-ew3lp
@DKMWALE-ew3lp 2 ай бұрын
Blood of innocent pple
@clesheinvestments
@clesheinvestments 2 ай бұрын
Agalu inu siyani Bodza. Ndipotu ukamamupekera bodza m'dani wako zimakhala ngati kuti iweyo opeka bodzawe ndiwe CHITSILU komanso wa Nsanje ndi osowa zochita. Kukhala wa dpp ndi Njira imodzi yokalowera ku Gahena. Ndipotu mubangula simunati komanso Chakwera akulamulirani mpaka 2030 wooooooo
@SilajuJenala
@SilajuJenala 2 ай бұрын
Allah knows the truth
@christophergibson72
@christophergibson72 2 ай бұрын
Iwe nde msaname umandinyasa wava umsowa zochita eti
@YankhoRumwila
@YankhoRumwila 2 ай бұрын
Ada uli ngati ine, ada amenewa ineso amandinyasa
@NoorRasheed-re5vh
@NoorRasheed-re5vh 2 ай бұрын
Komabe zonse mukupekazo pofuna ulamulilo wa Dpp odzavota ndife ulapa
@AckimKasiya-u7q
@AckimKasiya-u7q 2 ай бұрын
Awawa too much mabodza
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 2 ай бұрын
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa
@LisaKamanga-l3z
@LisaKamanga-l3z 2 ай бұрын
Kkkkkkkkk akuti Lapken anafika ndi mfuti
@FazirahCoster-o4c
@FazirahCoster-o4c 2 ай бұрын
Chakwera and his priest, am talking about papa both of them they have most sins, repentance can't work if you are asking a person, no!!! , but in only one God can work, otherwise they will just worst their time
@AnthonyChirwa-t4g
@AnthonyChirwa-t4g 2 ай бұрын
cha nambar one anyamata akhanga zaon ulemu wanu mmatisangalasa komaso kutionesa zithu zoti enefe sitikuziziwa mwaichi ulemu wanu
@NtchindiChirwa-l8o
@NtchindiChirwa-l8o 2 ай бұрын
Akuma report alibe kkkk any way pot lumalawi kuno umbuli ngosayamba
@ubs7030
@ubs7030 2 ай бұрын
Nonse mukunyoza president ndinu alomwe nokhanokha.
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 2 ай бұрын
Ochewa tili nkatimo aise
@CatherineMbela
@CatherineMbela 2 ай бұрын
Muuze avesese aise
@HawardStainly
@HawardStainly 2 ай бұрын
Iwe monga mchewa?mbava ya mcp iwe
@JamiluSunday
@JamiluSunday 2 ай бұрын
Muli ndivuto ndi alomwe eti?
@FumbwaLyson-3710
@FumbwaLyson-3710 2 ай бұрын
Kukamba chilungamo imfa ya chilima ikupweteka mmalawi aliyese koma akulu awa asamatinamizepo coz itangochitika ngozi adati ali ndi umboni onse pa imfa ya chilima maso athu anali kwa iwo koma mpaka pano kuli ziiii apa akutiuza zina haaaaa uyuu asamatipepeletse😂😂😂😂😂
@EuritaDeric-fz3ds
@EuritaDeric-fz3ds 2 ай бұрын
Mulungu wathu ndi wamoyo
@PERRINGSKACHOKOCHA
@PERRINGSKACHOKOCHA 2 ай бұрын
Akulu bodza musiyw kma ndinu mbuli yakulu radio yabodza iyo
@MeniyaMikaya
@MeniyaMikaya 2 ай бұрын
Kd MOTi ngozi yadzuloyi aphas ndi a mcp machende Ako iwe chilimayis mulungu anapangila dala kt zichitike izi dziko la Malawi likanakhala pamavuto ndiye iwe pathako Pako limpompo ndipo mulungu akukanthe iweyo shupt yese amavomeleza izi ndiwopepela
@christophergibson72
@christophergibson72 2 ай бұрын
Ndipo zoona ase
@YankhoRumwila
@YankhoRumwila 2 ай бұрын
Ndipo ka radio station ka mbuli ngati aka sindinakaone
@FaithDonald-ts2pp
@FaithDonald-ts2pp 2 ай бұрын
Kodi munthu amalapa machimo ake kwa papa?🤣🤣🙌🙌
@JamiluSunday
@JamiluSunday 2 ай бұрын
😢😢 rip chilima
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Komabodza kamabodza kamabodza kamabodza kambodza kamabodza kamabodza palibe chimene amalakhula choona mabodza 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@AnnieKwisanja
@AnnieKwisanja 2 ай бұрын
Nawenso ulibe matsiku osatila munthu wakupha iweee
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 2 ай бұрын
Ndiwe oipa iweyo ulibe mzelu poti sadaphe m,bale wako
@migneslutepo221
@migneslutepo221 2 ай бұрын
,,😂😂😂😂 Koma abare boza mumaliziwa mulungu adakhara pasi pano bwezi tose anati ononga 🤣🤣🤣
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 2 ай бұрын
Nankhumwa ndi mbudzi ya munthu koposa mbudzi zonse, chimunthu chopanda mzeru.
@Martha-m6e
@Martha-m6e 2 ай бұрын
Ambuye ntchito ndi yanu.asowe mtendele onse amene anaikapo mau.
@NaomieBanda-t6g
@NaomieBanda-t6g 2 ай бұрын
Ndipo pemphelo la papa wawoyo siligwila ntchito mpaka iwoso apume kuti chilima naye apume
@rashidadan2533
@rashidadan2533 2 ай бұрын
This is one of useless president in Africa , Am sorry my fellow malawians , big head but empty
@MandalaChaona
@MandalaChaona 2 ай бұрын
Lazarus Macathy Chikangawa as a leader of Chikangawa Party,you will never have peace in this peaceful country Malawi. Lazarus evil man 👹 🔨 ⚒️ ⛏️ ⚒️ 👹. Uzisowa Mtendere choncho kumapeto kwake mkuzimangirira .
@LaitoneJefitala
@LaitoneJefitala 2 ай бұрын
Ukunama phwanga
@GonjetsoBonface
@GonjetsoBonface 2 ай бұрын
😭😭😭😭😭 rest well
@FeliaNgunga
@FeliaNgunga Ай бұрын
So we have no God in malawi😂?
@HenryLikaswe
@HenryLikaswe 2 ай бұрын
😂😂😂😂
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
achimwene munthu alibe mphabvu zokhululukila machimo amunthu mzake ai nanu please nthawi zina dzilakhulako zoona abale mabodza daily kodi mmaona ngati mene munayambila kuwanamiza mukuona ngati sadziwabkuti ndimabodza?
@PatrickNgonya
@PatrickNgonya Ай бұрын
Mulungu ndi mulungu palibe chobisika pa dziko la pansi
@MeniyaMikaya
@MeniyaMikaya 2 ай бұрын
Ndipo chakwela wachita kuyitanidwa osati mabodza anuwa ai kmso chakwela sakufa ai chifukwa ndiwosalakwa atafe ndi petulo wanuyo nkhalamba vimilomo ngati zokuna za alonwe kuyankhula ngati wagona kubumbu kwa get shupt alonwe mademo mungapange ndife achewa inu ? Mwachepa muzingolila choncho munya mesa mtanyiwa wanu yemweyi anakuuzani kt mangochi DPP yawina ndiye sinunaona inawinila kumapwala akew😊
@chiletsokazembe-ri4ic
@chiletsokazembe-ri4ic 2 ай бұрын
mmm; udziyankhula moopa mulungu, inuyo wakuuzani ndindani? mmalo mopemphelela dziko lathu kut chikondi chipite patsogoro kom muli busy kufalitsa uthenga olakwika omwe satana akusangalala nawo, kod ndinu anthu otani iwe ndiwe wasataniki munthu oipa mulungu wa malawi salora kut zomwe mukufuna zichitike.
@AshimayeGama
@AshimayeGama 2 ай бұрын
Chakwela ndi chilima dzawo dzinali dzimodzi chilima oyipa kwambili ndamene wawonongetsa dziko lamalawi mbudzi ikasangalala amalonda alipafu
@FazirahCoster-o4c
@FazirahCoster-o4c 2 ай бұрын
Kulapa sitimalapa kwa munthu ot nayeso akuyenera Kulapa, at, km kwa mulungu mmoz yekha bas
@fannyzimba149
@fannyzimba149 2 ай бұрын
Ndiye pope ndi mulungu ?Azionatu awa asowe ndithu mtendere mulungu awakanthe chilungamo chioneke may the souls of those who died in Chikangawa Continue to be Resting in peace 😭 😭 😭 😭 💔 💔 💔
@HarveynsonthiNsonthi-u4n
@HarveynsonthiNsonthi-u4n 2 ай бұрын
M'mesa iwowo ndi abusa akupita Kwa papa bwanji ... abvomereze pamaso pa a Malawi ambuye achitira chifundo palibenso njira ina
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 2 ай бұрын
Apule awona nyekwe pankhani ya ndege. Mizimu ya anthu 9 iwonesa Malawi nyekwe. Akumana ndi papa koma papa si Mulungu koma ndimutumiki chabe. Ndipo wasiya mupingo wake wa assembly of God chimwalilire anthu 9 aja ali busy kupita ku Roma ccap seventh day. Cholinga amupemphere kwa Mulungu koma Mulungu akukantha
@bamusilabana6423
@bamusilabana6423 Ай бұрын
Mulungu sanyengeka, mawu amatelo
@JaydragaFelisiya-hz2km
@JaydragaFelisiya-hz2km 2 ай бұрын
Munthu woi uyu😢😢😢😢
@joebrown1158
@joebrown1158 2 ай бұрын
Was Chakwera really Was a pastor of what ? Which Bible Chakwera was reading?
@ImmanuelndagomaKondowe-n1v
@ImmanuelndagomaKondowe-n1v 2 ай бұрын
Ku italy kukapempheleredwa,ku germany kukaphiphilisa umboni wa ndege koma abale,chakwera alangidwe anakali moyo
@YankhoRumwila
@YankhoRumwila 2 ай бұрын
Iwe galu wa Limpopo pita ukabibe ndi bodza lakolo and ulibe nzeru .pathako pakoso ndipo.
@ElizabethMaononga
@ElizabethMaononga 2 ай бұрын
Muonda nawo mabodza anuwotu
@zelliachamboto5744
@zelliachamboto5744 2 ай бұрын
Waonda kale Gogo wakoyo can't you feel the heat already 😂😂😂😂 blood ya munthu njoopsa munya
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 2 ай бұрын
Umakondanso kumvera LIMPOPO eti? Carry on Ccta.
@zelliachamboto5744
@zelliachamboto5744 2 ай бұрын
@@EmmanuelGasiten-fo5dr imatitsegula mmaso , 😂
@IshmaelChimtanga
@IshmaelChimtanga 2 ай бұрын
Utaonde ndi iweyo uziona ndi bale wakoyo chakwerayo
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 2 ай бұрын
Kape muziona nonse
@JimmyMkandawire-f8g
@JimmyMkandawire-f8g 2 ай бұрын
Kkkkkk koma wabisala m'mbatata nsana ukuoneka. Kkkkkk ndaseka kwambiri
@michaelmvula134
@michaelmvula134 2 ай бұрын
Waboza iwe. Chakwerayo amagona ndi iwe? Anamuuza ndani zomwe ukunenazo? Kulibe wayilesi yotchedwa Limpopo FM. Kafunse Kamlepo wa Channel Africa.
@NancyNyelenda
@NancyNyelenda 2 ай бұрын
Tanyiwa usazafe uzangosowa 😂😂😂😂😂 umandivetsa😂😂😂😂😂😂
@maxwellofficialmusicartist1881
@maxwellofficialmusicartist1881 2 ай бұрын
385 ndi Ndege zingati? Ndiye Mapemphero achita kugula?
@michaelmvula134
@michaelmvula134 2 ай бұрын
We are tired of talking about maliro amodzimodzi as if onse akumwalirawa sianthu. We get no food from your cheap lies on media.
@InnocentPemba
@InnocentPemba 2 ай бұрын
Kwasala ndi kupenga basi
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 2 ай бұрын
Makendulo aja osazawaphwekesa
@christopherMacheso
@christopherMacheso 2 ай бұрын
Choipa chisata mwini
@michaelmvula134
@michaelmvula134 2 ай бұрын
Unfortunately, you don't know how God operates. God will never accept any prayer that is evil in nature. Just wait for your day of the Lord. Accusations will not qualify you for righteousness.
@JOSEPHPHIRI-ve6ls
@JOSEPHPHIRI-ve6ls 2 ай бұрын
Kwinako ndikufuna ma followers chabe
@juliochiwalo
@juliochiwalo 2 ай бұрын
Anthu onse atengedwawo kuononga ndalama zaboma basi akulephera kuwapasa ndalama zao amalawi omwe anapuma ntchito zaka zitatu zapitazo what a shame to chakwera and his mcp govt
@ubs7030
@ubs7030 2 ай бұрын
Iwe ndi Limpopo wakoyo ndiwe opusa, wava, ukulankhula zopusa.
@RhodaBandah-sh1ir
@RhodaBandah-sh1ir 2 ай бұрын
Wina uyo ambuye chitaninayeni
@ShearstonNyirenda
@ShearstonNyirenda 2 ай бұрын
Vitsilu ntanyiwa umboni wonama
@TamiaChimpeni
@TamiaChimpeni 2 ай бұрын
Only God knows this word is full of evils atichitile chifundo mulungu
@PhalesNotta
@PhalesNotta 2 ай бұрын
Chikangawa samakalapa koma kukasayinira usataniki koma mulungu wathu ndi wabwino ndipo atimenyera nkhondo ndipo chakwela akanthidwa ndithu
@LexaKamanga-y6d
@LexaKamanga-y6d 2 ай бұрын
Muyamba kulangidwa musanamwalire
@ubs7030
@ubs7030 2 ай бұрын
Iwe mtanyiwa, ndiwe chitsilu, ukumanyoza president osalakwa, macadet sangaloweso mboma.
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 ай бұрын
Oyenda ndi lupanga lupanga lomwelo lidzamupha yekha Mulungu kanthani wonse womwe anatenga po mbali pa za imfa ya Chilima ndi anthu wonse mizimu yosalakwa zombvetsa chisoni ndithu SKC ngati anangochoka kuti abweranso
@ubs7030
@ubs7030 2 ай бұрын
Nthawi ya DPP, munkanyoza mcp, pano muli ku opposition, mukunyoza mcp, mmayiwopa.
@EthelOsman
@EthelOsman 2 ай бұрын
Kuti tidziwe chilima wamwalila tinadziwila radio imeneyi koma anthu inu kutukwana makudziwadi koma mulungu akukhulukileni
@ubs7030
@ubs7030 2 ай бұрын
Kodi a DPP mwaiwala kale zomwe anthu amakumachilani komaso anthu anakuchotsan mmboma, I hope you are worse now than before.
@MeniyaMikaya
@MeniyaMikaya 2 ай бұрын
Kd mukamati chilima analowetsa mboma mumatanthauzanji kd Ali ndi aphungu angati? Aaaa ambilinu ndinuso fiti zamubongo zopanda ntchito aaa kumangotsimikiza ndizopusa zomwe ?
@PatrickChagaka
@PatrickChagaka 2 ай бұрын
Chakwera pantumbopake chitsiru chongopha anthu ameneyi amandinyansa kwambiri ndikamaona nkhope yake
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 2 ай бұрын
Kodi akusowa ntendele ndi chani zinthu zoti amachita kungwilizana Kuti amphe chilima asatenge boma sakufuna mupitaso Ku opposition ,, chilima amamuopa Kuti ndiochenjela mayankhulidwe Ake antha kulamulila dzikoli ndiye mulusowa ntendele ndichani zochita kupangana inu anyamata A M CP ,,, yomweyo chikangawa munya simunati ,,,,
@MrBanda-w6o
@MrBanda-w6o 2 ай бұрын
Big up urself ❤
@jixonromeo4111
@jixonromeo4111 2 ай бұрын
Kuchokela ku Blantyre 😂
@GregoryMatambo-m6y
@GregoryMatambo-m6y 2 ай бұрын
Kkkkkk koma muli ndi bodza lamkukhuniza kkkkkk
@FWhite-w3l
@FWhite-w3l 2 ай бұрын
Inu osati apita kukalapa anthuwa onse ndi asatanic including papayo
@JimmyMkandawire-f8g
@JimmyMkandawire-f8g 2 ай бұрын
Alangidwe ameneyi palibe kumubakira and tikusintha boma afune asafune
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj 2 ай бұрын
Mtanyiwwa ulemu wanuw osawopha bwanji malipot andege ankushedwaso after meeting yyaitarry ndi phamene abwellese bakili muluzi TV mtanyiwwa Walipopo fm redio ankalindo bwanj dsinkutenka bwanji mullipo km online ausen amalawi sonkusana ndege ashankwela agwidwa ndi nkango nkushikangawaw 😅😂😅😂
@SellinaManda-z8h
@SellinaManda-z8h 2 ай бұрын
Mulungu alipo
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 ай бұрын
Kungowononga ndalama za ziiii mzipatala mulibe mankhwala shame
@samuelsaizi2463
@samuelsaizi2463 2 ай бұрын
I don't believe that 384 apple are among the president of Malawi trip.
@AnthonyChirwa-t4g
@AnthonyChirwa-t4g 2 ай бұрын
sopano ine ndilindifuso ngakhale lilibe yakho code chakwela kuzela mmufunde woti MR chikangawa samaziwa kut ife mabwanaake timuvutika munomalawi ndipo iyeyo akupangila mwano ife mabwana ake musiyeni orembedwa ntchito amachosedwa ndiwana wake ife ndiye mwabwana tinamuvotela Garu ameneyo
@MandevuJulius-r1k
@MandevuJulius-r1k 23 күн бұрын
Eya
@LiamTennessee
@LiamTennessee 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 iwe lazalo chikangawa sunati uwona nyekhwe,papa si Mulungu 😂😂😂😂😂😂😂😂 nanga mpaka kukagula ma pemphero olo utati uzigona Bed imodzi ndi papayo komabe mizimu ya anthu udapha aja izibwera kukukwapula makofi pa bed pompo😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂,iwe unkawona ngati ukupha nkhuku,kapena abakha,mwina nkhunda,iwe sudzapeza mtendele moyo wako onse kufikira udzalape on publick komanso ku ma banja onse a anthu udapha aja,then you will be ok, kodi mesa mneneli wina adakuuza kuti ukapangisa mapemphero adziko lonse la malawi basi you are free😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 lazalo lazalo lazalo udaziyambilanji idzi, papa has no power to forgivee sins only Jesus can
@RobertEsinat
@RobertEsinat 2 ай бұрын
Mpaka anthu 3hunz
@RahimLuemba
@RahimLuemba 2 ай бұрын
Asabwererens namkumwa malemia stkumfna , nkholokolo yachabe chabe
@marthaP-o2o
@marthaP-o2o 2 ай бұрын
Ntchimo limadzudza
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 2 ай бұрын
Apite Ku assembly chakwela akupita vacatin chifukwa chani kkkkkkkk
@CharityMhone-uk9ym
@CharityMhone-uk9ym 2 ай бұрын
Ku Vatican ndkumene kuli satana wamkulu Tate wake,sanapitilre mapemphero koma kukapereka magazi anthu kwa papa
@WILFREDBANDA-o3r
@WILFREDBANDA-o3r 2 ай бұрын
DPP propaganda, simupindula, simuwinaso. Chakwera m'paka 2030, God chosen servant.
@AnnahMpamati
@AnnahMpamati 2 ай бұрын
Ndipo iwee usazayambireso mawu awa kuyakhula otherwise tithana Nanu, usamawone ngati mene mwamphera chilima ndife okondwa, stop talking no sense Mcp mpaka 2030 Malawi ndiwa ambuye ako asaa
@KamkhatePrimaryschool
@KamkhatePrimaryschool 2 ай бұрын
Ukavotera wekha dpp
Fortune Mwikali’s Wedding. Landing in a helicopter.. See full video
10:40
Stephen Kasolo Official
Рет қаралды 2,1 МЛН
Try Not To Laugh 😅 the Best of BoxtoxTv 👌
00:18
boxtoxtv
Рет қаралды 7 МЛН
ПРЯМОЙ ЭФИР. Золотой мяч France Football 2024
4:41:06
ROSÉ & Bruno Mars - APT. (Official Music Video)
02:54
ROSÉ
Рет қаралды 261 МЛН
KUSEMPHANITSA KWA ZIZIMBA, ZOMWE ZINAPHETSA SAULOS CHILIMA 🤯😭
35:46
MUSEVENI BEYALI AYIMIRIDDE NABO NGA ALAYIRA MU 1986
6:53
Lubega Ibrahim Kasinga
Рет қаралды 15 М.