That's true brother but vuto la mwafulika anthu amangosati zinthu zoti saziziwa khomwe kuti izizi zimatanthauza chani then ndichani zimene akuyenela kuchita pa tsikulo izi ndizomwe zingapangitse kuti tsiku lomaliza tizangwele m,mavuto akulu kwambiri
@kubengovender69964 ай бұрын
Big up!!
@JailosFirston5 күн бұрын
Inu nd aboss
@LysonMtalika-tb6fk4 ай бұрын
I salute you Biggy, proud of you always
@clubjunta4 ай бұрын
Bro inuyo ndikukuonana Pama video ambili mukupeleka ma comments Anu ine Monga Admin WA channel Ichi cha club junta Nditumizileni number yanu Ku email iyi clubjunta@gmail.com ndikupatseni airtime mugule ma bundle basi inuyo mumakwana
@user-uc1pd1tc2x4 ай бұрын
Thanks brother umaitha zedi umatiimilira❤❤❤❤
@rafiqlimbilira9405 күн бұрын
Muchose chi Belu cho aah
@cassimyusuf66834 ай бұрын
Bakili muluzi wafegi uyu, izi zobela basi .
@user-xm3zl5cg6x4 ай бұрын
Ine Frank pa keep town ndimakonda kuvela nkhan imeneyi Kwambili pa Moyo wanga
Is this the true channel because this was already done by bakili muluzi TV not club unless club junta will been steeling these nice video from mighty Gregory
@clubjunta4 ай бұрын
Just take a look how many videos does this channel have and how many videos from my brother do I post .........and it was post to post them without mentioning his name but bcz I respect him I hive him his credit that's why I have to mention his name if I post his video
@greychizaka40884 ай бұрын
King i will follow you till
@clubjunta4 ай бұрын
Thanks very much
@user-lu8px7td6p4 ай бұрын
Sure
@BenissoneErnesto-eh6zs4 ай бұрын
Sibakil muluz tv WA original ay imeneyi inatuluka Chaka chapitacho pamenepa yangopangidwa copy right basi watching from Mozambique 🇲🇿
@clubjunta4 ай бұрын
Te entend meu irmao ...mas deixa EU te expricar Este video for feito anos atraz e video fala sobre Sao Valentina e Valentina acontece em Cada ano Uma vez ....Agora o video foi ransado com aqueles jovems que voce conhece que Sao chamado BAKILI maluzi TV canal tambem Sao eles mesm que editarao o video apena que a mesma message EU Poste e escrev que quem fez Este video è os mesmos jovem d canal bakili muluzi TV para que as pessoa nao disser que robei o video d outro
@user-bh4zb7ji3o4 ай бұрын
Kod mwastha deep mutisokoneza tikuganiza mwna iyi sieniyen bakili muluz
Ubwino wake satana emwe mukumunenayo anthu otsatira iye sapanga nawo nyasi izizi km inuyo olungamanu ndiomwe mumazitsatira kwambiri ndiye pakat pa inu ndi Muhammad chigawenga ndindan
@RahmanWetor4 ай бұрын
Ife sitinyodza mtumiki bro koma kufunila zabwino bass tikava kuti zinalake kuti yesu