OLANDIDWA PASSPORT AKUPITA KU TANZANIA-🤔🤔🙌🙌😀

  Рет қаралды 5,577

HOT 265

HOT 265

23 күн бұрын

Пікірлер: 25
@LecknardPhiri
@LecknardPhiri 20 күн бұрын
those who love DC the first president of poor people in malawi the one n only let's gather here ❤❤
@George-zd5le
@George-zd5le 20 күн бұрын
Awiria ndimbava zone ndiye zikubisana . Nawaz ma judges akumalawi aaaaa mbava zokha zokha
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 20 күн бұрын
Monga ine ndimazidziwa kwambili, kuti chilima, chakwela alilimodzi mukhani yazabubazi
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 20 күн бұрын
Amagwira ntchito kumene inu munali kuti wangotumidwa apapa koma ntchito adalandidwa nde azintumwa okha popanda chiweruzo akupasa koyamba chimusisile ntchito yo ndi pamene mungachidziwe kuti kunja kuno kuli Mulungu ndipo amaona zonse komanso amamasula SKC 2025 BOMA ❤❤❤❤
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 19 күн бұрын
Uzamuvotela wekhatu wathu APM
@AbuOsman-ts6ef
@AbuOsman-ts6ef 20 күн бұрын
Kungoti misala ya zaza mutu mwachakwera
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 20 күн бұрын
Good Message Mr Bon kalindo ❤
@uchizJoelMumba
@uchizJoelMumba 20 күн бұрын
Mbuzi yamunthu boni kalindo galu wa dpp mukhaula mpaka 2030 woooo!!!!
@IsaacBlazio-je4tf
@IsaacBlazio-je4tf 20 күн бұрын
Kumalawi kulibe ma court omwe amaziwa malamulo adziko chifukwa nkhani zimstenga nthawi kuti zithe
@homeremedys3748
@homeremedys3748 20 күн бұрын
Masankho ayandikila that's why ayamba kumuuza chilima
@TonicBeza
@TonicBeza 20 күн бұрын
Mbuli iwe
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 20 күн бұрын
Kumalawi tili ndi atsogoleri amene amazitenga ngati ndiwo wokha azeru bwanji makhoti amulese chilima yo kuti asapite akadali pamulando. Komoso asusa bwanji apite ku khoti kukatenga chileso kuti vice akadali pamulando
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 20 күн бұрын
Makhothi Kulibe kumalawi
@johnkambala692
@johnkambala692 20 күн бұрын
Opanda mzeru awa
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f 20 күн бұрын
Oopya samagona ku selo
@user-dy4gc2hr5e
@user-dy4gc2hr5e 18 күн бұрын
Ulemu wako bon kalindo munthu wankulu samaopa munthu timafuna anthu ngati amenewa olimba mtima
@HappyJosephy
@HappyJosephy 20 күн бұрын
Opusazedi iwe
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f 20 күн бұрын
Ndiye vuto ndichani
@henryhenry6632
@henryhenry6632 20 күн бұрын
Chimphwala cha munthu
@godrickmapepu2754
@godrickmapepu2754 20 күн бұрын
Mwafatsa kuno ma cadet eti. Mitu yanu mwava. Chilima ndi mbava anaba chani?. Kodi inuyo simunayambe mwanamizilidwa eti. Ifeyo tili pa mbuyo pa Chilimayo or mutamuyipitsa bwanji. Mbuzi
@ZelinaKisswell
@ZelinaKisswell 19 күн бұрын
Sikuti anthu anyasidwa kumutuma chilima ai kmano mmene amampangira treat mmisonkhan kungokhala ngt chikwangwani , kumudzutsa president ndi kwanduna yet vice alipompo mesa ankati anamulanda maudindo alibe mphavu nde lero lokha kwatan akapange zimenez since 2022 a ple amayenda okha mmaiko onse omwe akhala akupita , ine ndi fan wa chilima apopo sanaganize bho skc akanakana amutola kwambiri
@user-rf4br1fv2z
@user-rf4br1fv2z 20 күн бұрын
Utsongolera anthu zithu zoipa anthu amati chilima sakungwira ntchito pano amutumiza kunja walakwaso mwati timafuna chiyani
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 20 күн бұрын
Koma asamatinamize
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 20 күн бұрын
Timafuna ndondomeko abwere so poyera kuti chilima milandu yatha asamatinamize..
路飞关冰箱怎么关不上#海贼王 #路飞
00:12
路飞与唐舞桐
Рет қаралды 3,6 МЛН
Surprise Gifts #couplegoals
00:21
Jay & Sharon
Рет қаралды 30 МЛН
Trágico final :(
01:00
Juan De Dios Pantoja
Рет қаралды 19 МЛН
Budiriro tragedy : Driver weKombi akatsikwa neKombi yake
39:30
Destiny TV
Рет қаралды 54 М.
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
NSOKHANO WA UDF KU BLANTYRE 🙌🙌🙌🙌
14:30
HOT 265
Рет қаралды 15 М.
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
Mai Mutsvangwa finally speaks
6:54
Rory Studios News
Рет қаралды 67 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
INE NDI BON KALINDO MWANA OWOPYA KWAMBIRI/13 May 2024
14:14
路飞关冰箱怎么关不上#海贼王 #路飞
00:12
路飞与唐舞桐
Рет қаралды 3,6 МЛН