BON KALINDO 7 JULY 2024 KUKHDZULASO PA CHI SUNDAY

  Рет қаралды 32,989

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

12 күн бұрын

Пікірлер: 115
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 10 күн бұрын
Nanuso bwanji Joyce Banda mbuzi yamunthu chakwera mutu ngati phwala lambuzi
@limbanimtitima9170
@limbanimtitima9170 10 күн бұрын
Born you always talk the truth ❤❤😂
@KelvinMangwengwe
@KelvinMangwengwe 9 күн бұрын
Kuyankhula zomveka bwino ndipo zaphindu zokhazokha congratulation boss
@chiefjusticie
@chiefjusticie 9 күн бұрын
Ulemu wanu
@BinwelLukali
@BinwelLukali 10 күн бұрын
The DC bon kalindo the great 💪💪💪💪
@MacreaChilingulo-ob9gb
@MacreaChilingulo-ob9gb 9 күн бұрын
Long live Boooon Kalindo !!!!! The D C ccc !!!! The Wise Guy !!! Iweyo palibenso !!
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 9 күн бұрын
azibale athu amene anaphedwa ndi chakwera kuchikangawa ndi zomvesa chison kudziko lino chakwera ndi chigawenga
@WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un
@WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un 9 күн бұрын
The DC akamuna okakha NDI mawaya
@owenmanda1741
@owenmanda1741 9 күн бұрын
The problem with Malawi is nkhondo timawasiira anthu ochepa kumenyera ufulu,no wonder akalowa mu boma amakasakaza chuma.We all need to fight for our freedom
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 10 күн бұрын
Akhwakhwananda amenewa 🐊🐊🐊🐊 atitola kwambiri
@pempheroraynnoxmpesi8713
@pempheroraynnoxmpesi8713 9 күн бұрын
Ati bon Kalindo amangidwebe😂
@DYSONKUMPEREMBE
@DYSONKUMPEREMBE 9 күн бұрын
Machine bon kalindo ❤❤❤❤
@AustinMangani
@AustinMangani 9 күн бұрын
Mbambande Mr
@JosephMichael-x7v
@JosephMichael-x7v 9 күн бұрын
Bon kalindo our president
@DanielChima-zl2uo
@DanielChima-zl2uo 9 күн бұрын
zoona Bon kalindo ngakhale kuno ku south Africa zimatikwana kwa basi zimene akupanga president
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 10 күн бұрын
60 years subtract 4 years yamazumzo ya chakwela
@RichardMedi
@RichardMedi 9 күн бұрын
😅😅😅😅😅 Kakakakakakakakaka DC 😂 our president kkkkmwana owopsa heav😂😂😂
@ShaibMusa
@ShaibMusa 10 күн бұрын
My Hero..The Dc
@HallimaMakwinja
@HallimaMakwinja 10 күн бұрын
Zoonadi Mr Kalindo simukunama Chakwera ndi gulu lake they are mbunzi za anthu they are fools
@EstherNangomba
@EstherNangomba 9 күн бұрын
😂🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥kuti buuuuuuuuuuuuuu
@eliaschinoko2086
@eliaschinoko2086 9 күн бұрын
THE D C BOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOON KALINDO 💪💪💪💪💪💪💪💪🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 9 күн бұрын
Zakeyu powonetsa kubadwa mwatsopano anabweza theka lachuma cheke kwawomwe anawabera ndiye Chakwera pamodzi ndi amithenga Ake onse abweze zomwe atiberazo powonetsa kubadwa mwatsopano
@BeatrizUlanda-ht2th
@BeatrizUlanda-ht2th 9 күн бұрын
Mumakwana Avon karindo ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@blessingsmwale6007
@blessingsmwale6007 8 күн бұрын
Izoooh Hankonnani pwiya aleleni iiwesese😂
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er 10 күн бұрын
Mumakwana boss,osawanyengerera makape achina kumkuyu,zikhale ndi chakwera yemwe😙😙
@user-ty5zh2xi9b
@user-ty5zh2xi9b 9 күн бұрын
Sowuna auseni agalu amenewa achakwera
@ChikumbutsoTsalangu
@ChikumbutsoTsalangu 10 күн бұрын
Iwo andale si bola akhutitsa mimba zawo
@user-ve7rx7vj1g
@user-ve7rx7vj1g 9 күн бұрын
I agree with Kalindo..the #thinkalike
@EllenPhiri-xt8pt
@EllenPhiri-xt8pt 9 күн бұрын
Bon k amatha ❤
@AbondBolbo
@AbondBolbo 10 күн бұрын
Abon kuyilawilira😂😂😂
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 9 күн бұрын
Chakwela mhuzi ya muthu
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 9 күн бұрын
Or abadwe mwatsopano Koma mizimu ya anthu anapha ija imufafanthabe Mulungu wake uti okumba mapemphero a munthu opondeleza oipa wakupha okondela ngati ameneyo
@IanChidothe
@IanChidothe 9 күн бұрын
You saying the truth
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 9 күн бұрын
kkkk mwakumana usazindikila nokha nokha vuto mli busy pa ma phone mwayiwala kuti azanu ali pa ground . zoti peter analamula bwino mkunama matha ma albino ambiri
@trifoniachilunda6263
@trifoniachilunda6263 9 күн бұрын
Iweyo umandiwaza chifukwa umayankhula chilungamo. Palisouyu Limpopo FM NDI bakili muluzi TV anthuinu ndinu madolo❤
@MarkinaJohn
@MarkinaJohn 7 күн бұрын
The DC
@SilverMkwatula
@SilverMkwatula 9 күн бұрын
Bon muuzeni chakwera kuno ku mangochi asazafike tizapha tokha ndi galu
@AliceMpaso
@AliceMpaso 9 күн бұрын
Kkkkkk winiko samatopa mumamuseweletsa😂
@TorshKadango
@TorshKadango 10 күн бұрын
Iweyo ndi one
@charlesmataka1700
@charlesmataka1700 9 күн бұрын
Machende awo awa
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana 9 күн бұрын
Koma thawi ikubwera ndithu mlungu atiyakha ndithu mlungu wathu salephera❤
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 9 күн бұрын
The D.C.
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 9 күн бұрын
President omvetsa chisoni chakwera ulamuliro wake ngati dzaka 100 chifukwa cha dyera
@marychavula698
@marychavula698 10 күн бұрын
Our Hero
@KhumboMunthali-jx5me
@KhumboMunthali-jx5me 9 күн бұрын
Terelini
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 9 күн бұрын
Mwana oopsa kwambiri
@AustinMangani
@AustinMangani 9 күн бұрын
Morning
@KennethChazama
@KennethChazama 9 күн бұрын
Inetu ndi mchewa koma nyasi izii sitikukondwa Nazo ,from nathenje
@EliaMhone
@EliaMhone 8 күн бұрын
Koma opposition ikalowa mu boma imasinthanso kuiwala zomwe ife amalawi tinkalira .
@PatronChanza
@PatronChanza 10 күн бұрын
The dc
@yusufbreak905
@yusufbreak905 9 күн бұрын
Kkk
@CollinsHala
@CollinsHala 9 күн бұрын
Vuto a Malawi ife mantha
@IbrahimRaphael-z3l
@IbrahimRaphael-z3l 9 күн бұрын
💪💪💪💪
@AffickChaona
@AffickChaona 9 күн бұрын
The DC Bon kalindo ❤
@AndrewChitsamba
@AndrewChitsamba 9 күн бұрын
We respect fools so no need to reply... 😂😂😂😂
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 9 күн бұрын
Kodi cakwera akufuna anthu amuvotere 2025 afuna adzidzatani poti iye sadziwa kanthu akufuna adzapitilidze kuba conde. Cakwera usavutike amalawi sitikukufuna ngakhale pangono watilidzatu iwe watidzudza dzaka 5 ngati dzaka hundred
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 9 күн бұрын
Aaaa kuba mistake kuyika MCP papando iiiiiii tinalakwitsa
@user-ss9bj5eh6b
@user-ss9bj5eh6b 9 күн бұрын
madala madala born k
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 9 күн бұрын
The DC 💥💥💥💥💥
@HarryYottam-ft1bo
@HarryYottam-ft1bo 9 күн бұрын
Ulemu wanu comrade
@ShafieIdrissah
@ShafieIdrissah 9 күн бұрын
❤❤❤❤❤
@chestermajora
@chestermajora 9 күн бұрын
awa akungolankhula Loma palibe zomwe zikuchitika.mmalo mot tipange zinthu ngat kukenya.
@rhinovaheke6614
@rhinovaheke6614 9 күн бұрын
I just watch so that kalindo can make some money
@oskidooscar7468
@oskidooscar7468 9 күн бұрын
Koma why sakuyamkhulapo za manganya vice president ku mcp
@JeremiahChilenje
@JeremiahChilenje 9 күн бұрын
Dziko lamkaka ndi uchi lija pano ndi sabora ekhaekha😢😢😢😢
@ClementChisemphele
@ClementChisemphele 9 күн бұрын
Wamsala iwe amalawi umanenawo ndi ati? enafetu sutifuna zolandila zimene umafuna iwezo ife amene timalima tikusangalala kabwebweta ndi misala yakoyo
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 9 күн бұрын
Truth must be told plainly without fear
@KennethChazama
@KennethChazama 9 күн бұрын
Nkhani ya ma ID muikokomeze kt apart from mcp zipani Zina taonetsetsani zomwe zikuchika mmaderamu,tabwerani kunathenje midzi ngati monga mphete village,mtsotsa, sanjiko,nyama ,kaphala ,matapira,Chatha ana osafikamo Zaka,
@HamitonFrank
@HamitonFrank 10 күн бұрын
60years of independence but nothing to show
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z 9 күн бұрын
6 July ndiye chani
@allansili-rc9gc
@allansili-rc9gc 9 күн бұрын
Wow
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 9 күн бұрын
Vuto amalawi mumawombele mmanje fiti kodi simudziwa kut mtambo ni akalindo vinanyeza kwambili pita muthali mpaka apita analuza masankho anazikambe amenewa
@AndrewChitsamba
@AndrewChitsamba 9 күн бұрын
Empty tins
@yobesaikonde6166
@yobesaikonde6166 9 күн бұрын
Chamba kkkkkkkkkk
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 9 күн бұрын
Komanso boma ili manyaka eni eni koma ndlama zikuwonongedwazi ndi zabwino bwino? Mzipatala mulibe mankhwala koma ndlama zogula anthu muli nazo shame Malawi government shame Mulungu kumwambako muzimutetezera Bon kalindo kwina kuli konse angapite
@elishamael-shadai
@elishamael-shadai 9 күн бұрын
Tell them where to get off your ass The DC. Chakwera amadya maliro
@feehasaidid.r.d
@feehasaidid.r.d 9 күн бұрын
Koma akamati abadwa mwasopani akuyesa kuti ndiopusa Never ever changes my mindset
@FaruckMuhammad
@FaruckMuhammad 9 күн бұрын
Mutayeni uko Joyce Banda ndihule wachabe chabe
@medicoastkzn
@medicoastkzn 9 күн бұрын
Wapenga chakwerayu
@AbondBolbo
@AbondBolbo 10 күн бұрын
Abon kuyilawilira😂
@ChikuMatemba
@ChikuMatemba 9 күн бұрын
ine Mchewa Koma Chakwera Guy osamuvoteraso
@user-kw7wr4kq9w
@user-kw7wr4kq9w 9 күн бұрын
Let's not be negative for everything. Peter was also useless
@user-dd1qq5xq1k
@user-dd1qq5xq1k 9 күн бұрын
Ufulu unali mbuyomu koma pano ufulu uja anatilanda,kumangomangidwa ...Boma ili lankhaza zedi.
@MphatsoGowero
@MphatsoGowero 9 күн бұрын
😂😂100%
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 9 күн бұрын
Kuyankhula mwachulumgamo
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 9 күн бұрын
Chakwera wationjedza
@mikeasmachine4581
@mikeasmachine4581 9 күн бұрын
Chakwera ndi pa msete seriously
@mkupabanda-nd2vb
@mkupabanda-nd2vb 9 күн бұрын
😂😂 telelini
@ChisamiMalota
@ChisamiMalota 9 күн бұрын
Kkkkkkkk Born K the DC
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness 9 күн бұрын
Kodi aborn kalindo mapemphero ndikuti ndichinthu choyipa kodi nayesa unali mwambo wamapemphero koma inuso zina mumangolankhura zopepela zokhazokha ndipo amene amakupasani ma coment okutamandani nkupanda nzeru pa inuyo tikuwona ndipanja zowona dairy kubwera pa air basi nkhani za ziii zopanda phindu
@StanleyChirwa-d6b
@StanleyChirwa-d6b 9 күн бұрын
Kungosiya kuvera bas coz mutopa🥺
@WisdomMaseko-fi5sv
@WisdomMaseko-fi5sv 9 күн бұрын
Koma muli nkuchikanwa kosatopa now it's boring
@nafejonga972
@nafejonga972 9 күн бұрын
Kodi zinachitikira kuti? Sindizisate nane 😂😂😂
@InnocentKandaya
@InnocentKandaya 9 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@HamitonFrank
@HamitonFrank 10 күн бұрын
Bon kalindo the great💪💪💪💪💪
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 10 күн бұрын
Pangoline the DC ❤❤
@medicoastkzn
@medicoastkzn 9 күн бұрын
Wapengatu chakwelayu😂😂😂😂is Dog.
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 9 күн бұрын
Kalinda mtambo niamene anayika chakwela paudindo vitsilu vimenevi vikutenga ngati amalawi opusa amene omatsatila zokamba zanu nose awili ndinu munayika amcp pampando mwemwe vitsilu amalawi osavela viwanthu vimenevi😅😂😊😊
@PhillspicJere
@PhillspicJere 10 күн бұрын
Mumuuze Kalindoyo kuti ndiodwala komaso ndichitsiru kwabasi zinthu zinaipa kuyambila pa Bakili mpaka pano
@felixmaluku5077
@felixmaluku5077 10 күн бұрын
Iwe osamuudza wekha bwanji
@JosephChatama
@JosephChatama 10 күн бұрын
Iwe ndi mbudzi kwabasi, zitaipa nthawi imeneyo unapangapo chani😂😂
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 9 күн бұрын
Iwe ndi chisiru nthawi ya maprezdent enawo fanta timagula 200 kwaca nthawi yachakwera 750 wakumudzi angamugulire mwana fanta manyi amako wava cakwera waononga dziko kukwera kwa zinthu ndiye anthu tikamalira iwe wati tikunama mbusa wasatanic akucoka 2025 mdipo adzamumanha ndende yace tikumba dzenje mpaka adzafera momwemo munthu oipa mtima ngati konyera
@ChrisMsonyo-yq2ko
@ChrisMsonyo-yq2ko 9 күн бұрын
@@user-hm9nc7lz6e galu kwabas
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 9 күн бұрын
Mwapenga inu eti
@FrancoKaunga-rq2ki
@FrancoKaunga-rq2ki 10 күн бұрын
Chakwera ndi bakha weniweni.
@jamesmsonkho4830
@jamesmsonkho4830 9 күн бұрын
Wandiwazaso ndi busa ujayo wamzeru kwambiri kulalikila mwaphavu
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 9 күн бұрын
The DC
A Opposition Simukudziwa Mmene A Malawi Amakukondelani - Bon Kalindo
16:49
I CAN’T BELIEVE I LOST 😱
00:46
Topper Guild
Рет қаралды 118 МЛН
Who has won ?? 😀 #shortvideo #lizzyisaeva
00:24
Lizzy Isaeva
Рет қаралды 62 МЛН
Heartwarming: Stranger Saves Puppy from Hot Car #shorts
00:22
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 22 МЛН
BON KALINDO 17 JULY 2024 BIG MAN KUPHEDULA PA WEDNESDAY
17:05
Malawi Trends TV
Рет қаралды 1,1 М.
Maxkamadda Sare ee ciidamada oo soo gabagabeysay kiiska dilkii Ganacsade Abuukar Kaabax.
13:44
Olo Anthu A Ku Kasiya MCP Sakuyifuna - Comrade Ntanyiwa
21:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 22 М.
I CAN’T BELIEVE I LOST 😱
00:46
Topper Guild
Рет қаралды 118 МЛН