Muziononga ndarama simungamugwire ndi oowa kwambiri mufuse ine nose AMcp ndi ana muzingononga ndalama tipezeni ife makape
@BatumeyoChikopaАй бұрын
Langa ndi pemphelo kwa inu comrade mtanyiwa kt mwina tidzaone malawi osinthika wa mkaka ndi uchi, 😊😊😊😊
@VictoriaBakuliАй бұрын
Keep it up comrade ❤❤❤ Umaseka mwachikuwawe 😂😂
@RuthChilobweАй бұрын
A mr Ntanyiwa .comead of malawi.mukuithatu.ya zimene ankacuta Kanyama chiume ndi kamuzu Banda kanyama chiume ankamuopsyeza kwambiri .ndipo inu pangani zomwezo.amen..comrad
@GabrielSabuduАй бұрын
Mbambande bravo ntanyiwa
@Musa1828-l5dАй бұрын
Mtangiwa machine 🔥🔥🔥🔥
@JohnWame-u3lАй бұрын
Keep it up mtanyiwa❤,,,ka volume koka enough is enough
@MiddayDelezaАй бұрын
Ipatse moto ntanyiwa we love you ❤❤❤your indeed sended by our almighty God
@kubengovender6996Ай бұрын
Timakudyadirani big man!!
@WarriorKB-u3kАй бұрын
Ndizoona mcp yabeka kale mavoti chifukwa akudziwa kuti aluza kale .Koma akunama dzikoli tiligawanapo chikangawa adziwe zimenezi APM voti yathu
@SpencerKadewere-cd5okАй бұрын
Ntanyiwa mbambande 💪💪😅😅😅🎉🎉🎉
@ZayaweStoneАй бұрын
Live from Cape town
@ChanceZambikaАй бұрын
Umakwanaa boss ❤❤❤❤❤
@GeofreyRhonardАй бұрын
Mumatimilira mr comrade mcp ikunama
@dondamissonchdziwe3958Ай бұрын
Okeee, senhor Ntanhiwa você diz apesoa matou o nosso Advogado ak,em Maputo é Malawi ano, tem certeza, foi combinado com senhor Nyusi tabom vamos investigar bem esse assunto Obrigado pra te, informaram isso nos não sabemos
@augustinechibbalazi8897Ай бұрын
Msundwe barracks in Malawi ? It's news to me !
@MiddayDelezaАй бұрын
Koma achimwendo God is watching chilichonse chingowululika
@FredKanyerereАй бұрын
Comrade good job.
@ElizabethFatch-o3wАй бұрын
😂😂😂😂😂kupanda kukumverani mau anu a comrade timadwala kananji mukamaseka muja kawabayatu 😂😂😂😂😂😂
@GiftNgwira-e8lАй бұрын
More fireee ntayiwa tilinanu pambuyo tikudalira inuyo
@RuthChilobweАй бұрын
One of them malawis freedom fighters
@GiftNed-n2uАй бұрын
😂😂 Ndodo ituluke basi
@MikeGomani-tb9npАй бұрын
Ndema judge akumalawi ameneo😂😂😂😂😂
@KentWilliam-r2vАй бұрын
Keep it up bro
@StaffordNgolekaАй бұрын
Musyeni aitulutse ndodoyo the Dc bon kalindo mwana oyipa kwabas agalu amenewa ajaira kwa achina chikangawa
@GeshoMwakitwileАй бұрын
Za ziiii
@paulpaseli6310Ай бұрын
Kanyimbo kali bho
@dondamissonchdziwe3958Ай бұрын
Amwene Antanyiwa tatchulani Maina awanthu amene abwera kuno Ku Moçambique kuzapha Wanthu athu powa ombera zipolo polo 26 okeee,kunoko kwavuta Wanthu Dziko lonse Lino kuli mapokoso owopsya moti mwina nkhondo ikhonza kuyambika.bola tamva kunoko.nyusiyo tithana,mosavuta,mwapwiya mualota phama,Me here a'm A president of another Association of the whole Nation okay, thanks for your information it means that you will be a witness, você tem BOM informações pra asua testemunhas tabom obrigado muito One Day we will be there.
@ShahidahLondonАй бұрын
Aona nyekhwe 😂😂😂 kanyimboko Kali bho
@WanangwaMfuneАй бұрын
Koma Kuti ukapita ku court, Choyamba kuyembekedzela zinthu ziwirir kuwina or kuludza. Koma vuto lathu timafuna tikapita ndi nkhuni mmutu mmalemba Kuti akavela zaine