DR CHAKWELA CHOZUZULA AMERICA 🙌🙌🙌🤔🤔 NKHANI YONSE MWATSATANI

  Рет қаралды 16,240

HOT 265

HOT 265

27 күн бұрын

Пікірлер: 184
@user-ez8uk7py8n
@user-ez8uk7py8n 25 күн бұрын
Mr president you mean that in Malawi there's no corruption,? Even your self is Mr corruption as well why,,!!??
@user-wq3uq2lt7v
@user-wq3uq2lt7v 25 күн бұрын
Ngakhale ulankule chichewa?? akunama ameneyi ineyo ndiwafotokozela angeleziwo Pazomwe wanenazi iweyo Lazalo
@richarddoctor4746
@richarddoctor4746 25 күн бұрын
Anayamba kulakwitsa ndi iwowa powalanda a vice president awo mphamvu zina kamba kongoganiziridwa za katangale
@user-ib7ig3xd2h
@user-ib7ig3xd2h 25 күн бұрын
Akuluwa afika pochititsa manyaz akuipitsa mbir ya dziko nd kuba kwa nduna xawo😢
@user-ul5hh3cz8z
@user-ul5hh3cz8z 25 күн бұрын
The world winer of preaching to day is çhakwela .he is defining hem self zalu zamuthela ameneyu athu ndizoomba mwanja zimenezi
@isaaczuze
@isaaczuze 25 күн бұрын
Chisilu china ndiye chikuti alomwe amatukwana ndizoona ndthu amatukwa kwambili chifukwa cha zimene mbuzi yakoyi kaya ndimbwiyako nonse ndizisilu ....mlomwe amakana zopusa ngati akupanga chakwera .....amafuna kulamula zaiko asakuziwa kuti kodi kulamula ziko ndichiyani
@MathewsMANDUTU-lh6oo
@MathewsMANDUTU-lh6oo 24 күн бұрын
Auze amve nanga m'chewa uyu ndye bola mbuzi imaganiza
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 25 күн бұрын
Chanzeru palibee 😢😢 . Akuku awa tikawachotse ndi voting mwake muno ndikudzawazenga mlandu pa cashy yathu yomwe akutibera 😢😢😢😢
@user-cw9is2lm2x
@user-cw9is2lm2x 25 күн бұрын
Ndiyekubako galuiwe
@AliSalimu-wl3vi
@AliSalimu-wl3vi 25 күн бұрын
Mbuzi ya muthu
@francisvisage2705
@francisvisage2705 24 күн бұрын
Apulesidenti zunulanipo chimoza waka icho wanyithu wakudokera kwa ise, uwu mbutesi abwana. Panji titi apo mwateta
@user-wx5fq7gg7d
@user-wx5fq7gg7d 24 күн бұрын
Kkkkkk ndipo wazunule nadi akee😂
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 25 күн бұрын
Mbuzi ya Muthu
@GrecianWyson
@GrecianWyson 25 күн бұрын
Oloko ukanapanda kuyakhulapo Kathu zakudzudzulidwako.kudzikweza kopusa shupiti
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 24 күн бұрын
Awawa ndioyanhulitsa pambali zedi no comment.
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 25 күн бұрын
Amalawi tinabetsa dziko zedi....God plz bless APM
@ThokiseWiriyam-ws1ec
@ThokiseWiriyam-ws1ec 25 күн бұрын
Shupiti mbava iwe
@user-xt2gu9yt9q
@user-xt2gu9yt9q 25 күн бұрын
Kuomba manja kusonyedza apule akulakhula dzazelu koma Malawi wazaza ndi dzipukwa dzawathu dziathu dzovala masuti dzongosamba ndindalama dzakuba ska lapamalawi
@user-yn4ee1qn2j
@user-yn4ee1qn2j 20 күн бұрын
Akuluwa ndiabonza zedi
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z 25 күн бұрын
NO PAIN NO GAIN PLEASE NYAN IWE YAKULA CHIZUNGU AKUVE AMELIKA KUTHI AKUBANESO NAWE
@giftjamali8204
@giftjamali8204 25 күн бұрын
Mr president you need to know kuti American peaple don't love corruption 😊
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 25 күн бұрын
Chakwera mapazi ako iwe mbava iwe sataniki ingokhara chete paribe chazeru chomwe ukunenapo kamboro kako kodura ni sowo
@InnocentMmanga
@InnocentMmanga 24 күн бұрын
Mmmm vaboza zalalo ndiwe wakwiba suka
@user-ln5hw7dn9g
@user-ln5hw7dn9g 23 күн бұрын
Akuona waku dengayo
@user-ie5pc4ox8i
@user-ie5pc4ox8i 25 күн бұрын
Ukuopa chan kuyankhula chizungu 😂😂😂kuti america ikuve bwino bwino 😂😂uli ndichibwana kumenekuja olo iweo chakwera atha kukubana
@arnoldkamanga1335
@arnoldkamanga1335 24 күн бұрын
Akuopa English kuti amumva, Koditu nayeso Ali ndi mantha😂😂
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 25 күн бұрын
Chakwela bagamoyo mbuzii
@victorauwana7258
@victorauwana7258 22 күн бұрын
Akubawo
@user-xb2dz8vo5z
@user-xb2dz8vo5z 24 күн бұрын
Bwana musamikire kumbuyo katangale
@ophlexmkondowe8107
@ophlexmkondowe8107 24 күн бұрын
Akanamuuza asiye kukabweleka ndalama ku amerikako.
@owenmoses9434
@owenmoses9434 25 күн бұрын
Kodi guys amene amamulembela uyu zimenezi ndani? I think there is somebody behind this guys who is governing us😢
@AnusaAwali-yh3wf
@AnusaAwali-yh3wf 13 күн бұрын
Ubwino wake zinathera mu chichewa izi kkk😅😅 km khongwe uyu 😂😂 sazatheka
@oscarnamirecah5386
@oscarnamirecah5386 25 күн бұрын
It's a pity tafika apapa kuipatsa moto pokuba
@KnowxySainet
@KnowxySainet 25 күн бұрын
MCP yakuba azipanga bwanj ziiii nonsense basi kuchonsa vice wawo cholinga aziba ndalama koma kumanamidzira wina kumavutitsa apatimat mulungu ayankha Chilima fire....
@user-wp1xh6if2r
@user-wp1xh6if2r 25 күн бұрын
Hot 265 umatiyimilira🔥🔥🔥
@vincentmakotho
@vincentmakotho 25 күн бұрын
Mbuzi iyi
@FunnyCardGame-kl3eo
@FunnyCardGame-kl3eo 23 күн бұрын
Kuyankhula mopusa uku ukutiudza kut katangele kumalawi Kuno anthu tizipanga za umbava ndi kuba ndi mifuti chifukwa America imapanganso ndikanakutukwana wamva
@NditajiMaxwell-cz8ir
@NditajiMaxwell-cz8ir 24 күн бұрын
Inu munawalanda mphavu a vice anu kamba koganizilidwa pa zakatangale asanagamulidwe kt ndi olakwa nde zikusiyana pati ndi Americayo
@nahayopaulkim9097
@nahayopaulkim9097 25 күн бұрын
Agriculture mukuti yayambibwino???? So why last month munadandaula zoti kuMalawi kwagwa njala
@dianajobe4162
@dianajobe4162 24 күн бұрын
Mmmmm akulunu mutiphetsa. America mukumuputayo amfunseni anzanu they'll tell u
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m 25 күн бұрын
Ukafna kuzuzula uzyakhula chizunga azkuva mbuz iwe
@IbrahimMatias-te1kc
@IbrahimMatias-te1kc 25 күн бұрын
Kkkkkkkk
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg 25 күн бұрын
Akut tinve zomwe awerenge pa chipepala kkkkkkk koma hot 265😅😅😅😅
@lymonmanda-cd8ol
@lymonmanda-cd8ol 23 күн бұрын
He could address in English so that the US citizen themselves could hear or understand him properly, why he is addressing in chichewa today? Something is hidden. He is complaining about the American behaviour in a local language that's a sign of corruption hidden and defending which has taken place in Malawi
@user-yi4oc4xz4v
@user-yi4oc4xz4v 25 күн бұрын
Koma izi ndi nyawudi
@yamikanismith5904
@yamikanismith5904 24 күн бұрын
Kkkkkk ndinasankha kukhala chete poopa kuchimwira yehova
@SteveShaya
@SteveShaya 25 күн бұрын
Chizungu America imve ankolo ukhawule uwone
@basheeribrahim1050
@basheeribrahim1050 25 күн бұрын
😂😂😂 sangayelekeze galu uyu
@MathewsMANDUTU-lh6oo
@MathewsMANDUTU-lh6oo 24 күн бұрын
Awa nzeru alibe akutitayisa nthawi dziko muno, Amalawi tisungilanji ameneyu
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 25 күн бұрын
Eti mbuzi zawanthu zina mkumaombera mmanja zopeperazo
@EdwardBarnaba
@EdwardBarnaba 21 күн бұрын
Ma judge kapena ma court amatha ntchito yawo bwezi suli president wathu
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m 25 күн бұрын
Iwe ndye umayakhula zopanda pake bwanj chisilu iwe ukuykila kumbuyo nyasi bwanj
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 25 күн бұрын
Anthu mukuombera manja zitizo
@user-xd6hq1pp4d
@user-xd6hq1pp4d 24 күн бұрын
Ndinu mbava zazikulu
@MavutoNgoma-kk6lq
@MavutoNgoma-kk6lq 25 күн бұрын
Uyo ndi garu yamunthu chakwera
@StevenFombe
@StevenFombe 25 күн бұрын
Azimai omvetsa cisoni
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 25 күн бұрын
Muli ubwino wanji mmalawi kodi nkhumba
@HalordBandah
@HalordBandah 24 күн бұрын
Mmm anaziyamba ndi iyeyu
@user-cp7hu6xu8h
@user-cp7hu6xu8h 24 күн бұрын
Izizi dziko la malawi siringatukuke chakwera ndiwakuba nayeso wazidabwa
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 25 күн бұрын
Aaaa chidwi chothetsa katangale chili kuti Popeza mukuba ndinuyo!!!apule bodzatu musiye please
@storytambala6088
@storytambala6088 25 күн бұрын
Tsopano, ngati ndichoncho, iweyo dziko lako bwanji silikuwaletsa anthu aku America kulowa muno bwanji?
@maxwellmajawa6091
@maxwellmajawa6091 21 күн бұрын
U could have used english to send the massage clear to the west
@StevenFombe
@StevenFombe 25 күн бұрын
Azunguwo sakumva
@duncainjimmy
@duncainjimmy 25 күн бұрын
Ku Malawi kulichidwi chofuna kuthetsa chilungamo pansi pa ulamuliro wa a Chakwera
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 25 күн бұрын
Tikupempheni ngati mukufuna kuti tv yanu ikondedwe mudzisankha mawu pofuna kunena muwona ikulamosachedwa wosamachita kuwonetseratu mbali yomwe muli .(eg zomwe awerenga lero apule .) Pezani mawu ena abwino kuti business yanu ikule mofulumila .
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 25 күн бұрын
Makhoti athu ndi a MCP ndi achipani,makhoti athu ndiwokuba
@isaaczuze
@isaaczuze 25 күн бұрын
Uyu ndiye ndichisilu mwa zisilu zonse pa ziko lapansi .....mbuzi yeniyeni ....munthu okuba ngati ameneyi angamayankhula zopusa ngati zimenezi .....mbuzi yeniyeni
@user-ms2dn7hh4d
@user-ms2dn7hh4d 24 күн бұрын
Awa zeru alibe aaa
@oscarnamirecah5386
@oscarnamirecah5386 25 күн бұрын
Malawi dziko lomvetsa chisoni chifukwa chabodza
@StevenFombe
@StevenFombe 25 күн бұрын
Ask America Biden that question next it's yuo under pressure
@storytambala6088
@storytambala6088 25 күн бұрын
Kodi kalata imeneyi, wamulembera fisi ameneyu ndindani?
@user-kd8ce8iw1k
@user-kd8ce8iw1k 25 күн бұрын
Uyuso akanamulesa ku America zikanakhala bwino
@PiusChawinga
@PiusChawinga 25 күн бұрын
Mabigidi inu
@thomchiphwanya3451
@thomchiphwanya3451 25 күн бұрын
Bwana lankhulani chilungamo musamanamize anthuyi Kodi adamanga Malita uja amkammangiranji paja ?
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d 25 күн бұрын
Chakwera kutumbu kwako wamva America ikunama mesa ukungokhalira kuba
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 25 күн бұрын
America no 1 ku Africa kunu mumadama ndi America chifukwa anakuzindikirani kuti ndinu akatangale. Alakwisa kulesa anthu 4 okha koma akanalesa nose muzikhala kumalawi komweko. Nose atsogoleri akanakupanga chimozimozi.
@StevenFombe
@StevenFombe 25 күн бұрын
Time will judge you sir
@user-xo2hi3vu8k
@user-xo2hi3vu8k 25 күн бұрын
Ndidzapezaso kt pulezident ngt uyu
@user-ru4px8os2v
@user-ru4px8os2v 25 күн бұрын
U.S.A. sikunama akulu inu dzelu mulibe ayi olo pang'ono takutopela chakwela
@victorauwana7258
@victorauwana7258 22 күн бұрын
Opusa uyu
@user-vc8ko3yc6y
@user-vc8ko3yc6y 21 күн бұрын
Mbuz ya munthu imenei palibe chamzelu chomwe angaonene fisi uyu
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 24 күн бұрын
Be honest, Mr president you have to speak in English speech. So that America and everyone to understand clearly
@arnoldkamanga1335
@arnoldkamanga1335 24 күн бұрын
😂😂Akuopa kuti America itha kumumva
@davidjames9711
@davidjames9711 22 күн бұрын
Awa ndi ochimwitsa
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 25 күн бұрын
Sir nthawi yanu yatha mudzakhumudwa
@isaaczuze
@isaaczuze 25 күн бұрын
Achakwera amaganiza bwanji akuona ngati as kulamulila mbuli kapena .....
@KennedyJames-ve7kp
@KennedyJames-ve7kp 25 күн бұрын
Wayamba campaign tsopano,
@harrymicah6140
@harrymicah6140 22 күн бұрын
Aziyakhura English azunguwo azinva nawo😂😂😂
@hardworkkayuza6353
@hardworkkayuza6353 25 күн бұрын
Rest in peace my bundle
@WakuMalawi
@WakuMalawi 25 күн бұрын
Zimandipangitsa kulira kuti Purezidenti wanga akunena Kulima ndi momwe mumatukula Dziko. Nanga bwanji maphunziro, Engineering ndi Technology ...?
@brightjawado9367
@brightjawado9367 25 күн бұрын
😂😂😂😂 koma mbuzi iyi
@SullyBartsony
@SullyBartsony 25 күн бұрын
Kuyikira kumbuyo mbava
@user-pc5ws7sv4r
@user-pc5ws7sv4r 25 күн бұрын
Kuba anthu inu makape
@user-xy4hq6sx7v
@user-xy4hq6sx7v 25 күн бұрын
Wakuba amayikila kumbuyo wakuba mzake
@StevenFombe
@StevenFombe 25 күн бұрын
Waonekera malonda okuba
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 25 күн бұрын
Udziyakhula English not chichewa unye uwone
@jamesgama5489
@jamesgama5489 25 күн бұрын
Kodi akuwerenga ndakatulo?
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 25 күн бұрын
Zowelenga zake zimenezo American sinalakwitse, chakwala ndisilu
@WysonMpatama-cv1mc
@WysonMpatama-cv1mc 25 күн бұрын
Ndie iweyo chakwera wamanga ndani pa nkhani ya kathangale mbuzi ya presdent ya dziko la malawi
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 25 күн бұрын
Bingu amkadandaulira dziko lino moteremuso
@samsonhavenoyayshonga2609
@samsonhavenoyayshonga2609 25 күн бұрын
Koma America imanena zoona,inu muukufuna kuti muziba , very bad
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 25 күн бұрын
Misonkho ya Amalawi kuiswanya
@user-pw2dq1yw4b
@user-pw2dq1yw4b 25 күн бұрын
Munthu waboza uyuu president vuto mukumaba kwambili a chakwela ndi nduna zanu
@thomchiphwanya3451
@thomchiphwanya3451 25 күн бұрын
Zabwino zake ziti bwana ?
@user-ov6jl8br7p
@user-ov6jl8br7p 25 күн бұрын
Uyuyu zamukulila gys akuyesetsa kudzikoza koma akudzipakaso
@Moses51
@Moses51 25 күн бұрын
Galu ameneyo
Eli Njuchi - Tempolale Visualiser
4:23
Eli Njuchi
Рет қаралды 1,3 МЛН
I PEELED OFF THE CARDBOARD WATERMELON!#asmr
00:56
HAYATAKU はやたく
Рет қаралды 26 МЛН
Мы играли всей семьей
00:27
Даша Боровик
Рет қаралды 3,8 МЛН
ПЕЙ МОЛОКО КАК ФОКУСНИК
00:37
Masomka
Рет қаралды 4,5 МЛН
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
INE NDI BON KALINDO MWANA OWOPYA KWAMBIRI/13 May 2024
14:14
NSOKHANO WA UDF KU BLANTYRE 🙌🙌🙌🙌
14:30
HOT 265
Рет қаралды 15 М.
Andrew Azzopardi on RTK103 | 11 ta' Mejju 2024
2:56:43
Newsbook Malta
Рет қаралды 4,7 М.
I PEELED OFF THE CARDBOARD WATERMELON!#asmr
00:56
HAYATAKU はやたく
Рет қаралды 26 МЛН