Zosatila Za Skeffa chimoto pamene wayamba ndale

  Рет қаралды 39,896

Sam Malvitha

Sam Malvitha

Күн бұрын

Пікірлер: 56
@andrewchirwa2193
@andrewchirwa2193 Жыл бұрын
Ndale sizoyipa ngakhale nyimbo za skeffa chimoto siwose amazikonda ngakhale ma musician ndi ndale sizikusiyana kwenikweni love you all musicians
@hanafi4766
@hanafi4766 Жыл бұрын
Tisamuweruze tidikile Kaye tizamuzudzule akazayamba kuyimba za ndale komanso zoti munthu amatha osatchukanso akayamba ndale nzabodza Lushasi banda sanathe bwanji biry kaunda sanathe bwanji funso nali Nsako mlaka chibade and many more anatha chifukwa cha ndale? Munthu kungolowa ndale amaremera Moti enanu yakula ndi nsanje
@christopherchikowi4864
@christopherchikowi4864 Жыл бұрын
Ankolo muli nkukokomeza zinthu. He has every right to join politics. He was not ready/willing to join politics then, he is ready/willing to do that now, there is nothing wrong.
@mgulaheritage105
@mgulaheritage105 Жыл бұрын
Ameneyu kuno ku nkhotakota tikumufuna zediiiiii ndipo ndi wowinawina kale
@sammalvitha
@sammalvitha Жыл бұрын
Zosangalasa kwambili
@geraldomaida8750
@geraldomaida8750 Жыл бұрын
Chiyambi chogwetsa mbiri yawo ya umunthu ndi kuyamba kwalakwina anthu amene anali abwenzi awo pa nyimbo, kapena kuti ma customers awo
@lithembajujwana5577
@lithembajujwana5577 Жыл бұрын
Musiyeni alowe ndale ali ndi ufulu opanga zomwe akufuna,akufuna kuthandiza dela la kwawo ku nkhotakota akukhuxidwa ndi mmene kulili,aaaa mind your own business guys,azipanga zonse 💪🏽 muzadabwaso
@petertambala2569
@petertambala2569 Жыл бұрын
Aliyense ndiwandale adah n skeffa apitiliza kutipasa nyimbo Zabwino
@sammalvitha
@sammalvitha Жыл бұрын
Kumbukirani kuchita subscribe 💗 Like 👍 Comment ❤️😍
@mervingaxyofficial
@mervingaxyofficial Жыл бұрын
Nyimbo ya ndale anayimba ndi Azizi but beat is produced by seven o more
@sammalvitha
@sammalvitha Жыл бұрын
You are right
@mikebanda7339
@mikebanda7339 Жыл бұрын
Pangani zanu musali mbane naye Skeffa muchedwa nazo, kaya apanga zandale kaya azingoimba nyimbo ndi chisankho cha mtima wake monga inuso mungakondere kusamkha chinthu chokusangalatsani pa moyo wanu, musataye nthawi yanu kupanga za anthu ena koma limbakirani kupanga zinthu zothandiza moyo wanu komaso banja lanu. what Skeffa is doing is a betterment for him and his family basi. muchedwa nazo izi abwana.
@maxwellchimera8078
@maxwellchimera8078 Жыл бұрын
Nde muti ife titani osamuza direct nokha bwanji ife sitidya nimbombotu kapena ndale timapanga zathu Nanu pangani zanu basi wapulika?!!!!
@JosephyMajamanda-ov3xd
@JosephyMajamanda-ov3xd Жыл бұрын
Ndichisankho chake akudziwa chomwe akuchita mwini wake Aliyese amakoza yekha tsogolo lake Anthu mumangodziwa kuyañkhula koma kuti mumuthandizi munthu akayamba kuvutika ai Kudali chibade akaimba zokomera amalawi koma pano akuvutika bwanji simukuthandiza Sionse aise omwe anayamba ndale ndikuvutika Muoneni billy kaunda akusangalara pano Mkasa akangoumba za ndale not kulowamo mu ndalemo
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 18 күн бұрын
Chisakho Chawo aleken😂
@peterandre8262
@peterandre8262 Жыл бұрын
Kulowa ndale kuli ngati kulowa ufiti
@trysonchimenya8795
@trysonchimenya8795 Жыл бұрын
Basi mlekeni decisions on what to do in life imatha kusintha We are human beings who always run for green pastures
@amabhohlela.3492
@amabhohlela.3492 Жыл бұрын
Kuthabasi Skeffa....aziona mulekeni..
@magretkalimba-ov6kn
@magretkalimba-ov6kn Жыл бұрын
jearous lilipalipose pangani zanu
@pinkiemanuel6005
@pinkiemanuel6005 Жыл бұрын
Iiiiii 2023 iyi people can change
@miriammhango6393
@miriammhango6393 Жыл бұрын
Utsogoleli umafunika kulimba mtima
@maxgulani1391
@maxgulani1391 Жыл бұрын
Ndiyenso bola akadasankha chipani china koma osati Mcp ayi
@lukainnocent5380
@lukainnocent5380 Жыл бұрын
Wasankha bwino ndi straight win
@Thembokatuli
@Thembokatuli 27 күн бұрын
Bola awine koma akaluza zose zimada
@HAWAHANDRWE
@HAWAHANDRWE Жыл бұрын
Chilungamo anthu chimavuta zikomo kwambili tadziwa nawo
@Thembokatuli
@Thembokatuli 27 күн бұрын
Kundale kuli ndalama pitani muli paziko kufunafuna chuma simukulakwitsa bola muzawine ndithu
@blessingsgowelo142
@blessingsgowelo142 Жыл бұрын
Go well bye bye in music industry nkothela kumeneko
@evancekandodo-mw8kq
@evancekandodo-mw8kq Жыл бұрын
Y sana the billy kaunda . Y sanathe lucias banda mmmm ndale sikothela
@user-hn8sr9oc7k
@user-hn8sr9oc7k 4 ай бұрын
A skeffa sankhani chipani china osati mcp ayi
@eversonsalani280
@eversonsalani280 Жыл бұрын
Aziona musiyeni
@maxgulani1391
@maxgulani1391 Жыл бұрын
Anthu andale sapanganika amufuse Mkasa
@wysonmatiki2076
@wysonmatiki2076 Жыл бұрын
Sadalakwitse ndipo akukwanila musamujaje.
@fraserbereck2269
@fraserbereck2269 Жыл бұрын
Waona kt watha kale that's why akupita ku ndaleko
@sammalvitha
@sammalvitha Жыл бұрын
😂😂
@chifundonkhoma3642
@chifundonkhoma3642 Жыл бұрын
Eya Kaya sakuona chachilendo chimene angaimbeso..... Let him extend his time to politics, sakulakwitsa carier iri yonse when retire amapita ku ndale.....
@paulkaunda6780
@paulkaunda6780 Жыл бұрын
Ndi opusa uyo
@blessingsmasakala3285
@blessingsmasakala3285 Жыл бұрын
Ndipo iyeyu anthu ambl amutuluka alindimbali
@christopherchimenya7259
@christopherchimenya7259 Жыл бұрын
tamuyeni wafuna yekha
@danielmaenda
@danielmaenda Жыл бұрын
Ngati atayamba ndale akupita ku mapeto kwa luso lake
@chifundonkhoma3642
@chifundonkhoma3642 Жыл бұрын
Even most civil servants when they retire they join politics..... Let him retire from music in peace 😂😂😂😂
@pinkiemanuel6005
@pinkiemanuel6005 Жыл бұрын
Koma ndaseka iiiii
@evancekandodo-mw8kq
@evancekandodo-mw8kq Жыл бұрын
Vuto ndilot anthu tili ndi bad attitude ku ndale. And like example ya eli njuch being bb ambersader sizikusiyana nd kukhala sapta wa chipan coz you belong to wat you hav like. But the. Main problem is bad idea that most pple have upon polics. But polics is so good and must be loved and follows up postivly. Not as wrong as you are thinking.
@ibsonlinetv3777
@ibsonlinetv3777 Жыл бұрын
Point of correction wandale ndi nyimbo ya Azizi and not sevenomore
@sammalvitha
@sammalvitha Жыл бұрын
Thanks for correction sir, Subscribing to Chanel will be great as well . . Thanks
@hanabrighton9903
@hanabrighton9903 Жыл бұрын
No comment
@omarrashid5854
@omarrashid5854 Жыл бұрын
kapange ndalama ase zandale zimabwela mofewa
@happymguza1136
@happymguza1136 Жыл бұрын
Nthawi imeney analibetu certificate ya form 4 mpno anaiprdza
@thomastenes949
@thomastenes949 Жыл бұрын
😂😂😂mcp is going to lose
@francismbewe153
@francismbewe153 Жыл бұрын
Skeffa will fall
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Жыл бұрын
Amalawi tili ndivuto kwambiri ndichifukwa ziko lathu silingapite patsogolo. Ngati Mulungu akusakha kuti uziyimba panga chomwecho. Asiyeni andale azjpanga zandala bwanji oyimba ambiri aku Malawi akukonda kulowa ndale? Kupitaso kundale samakhalaso azeru kuyerekeza ndikale pamere sanali kupanga ndale. Tiyeni amalawi ngati woyimba akufuna kulowa ndale wosawavotera amenewo ndi anthu amozi oti sakuziwa kanthu poyendesa boma lamalawi
@happymbewesimms6951
@happymbewesimms6951 Жыл бұрын
Iwe oyamba ndale siyekhawo kamba Zina iwe
@s-onebeatsmw
@s-onebeatsmw Жыл бұрын
Moto
@sammalvitha
@sammalvitha Жыл бұрын
Thanks brother
@freddyndzukuma1357
@freddyndzukuma1357 Жыл бұрын
It's his choice. Done lu ndi oimba komanso wandale. Ndipo timamukondabe. Lucias banda nayeso chimodzi modzi. They are all Malawian beside zipani. We will love u all. May God bless malawi
@sammalvitha
@sammalvitha Жыл бұрын
Amen
Chachitisa ndi Chan Kut JB ayambe kunyoza Lulu, Komanso Tygrin?
8:56
Шок. Никокадо Авокадо похудел на 110 кг
00:44
when you have plan B 😂
00:11
Andrey Grechka
Рет қаралды 50 МЛН
Underwater Challenge 😱
00:37
Topper Guild
Рет қаралды 48 МЛН
Oyimba omwe ananyozapo bushiri part 2,
5:58
Sam Malvitha
Рет қаралды 30 М.
REPORT LA NDEGE MU CHICHEWA NDIKUYANKHA MAFUSO ATOLANKHANI
47:28
Skeffa Chimoto - Extended Perfomance (New Songs)
49:55
Venture Filmz
Рет қаралды 64 М.
Lulu wabweza mwano nayenso ndi munthu amatopa
8:50
Sam Malvitha
Рет қаралды 135 М.
Malemu John Tembo; Tidzamukumbukira bwanji ngati amalawi
22:38
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 64 М.