RICHARD MPHEPO ICHI NDE CHILUNGAMO BASI KUDZUDZULA APULE ASAMANAMIZE ANTHU KUTI AMAPEPHELA

  Рет қаралды 17,770

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 83
@MussaHassani-zg1hm
@MussaHassani-zg1hm 23 күн бұрын
Koma mkuluyu amadziwa kunyangula thanks so much
@GodfreChayamba
@GodfreChayamba 20 күн бұрын
Bwana lichard mphepo mulungu azikudalisani mumakamba zoona zake pitilizani kutiziwisa chilungamo god bless you
@JonesBenNgaiyaye
@JonesBenNgaiyaye 24 күн бұрын
Mulungu apitiriize kukupatsani moyo wautali pamene mukupulumutsa malawi polankhula choonadi comrade Mphepo
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 24 күн бұрын
Well said Comrade mphepo 🔥🔥
@udkconsultancy5567
@udkconsultancy5567 24 күн бұрын
God loves Malawi.. so much ... Malawi will rise again in Jesus name. God is love
@ZainthwaSikelo
@ZainthwaSikelo 23 күн бұрын
Uthenga wamphamvu Mr Mphepo,ankonkha panyowa apite
@JulioChiwalo-t4f
@JulioChiwalo-t4f 21 күн бұрын
Powerful message indeed okumva wamva Osamva ngosamva
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 24 күн бұрын
Anthu mukuseweresa chipembedzo bwanji amaveka zovala zimenezo ndani ndne msilamu koma asilamu pena pake ngt mukufuna ndlama ayi Inshaa Allah Allah adzaweruza
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 24 күн бұрын
Ine si msilamu koma kunena zoona Asilamu mwapeputsa chipembedzo chanu. Zoona mukamumveke Satana ngati uyu mikanjo ya chipembedzo chanu zoona zimenezo????????
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga 22 күн бұрын
Kkkkkkkk paja apule amadzimva mphamvutu, ndi mkulu wa chirichonse mdziko. Mpake Chilima adanenapo kuti mphamvu za president mzofuna kuzichepetsa kuti nayenso akalakwitsa adziweruzidwa.
@RashidLaston
@RashidLaston 19 күн бұрын
Zomwe anachita asilamu adyara pomuveka satana chilangawa mkanjo,ndi chimozi mozi kuyika chipini Cha golide pa mphuno ya nkhumba.
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 18 күн бұрын
Chakwera ndiwachinyengo, iye akuziwa kut si msilamu koma akuvala ngat msilamu kut ati afanane ndi asilamu, chonsecho si msilamu. Si mwano umenewo?????? Watembereretsa dziko chakwera.
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 24 күн бұрын
God z alive,,ciliconse cikhala pabalambanda,,thx sir,,,God b with yu sir
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 24 күн бұрын
Munthu oyipa kwambiri ameneyu zoona kumupha munthu chifukwa cha udindo
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga 22 күн бұрын
Mpando wa 5 yrs for that matter. Evil man
@IbrahimIsmael-h2w
@IbrahimIsmael-h2w 23 күн бұрын
Comrade mphepo ing'aluleni😂😂
@MarthaGama-q1o
@MarthaGama-q1o 24 күн бұрын
Koma ndiye mwayamkhula chilungamo chokha chokha more fire 🔥🔥🔥
@DavesonMoffat
@DavesonMoffat 19 күн бұрын
Zoona zenizeni kudula kwazinthu kumangolondola dzina la M'tsogoleri kkkkkk
@LumbaniNeba-d9n
@LumbaniNeba-d9n 24 күн бұрын
Proud of you my brother Mphepo
@HamzahTwaib
@HamzahTwaib 24 күн бұрын
Amenewo ndiye mawu MR fuso chimayendesa ndichimphasocho kapena munthu kutha kwachimphaso sikungapangise ndege kugwa ndi afiti amenewa as aduse 2025 please my people
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi 23 күн бұрын
Pochoka ku sauth corea Dr chilima sanakumane Ndi chakwela Pana anaphedwa pangozi yonamizila koma Ali amalinyelo mamafiya mwene
@gmxplayboy6559
@gmxplayboy6559 23 күн бұрын
Zikomo kwambiri big man, uku ndiye kulankhula mopanda mantha. Mulungu apitirize kuteteza anthu ngati awa
@ZebaNgaunje
@ZebaNgaunje 21 күн бұрын
Chilungamo🔥🔥
@DaudBonomali
@DaudBonomali 24 күн бұрын
Ndiye chikangawa mmene wawona kuti ambuye yesu amukana kuti sakufuna kuona nkhope yachikangawa ndiye waganiza kuti apiti kwa muhamad kuti mwina amukululukila palibe achimwene iwe ndiye wa ng'anjo ukakumane ndi lusifara munthu oipa nkhope ndi mtima omwe
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 24 күн бұрын
Ndipo mulungu sachedwa safulumila koma naga pokhapo mulungu asachedwe ndithu chakwela akumazitenga ngati mulibe koma tsiku lina nose amene mulumbila pa maso pa mulungu koma mukunama mulungu akukatheni posachedwa
@bensonmanda235
@bensonmanda235 21 күн бұрын
Apa mwayankhula chilungamo ndi moona. Vuto anthu sitifuna kumva chilungamo. Timaona ngati mwano
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 24 күн бұрын
KUMANGAKÒ ONSE AMENE AZILANKHULA ZANKHANI IMENEYI NDIYE KUTÌ CHIYANI CHIKANGAWA IWE .!!ÙKUBISA CHÌYANI.KAPENA KUOPA CHIYANI ? AMALAWÌ AĶUÐZIWÀNIBE KUTI MCP NDI A CHAKWERA NDI AKUPHA NDIPO.ZISANKHO SAKUSANKHANI
@wilsonchimtikaphiri9496
@wilsonchimtikaphiri9496 23 күн бұрын
Auzzee sakudziwA
@MathiasJoseph-xv1hj
@MathiasJoseph-xv1hj 24 күн бұрын
.mulichilungamo mu uthenga wamphamvu
@AlgentChilanga
@AlgentChilanga 23 күн бұрын
Comrade mphepo koma ndiye mwayankhula moveka bwino mulungu akudaliseni kwambiri
@IbrahimUseni-p8f
@IbrahimUseni-p8f 24 күн бұрын
Komaditu amwene dzikolitu Lori ndi utsogoreri wa minyama
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 24 күн бұрын
Koma nkhani ya ngoziyi itiphetsa a Malawi ambiri , popeza kukhaulitsa anthu ofzudzula boma akumaphedwa
@RosePhiri-n8q
@RosePhiri-n8q 24 күн бұрын
Amakamba kuti sanyengerera aslamu ndiye wavala bwanji zachisilam? Aslamuso simuganiza bwino iiiyaaa
@JulioChiwalo-t4f
@JulioChiwalo-t4f 21 күн бұрын
Dziwani ichi pangatalike bwanji chilungamo cha nkhani ya ndege chiziwika
@FWhite-w3l
@FWhite-w3l 23 күн бұрын
Koma ma Sheikh athu kumalawi Mmmm mukutinyasa
@frankmalikebu960
@frankmalikebu960 23 күн бұрын
More fire
@AugustineTheu-of6nv
@AugustineTheu-of6nv 24 күн бұрын
Mtsogoleri president mbusa, mbusa wake uti? Chitsirocho?
@IbrahimIsmael-h2w
@IbrahimIsmael-h2w 23 күн бұрын
Chikangawa dziko lamukanika
@ABDURASHEEDMATEMBA-b2b
@ABDURASHEEDMATEMBA-b2b 16 күн бұрын
Chakwela pomapanga zakozo musamavale madras achislam chifukwa pazomwe mukupangazo angakhale kumpingo kwakoko m'bukhu mulibemo
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 24 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥 fire
@JulioChiwalo-t4f
@JulioChiwalo-t4f 21 күн бұрын
Ngakhale manganya anaziwa zakugwa kwa ndege kuzera ku social media
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 23 күн бұрын
Nkazi wa chakwera hijab ndeinamukhalatu 😂😂😂
@PhillipNyaugwe
@PhillipNyaugwe 24 күн бұрын
Nkhani ya chilima ndikanakonda titaisiya chifukwa chilima anaphedwa ndi chakwela ndipati simukuvesa bwanji mukukokankhani yopanda mutu ndindani yemwe anga vomere chisawawa bwanji osadikila tivote azayakhe pa khoti
@JulioChiwalo-t4f
@JulioChiwalo-t4f 21 күн бұрын
Dziko la Malawi Mulungu analiyang"anira kumbali kamba Ka utsogoleri umene ulipo werengani 2mbiri 15 vs 1 to 5
@PhiripChinkango-k5p
@PhiripChinkango-k5p 23 күн бұрын
Koma zoonadi chilungamo walankhula mkuluyi eee
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga 22 күн бұрын
Corruption idamera mizu ku Malawi 🇲🇼
@JamesYusufu-l6d
@JamesYusufu-l6d 19 күн бұрын
koma kodi ndindani amene akumaveka mikanjo amenewa ndiye masela iwe sisilamu usatiyipisile pingo kupingo kwathu kulibe banja loipatima ngati limeneli mbava yachabechabe
@JulioChiwalo-t4f
@JulioChiwalo-t4f 21 күн бұрын
A kugwiritsa ntchito ndalama kumapanga chilichonse
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di 20 күн бұрын
Chifukwa cha kufa kwa anthu 9 ndi omwe dziko likuyendela chofunika ndi kubwela pamodzi nkupemphela
@udkconsultancy5567
@udkconsultancy5567 24 күн бұрын
God did not fail to deal with satan...
@raffickaffick
@raffickaffick 24 күн бұрын
guyz sheikh akuoneka pachithuzipo waika skaff yoyelayo or ife kumtundu kwathu tinamuda simmene analili kale pano chilichose chimene amachita nchoipa ati anayamba ndale mmmmhhh , sheikh kawinga ameneyo
@BwanaGD
@BwanaGD 24 күн бұрын
Mayimawaso iiii tiziwona chakwera kakwezeee mmmh petar katumikireeee kkkkk eee ndawona mayimadi akusiyana
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 24 күн бұрын
Ku Malawi kuno kuli ndende zazikulu bwanji ndi makhothi achangu bwanji kuti athe kumanga onse apa Social media ?
@GabrielMzich
@GabrielMzich 23 күн бұрын
Mnasamkha mbava ya mtsogoleri MULUNGU anva bwanji?
@SostenPiyo
@SostenPiyo 24 күн бұрын
Mulungu wakwiya nawo a pule anathawa ntchito yake
@LaynaAdam
@LaynaAdam 24 күн бұрын
Munthu osapita kujando akalowa muzikiti mmmmmmm
@MandalaChaona
@MandalaChaona 23 күн бұрын
Fake Report Just to Cover the big Vampire Mr Smartmatic,the Blood Sucker mix Mikodzo. Ndiye mumanga Dziko lonsetu hahaha 😂😂 . Munapha Chilima mwadzigwiritsa . Munthu Woyipa iwe Lazalo MCP 😂😂😂😂😂😂 mbola Boma ndilomweli la Dzilope M'busa wabodza,wokupha, Blood sucker mix Mikodzo Bravooooooo brother Richard Mphepo.
@RosePhiri-n8q
@RosePhiri-n8q 24 күн бұрын
Ndi m busa wang'ombe osati wanthu fiti osayipatsa vote amene akavotere chakwera nayeso ndi wakupha
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 24 күн бұрын
Zoonadi
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 24 күн бұрын
Ndiye uchitsiruwo chomangira anthu ndi chani?
@MacxwellStuarts-h9r
@MacxwellStuarts-h9r 9 күн бұрын
Chakwera akungoziyenjezerabe matembererowo akamabvala mikanjoyi
@Mirriumkamwendo
@Mirriumkamwendo 22 сағат бұрын
Chakwera asamavale za chislam ali ndi khalidwe loipa
@AlexanderMateketa-i8l
@AlexanderMateketa-i8l 19 күн бұрын
Mkhaniyo ndi yoona simukunama.
@MathewsDyson-z6z
@MathewsDyson-z6z 20 күн бұрын
Ndiwe chitsilu chamunthu ndimako yemwe wava? Zikugwilizana pati?
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 21 күн бұрын
Abusa palibe ciliconse cikumveka pa lipoti limeneli mbwelela zokha zokha basi.koma monga mwanena kale 2025 mulungu aweluza yekha nyau imenei yatikwana.mmutu mwa cikangawa mulibe ciliconse mamina okha okha.
@wilsonchimtikaphiri9496
@wilsonchimtikaphiri9496 23 күн бұрын
Zoonadi, and mafumu akumaitanitsa ziphaso za vote,(
@JonathanMunthali-n3c
@JonathanMunthali-n3c 24 күн бұрын
A police amene anayamba kufikapo ndi amene akuziwa kumene Kuli black box Plus uja amayang,anira kuwuLuka ndikutela
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 24 күн бұрын
Kodi akumamuveka zovala izi chitsiru ameneu ndindani???
@omarejussa8703
@omarejussa8703 24 күн бұрын
Dziko ndi la Mulungu koma nyumba ndi ya munthu
@IvyKaludzu
@IvyKaludzu 24 күн бұрын
Apatu ndiye chilungamo atiuze zoona
@wilsonchimtikaphiri9496
@wilsonchimtikaphiri9496 23 күн бұрын
Mbuzz ya pule
@JonathanMunthali-n3c
@JonathanMunthali-n3c 24 күн бұрын
Awaasiyeni tizawakhaulisa likalowa DPP and tizalanda ma hotel Evelyn things
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 23 күн бұрын
Achina chikangwa mcp machimo
@yasiniKalonga
@yasiniKalonga 23 күн бұрын
Unu munthu okoledzela nkhondo kt Aslam aziphedwa mpa kumveka nkanjo😢😢😢😢 nonsense
@christopherchikankhen
@christopherchikankhen 23 күн бұрын
Mulungu salakwitsa
@MartinMajola
@MartinMajola 19 күн бұрын
Chakwela mbuzi kupha zake chifukwa chaa udindo
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 20 күн бұрын
Tchu tchu tchu
@ZEZEChipewa
@ZEZEChipewa 22 күн бұрын
Chakwera May God punish him 😭😭😭😭😭😭😭
@khwimaBanda-s3u
@khwimaBanda-s3u 24 күн бұрын
mapulezidenti ambili alamulapo apangaposo zoba ndalama aononga poso zina ndan adamangidwapo palibe lelo mukuchuluka zoyankgula jala zadusapo zingat zoopsa ndikukumbusen imo mwa iyo 2001 to 2002 kudali njala yoopsa kwambili padalibe msogoleli kusowa zoyankhula anthuni bwanji nanuso ndinu oipa
@MandalaChaona
@MandalaChaona 23 күн бұрын
👹🐊👹🐊👹🐊⚒️🔨⛏️🤪🤪
IL'HAN - Qalqam | Official Music Video
03:17
Ilhan Ihsanov
Рет қаралды 700 М.
Zitsiru Zitatu by Pastor TY Nyirenda
14:03
Charles Shonga
Рет қаралды 31 М.
Palibe Chinsinsi! Imfa ya Saulos Chilima 2025 Revelation.
24:34
Human Rights Consultants TV
Рет қаралды 75 М.