MCP YAVOMELEZA KUTI DPP IWINA 2025

  Рет қаралды 42,622

Club Junta

Club Junta

Күн бұрын

Пікірлер: 249
@GeorgeTembo-v6i
@GeorgeTembo-v6i 3 ай бұрын
Apm my vote
@isaaczuze
@isaaczuze 3 ай бұрын
To me I will vote for Apm osati chakwera ongoziwa kuyankhula koma kupanga ayi .... Kodi kuyankhula English kuli ndi phindu lanji Kwa munthu wosauka
@isaaczuze
@isaaczuze 3 ай бұрын
Nchewa wanzelu uyu akunena zoona ....chakwera sanachite bwino pa zinthu zambili ......katangale wapita pasogolo kwambili ....mmalawi muno muli njala komanso anthu akupangidwa nkhanza kwambili ......chakwera atha kuchoka mosavuta chifukwa anthu ndiokwiya kwambili
@WestonRoben
@WestonRoben 17 күн бұрын
Ine odala saname adati amupha chilima tchakwera ndidawatuluka
@Austinyonah
@Austinyonah 3 ай бұрын
Dpp my vote
@StellaChimwalaKapalepale
@StellaChimwalaKapalepale 2 ай бұрын
MCP singawine anthu akuvutika kwambiri mmamizi ,komanso MCP ikungodziwa kugula oyimba Basi ndiye kuti oyimbawa adzavuter okha Basi
@CharlesMvunguti-vy6pn
@CharlesMvunguti-vy6pn 3 ай бұрын
Komanso mistake yaikulu ndi kipha vice wake
@samsonhavenoyayshonga2609
@samsonhavenoyayshonga2609 2 ай бұрын
Aliyense akuziwa kuti DPP ndiiimene ikulowa m'boma next year
@TravelodgeMalawi
@TravelodgeMalawi 19 күн бұрын
Ndipo ndizoona anthu awa awononga kwambiri ,Dziko labvunda mapeto ake lithapo ,toyeni tilikonde ..
@saidichirwa5456
@saidichirwa5456 3 ай бұрын
Aluza kale awo a Mcp zifukwa nzambiri.Chibwendo banda amalankhula zinthu zopusa ngati kuti akulankhula ndi ana ake koma chonsecho akulankhula ku ma millions aanthu .Amaona ngati kuti ife ndife opepela?Anthuwo akuyiwala kuti akhoza kumagulana okhaokha iwo otchuka koma sikuti zidzawapi dulila povota,ovota ndi ma million aanthu koma iwo akugulama a thu osakwa a ndi 30 ayi.Komaso adziwe kuti compaain ikayamba anthu ambiri adzathamangila kuti ndalowa mcp koma lilibodza,anthu ali after kukapezelakotu ma capita odzayambira ma business next year boma lenileni likadzayambika.voti zawo nzachinsisi chilungamo akuchidziwa anthuwo.uko ndalama zaphweka ndimkana kukuthamangila anthu
@shepherdkingston
@shepherdkingston 3 ай бұрын
DPP Boma tidye katatu patsiku chikagawa watikwana akapume
@emilynthite6545
@emilynthite6545 3 ай бұрын
Nyamatayo mulungu amudalitse osamango ikila kumbuyo zilizonse ayi anthu akuona pa graundi
@BrianNowa
@BrianNowa 15 күн бұрын
Utm my vote, mmphechepeche mwanjovu sapitamo kawiri, adakakhala Bingu alimoyo mkadavotera dpp koma apm aaaaa amagona pa mpando, DK my vote
@ambassadorsaul3980
@ambassadorsaul3980 3 ай бұрын
Mark my words MCP cant win against DPP and it will never win anyachula zedi
@Frederick-s4h
@Frederick-s4h 20 күн бұрын
Much more fire muthallka ndlkatundu pachitukuko amakwana anakoza mesiya wakumalawi apm going to parice dpp oooza my
@blessjare
@blessjare 25 күн бұрын
Kodi olo kubera mavoti ku LL ndi dowa ndimene idzawinitse mcp poti ntcheu, mchinji,kasungu,Salima ,mpoto yonse kummwera konse ndi kwa adad
@tasmania527
@tasmania527 8 күн бұрын
Kkkkkkkk. If wishes were horses beggers would ride. Zoona thinking kuti mpoto or Kasungu angavotere DPP? Are you crazy?
@Maxielyies
@Maxielyies 2 ай бұрын
Powerful advise ❤❤❤❤
@JogaJoseph
@JogaJoseph 3 ай бұрын
Chakwela ayende bwino akapume
@ChimwemweMathyola
@ChimwemweMathyola 22 күн бұрын
ndizoona MCP analonjeza zithu zomwe sanapange zimene akuziwa ndi kupha basi 2025 chawo kulibe
@juliussamson6212
@juliussamson6212 19 күн бұрын
MCP YATHA KOMASO TONSE AMALAWIAN TIKUFUNA MASHINI ASADZAGWIRE NTCHITO
@MatolasiReginaKasote
@MatolasiReginaKasote 16 күн бұрын
Ndakukonda walankhulawe muluza ndithu chanu kulibe next year
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n 3 ай бұрын
Dpp woyee
@AlexanderBilliat
@AlexanderBilliat 2 ай бұрын
Agulukunya amenewa apita Palibe zokubwezeraniso pampando
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 ай бұрын
Mcp ikudziwika kuti idzaluza ndichifukwa ikufuna kudzabela , koma sidzitheka chifukwa opposition nayo ikumenya nkhondo yapansi,mcp 2025 ikupita ku kasiya APM akubwerela
@JoãoChirwa-n3l
@JoãoChirwa-n3l 3 ай бұрын
Mcp singawine olo zitavuta moti chani❤
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 ай бұрын
DPP 2025❤
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 3 ай бұрын
Mcp yatha basi chikangawa Bagamoyo 💔💔💔💔
@EmmanuelFrancisco-t7s
@EmmanuelFrancisco-t7s 20 күн бұрын
Boma LA ifeachewa zativuta dele
@MebleNgulinga-hi6rg
@MebleNgulinga-hi6rg 3 ай бұрын
Mcp ili m'madzi Cause ambiri sitinaikonde ngakhare pachiyambi ambiri anapitako chifukwa cha SKC. Now SKC kulibe munamupha nde anthu mmmmmmm nkwiyo ngosayamba now hope of Malawians ili mwa Dpp basi
@IgnatiousFote
@IgnatiousFote 20 күн бұрын
nduna za mcp nd president wawo mbuzi zokhazokha
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 3 ай бұрын
Aaaa chilungamo MCP yalephela KUYENDETSA DZIKO LA MALAWI
@BrianNowa
@BrianNowa 15 күн бұрын
UTM is a democratic party in Malawi and sichipani cha banja, Kabambe my vote, enawa adzikagona kumkeka mkumaotha dzuwa
@chrischelewani
@chrischelewani 20 күн бұрын
Dpp and MCP 🙌not again Amalawi tisamaone pa mwamba pokha tiyeni tiwonenso mkati Abwino mu Dpp ndi ochepa the rest ndi oipa omwe aja 😢😢
@TomasDzifoole
@TomasDzifoole 3 ай бұрын
Achoke Mr chikangawa.
@DicksonFranciscoLikongwe
@DicksonFranciscoLikongwe 13 күн бұрын
Its true akupelekeza anza0 chao nchibwana bas
@officechapota3301
@officechapota3301 3 ай бұрын
Dpp
@MonyaSaka
@MonyaSaka 14 күн бұрын
APM my vote,afune asafune ndi wam'boma 2025.DPP Woyeeeeee
@AnthonyKalosi
@AnthonyKalosi 18 күн бұрын
Yapita bomayi osakaika zinthu zawavuta a MCP
@juliussamson6212
@juliussamson6212 5 күн бұрын
NOSE MUNALANDULA NDALAMA KWA CHAKWERA ZACHINYENGO BWERANI POYERA ULULANI CHIFUKWA NDI NDALAMA ZOCHOKERA KWA SATANA CHAKWERA IYE CHAKWERA AMALAMBILA SATANA DZIWANI NGATI MUNACHITSAPO PA NDALAMA NDIKUGULILA KALIKOSE MULUNGU ANAKUYIKANI KUDZANJA LAMAZERE KUTI NDINU WAKUMOTO KOMA MUKAWURYRA MWALAPA KWA MULUNGU NGATI MUFUNA KUTI ASAKUDZIWENI UZANI WA BAKILI MULUZI IFE AMALAWIAN TIKAVA TIMUPEPHA MULUNGU KUTI AKUKHULULUKILENI CHIFUKWA MWAWULULU INU MAZIBU INU MAMFUMU NDI NOSE MUNALANDILA NDALAMA ZARYWAZI CHONDE KUMANANI NDI AMBUSA AMENE AMAWOPA MULUNGU AKUPEPHERERENI MUSAMUTENGE CHAKWERA NGATI MULUNGU AI MUKUYIWONA NKHOPE YA CHAKWERA PANOPA NGATI AKULILA MULUNGU WAYAMBA KUTCHOLA SADWANA ZA CHAKWERA AKAYIMA NGATI ACHITA NDEWO MANJA SAKUTAKA SUKA MUMUWONA WAYAMBA KULUMALA MIZUMU YAWANTHU 9 IKUGWILA NTCHITO KKKKK IWEYO UWINA MAZUZO CHAKWERA KUPHA ANTHU MULUNGU NGATI NKHUKU AHEE KAYA UZIWINA
@JeffreyKalepa
@JeffreyKalepa 2 ай бұрын
Palibenso njila imene MCP ingapange kumusintha munthu wakumudzi, akuluakuluwa saakuzana chilungamo
@JoshBranquinho
@JoshBranquinho 2 ай бұрын
😂KKKk mwatero
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 3 ай бұрын
Chikangawa Ali mumadzi sangamake bola kwa Apm ndi dolo
@MariamJack-df9xd
@MariamJack-df9xd 3 ай бұрын
Bravo uku nde kuyankhula moopa Mulungu uku bambo inu mmapempheladi
@SymonPaul-s8h
@SymonPaul-s8h 3 ай бұрын
Mcp sizalowanso boma ay
@JaneBanda-ht4ve
@JaneBanda-ht4ve 7 күн бұрын
Afiti inu mufuna DPP izizadya ma albino eti, mukhaula ndi mabodza anuwo, akulankhuyo akuchita kuonekelatu kuti ndi wa opposition. Palibe chipani chimene chingachotse MCP, Chakwera mpaka 2030 woooo
@Frederick-s4h
@Frederick-s4h 20 күн бұрын
Kkkkkk rapita boma ku dpp bas muthallka ndlkatundu pachitukuko amakwana anakoza mesiya wakumalawi apm ndlkatundu
@Dellingsmunthali
@Dellingsmunthali 3 ай бұрын
Koma bwa awa mulungu aziwa dalisa ndimunthu onena chilungamo ndipo ndimafuna nditawaziwa"awa ndamene akufunika kumakhara pafupi ndi president kut awiwauza zoona
@StenalaDuncan
@StenalaDuncan 21 күн бұрын
Ndipo asakaike ❤❤❤❤
@juliussamson6212
@juliussamson6212 5 күн бұрын
IZIPITA KU DASI BIN MCP ILIBE NTCHITO ONSE OIPA KWAMBILI AND MUNTHU UKALOWA MCP DZIWA KUTI NDIWE OTEMBELELEDWA KWA MULUNGU AMEN
@willy8384
@willy8384 3 ай бұрын
Wayankhula chilungamo ameneyi, boma la DPP 2025 ikulowa afune asafune.
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 3 ай бұрын
Wayankhula bwino, koma waiwala chinthu chimodzi, UMBAVA BOMA LANULI
@TiongeGondwe-g5l
@TiongeGondwe-g5l 17 күн бұрын
Akungoxilimbitsa koma mmmm mcp mpaulendo
@FelixMboma-o5v
@FelixMboma-o5v 17 күн бұрын
Zoona mcp sizibwino penyan nditu..😂
@CosmasTchuwa-bk3ck
@CosmasTchuwa-bk3ck 3 ай бұрын
Mcp mbola tikufuna DPP
@FavouredgrivinChikanda
@FavouredgrivinChikanda 22 күн бұрын
Aaaaa BOMA lapita Ili DPP 2025 Bomaaaaaa 🔥🔥🔥
@WilfordRobben-s8v
@WilfordRobben-s8v 20 күн бұрын
Oyankhulayu, wayankhula zoona omwe akuwonga Chipani cha MCP ndi Anthu atatu basi. Ndiwo akulamulila Dziko osat President, Chifukwa president yo sakudziwa Chilichonse. Achikulile awa ndi DIEHARDER wa MCP, Koma mwachedwa pano Anthu akwiya ndi mmene mwanenelamu. Nanga president kumamvela Anthu chifukwa sakhala pansi, chifukwa ali obalalika
@user-qq6xs5tm7z
@user-qq6xs5tm7z 20 күн бұрын
APM ..my vote
@Vwalavwata
@Vwalavwata 3 ай бұрын
Lazaro uyuyu achoka ndithu mungomuona chikhopecho chuonekerathu kuti ndichigawenga
@TobbiePahuwa
@TobbiePahuwa 17 күн бұрын
Chikangawa watha and gone
@AlabAjuli
@AlabAjuli 18 күн бұрын
😂😂😂😂 zoonad zake
@isaaczuze
@isaaczuze 19 күн бұрын
My vote is for Apm osati mbuzi ya munthu iyi akuti chakwera ..... Munthu oowono ga kwambili
@EMMANUELJsefasi
@EMMANUELJsefasi 22 күн бұрын
Iyi yapitadi linens mosaphatira wapakaliyala. Waphetemula beru
@LenzojChileka
@LenzojChileka 3 ай бұрын
DPP boma
@PembereJames-rn6bx
@PembereJames-rn6bx 3 ай бұрын
Dpp he come back again
@StanleyChabwera
@StanleyChabwera 10 күн бұрын
Zakanika chakwela kulephela kukonza malawi.... Malawi ndi muthu osafuna zambiri.....zithu za moyo wasikundisiku. Kungozintchipitsa... sugar both oil. Zipangizo za ulimi. Zipangizo zomanga manga....basi Malawi very simple
@MacEmmanuelMkhamula-sy1ff
@MacEmmanuelMkhamula-sy1ff 3 ай бұрын
Arudzakare chakwera
@mayenjefumu
@mayenjefumu 3 ай бұрын
Dpp boma basi olo mufune musafune tatenga boma
@BlessingsAyamie-n2m
@BlessingsAyamie-n2m 21 күн бұрын
Boma ili lalephela ndizomwe zikuonetsa kt MCP sidawina anatengela mphanvu bomali😮
@Alomwe
@Alomwe 2 ай бұрын
MCP lost game due power hungry individuals.
@RosinaPatel
@RosinaPatel 21 күн бұрын
Boma loipa kwambiri ndipo Ine sindikulifuna ..Boma lozunza
@mikekaliza-bw4yg
@mikekaliza-bw4yg 5 күн бұрын
ya ndizowona Dpp boma lapita ndithu vuto anthu mcp amatitenga ngati tikanali opusabe saziwa kuti ndife olimba ntima koma timati awona ngati Dpp yatituma
@VeronicaTime-jn7fp
@VeronicaTime-jn7fp 3 күн бұрын
Sakuwina mulungu wandionesela ine kucha kwa lelo
@MakhiMakhi-w6t
@MakhiMakhi-w6t 3 ай бұрын
Mungawanga muchisi chakwela awinaso mosakaika 🎉🎉🎉
@Staphelsavimbindhlovu
@Staphelsavimbindhlovu 21 күн бұрын
Dpp woyeeee ❤❤❤❤apheduka okha a mcp😂😂😂😂😂
@EnockBeston
@EnockBeston 13 күн бұрын
Auzen brother
@SoldieNdovie
@SoldieNdovie 20 күн бұрын
Bora Dpp yomweyo chifukwa vithu zadula kwambiri
@PetroMatias
@PetroMatias 3 ай бұрын
Dpp 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@BenjaminKapale-k1f
@BenjaminKapale-k1f 3 ай бұрын
alibe ntchito azipita
@Hambalisphiri
@Hambalisphiri 18 күн бұрын
Izo nde zoona mcp is cruel siyikudziwa zimene ikufuna kupanga in 5 years time palibe chimene angalodze kuba ndi nkhanza basi
@Short1212-ny4ng
@Short1212-ny4ng 3 ай бұрын
Chilingamo ngati sitikhoxa atilandadi
@JasonMailos
@JasonMailos 3 ай бұрын
Zosatheka MCP kuwina never ever
@LichapaJeffuly
@LichapaJeffuly 13 күн бұрын
Nthawi yomwe mudagwetsa ndege ija niyomwe MCP inapereka vote Kwa DPP tsano yapa kangoyalulani mudzipita kwanu kokaliyeka mkapumule vote mulijeee
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 2 ай бұрын
Kkkkkkk koma Pali kusinthatso boma kkkkkkk ngati umamva maloto ndiomwewo
@LuckyKalengo
@LuckyKalengo 17 күн бұрын
It's true
@GenitojosebingalaJosebingala
@GenitojosebingalaJosebingala 3 ай бұрын
Awuze chakwela atule pasinudindowo DPP idawina 2022 Apa ikungodikila palizati bass
@MandalaChaona
@MandalaChaona 25 күн бұрын
Ngakhale MCP ikudalira Smartmatic Koma sidzapindula nayo kanthu 🤪🤪🤪Ng'oooooooo . Zilope zikukudikirani kuchikangawa
@HawadiLuciano
@HawadiLuciano 23 күн бұрын
Ndizoona amenewo ndiye okonda chipani osachita dyela kumangonena bodza dyela ndilimene laononga chipani Cha mcp😮
@BurnertJomboliNyirenda
@BurnertJomboliNyirenda 2 ай бұрын
Akunena nzoona Chakwera akumunamiza kwambili nçhifukwa chake akupitiliza kukhala opusa amalawi Ife sitonse ndizitsilu kapena akhungu penanso oiwala msanga pachifukwa ichi ndizoona bomali likuchoka mumanja mwa achikangawa kupita kwa enaa dzikomo kwambili Ine BURNET Jomboli Nyirenda kuno ku karonga airport
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 3 ай бұрын
Chikangawa azipita watikwana
@DoniAliha
@DoniAliha 20 күн бұрын
Dpp woyeeeeee adad womwe kuti wawawawa
@SintilawuKhembo
@SintilawuKhembo 17 күн бұрын
palib chao ai
@MonicaMkandawire-s2o
@MonicaMkandawire-s2o 3 күн бұрын
Tiwone zina MCP DPP tatopa nawo
@FrancisChikazunga
@FrancisChikazunga Ай бұрын
Ndizoona mcp 2025 kulibe
@celesteRebelo-e5y
@celesteRebelo-e5y 3 ай бұрын
Zoona zokha zokha
@edwinchipikamtambo6686
@edwinchipikamtambo6686 3 ай бұрын
not today mbalame yanuyi ikalamulira kwanuko
@OssmanAbubaker-v7t
@OssmanAbubaker-v7t 2 ай бұрын
Chilungamo Osaopa osafooka osatopa power
@ImmanuelndagomaKondowe-n1v
@ImmanuelndagomaKondowe-n1v 2 ай бұрын
Boma linapita kale ku DPP ili,tikangovotera poti ndi lamuro kutero
@loneymagwera915
@loneymagwera915 3 ай бұрын
Lapita ili chikangawa
@DanielJuwawo-s5n
@DanielJuwawo-s5n 2 ай бұрын
Uyu akutha kuona mmene akuendetsera dzikori
@MayamikoMlenga
@MayamikoMlenga 19 күн бұрын
Chipanichi achulutsa zibwana kwambiri coz mudziko muno zinthu zikuvuta zitukuko akupangira ma banja awo
@JoelTchuma-g3s
@JoelTchuma-g3s 14 күн бұрын
MCP IDANAMA CHOTERO MUNTHU WANZERU SANGATSATIRE CHINTHU CHOMWE CHIKUMUPSINJA,KOMANSO CHIKUONETSA DZIKO NKHANZA ZOOPOSA ZA NYENGO YA ULAMULIRO WA MALEMU DR HKBANDA.KATUNDU YENSENGOKWERA MITENGO eg FERTERIZER HHHHHHH!!.
@GodfreyChauluka
@GodfreyChauluka 2 ай бұрын
Ine ndilibe mau ndi mcp eeee moto wokha wokha
Quando eu quero Sushi (sem desperdiçar) 🍣
00:26
Los Wagners
Рет қаралды 15 МЛН
The 100 year war on Palestine w/Rashid Khalidi | The Chris Hedges Report
1:01:11
The Real News Network
Рет қаралды 347 М.
Chombo chaonongeka kumwamba ndipo anthu awiri asowa mtengo ogwira
12:30
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 46 М.