Koma ineyo azikhalewa andisekesa,😂😂😂😂akut anaoneka bwino atawaika makutu afisi😂😂😂😂😂
@sharonicier0015 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣😂😂😂
@ChikuMega4 күн бұрын
Big up brother pitixan kutiphuzisa achinyamatafe ngt mne amatiphuzisira achilima❤💪
@marryphili54195 күн бұрын
Iwe wukutukwana apa zeru wulibe ngati ndiwe WA MCP tangokhara chete anthu akupha inu zisiru
@Anthonymendos5 күн бұрын
Zonse paja greci Chinga adayankhula zokhuza zokhuza kulanda u plezident, ndi asatanic a MCP
@cephasnkhoma23014 күн бұрын
Powerful TV
@marygoza12055 күн бұрын
Mu kuononga ndalama za anthu osauka zomwezi mpaka kuyitanitsa anthu from mapiko kunja kuti azafufuze are you serious Mr minister? Bakali muluzi ndi Munthalika akhala akujambulidwa a cartoon komanso kuyimbidwa mu nyimbo sanayambe amangapo munthu. Even Jacob Zuma mwakhala akutukwanidwa even kupangidwa cartoon but sanamangepo anthu. Osayiwala kuti ukakwera pa nsanga pa njovu osamati kunja kulibe mame. God is watching at Malawi one day is one day
Awatutse a Kamlepo Kalua ndi Bon Kalindo, tili mu democracy. Chakwera ndi boma lake la MCP lalephera, tatopanawo.
@JoybJohn-s6t5 күн бұрын
Ku Malawi kulibe freedom of expression 😢
@user-gg6uh2wo4x5 күн бұрын
Best tv
@sanuhabdullah59985 күн бұрын
Anduna awa di ambutuma kuyitana anthu kucha za nkhani imeneyi malo molimbana Dziko litukuke cmc
@brightcharlie23965 күн бұрын
Angoni analakwanji km RIP legend chilima 😭😭😭
@alexmkolongo30895 күн бұрын
Awa zimene akudziwa ndikugwetsa kwacha basi
@shayrafernandeslatif95565 күн бұрын
MTSRIP 🌹,we are all mourning with you the families ifeso takhudziwa kwambiri,imfa yosayiwalika😢
@user-cu8wy9rz3b5 күн бұрын
Boss you should be making your own vids koma. Leave bakili tvs videos to his channels, thus the problem yaife ku malawi...we take someone's song n put pa channels yathu😊....it's not own
@DinopianoVascoPianoVasco-m3g5 күн бұрын
Otukwana bakili muluzi tv simuthu ndi satana komanso ndi khumba
@DizayaLikhunye4 күн бұрын
Kkkkkk ifeyo tiripo mr kkkkkk akunama
@NoelKhwimba-bh3ts5 күн бұрын
Inutu akumanga bakiri muluzi TV sinu mungofuna ma views
@ChisomoKandikole4 күн бұрын
My God prossed keep kuti muzitiuxa zambiri
@user-vm7iz6oz6r5 күн бұрын
Maiko USi wamupereka chilima mm zimu wa chilima use mutendere😭
@sharifujoe76335 күн бұрын
Kkkkkkkkkk Skelton ngoma😂😂😂 yahhhh Malawi wanga ine
Iwe watukwana bakili tv naweso pathako pako nyawu mwapha chilima ndinu ndipo ziko likusawuka zinthu zamuvutani mu kuwona ngati anthu azakuvotelani palibe never never munthu, akamakususani basi mwayamba kumutukwana basi nyawu inu 2025 kuphana kuphana mu kuwona ngati tukuwopani iyaa
Chakwera asatirat chilima ngat akuona ngat iye ndiwa panazare tiona achakwera thawi yanu ikafika mufera nyumba inuyo
@user-co3wr3rn4h6 күн бұрын
Panji nikuyowoyele muchitumbuka pamatako pako ulichindele chomene nkhana vimavi vako we love bakili muluzi tv our best Chanel ise luta waka uko kutali ungatikwitiska
@rachelkaunda5 күн бұрын
Akulu Inu kutuka nthena yayi please fear God musanayulutse Mau mkamwa mwanu think about God first there is judgement day after this life your words are too much before it is too late receive Jesus Christ
@Extratremendouszeus5 күн бұрын
Mumatenga ma audio mochedwa Iyi inatuluka dzulo,inu mwapanga upload lero
@ChipilipiroMtsukwamwale5 күн бұрын
Big mutipatsireko mbiiri ya asing'anga abwino kumalawi kuno, mwina tiyeseko matsenga abwino. 14:36