History is the best teacher,kwa amene muri mburi pa tsogolo la dziko ndiomwe mukuwononga dziko. Afiti
@PempheroMoleniАй бұрын
Best teacher bwino 😂😂😂😂
@louisgolden2 ай бұрын
Is true bushiri akutha anthu Ku Malawi Kuno ndipo wokonda iyeyu ndi mfitiso
@DeenesNurudMeke2 ай бұрын
Eti esh
@mathewsmbaluko85222 ай бұрын
Koma😢
@patriciacraiton-sf5vu2 ай бұрын
Exactly eshiii 😢😢😢
@CatherineDesire2 ай бұрын
Kwabasi
@Musa1828-l5d2 ай бұрын
Kwabasi and ndimadabwa kuti anthu aku Malawi sanadzegukebe mmaso why, bushiri ndi wa satanic ndiopa heavy, Chakwera, Joyce Banda ndi asatana awa, anthu amati Bushiri alindi ndalama koma sungaloze church yoti anamanga ayi
@DauglasBowa2 ай бұрын
I remember Grace chinga zimene Anafotkoza asanamwalire
@ChikuMega2 ай бұрын
Ndpo nkhan imneyi yandikumbusa muthalika akumukana kt bushir azagawe chimanga ndpo boma la dpp linkaziwa kt bushir ndi wa magaz eish 😢😢
@cathylomoni7812 ай бұрын
Yaap
@viennasamuel29762 ай бұрын
Eyetu Peter amamudziwa bwino Bushiri koma timkamutukwana lero tazindikika kuti anthu adyelawa amkangowona za mpando wa u president lero ndi izi
@NellieMsamala2 ай бұрын
Anakanadi
@EdwardDixies2 ай бұрын
Ana Amma 2000 mumangosatira zili zonse. Makolo ankanena Kuti MCP ndi yoipa munkachita makani. Koma dziwani Kuti makolo athu anazunzidwa ndi chipani chimenechi.
@KingDavedNkhata2 ай бұрын
@@EdwardDixies Makolo kumene amanena Kuti ma card anali okakamiza mayi oyembekedzera amatha kuchilira pa njira kukanizidwa kudutsa kamba alibe a ndalama can you emergin ufiti ndeno ndi izi
@lloydkondowe2622 ай бұрын
Ana ama 2000 musamangiwanamizira ,ndi angat anakavotera MCP 2020,, your failure to confront the current problems its not as a result of a certain group that you see so fragile to attack,,kakonzenitu inuyo ama 80s n 90s pomwe analakwisa ama 2000po
@LeonardFolokiya2 ай бұрын
It's only believers who understand the current situation.The end is near musawasokoneze anthu kaganizidwe ayi
@francisntonya1712 ай бұрын
Grace Chinga . May your soul continue resting in peace. U said it, but people ignore that, and Joyce Banda and Bushiri indeed are included as you said earlier,,.. Where do Malawi going to,, we need to Pray hard against this satanism political party,,. Kulibe kanthu konse komwe yehova adzabisire Ana ake
@AgnesLeonard-e2j2 ай бұрын
Amalawi ndizimenezotu azabweza magazi
@MrThomas-j9d2 ай бұрын
All Allah make Easy this difficult things for us we can't do nothing it's only your Power chosani zoyipa zonse
Basi mungotenga magazi a chakwerayooo ,,,kusiyana mkutenga magazi aanthu osalakwa,,
@OliveiraEduardo-p6x2 ай бұрын
Koma ndiye zoopsya zomwe zikuchitika ku Malawi
@Giftjohn-q4s2 ай бұрын
Ndinkhope zingati pacithuzipa zikuonesa kuti ndi nfiti, iam waiting for the list 😮
@KingDavedNkhata2 ай бұрын
Ndipo olo ena akamati bola dzikoli akadalamulira ngt president Bushiri ine ndimangotseka a Malawi kutengeka ndikusamudziwa zintchito zake Pali mau amati: Kusadziwanso ndi kufa komwe. Osadabwa munthu opanda chisoni chifundo eeeeh kungoti zoopsa km
@JoyceBanda-k8t2 ай бұрын
Zoona
@LysonMshan-kf7rg2 ай бұрын
shalom shalom Malawi ndili ku USA inee 🙌
@EdwinThawani2 ай бұрын
I remember he said that "I will shed blood " "Ndikhetsa mwazi" 😭😭 Komabe Mulungu Wathu Ali maso
@FelistusTaulo2 ай бұрын
Kkkkk kumbukirani Grace chinga mai ake
@HawaMamo-q2v2 ай бұрын
🤞🤞
@MartinMateyu2 ай бұрын
Tiphedwa bas
@HalisonSolomon2 ай бұрын
INU AMENE MUKUTSUTSA NKHANIYI MITUYANU SIMAGWIRAYI , MUKUONA NGATI UYUYU ANGANGOZUKA NKUMAKAMBA IZIZI? DZIWANI KUTI PALIBE CHOMWE CHINGABISALE PANSI PATHAMBO ILI KUTI SICHIDZAULULIKAYI MULUNGU AMADZERA MWA ANTHU KUTI CHINSINSI CHIDZIWIKA NKHANIYI NDI YOONA MUKANE MUSAKANE WAYANKHULAZI NDI ZOONA VUTO A MALAWI SIMUCHEDWA KUIWALA KUTI MUKHULUPIRIRE MUKUMBUKIRE ULOSI WA MALEMU GRACE CHINGA MZIMU WAKE UUSE MUMTENDERE , MALAWI ATHA UYU TIKUPEMPHA BUSHIRI KATENGENI CHAKWERA NDI BANJA LAKE KOMANSO ABALE AKE CHIFUKWA KUMENE MUNKAPANGANA A MALAWI AKUFAO KUNALIBE MALAWI NDI OKOMA 😅😅😅😅😅
Ambuye mulungu bwerani mudzakanthe ana a njaka Abuka nmalawi wiwa iyhoooo malawi wanga
@YoungsonmSimkondaАй бұрын
Peter anatiphera Ana athu ku mzuzu mumaona ngat tkumaywara ife
@AbdulraheemWilliam-lv9ms2 ай бұрын
Subuhanallah
@licksopmachila67482 ай бұрын
respect the MAN OF GOD bushiri. i know a prophet is not respected by his own city or family but remember he brought millions to Christ and saved thousands of souls. if he is a Satanist then what are you? Satanism is done in secrecy so what were you doing to notice his satanism? on behalf of millions of his followers, we are not moved not even a single inche.
@finessechikaphonya24452 ай бұрын
Koma yaa
@LouisBanda-mz2gy2 ай бұрын
Amalawi tilindivuto munthu akankhala ndi ndalama mukuti ndi wasataniki koma bushiri akuyesesa kumbali yake
@BettyByson-t4z2 ай бұрын
Ause,mumtendere grace onalosera zaziko lanthu,
@OwenMajoni-qv3eg2 ай бұрын
Aaaaa pezani zochita abwana
@EnerstBanda-m4s2 ай бұрын
Kulakwa osamusokonezera mbiri mfana Bushiri chitsiru cha munthu ichi its true Anthu sitikufunadi mcp koma osamanamiza Anthu osaona patali Mbuzi ya munthu ikulakhulai
@MysonJussah2 ай бұрын
Palibe cisisi pansi panthambo, Mulungu sadzasitha adzakhala iyeyo paka kale
@AlexKaunda-ny2eg2 ай бұрын
Dzauchisilu mukupha anthu osalakwa 😢😢😢
@KarenBreggerАй бұрын
Koma zikufika Malawi gozi ndi deile 😮😮😮
@MariaAndrea-f9v2 ай бұрын
Mmmmm uphawitu ukukupangitsani zosezi bushili chikumukhudza ndichiyani pa zandale zanuzi
Komatu mukuchedwa ndikulankhula bola mukasake ndalama mugule chakudya mudyese family yanu
@AlexGowelo2 ай бұрын
Nkhomdo iyi sitilimbana ndi kuthupi koma ma ulamuliro adziko lino ndi mphamvu za kumidima Kubwela kwa bushiri zinthu zidaipa choncho tiyeni tipemphele molimba
Rest in peace Grace chinga, ur always in our heart
@finessechikaphonya24452 ай бұрын
Nkhani yoopsa iiih koma😢
@AminaPhiri-pp9tw2 ай бұрын
Zaugalu mukapangana kuti mupeleke mangadzi ndiye chifukwa kumalawi kuli mavuto ambili zingodzi tikuziwonazi musokhane nose mupeleke ana anu nosenu mbiri yabushiri mukuyiziwa mukusithanisa ndi magazi anthu moto wamulungu ukufikileni nonsenu nema of jesus fair
@ChristianMtambalika2 ай бұрын
Ndikumbuka yesu anati ndalama iyi ndiyandani yakayesara paseni mwini wake zamumulungu ndiye zanthu amalawi lero kayesara akufuna zake😂😂😂😂