A TIMOTHY NTAMBO AYANKHIDWA MOSAWANYENGELERA-Amalawi adakwiya

  Рет қаралды 11,258

HOT 265

HOT 265

17 күн бұрын

Пікірлер: 129
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 16 күн бұрын
APM my vote, president wa ntendere koopsa ndiwachilungamo🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥♥️♥️♥️
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x 14 күн бұрын
God bless you Mr game changer
@user-is5dl7np9g
@user-is5dl7np9g 16 күн бұрын
Ndathokoza bwana game changer Timothy mtambo ndi destroyer weni weni, let's unite let's think about Apm ndi ntchito zake as we're going to 2025 elections
@SteveShaya
@SteveShaya 16 күн бұрын
Ndale tipange koma osatukwanana... let's respect each other Malawians
@zencoczimbiri2262
@zencoczimbiri2262 10 күн бұрын
RSA, please Malawian to change Malawi is not good for us to revenge , not to kill, not fight but to love our enemies and humble am telling you God is going to fight for us I love you all
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 15 күн бұрын
Ntamboyo asayelekeze kufika ku mwela,kuno ndipo.timunokola,ngati akuona,ngati,tili okondwa.ameneyi,awonetsedwa nyenkhwe.komatso,akamatuluka nyumba mwachemo'asadzike.
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 13 күн бұрын
Apa ndie mwalakhulatu may God bless you Any way we love DPP
@zencoczimbiri2262
@zencoczimbiri2262 10 күн бұрын
RSA komaso we all we know that our country is walking but is dead, as you can see for now people they are walking with empty pockets, no food in their homes, just margin long back ago people they were enjoying with prenty of food and they were enjoying cooking a big pots, but today people they are cooking a small pot because we don't know where we are going, Am the man of God , this is my massage goes to all parties of opposition God said to me to rescue Malawi u must put your heart together , put your votes together as one and be Unity and strong, allayancy is a strong weapon for u to change Malawi God bless you Malawian, beleive we are going to change Malawi soon in Jesus name Amen
@JorgeSacuate
@JorgeSacuate 16 күн бұрын
Congratulations Mr. Auzeni amalawi movetsetsa. Ife tinathawa ku Malawi chifukwa cha khaza za afiti amenewo a MCP. MALAWI tiyeni tizavote bwino povotera DPP. Peter Wa Muthalika
@MabvutoMawindo
@MabvutoMawindo 13 күн бұрын
Game changer keep on telling us
@SecretNgala
@SecretNgala 13 күн бұрын
Game changer wayankhula ngati munthu wamkulu mulungu akudalitseni auzeni a Malawi opusawa ongotengeka ndi akubawa atuluka mzipani zakubazi
@user-pf5hu2pd2b
@user-pf5hu2pd2b 16 күн бұрын
Game changer you're the greatest Man , more fire 🔥🔥 🔥🔥🔥🔥🔥.
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 16 күн бұрын
Mwana mfiti Timothy watizunzitsa amalawi iwe ife mpaka ma demo kuchotsa boma labwino😢😢😢😢 ndipo ndiwe mbizi kwambiri
@zencoczimbiri2262
@zencoczimbiri2262 10 күн бұрын
RSA thank you Mr game changer my vote dpp, please my fellow Malawian let us vote dpp
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 16 күн бұрын
Big man game changer best activest in Malawi
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 16 күн бұрын
Let's all vote for DPP zinthu zitsikiretu ndipo njala itheretu guys
@user-cy7gd1go6y
@user-cy7gd1go6y 16 күн бұрын
Game changer ndi za power 💪💪 more fire 🔥🔥 game changer
@user-wi9pe2hz7e
@user-wi9pe2hz7e 16 күн бұрын
Kuyankhula uku keep it up
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 14 күн бұрын
Ndimaganiza kut ukuyankhulila a Malawi koma mbola yeniyeni yotumidwa ndi dpp ayi ife nganga nga pa mcp mpaka2030 woooo
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 14 күн бұрын
Zamphamvu Mr Mphepo, following from Balaka
@dreyervanheerden313
@dreyervanheerden313 13 күн бұрын
Dpp moto game changer
@user-rc3ze2oi7u
@user-rc3ze2oi7u 15 күн бұрын
Mr game changer ur no one God bless you ine vote yanga ndi dpp or udf 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@user-cy7gd1go6y
@user-cy7gd1go6y 16 күн бұрын
Tambo mapwala ake ndithu my vote is going to apm❤
@georgednthala-wh3pf
@georgednthala-wh3pf 15 күн бұрын
Ife ngati anthu opemphera, Timothy Ntambo tinamukhukulukila kale kale. Ngati Inu simukhululuka awo ndi mavuto anu
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 16 күн бұрын
Powerful mesg mr game changer 💪💪💪
@user-rk3jx3kg8i
@user-rk3jx3kg8i 15 күн бұрын
APM my vote
@user-lf6qf2tw5o
@user-lf6qf2tw5o 14 күн бұрын
Garu iyi kumavutisa anthu mademo akuziwa kt apeza cholowa
@user-bi6pb5gc8t
@user-bi6pb5gc8t 15 күн бұрын
Mulandu suvunda uyutu abweza zathu zonse zomwe anatiwonongela lelo wasanzidwa mkamwa mwa ngona momwe ankabisala tiyeni tonse amene tikudziwa Kuti zathu zidaima chifukwa chankulu ameneyi mtambo tipite kukhothi Kuti akatibwezele mabizinesi athu omwe adationongela Aja komanso able athu anawapha Aja
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 14 күн бұрын
God bless you Mr game changer dpp my vote
@SandiehRajab-vr6qo
@SandiehRajab-vr6qo 11 күн бұрын
komatu ngat mtambo umamva ukuyenera kumva Mau amunthu ameneyi
@GrecianWyson
@GrecianWyson 16 күн бұрын
Mr game changer keep it up
@user-qt2pl2yf2g
@user-qt2pl2yf2g 16 күн бұрын
Zona big mumatiimilila inuyo ❤❤❤
@user-uk3bz1hr5t
@user-uk3bz1hr5t 16 күн бұрын
Game Changer,,,God bless you also
@user-gg6uh2wo4x
@user-gg6uh2wo4x 15 күн бұрын
Big up mr game changer
@StanziaElias
@StanziaElias 15 күн бұрын
Timothy ntambo ukakhala wina ukanango lapa mwina mulungu akukhululukile
@MalakamMillie
@MalakamMillie 15 күн бұрын
Timothy ndigulu wamuthu akuvuna atipepeleseso mwana wagulu ameneyo
@user-kl1vk1gx2q
@user-kl1vk1gx2q 15 күн бұрын
Taponyani nambala ya m'tambo
@phirimacdonald8638
@phirimacdonald8638 14 күн бұрын
Uko ndiye kubwela man umaziwa kulankhula
@joicemumba3608
@joicemumba3608 14 күн бұрын
Ntambo nditambwali
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 16 күн бұрын
Tiye nazo game changer osafooka ndipo ndife ogani bwino
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 16 күн бұрын
Kukapanga mademo Ku boma la ntendere lotchipitsa zinthu lodziwa umoyo wa anthu ndikumakanyengelera Boma lokupha lozetsa njala lodulitsa zinthu la MCP
@MorganBanda-oc2jx
@MorganBanda-oc2jx 12 күн бұрын
Koma mulungu atithandize chifukwa anthu andalewa akungotizunguliza malo amodzi modzi ndipo kukubweraku tibwereranso ku ulamuliro wa atsamunda
@user-kw7yd2ie6h
@user-kw7yd2ie6h 16 күн бұрын
Welo Dan game changer
@mkhulukinyata5198
@mkhulukinyata5198 14 күн бұрын
Ulemu wanu bwana Mutholo.. Vote yanga ndi dpp basi. Timothy Mtambo apatu ndiye Bwana Murholo akukhadzuladitu yee kkkkk, Yes ndipo ukachita masewera uthera m'manja mwa an'thu pamodzi ndi timabawunsa tako tomwe ukudalirato ..Iwe ukuyenerano kugwidwa gwidwano basi...
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 16 күн бұрын
Congratulations comrade Timothy ndi galu kwambili
@samuzymkwanya8490
@samuzymkwanya8490 11 күн бұрын
A malawi tikuziwa zochitanawo
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 13 күн бұрын
Ndie iwe kutukwana konseku nzeruzo zilipati?
@user-rk3jx3kg8i
@user-rk3jx3kg8i 15 күн бұрын
Truth must be told
@user-ee6be5kl5o
@user-ee6be5kl5o 14 күн бұрын
Mukunena zoona Mr game changer BOMA limeneli lichoke basi atipweteka atonse alliance amenewa kwao kwatha, chimwendo Banda mutu wake sukuyenda Ali ndi misala kwambiri sangane kuti amalawi tikusangala pomwe amalawi akunzuzika kwambiri
@DaimonJulio-ce8mq
@DaimonJulio-ce8mq 16 күн бұрын
Perfect said Mr mn
@user-ep7gu2td6y
@user-ep7gu2td6y 15 күн бұрын
Apm ❤is all my family member's vote
@NKHANGANI
@NKHANGANI 16 күн бұрын
game changer amakwanira end akunena zoona ku Malawi kuli mavuto azaoneni
@StanziaElias
@StanziaElias 15 күн бұрын
Ndiwe munthu oyipa kwambiri mulungu akuchitile chifundo ulape
@KellyHart-pi4hd
@KellyHart-pi4hd 15 күн бұрын
Koma kunena zowona munthu uyuyu wakamba zowona ndipo. Zanzelu
@user-qv3bc4rv7q
@user-qv3bc4rv7q 16 күн бұрын
Tabho ndichisilu azikangolima
@WiseJordan-ds6km
@WiseJordan-ds6km 16 күн бұрын
Marvelous game changer
@simonpaul6567
@simonpaul6567 16 күн бұрын
You are talking very point
@yassinnandera5634
@yassinnandera5634 16 күн бұрын
Mambo ndiophunziratu uyu inunso ndinu a DPP mulekeninso Mtambo asankhe yekha osamukakamiza kuti asapote nkhalamba yanuyo
@user-lw9su5om5z
@user-lw9su5om5z 16 күн бұрын
Chisilu mtambo ma battery 🔋 ako iwe unadya ndrama
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 14 күн бұрын
Chilungamo chiyende ngati madzi tiyeni nazo a Gamechanger😅😅😅
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 16 күн бұрын
Cement inee ndikugura pano 29000 thousands chonsecho nthawi ya Peter Munthalika ndimamugura 5500 thousands
@KellyHart-pi4hd
@KellyHart-pi4hd 15 күн бұрын
Ndipo ine ndilibe mawu or pang'ono ndi MCP
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 15 күн бұрын
@@KellyHart-pi4hd Ndipo adha Kelly mmmmmm MCP afiti okhokha awaaaaa Zedi mmm
@Harlod5566
@Harlod5566 16 күн бұрын
Tikakuphera ku ma Demo komweko, uyereke za ma Demo zako dzija. Takwiya, takwiya, takwiya kopambana. 🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄😎😎😎😎😎😎😎😎😎😎😎😎😎😎
@thompsonchikhwaza2090
@thompsonchikhwaza2090 16 күн бұрын
That’s great talk
@user-hq6dq7zr1e
@user-hq6dq7zr1e 14 күн бұрын
Big muli bho kwambili
@user-uk3bz1hr5t
@user-uk3bz1hr5t 16 күн бұрын
Kuyankhura Mwamphamvu ndi mwachilungamo uku,,, Mtambo kapolo wamunthu
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 16 күн бұрын
Titukwana chifukwa tatopa nazo
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 15 күн бұрын
Uyu kaya mmati game change simunthu nkukuna mulungu anammana mau kulalata osayankhula nfundu chisilu
@AustinChiyembekezo-cx4mz
@AustinChiyembekezo-cx4mz 15 күн бұрын
Chisilu mtambo diso losaonalo ...ndipo umandinyasa kuchoka kale
@user-xv5pr3ji6w
@user-xv5pr3ji6w 15 күн бұрын
Mtambo ndiwe galu kwambiri
@TimeMbona
@TimeMbona 16 күн бұрын
𝙏𝙧𝙪𝙚 𝙨𝙩𝙤𝙧𝙮 𝙞 𝙡𝙤𝙫𝙚 𝙞𝙩
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 16 күн бұрын
Komaso pali abale ena omwe alibe ma 4n zonsezi sakumazimba pls tiyeni tiwasegula maso asatipusise ife we tired
@AjeliMw
@AjeliMw 16 күн бұрын
Galu ameneyu akuyesa ngat a Malawi alero ndiogona
@user-xt2gu9yt9q
@user-xt2gu9yt9q 10 күн бұрын
Malawi weni weni dziko anayamba kulitsata bwino dziko chakwela atatenga dziko ndipo mamvuto malawi waawona kamba kachakwela ndi camp yake michila yachamanu
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 16 күн бұрын
Timos ndichiwanda chachimbuzi choonyasa mtima
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k 16 күн бұрын
Ulemu wanu game changer, go deeper.
@kimukamawe1591
@kimukamawe1591 16 күн бұрын
Mukumva kupweteka coz mukunyambitira limodzi ndi achina chekwera wo anthu akutukwanani kumene
@user-pw2dq1yw4b
@user-pw2dq1yw4b 14 күн бұрын
Timothy sing'anga wachabe zithumwa kumavala ngakhale PA camera 😂😂😂😂😂 sing'anga wachabe Timothy ntambo
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 16 күн бұрын
Game changer thanks aot, and God bless you too🙏🏿🙏🏿
@owenmoses9434
@owenmoses9434 14 күн бұрын
TM ndimbusizixo timutuluke
@JamesMannuel
@JamesMannuel 16 күн бұрын
Uku ndiye kuyakhula mwanzeru
@user-fp3yy7go2k
@user-fp3yy7go2k 16 күн бұрын
Pali anthu ena amakhara ngati sali ku marawi achina ntambo zaka 4 osarankhura chilichonse?
@StanziaElias
@StanziaElias 15 күн бұрын
Ntambo koma umadziwa kuti kunja kuli mulungu?
@MalakamMillie
@MalakamMillie 15 күн бұрын
Timothy ndiwotembeleredwa ndthu
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 16 күн бұрын
Richard ndimwana wamayi oopusa kwambiri mayi ake anangovutika kubereka galu ameneyu
@user-zg9se4rw6v
@user-zg9se4rw6v 16 күн бұрын
Zinayamba kale zowonga chuma cha Boma UDF DPP, ndi amene anawonga, awa alipo a mangomaliza basi
@MikeMalinga-xx8ys
@MikeMalinga-xx8ys 16 күн бұрын
Inenso ndiri kunja!!!! Ntambo galu.... Mmbwa!!!!!.. akufuna auze chani AMALAWI???
@YawakaNyirenda-hu1hr
@YawakaNyirenda-hu1hr 16 күн бұрын
I we mbewe sangathandize
@GeoffreyMaulana-rh5rx
@GeoffreyMaulana-rh5rx 16 күн бұрын
❤❤❤❤
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 16 күн бұрын
Akumva kukoma ndi azibale awo
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 14 күн бұрын
Iwe naweso ndiwe chitsiru ukuganiza kut munthu wanzeru Malawi muno ndi peter yekha nayeso analephela kale sitikufunaso
@SecretNgala
@SecretNgala 13 күн бұрын
Mtambo ndi nyani wachabechabe
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 16 күн бұрын
Bvuto ndiloti mtambo siwakumalawi kuno ai ndi Burundi uyu siku Lina tizamusowesa
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 13 күн бұрын
Wamisala iwe,nawenso watumidwa ndi dpp kagwere uko mavuto onse ukunenawa adayambika nthawi ya udf up to now
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel 16 күн бұрын
Ndale zaphokosa munazolowera Inu ndindan angakuvelen ?
@InnocentNtambalika-ni3dl
@InnocentNtambalika-ni3dl 16 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 16 күн бұрын
Ndipo sindiwe mmalawi iweyo we knows you welcome
@FefieTenisha-du7ge
@FefieTenisha-du7ge 16 күн бұрын
Pure truth...keep on with this sir
@simonpaul6567
@simonpaul6567 16 күн бұрын
Tikukumvesesa
@jamesgama5489
@jamesgama5489 16 күн бұрын
Checking and balancing nthawi yonseyi unali kuti nthawi yatha kale iyi zingasinthe chani mbuzi iwe kwambiri
@jamesgama5489
@jamesgama5489 16 күн бұрын
Timothy mburundi mtambo nsing'anga wachabechabe iwe
NTAMBO ZAKE ZADA PALIBE ALIMBALIYAKE -HOT CURRENT
15:47
HOT 265
Рет қаралды 31 М.
Don’t take steroids ! 🙏🙏
00:16
Tibo InShape
Рет қаралды 25 МЛН
Не пей газировку у мамы в машине
00:28
Даша Боровик
Рет қаралды 4 МЛН
The World's Fastest Cleaners
00:35
MrBeast
Рет қаралды 131 МЛН
MAI JANE ANSAH (TIPPEX) part1....
41:52
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 28 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
MUNTHU WALANKHULA UYU...BON KALINDO, NANKHUMWA NDI A MTAMBO!!! ZOOPSA TAMVANI
20:10
CRUISE 5 WITH REV ALEXANDER KAMBIRI
46:48
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 172 М.
Don’t take steroids ! 🙏🙏
00:16
Tibo InShape
Рет қаралды 25 МЛН