KOMATU KU UTM KULI KULANKHULA MWA NYOO - FREDOKISS NDI NJAWALA KUNG'ALULA BOMA NGATI MAWA KULIBE MMH

  Рет қаралды 28,772

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

KOMATU KU UTM KULI KULANKHULA MWA NYOO - FREDOKISS NDI NJAWALA KUNG'ALULA BOMA NGATI MAWA KULIBE MMH
Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
#MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

Пікірлер: 94
@JamayakoJamayako-rv2he
@JamayakoJamayako-rv2he 16 сағат бұрын
Bwana zooona zimenezo We need to change our mind set Big up MK
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 22 сағат бұрын
Nanga ntengo ugwetsa bwanji Ndege ? Koma ntengowo wosagwa
@AmosPhilemon-y5e
@AmosPhilemon-y5e 21 сағат бұрын
Za mphavu chakwera wakupha
@OwenZimba-b4s
@OwenZimba-b4s Минут бұрын
Ndipo mulungu atithandize chikangawa asazaineso pobela zisankho 😢😢😢😢😢
@Esa-u3t
@Esa-u3t 12 сағат бұрын
Big up UTM POWERFUL 💪💪💪💪🎉🎉🎉🎉
@beatricenkhoma1109
@beatricenkhoma1109 23 сағат бұрын
❤❤❤
@GeoffreyBokosi
@GeoffreyBokosi 18 сағат бұрын
MCP MY VOTE
@StantchuAlex-s9x
@StantchuAlex-s9x 21 сағат бұрын
"Pa nkhani ya upulezidenti tidzabwelanso kudzakuuzani kuti mtsogoleri wathu ndi uyu". Ena amvekele " Peter!!!!!" 😂😂😂😂😂😂
@LovemoreChimatilo
@LovemoreChimatilo 11 сағат бұрын
Peter Yu Ku khwima 😅😅😅😅😅
@LangfordMabaso-z7u
@LangfordMabaso-z7u 15 сағат бұрын
Big up ❤❤
@StewartKalipinde-g2j
@StewartKalipinde-g2j 21 сағат бұрын
True
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 22 сағат бұрын
Ndipo fredo sakunama mcp inapha chirima Nanga black box akuyibisa chifukwa chani
@eliusdokowe4026
@eliusdokowe4026 19 сағат бұрын
🎉🎉🎉🎉Fredokiss ndi dolo kangapo
@josephymunthali
@josephymunthali 13 сағат бұрын
Ma Bodza okha okha awa, UTM.. Mulibe Mgwilizano, ngati ikugawikana panopa? Kweni Kweni atatenga Boma.
@MACDONADLITIA
@MACDONADLITIA 17 сағат бұрын
Koma Malawi wakhweka ndithu
@InnocentKissinger-jn5mn
@InnocentKissinger-jn5mn 13 сағат бұрын
Fredo✊
@SpencerKadewere-cd5ok
@SpencerKadewere-cd5ok 16 сағат бұрын
Sakunama chilungamo nchakut Chakwera adapha Chilima ndi Asilikali ena ozimva ukulu
@DaudiLashid
@DaudiLashid 20 сағат бұрын
100 percent good point
@khasimMusa-d3w
@khasimMusa-d3w 22 сағат бұрын
Umakwana Fred ❤
@ArronBenson-g6d
@ArronBenson-g6d 17 сағат бұрын
Chikangawa party ikagwere uko
@AyasiWhite-l6s
@AyasiWhite-l6s 16 сағат бұрын
Zoonadi bvuto achikangawa party km umfiti
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 19 сағат бұрын
Mcp ichoke Ambuye mtengeni 😂😂😅
@MuhammadSamson-yz1kl
@MuhammadSamson-yz1kl 16 сағат бұрын
Chi fredo chili ndi mbalume
@BiasElliot
@BiasElliot Күн бұрын
Ndi choncho kumene
@johnbullyohanittokasikizim7127
@johnbullyohanittokasikizim7127 8 сағат бұрын
Njawala ndi munthu wachitukuko
@GeoffreyPhiri-qy5gq
@GeoffreyPhiri-qy5gq 15 сағат бұрын
Fire 🎉🎉🎉
@AwetuAmidu-u2j
@AwetuAmidu-u2j 17 сағат бұрын
💪🏿💪🏿💪🏿💪🏿💪🏿💪🏿
@MkwandaFaiz
@MkwandaFaiz 16 сағат бұрын
Zowonadi
@OssmanAbubaker-m5u
@OssmanAbubaker-m5u 4 сағат бұрын
Zoonadi boma la MCP linapha chilima ndipo zomwe akunena makosanawa ndizoonadi
@VinciusmajiduMchepaanaffi
@VinciusmajiduMchepaanaffi 11 сағат бұрын
Umboni mesa ndchikangawa
@LinlyMatheweKufakwina
@LinlyMatheweKufakwina 19 сағат бұрын
Nde iweyo ukuona ngati uzavotere chakwera kuona ngati ndi tonse mwana wa njoka iwe kgwere ndi chikangawa wakoyo
@chrismkupatira8321
@chrismkupatira8321 9 сағат бұрын
Azimayi angooneka onyasidwa 😂😂
@JimmyDyton
@JimmyDyton 14 сағат бұрын
Ndizoona fredo
@RevHenryNkosi
@RevHenryNkosi 18 сағат бұрын
Inu a utm munawina panokha?
@stephanonkungula5858
@stephanonkungula5858 13 сағат бұрын
Mcp ndimakape onse
@benardnkhalamo3921
@benardnkhalamo3921 15 сағат бұрын
Ife ndinganga pambuyo pa LC
@MemoryGiftKumfela
@MemoryGiftKumfela 13 сағат бұрын
Ndizoona zimenezi
@FrankKandikole-z9v
@FrankKandikole-z9v 4 сағат бұрын
Aaaaaa wabodza iwe or utakamba bwanji boma ndi mcp. Ukufuna utichedwetse pa zitukuko mmalo moti tizipita pa sogolo. Boma ndi lomweli
@FreddieNkhoma
@FreddieNkhoma 21 сағат бұрын
Ndizooona
@BernadettaPhulusa
@BernadettaPhulusa 23 сағат бұрын
Sakunama chweeee
@josephymunthali
@josephymunthali 13 сағат бұрын
Miseu yoseyi ayiwona lero
@MuhammadAlie-u5n
@MuhammadAlie-u5n 17 сағат бұрын
😢osaopa osadooka. Chakwela out
@JamayakoJamayako-rv2he
@JamayakoJamayako-rv2he 16 сағат бұрын
2000 yaononga Koma K 2000 on that time inali mwala ku golosale
@SamuelKhumbiwa
@SamuelKhumbiwa 18 сағат бұрын
Mcp ndani sakuyiziwa za mbiri yawo ,ng'ona singakhale mbuzi.ndiwonesese chidsnthetsa nkhuku pamuz.
@samuelmoloko3939
@samuelmoloko3939 17 сағат бұрын
Umboni woyamba ndiwomwe udayankhulidwa ndi member wa UDF
@JamesDzonzi-t7u
@JamesDzonzi-t7u 12 сағат бұрын
Maloto a gocho
@jacquelynemambala1931
@jacquelynemambala1931 Күн бұрын
Koma fredokis taziyankhulako mwamphanvu mmene umayankhulira ngati zonse ukunamatu apa 😂😂😂😂😂😂
@user-ii9ch7oz8n
@user-ii9ch7oz8n 12 сағат бұрын
Pamatakhko fredo musunu wako skc anamwalira auzeni anthh zomwe mkufuna kupanga osatai muzipanga zamanyi ai machendeabambo msunu
@juliussamson6212
@juliussamson6212 Күн бұрын
YES ZONSE IMAKAMBA UTM AMAKAMBA ZOWONA
@EdwardRichman-zs5pl
@EdwardRichman-zs5pl 22 сағат бұрын
Kuyambila litilo ana osapola panchombo
@JamayakoJamayako-rv2he
@JamayakoJamayako-rv2he 16 сағат бұрын
Chikangawa government
@JoneeYolamu-d9g
@JoneeYolamu-d9g 17 сағат бұрын
Adzidzimuka mochedwa a UTM
@lyiemax
@lyiemax 20 сағат бұрын
Fredokis ndi akatundu❤❤❤
@RevHenryNkosi
@RevHenryNkosi 18 сағат бұрын
Ukatundu wake ukuchokera pati? Za ziiiii 😅😅
@RevHenryNkosi
@RevHenryNkosi 18 сағат бұрын
Ukatundu wake ukuchokera pati? Za ziiiii 😅😅
@MosesTangwe
@MosesTangwe 23 сағат бұрын
Nawenso nzimai iwe ukamati Kaya alindi umboni wanji what do you mean? Akukanika kufotokoza za crash yandege ija akuopa chani ndie umboni upose pamenepo
@BressingsMahele
@BressingsMahele 23 сағат бұрын
Zamphamvu
@DavidKanyemba-n2s
@DavidKanyemba-n2s 19 сағат бұрын
Tchweee mwana tchweee😂
@BiasElliot
@BiasElliot Күн бұрын
Eya kumeneko
@IsmaelBilal-lh1pi
@IsmaelBilal-lh1pi 19 сағат бұрын
Kopanda kulandira ma 2000
@MonicatimanyeShaba
@MonicatimanyeShaba 21 сағат бұрын
Zoona bige zachikangawa zikuti vutisa kwambili
@HildaMbizi
@HildaMbizi Күн бұрын
Ivi vaunenesko vamugwirizano wa MCP wakavileka nakuona Waka kuti mpando wanowa nakuyanayana nthowa zaumo wangamuuskilapo chilima basi kumalana Naye basi
@Malume2024
@Malume2024 23 сағат бұрын
Ndi zoona sakunama
@JamesMwale-o6i
@JamesMwale-o6i 23 сағат бұрын
Zoona paja chakwera sakumva
@CyrusBanda-p4x
@CyrusBanda-p4x 23 сағат бұрын
Zabodza
@StainDandize
@StainDandize 22 сағат бұрын
🎉
@npc4707
@npc4707 19 сағат бұрын
Iwe fundo ulbe wayesa ngat ukukpangitsa show ap
@Howard-c1q
@Howard-c1q 18 сағат бұрын
Anainu osamayankhula maboza pamisonkhano yanu amalawi ,vot for mcp basi
@KingsMtiyesanji
@KingsMtiyesanji 17 сағат бұрын
Munapepetulidwa ndi DPP simukudziwa komwe mukulowela mudzazindikila kutsogoloku
@AngelineDumha-ec5le
@AngelineDumha-ec5le 22 сағат бұрын
Musayambeso kunamiza anthu za kudya katatu you will make alliance with DPP how sure are you kut Your manifesto will be followed now
@elvisnjoka8428
@elvisnjoka8428 21 сағат бұрын
Ndipo nde asatinyaseponso ife....
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 20 сағат бұрын
my vote MCP ❤ 🙏 🗳
@robsontyg3928
@robsontyg3928 22 сағат бұрын
Ana osapola panchombo, mboli zanu
@Annie-ls7po
@Annie-ls7po 21 сағат бұрын
Abambo abwino wino inu kutukwana
@robsontyg3928
@robsontyg3928 20 сағат бұрын
@@Annie-ls7po dzipatse ulemu ndiye mzimai ndikuyalutsa
@NoelKhwimba-bh3ts
@NoelKhwimba-bh3ts 15 сағат бұрын
Chitsiru iweyo mbolo ya mayi ako
@noelliwonde8661
@noelliwonde8661 15 сағат бұрын
Mbole yako nawe, patumbo pako tamuonene
@NoelKhwimba-bh3ts
@NoelKhwimba-bh3ts 15 сағат бұрын
@@noelliwonde8661 awaone ambuyako
@EdwardRichman-zs5pl
@EdwardRichman-zs5pl 22 сағат бұрын
Mwangopenga ku UTM kuli be akugawa ndalama km MCP anthu akuyikonda kwambiri osati monga momwe mukuganizila ndale zopusa zimenezo fundo mulibe mukanali ana simunadziwe ndale iyiii si music ayiii phuzilani Kaye ndale
@raphaelsamala3792
@raphaelsamala3792 22 сағат бұрын
Maganizo anu onse mwaganiza kuti mutsutsane ndizonse zakambidwazo??
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 22 сағат бұрын
Ikamakondedwa ndi banja lanu sizikutathauza kt Malawi yonse ikukonda musamazinamize
@SamboRuphan
@SamboRuphan 21 сағат бұрын
Mwapenga ndinu madala 😂😂😂anthu momwe akufela,,,MCP ikuchoka mu boma
@raphaelsamala3792
@raphaelsamala3792 21 сағат бұрын
@@SamboRuphan mutu wake sukugwila ntchito akuona ngati amalawi akukondwa ndizomwe chakwera akupanga
@PhillspicJere
@PhillspicJere 19 сағат бұрын
Penjani kaluwa ndale zake same same ndi abambo ake zopanda mfundo basi
@MosesMphande-r2g
@MosesMphande-r2g 15 сағат бұрын
❤❤❤❤
@npc4707
@npc4707 19 сағат бұрын
MCP my vote
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 19 сағат бұрын
That is the beauty of democracy. As a Citizen it is your right to vote for MCP just as much as others love other Parties.
@MkwandaFaiz
@MkwandaFaiz 16 сағат бұрын
Machende ako ndi chakwera wanuyo
@SimbeyeSimbeye-z7l
@SimbeyeSimbeye-z7l 16 сағат бұрын
Misala eti
@MercymithiMithi
@MercymithiMithi 22 сағат бұрын
❤❤❤❤❤
🍉😋 #shorts
00:24
Денис Кукояка
Рет қаралды 3,9 МЛН
Synyptas 4 | Жігіттер сынып қалды| 3 Bolim
19:27
JUDICIARY OPEN DAY 2024 LIVE CHE MANDOTA PERFORMANCE
14:19
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 60 М.
MUIMBI HOSIAH CHIPANGA MUDARE RAMAMBO MUTASA VS LEON MATESVA  KARANGANDA TV KUTORWA KWEMUNDA
18:01