Thank you My President 🎉🎉 the bright future of Malawi
@AshimayeGamaАй бұрын
Iwe atupele dzobela ndidzona utsakane ayi kapena iweso uli mugulumo dzimenedzo usiletu. Tinavaso kale kuti ukupànga ubale ndi mcp
@EreniMakhazaАй бұрын
Thanks may president of 2025 boma🎉🎉🎉🎉
@AndrewYasinАй бұрын
My president ATUPELE MULUZI
@WarriorKB-l3iАй бұрын
Atupele akunena zoona mapulezidenti ambuyomu samaona mtundu koma uyu cikangawayi nduna zonse zikucokela kukasiya ndipo ameneyi mumuze pa u cisilu p mache ndi uyu anabelo mwana wa ng'onayi.Amawo akadziwa mimba zawo akanangotaya anthu opanda tcito fotsake!
@JohnJohn-og8rtАй бұрын
Phulesindet watu ndiuyu watuwatu kumalawiko 2925boma tupere mulungu akudalisene moyo wako tupere ndikuphemphela zabwino zose inshall allah
@MussahJdabdullah-l7lАй бұрын
Osazachita mistake atupele muluzi 2025
@HassanMia-c2eАй бұрын
Mr presdent that is how a readership is keep it bwana presdent❤
@KumbukaniLloydChokothoАй бұрын
Praising your father the worst president Malawi has ever had,mind you the worst turning point for Malawi was the UDF government from kamuzu's MCP..., the foundation of today's Malawi was first democratic governme Muluzi's UDF
A NEW THINKER WISE WILL GOVERN OUR LAND AM GOING TO END ALL NONSENSE GARBAGE FOOLISHNESS EVIL HAPPENING TO OUR BEAUTIFUL LAND SO HELP ME GOD
@OretarbadrBwanaliАй бұрын
❤❤❤Beautiful
@AlexWalter-s4bАй бұрын
Vision president keep it going Mr Atupele Muluzi
@LilianKachala-yz2xfАй бұрын
M,mene mwalankhula zolembetsa Simene akuyankhula a MEC.ndi a NRP akusokonezadi anthufe.
@0wenNkhambuleАй бұрын
Good Messnge Atupele
@RaffickAllieАй бұрын
Uyutu ndi Sogoreri.marankhulidwe Ake omveka bwino kwambiri ndipo ndavesetsa ..
@MarkoHoda-d7eАй бұрын
Komatu mukuyankhula zoona
@AsaniFelixАй бұрын
I need to ask Mr atupele, hw possible was that to issue I'd card with expiry date?
@AgnesMatolaАй бұрын
Machine amenewo sitikuwafuna ife
@MoyendaChilekaАй бұрын
Yakuona baba tupele
@AMIDUKAUNDA-t2sАй бұрын
I love your ideas always
@MussahJdabdullah-l7lАй бұрын
MUSSAH JD ABDULLAH FROM MUVI WACHILUNGAMO TIKUKUMEMANI AMALAWI TIKHULUPILENI IFE LIMOZI NDI ATUPELE TIKUFUNA KUSINTHA DZIKO LATHU ATUPELE MULUZI IS ONLY AGENDER FOR CHANGE
@actuarialscience2283Ай бұрын
UDF my vote
@asahelmachila3026Ай бұрын
Bambo wawo Atupele mmasiku aKamuzu anali secretary general waMCP nde anali mugulu lopha anthu kuaponyera kung'ona. Nde ine Bakili sindimukulupirila
@ahmadjamahiryajuma6456Ай бұрын
Zoonadi mwalankhula izo. Komano dzukani anthu aku oneni akumpoto, pakati, kum'mawa ndi kumwera, Musadikire campaign time ayiii. Anthu akuvutika ndi kufa ndi njala. Koma Mwangoti pheeee. Bwanji? Munthawi ya Covid19 mukatuluka kumathandiza anthu koma panopa bwanji?
I'm coming now to vote,I don't want shirt government like mcp
@mutumwathongethonge7892Ай бұрын
Ife sitikudabwa ndi mau a Atupele Muluzi! Tikudziwa kuti mukugwira ntchito ndi MCP! Shame on you, too much greed!
@MussahJdabdullah-l7lАй бұрын
Umbuli atupele muluzi sakupita kulikose
@georgenewa3508Ай бұрын
UDF is family investment for Mluzi family they just use people for personal and family benefits... Running mate wa MCP 2025 but dnt forget UDF unalanda boma Akamuzu and they still remember
@MussahJdabdullah-l7lАй бұрын
What about aford and dpp
@pauljosephmakaula6835Ай бұрын
Mwachedwa abwana koma
@JohnJohn-og8rtАй бұрын
Zanachedwe kom umuthu alibwino aliyese smene ali ndiumuthu popanga zithu uyembe kuganisa kare boma ili 2025 tupere
@MussahJdabdullah-l7lАй бұрын
Wachedwa bwanji campaign siinati anthu akukoza zipani zawo kuthamanga sikufika our vote is for atupele muluzi
@Rasheedissa-f3qАй бұрын
Mawu ovenka nkwambilli Mr athuphelle😊🎉 live in estan cap
@mishecksipolo7153Ай бұрын
Who is fooling who here? By the way what is your take on smartmatic before I conclude that your are part and parcel of MCP
@lastonekaponya7675Ай бұрын
Atupere ndi wa congress usapusitse anthu ife tinakuzumula kale ukufuna udindo ku congress
@OkalekaleАй бұрын
Ndale za uchitsiru zogawa mitundu zinabwera ndi mbuli iyi akuti Peter,anthu amayesa Peter ndi wa nzeru koma ndi mbuli,amadziwa law yake yokhayo, galu ameneyi ndi amene wagawa Malawi
@FatimaJuma-k3kАй бұрын
Nzeru ulibe galu iwe uphuzire kupereka ulemu kwa kuluakulu wakuputa chani Peter nyapapi iwe?
@OkalekaleАй бұрын
@FatimaJuma-k3k galu iwe ndi a dad akowo,sukuona kuti chimunthu ndi chogawa mitundu ichi?,Bingu anali machine osati uyu.
@OkalekaleАй бұрын
Kuti udziwe kutidi a dad akowo law inalephera kuwachotsa umbuli,DPP inayisandutsa chipani cha a Lhomwe okha pamene akudziwa kuti a Chewa ndi amene ali ochuluka m'Malawi,ndiye ingadzawinenso? Ngati ankadalira kubera nanga lero atha ali ndi kunja kwa boma?