This is reality the first thing is leader of opposition do not allow parliament to Biggin without the leader of opposition if it is so postpone the meeting of parliament until the leader have elected the second thing, make sure the DPP party have a diolegue between them to hit the nail on there head because you're the eyes of Malawian may good God be with you and protect you during the meetings thank you
@andsenJeke7 ай бұрын
Dccccccc 🔥 nankhumwa ndi chakwera watikwana ambuye tichotseleni
@PizoZopi-w2g8 ай бұрын
Apm my vote ✊
@JosephMwenyali7 ай бұрын
Dpp,mps u need to stand strong
@oliviamphande19008 ай бұрын
The only one freedom fighter Mr bon kalindo
@ChisomoNkhata-f7i7 ай бұрын
Ndizoona aphuzitsi asavomele kumasonkha ndalama
@GiftFrancesco8 ай бұрын
❤❤❤ the DC
@Homeofpeace3218 ай бұрын
Rest in peace Kondwani Nankhumwa
@thomasmalupi66248 ай бұрын
Bon Kalindo only the last standing man in Malawi. Mwana wa kwathu ku Mulanje kwa T/A Mabuka
@OsmanMailosi8 ай бұрын
I totally agree with Bon Kalindo's advice.please DPP, do not accept Nankhumwa, to lead delegation in the house otherwise adjourn the house and get injunction.we want better Malawi
Ndizoona akunena the DC able a DPP akugonana analanditsa Boma 2019 panopa Adina arhetse chipanichi
@LonexKachepa8 ай бұрын
Zoonaditu koma ofunika akonzekere bwino zochita a dpp
@KumbukaniChimbalanga8 ай бұрын
Iwe bon kalindo usamayankhule mau ochita frustrate anthu ndi maganizo ako opusawo wamva nkhani zotembelera DPP timadana nazo kaya amachita kukutuma izo ndi zako
@mateyomarindi8 ай бұрын
Akunena zoona palibe chimene akulakwa akalindo mcp Akuma khalila Kuna miza anthu bas achoke Siti kuwa funaso feteleza panopa tikuma Gula 85000 thawi ya Peter tima Gula 22 ,500 chakwela asiye udindo
@ThomasDulla-g1n8 ай бұрын
Komano amavera DPP
@JumaAlli-vf6jp8 ай бұрын
Kalindo akunena dzoona ndithu a d.p.p. asamale ndikuchenjera komwe
@GreyMponda8 ай бұрын
Rubish people s are supporting MCP anthu adyera
@HenryManda-m9h8 ай бұрын
ADPP choyamba musanayambe zokamborana zanu munyumba ya malamulo muyambe kaye mwakhala pansi mu nyumba yanuyo ya DPP kuuzana kapena kukambirana zokachita ku parliament ko leader of opposition first budget second ndizimene anthu amene tilikumodzi kuno tizizamva chifukwa ndipamene tizawonere kiti ndinudi opposition ya mphamvu asakutoleni a mca ndi yonse allaoance yawo yo iyayi.chonde chondr chonde ndipamene tizakikhulupitilani amayi Navitcha mukawonese uzimayi wanu ndipamenepa chonde kuno ku Muzi chikhulupiliro chathu chili mwa inu a DPP
@wellingtonmtoso20748 ай бұрын
Za parliament zithela ku parliament. Za chipani zithela ku chipani.Otuminidwa amathela kwa omutuma.
Koma avunva a DPP wo? Ifetu tikuyembekeza iwowo apulumutse amalawi
@abdul-rasheedsalika7 ай бұрын
Zikt Bwanji kd pamenepo????
@muhammadjuma33178 ай бұрын
Ukhaula iwe udzakhala kunja kwa boma mpakana kale kale . President wa amphawi alipo kale ndi mkasa. Adzako adakutuluka kale chifukwa chakuti ndalama umangodya wekha
@VincentNgabuh7 ай бұрын
akulu mukulankhula palibe chipani cha MCP zikupanga iwo zikukutsangalani anthu opusa amene mukuyikira kumbuyo MCP the DC ndi omenyera ufulu ku mtunda wa amalawi osauka
@ChristopherKabanga8 ай бұрын
paja adayambira kugura lweyotu usaiware
@jomochirwa8 ай бұрын
Katundu kapena zinthu zakwela mtengo kumayiko onse makamakaso mayiko amene ali ndi chuma.chitsanzo kuno ku southafrica katundu akudula zeedi koma chikhalile katunduyo akupangidwila kuno.ku mozambique anthu wogwila ntchito za boma maka police ,asilikali pano 4 month no salaries.kukwela ntengo sikumalawi kokha ayi.koma mtsogoleli wathu akayesa kupeza njila zabwino zochepetsela mavuto komanso katangale.anthu sitingavomeleze zakudula kwa zinthu pamene atsogoleli anthu akungokhalila kuba komanso ma alawasi akulandila ,masalale awo sadadulidwe.
Ugalu opose wakowo mwana hule iwe.mwana oleledwa ndi agogo mai ako ali ku bar,chitsilu, mbuzi ya munthu ngati mkotero bwanji ukawafunse agogo akowo kut kodi dziko likuyenda bwanji,,,,,,, umve iwo mkutheka za bon kalindo siukumva ndipo ngati ndi chamba or tindalama tonyenyekato ta MCP m'phwanga tikupweteketsa ukalimbana ndi bon kalindo ulidziwano dziko ndipo choti udziwe ma bwana ako a MCP onse ndi ana kwa kalindo, iwe mantha ai ,monse adayambila kulimbana ndi boma muja akutaninae? Wamba wamba bwenzi ataphedwa kale koma uwu ndi mtunda,,,,,, dikila akayamba misonkhano tiwagenda mapwala awo!
@cjaylucky8 ай бұрын
Sugayakhe coz ndiwe mwana wangon buzi sml boy 😊
@BFWCPHIRI19788 ай бұрын
Cjay lucky,,,,,,, chitsilu cha MCP ndipo nonse munya 2025
@XasankaalibeeyNuur8 ай бұрын
Ndimwana oti anaphulika chishango patumbo pa make akanyoze the DC wachilungamo
@BFWCPHIRI19788 ай бұрын
The DC machine original than all
@PaulMvuma8 ай бұрын
This man is hopeless, and u can see from far this man is hungry now he has joined dpp