PP YAZUZULA MCP26 April 2024

  Рет қаралды 15,954

HOT 265

HOT 265

20 күн бұрын

Пікірлер: 28
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 19 күн бұрын
Ngati saulula zomwe agwizana ku Israel, ndiye bwanji amaitana atola nkhani? Za ziii!
@user-tg1ms3us6k
@user-tg1ms3us6k 18 күн бұрын
Ashilungamo amakhala opondelezedwa bass asule MN akwalakwila kukamba shilungamo
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 18 күн бұрын
Nyanja yagulitsidwa ku Tanzania now anthuno kumalawikuno tikugulisidwanso ku Israel ndi MCP😢😢😢😢
@FefieTenisha-du7ge
@FefieTenisha-du7ge 18 күн бұрын
Everything that is hidden carries some air of being sinister...
@abdulrafiquekalembo469
@abdulrafiquekalembo469 18 күн бұрын
Iwe mzimayi joyce ndiwe osokoneza.unawatengera a Malawi ku ulamuliro wa nkhanza.
@user-yg9em7qq2v
@user-yg9em7qq2v 18 күн бұрын
Mama nthawi ya Amai idatha,,,,,inu or nokha azkhare Zaka ziwiri mongogwirizira mwaruza kkkkkk musiyeni Peter or atupeli alamure Malawi
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 18 күн бұрын
Joyce Banda asamadandaule, coz iyeyo ndiamene amatilozera kwa chakwera kumat ndi m'busa ndie lero astitopese ife tili ndi maso ndipo tikuona zonse zikuchitika.
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 18 күн бұрын
Chabwino sindikuchiona ulamuliro wa chakwera
@mchipengule
@mchipengule 18 күн бұрын
A Joyce Banda mwakalamba inuuuu. Punulani a Mai.
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w 18 күн бұрын
I want my Job ,as the president promised me ,1000 jobs😂😂
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 18 күн бұрын
Ukuyitha hot 265
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 18 күн бұрын
Kodi chakwera ndi nkhumba chadzelu ndi chiti
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 18 күн бұрын
Makape bwanji mukubisa zomwe zili mu mgwilizano wanu ndi Israeli? Kapana mukuwagulitsa anthuwa etill?😢😢😢😢😢😢
@user-dy4gc2hr5e
@user-dy4gc2hr5e 18 күн бұрын
Chimene akubisira ndichani
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 18 күн бұрын
Amukazaona mtsogoleri akuti zina tinena koma zina ayi ndizachisisi muziwe kuti musogoleri yo alibe zeru akuziwa kuti zachisisizo ndizopanda pake anthu azeru akana ndichifukwa akunena kuti ndizazisisi paja mukuziwa kuti tili ndi atsogoleri a mbuli zaku Israeli zo sakuwuzani
@mchipengule
@mchipengule 18 күн бұрын
Akayambe zaulimi ku Mallawi kuno muwapatsa chiyani ku Malawi kuno anyamatawo 😂😂😂
@user-tb6yh1kx3o
@user-tb6yh1kx3o 17 күн бұрын
Kodi mayi Inu mesa chipani chanu munachigulitsa ku MCP inu
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 19 күн бұрын
Boma lalephera apa, chifukwa akanayamba ntchito za ulimi kokuno ku Malawi kuti achinyamatawa adzigwila ntchito konkuno.
@gabrielben-vj2eb
@gabrielben-vj2eb 19 күн бұрын
Wanzelu sanganyamukile dala waku Israel
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z 19 күн бұрын
NO PAIN NO GAIN MALAW PAMALONDA MALAW 4SALE
@HanishaissahKagansa
@HanishaissahKagansa 19 күн бұрын
One million jobs 😢😢😢
@KimChisola-gm7yw
@KimChisola-gm7yw 19 күн бұрын
Zomwe akuti saululazo ndiye kuti ndi ukapolo umenewo,ngati ndizabwino bwanji sakuulula
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 18 күн бұрын
Ndipo muli Zoopsa mumgwirizanowo
@malawigeneralguide1646
@malawigeneralguide1646 19 күн бұрын
Why not saying the agreement with Israel.....? We got friends and families there😢 Eeeeeish this is hectic 💔
@mchipengule
@mchipengule 18 күн бұрын
A Malawi tiyeni tiphuzile kuyamika 😂😂😂😂
@Austinnkhula
@Austinnkhula 18 күн бұрын
Chomwe ungayamikile apa ndichani? Chamzelu apa ndicha
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 18 күн бұрын
Mayi Joyce banda akudandaula chani poti ali mu mcp mo paja musayiwale kuti mcp imatenga nyasi. Za suleman ndizovesa chisoni ngati akuti sangaitanidwe kumukumano poti ali ndichileso nanga chilima wapita bwanji ku Tanzania pamene ali ndichileso. Kodi boma la mcp mitu yikuyenda koma mwina wose ndiopenga akupanga zinthu mopeoera wina kumulesa wina ayi useless people
Assista na íntegra o Balanço Geral  15/05/2024
MIRAMAR
Рет қаралды 1,1 М.
маленький брат прыгает в бассейн
00:15
GL Show Russian
Рет қаралды 3,8 МЛН
Зу-зу Күлпәш. Стоп. (1-бөлім)
52:33
ASTANATV Movie
Рет қаралды 813 М.
Glow Stick Secret (part 2) 😱 #shorts
00:33
Mr DegrEE
Рет қаралды 34 МЛН
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 13 М.
CRUISE 5 WITH LILIAN ESTELLA PATEL PART 2
1:03:38
Zodiak Malawi
Рет қаралды 6 М.
Times Exclusive featuring Richard Chimwendo Banda - 27 April 2024
59:44
Times 360 Malawi
Рет қаралды 25 М.
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 17 М.
Bingu from Perth & Asia Part 8 - Press Questions 1
13:21
Nkhani Digest
Рет қаралды 177 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
маленький брат прыгает в бассейн
00:15
GL Show Russian
Рет қаралды 3,8 МЛН