M'busa Yasin kularika mwa mphavu pa maso pa Chakwera ndi anthu onse

  Рет қаралды 65,776

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

6 күн бұрын

Пікірлер: 215
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 5 күн бұрын
Mau amphambvu ndithu Mulungu apitilirebe kukhala nanu kukutetezerani komanso akulitse malire amoyo wanu abusa Amen
@user-hi2rh8ks3r
@user-hi2rh8ks3r Күн бұрын
Very good preacher.very good preaching for everyone
@TamandaWekha
@TamandaWekha 2 күн бұрын
Awawa amalalika okunva wanva osanvaso akhale mosanva momwemo. Powerful preaching
@MosesPhiri-q7x
@MosesPhiri-q7x Күн бұрын
Wow great preaching man of God ❤❤
@user-vn2mz7qd5i
@user-vn2mz7qd5i 2 күн бұрын
Uyu ukuyenera kukhala mlangizi wa a president on religious affairs l ❤ you Rev Yasin Gama
@DolicahGift
@DolicahGift Күн бұрын
Amen and amen Ambuye azikudaritsani abusa🙏💕🔥
@namasawaninkhoma3856
@namasawaninkhoma3856 5 күн бұрын
Zikomo Abusa Mau Achilimbikitso. To God be all the glory.
@davidngomaministry
@davidngomaministry 2 күн бұрын
Amen powerful message 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🔥🔥🔥
@CharlesFalakeza
@CharlesFalakeza 3 күн бұрын
Amen and amen Abusa uthenga wachilimbikitso Amen
@ernestjuniormbanga3370
@ernestjuniormbanga3370 5 күн бұрын
Powerful preaching
@marydaka3207
@marydaka3207 4 күн бұрын
Amen. Very powerful message!!
@vincentlamanmathebulamwana5697
@vincentlamanmathebulamwana5697 23 сағат бұрын
Mashallah 🙏 abusa,mau anu,nkhope yanu,thupi lanu likutipasa ma answers abwino,mulungu azikudalisani😢
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 4 күн бұрын
Very powerful preaching 👏 🙌 🙏
@benedictchiwaya3043
@benedictchiwaya3043 5 күн бұрын
May God bless you&protect you in all aspects. Chakwera must listen &change
@QueenKumbuyo
@QueenKumbuyo 8 сағат бұрын
Amen pastor 🙏
@MaryNgwira-s5z
@MaryNgwira-s5z 5 күн бұрын
Inu nda busa weniweni osati akupha wanthu ambuye akuze malile amoyo wanu ndi masithika ndi ulaliki wanu amen and amen
@immaculatechitsakamile252
@immaculatechitsakamile252 4 күн бұрын
Iiiih😂😂
@RachelNathan-yv5zc
@RachelNathan-yv5zc 5 күн бұрын
Ameni ameni ameeen . MULUNGU akudalitsen Abusa Amen
@Chifundoaustin
@Chifundoaustin 5 күн бұрын
Amen. Powerful massage
@Martha-m6e
@Martha-m6e 2 күн бұрын
Amen and Amen powerful 🙏 🙌 👏
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 5 күн бұрын
You are blessed sir. God continue to bless you
@MaryChihana-bm9jo
@MaryChihana-bm9jo 4 күн бұрын
Ambuye alemekezeke ,ndipo Mulungu apitilize kudalitsa ndikuchjitira chifundo Malawi AMEN.
@AkusankhaNkhoma
@AkusankhaNkhoma 19 сағат бұрын
God bless pastor yasin
@CosimassShyman
@CosimassShyman 5 күн бұрын
This is powerfully teaching that is affecting full life
@user-di4ry5pi1e
@user-di4ry5pi1e 4 күн бұрын
Amen powerful message ❤
@phillipmphanda2163
@phillipmphanda2163 4 күн бұрын
Mawu ogwila ntima ambuye adalitse mawu amenewa Amen 🙏
@NDHLOVULASTON
@NDHLOVULASTON 21 сағат бұрын
Powerful message
@reubenphiri4907
@reubenphiri4907 5 күн бұрын
2:08 Ambuye alemekezeke chifukwa cha uthenga umenewu. Ndikungoganizira kuti abusawa akanakhala ndi nthawi yokwanira, chachitatu chomwe Yobu anachichitabe modabwitsa tonse ndi chakuti, ngakhale anzake a mkulu ameneyi anamunyozanso kufikira kunena kuti analuza zonse chifukwa choti anachimwira Mulungu, koma iyeyu sanawamvere, koma analankhulabe zomutama Mulungu pa moyo wake. Yobu 13vs13-15
@reubenphiri4907
@reubenphiri4907 5 күн бұрын
Yobu 13 Vs 13-15
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 5 күн бұрын
A gama lalikirani amve a chakwera mau amvetsetse kuti mulungu ndiyankho nthawi zomse
@GeorgeKafaamveka
@GeorgeKafaamveka 4 күн бұрын
To I very sorry to those who didn't listen properly the preaching, it's not Chakwera, it was a general powerful preaching even to those in a opposition who chose not to attend the function. Those are real witches and thieves
@AlfredNazombe-me2ly
@AlfredNazombe-me2ly 5 күн бұрын
Ndiye mumuone kunkuyu ndizikhaleyo kkkkkk ngat akudabwatu afiti kkkkk mukanthidwa kuli Mwari kudenga just wait chakwela ngat akumva nkhutukumve yeniyeni Mulungu akupeleka uthenga tiyenazoni
@NoahChikweza-xn1fh
@NoahChikweza-xn1fh 5 күн бұрын
❤m'busa kulalikira Kwa m'busa Zake😂😂
@hughmankalonga3769
@hughmankalonga3769 5 күн бұрын
Galimoto yamafuta imathiritsanso mafuta
@monicamatambo6969
@monicamatambo6969 4 күн бұрын
Glory be to God. My faith is lifted up.
@EmilyKabaride
@EmilyKabaride 5 күн бұрын
Amen 🔥🔥🔥mwawuka amveka
@MaxwellChiwaya-tv7kn
@MaxwellChiwaya-tv7kn 5 күн бұрын
God bless you pastor Gamba
@user-js6xn9qj1r
@user-js6xn9qj1r 5 күн бұрын
Powerful man of God 🙏🙏 Amen
@MarkManyowa
@MarkManyowa 5 күн бұрын
You're our own Prof Lumumba In Malawi Love you
@user-uv3gm5bb8x
@user-uv3gm5bb8x 5 күн бұрын
0:42 Powerful massage Amen and Amen
@Patricia_Chisankha
@Patricia_Chisankha 4 күн бұрын
Amen Pastor!
@user-dz5go4dd8i
@user-dz5go4dd8i 5 күн бұрын
Great preaching
@Albertngwira-vy3th
@Albertngwira-vy3th 3 күн бұрын
Amen more wisdom
@user-qz1jm5nm6d
@user-qz1jm5nm6d 5 күн бұрын
Powerful massage 💪💪💪
@thokokankhunda7725
@thokokankhunda7725 5 күн бұрын
ulendo uno i give salute ...amen osati kumalalika za ma buckets
@FrankKambwani
@FrankKambwani 5 күн бұрын
Ufulu wanokha a mcp umenewu mwatiphera Chilima ndiye nkumati tilimu ufulu?
@evelynmakhaya2756
@evelynmakhaya2756 4 күн бұрын
powerful preaching
@fannyeric
@fannyeric 3 күн бұрын
So powerful 👏
@JMB804
@JMB804 5 күн бұрын
Amen pastor
@user-wt5mf5kv6u
@user-wt5mf5kv6u 3 күн бұрын
Amen Abusa wakumva wamva
@NellyMasakatira
@NellyMasakatira 3 күн бұрын
Amen abusa mau amphamvu.
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 5 күн бұрын
Amene koma asogoleli osaopa mulungu akumangobela a Malawi osauka kumangolemela amodzi modzi mulungu awayankhule mwapadela
@John-to8gl
@John-to8gl 4 күн бұрын
Amen abusa ulaliki wamphamvu ❤❤
@VicterKumanda
@VicterKumanda 2 күн бұрын
Amen ndizowonadi
@Sammy-vb1ed
@Sammy-vb1ed 3 күн бұрын
Amen abusa God bless you ❤❤❤❤.
@SallamDishan
@SallamDishan 4 күн бұрын
amen mawu achilimbikitso may God be with you
@BenGravelNkhoma-tw4vu
@BenGravelNkhoma-tw4vu 18 сағат бұрын
AMBUYE alemekezeke cifukwa cauthenga wabwino
@stelladolizyi
@stelladolizyi Күн бұрын
A yasin Gama kulalika mopanda mantha ngati akhalira mfuti
@BernardoHonorio-ir2io
@BernardoHonorio-ir2io 5 күн бұрын
Amén!!!
@GeniusLloyd
@GeniusLloyd 5 күн бұрын
Powerful words
@KingNgOma
@KingNgOma 5 күн бұрын
Chirungam mwayankhura abusa amen
@user-lc4ll8td5f
@user-lc4ll8td5f 4 күн бұрын
Always God news is powerful big up of God!!!
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 5 күн бұрын
Amen amen Mtumiki 🙏🙏🙏🙏🙏
@user-gm3cx2xn9o
@user-gm3cx2xn9o 5 күн бұрын
Tikamati uyuyu anabwera kuzatumikira anthu ku umzimu ❤❤❤ amen
@IbrahimPhiri-ky5jk
@IbrahimPhiri-ky5jk 5 күн бұрын
Mulungu akudalinseni chifukwa chachinthunji kulinga ndi dziko lamalawi komanso ndimiyoyo yamansiku ano yomwe tilikudunsamo 🙏🙏🙏
@GladysKapasula-x6w
@GladysKapasula-x6w 2 күн бұрын
Amene abusa mumtidaritsa
@JessicaManda-zm1ug
@JessicaManda-zm1ug 4 күн бұрын
Amen powerful
@AyandaJanga-fe7wp
@AyandaJanga-fe7wp 4 күн бұрын
Powerful man of God
@GetrudeKambwazira
@GetrudeKambwazira 3 күн бұрын
Wow powerful
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l 3 күн бұрын
Amen amen and amen
@PempheroAlufandika
@PempheroAlufandika 4 күн бұрын
Mbusa uyo aaaaa Ali ndi ndi mulungu wapepheratu mwa maso a tsogoleri
@user-yu9fe5nv1u
@user-yu9fe5nv1u 3 күн бұрын
Amen and amen 🙏
@spargomw
@spargomw 5 күн бұрын
Amen Abusa
@user-vm1pq3ks4g
@user-vm1pq3ks4g 4 күн бұрын
Amen and amen
@flourencejamu6455
@flourencejamu6455 5 күн бұрын
Amen Amen and Amen
@user-qu5cv9ex4j
@user-qu5cv9ex4j 5 күн бұрын
Amen and Amen 🙏
@user-ce4ee7fx2w
@user-ce4ee7fx2w 3 күн бұрын
Amen and Amen
@BakaliPhili-es3xj
@BakaliPhili-es3xj 8 сағат бұрын
Ulaliki uwu wandigwra mtima
@cathbertkadammanja3446
@cathbertkadammanja3446 4 күн бұрын
Yobu had one wife and David had many wives but the commonly recognized wives were 8 Bible limodzi lomwelo lomwe timati buku lopatulika la mawu a Mulungu. I wonder why many people run away from that uncircumcised truth. Indirectly a Yasini Gama akuti kukhala nd akazi oposela mmodzi ndi ntchimo zomwe zili zosemphana ndi zomwe limafotokoza buku lopatulika.
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv 4 күн бұрын
Mamvuto athu siwochokeka Kwa Mulungu ayi Koma ndiochita kupanga afisi ena Ake , Ati kuzilemeletsa okha nde must mpaka liti pepeza simufika angakhale 150 years muli Moyo , mukafika 100 years mwakhala Kona kuyika shugar mkamwa mwanumo osamumvayi kumangotuluka thofu ,mukankhanthidwayinu musiku lomaliza nde popeza simuopa hayi chabwino
@blessingmanda
@blessingmanda 4 күн бұрын
this was powerful
@corneliusthindwa
@corneliusthindwa 4 күн бұрын
nice paster
@hudycorex1893
@hudycorex1893 5 күн бұрын
Powerful!!!
@user-fe7fb3nw5h
@user-fe7fb3nw5h 5 күн бұрын
Emeni auzeni mopanda matha mulungu awa Kathe zed
@fikiremussa5961
@fikiremussa5961 2 күн бұрын
Mawu achilimbikitso. Ambuye adalitse mawu ake
@moureenmolesi
@moureenmolesi 3 күн бұрын
amen papa
@JowasiMasina-fy8ji
@JowasiMasina-fy8ji 4 күн бұрын
Mau amphavu wakuva wamva osamvaso sanave koma ambuye adalitse mau amene
@user-qh1dm1my3m
@user-qh1dm1my3m 4 күн бұрын
Amen
@moseskavalo3304
@moseskavalo3304 4 күн бұрын
Azikazi aYobu onsewo analikumenekowo in men's suits wo
@LizzieBanda-y8g
@LizzieBanda-y8g 4 күн бұрын
Amen n Amen
@JozyLuhanga
@JozyLuhanga 5 күн бұрын
Amen abus
@moureenmolesi
@moureenmolesi 3 күн бұрын
amen postar
@user-dt4tk1jq5z
@user-dt4tk1jq5z Күн бұрын
Zikomo kwambir Mulungu akudaliseni abusa
@user-sy6sy9lg2b
@user-sy6sy9lg2b 4 күн бұрын
Muwuzeni chakwela aside khupa anthu wosalakwa
@PatriciaMkwenda-xc4mh
@PatriciaMkwenda-xc4mh 5 күн бұрын
Amen amen
@ritchardchakuma5725
@ritchardchakuma5725 4 күн бұрын
Thanks baba ndimawu
@AlepharMakawa
@AlepharMakawa 4 күн бұрын
Abusa mulungu akudalitseni osati Ena woyipawo
@LytoneMwatibu-gk6il
@LytoneMwatibu-gk6il 3 күн бұрын
Alalikira bwino abusawa🙏
@meldervictor
@meldervictor 4 күн бұрын
Fine emen
@PeterGabriel-uh2lh
@PeterGabriel-uh2lh 5 күн бұрын
Amen ❤
@IsaacAlfredoinacioInacio
@IsaacAlfredoinacioInacio 5 күн бұрын
Amene abusa
@IsmaelBilal-lh1pi
@IsmaelBilal-lh1pi 5 күн бұрын
Masha Allah
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 4 күн бұрын
Kodi inuso abusa mwaganidza kudya nao ndalama dzamagazi 😢😢
МАМА И STANDOFF 2 😳 !FAKE GUN! #shorts
00:34
INNA SERG
Рет қаралды 4,9 МЛН
Wait for the last one! 👀
00:28
Josh Horton
Рет қаралды 156 МЛН
ОСКАР vs БАДАБУМЧИК БОЙ!  УВЕЗЛИ на СКОРОЙ!
13:45
Бадабумчик
Рет қаралды 4,3 МЛН
KWANUNKHA MWAZI KU MCP.
1:02:17
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 33 М.
Rev Alexander Kambiri preaching at Malawi Immigration Head Office -Lilongwe Malawi
19:34
ANG'ALULA MOSAIPA LERO PA 10 July 2024
27:53
HOT 265
Рет қаралды 17 М.
LUNTHA TV  | FAITH CONFERENCE ON CHOLERA RESPONSE |  08 MARCH 2023
44:51
Luntha TV official
Рет қаралды 11 М.
Rev Alexander Kambiri  kupeleka uthenga wachipepeso pa ifa ya Dr  Chilima
28:50
mabena Studio channel
Рет қаралды 21 М.
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
33:23
BON KALINDO LERO PA  11 JULY 2024 |
18:46
DZIWE TV
Рет қаралды 10 М.
ATUPERE MULUZI WAKONZEKA
19:21
HOT 265
Рет қаралды 7 М.
МАМА И STANDOFF 2 😳 !FAKE GUN! #shorts
00:34
INNA SERG
Рет қаралды 4,9 МЛН