SAMEER SULEMAN WASAMBWANZA PRESIDENT CHAKWERA NDI MCP YONSE PA INTERVIEW LERO NDI BRIAN BANDA

  Рет қаралды 43,542

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 173
@andreabanda7838
@andreabanda7838 5 күн бұрын
Parliament needs to be revamped seriously speaking. You can have the speaker from the ruling party. You can not have a speaker from the opposition party. There is need to have an independent person chosen from the public domain eg the judiciary or Malawi law society, or from retired private/civil servants. Mr sulemani is quite right. Komanso bwana wa eeee he loves his country. Chonde bwana musatope ndi matope akukupakani a MCP. You are a man of the people. God will bless you.
@MicksonPakhota-j1q
@MicksonPakhota-j1q 5 күн бұрын
This MP is so strong and got alot of things to say, why they didnt took him as a Leader of opposition? He can stand with real isues.
@PatienceMwandosya
@PatienceMwandosya 5 күн бұрын
Akatundu I like this man heavy
@FelixTsabolaNamaya
@FelixTsabolaNamaya 5 күн бұрын
I support this man would be better if he was chosen as the Leader of opposition. He indeed stands for his people
@sixtosix-pz8wu
@sixtosix-pz8wu 5 күн бұрын
He understands the true meaning of democracy and the role of an M,P, Suleiman ,the heart you have is genuine for the poor people,Fight for the good course ,God will reward you parliament Agood M,P, should only smile when the poor people have three basic issues ,Food,Shelter and clothes
@BrightZionga
@BrightZionga 5 күн бұрын
Kwathu ku Neno from next week tiyamba kubandila chimanga koma za fertilizer kuli ziii bravo Mr Suleman 🎉🎉🎉🎉we need more people like you may the good Lord bless you
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy 6 күн бұрын
Live wired MACHINE bambo❤❤❤🔥🔥🔥
@ChrispinJohnson-py5ie
@ChrispinJohnson-py5ie 5 күн бұрын
suleman muli nzelu osati afinye enanu big up we support u brother,awonese 5 days yatha akunjenjemela
@sthoramexjrsa902
@sthoramexjrsa902 5 күн бұрын
You are next minster of agriculture next year 💙💙💙
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko 6 күн бұрын
Sulemani ndikatundu oyimirila ife amalawi nkulu ameneyi amayenela kukhala rider of opposition 🎉🎉
@HarodLikanga
@HarodLikanga 5 күн бұрын
Nanuso sandidziwa ndale awa kape wachabechabe
@FelistusTaulo
@FelistusTaulo 6 күн бұрын
He deserves to be leader of opposition
@WilsonKaunga
@WilsonKaunga 5 күн бұрын
I have liked this interview!
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr 6 күн бұрын
Kodi TTV Thursday kunalibeko hot current? Ine sindinaionele nduku KZbin sinduipeza since dzulo. A Peter Muntharika mukamusankha Samir Suleman kukhala president waku DPP or leader of opposition chifukwatu amatha kuima pa ground 😊 Brian Banda kumva kukoma ndikumva za Chikangawa akusambwazidwa 😅😅😅 l love you both TTV ❤❤🔥🔥
@FelistusTaulo
@FelistusTaulo 6 күн бұрын
Zoona he deserves to be leader of opposition
@browncoffee9164
@browncoffee9164 4 күн бұрын
true spoken and louder i love it
@LucksonKumwenda-p2f
@LucksonKumwenda-p2f 5 күн бұрын
❤ Big Up Boss Suleiman 🎉🎉❤❤❤❤❤❤❤❤
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 5 күн бұрын
Sameer Sulemani your best of the best man 👨 ulemu wanu big brother be strong 💪 🙏 and God bless you mr Suleman and give you more years 🙏 ❤️ 🙌 💙
@richardkachulu8669
@richardkachulu8669 4 күн бұрын
On roadtraffic issue you can underline Brian😅😂
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 5 күн бұрын
Sameer Suleman deserves to be the leader of this country long live Mr suleman❤may the almighty bless and protect you wherever you shall go in the mighty name of jesus
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl 5 күн бұрын
That's great leader anthu ngati Inu muchuluke tikomze dziko lathu
@LukeMapukusa
@LukeMapukusa 5 күн бұрын
Big boss Mr Suleman you deserve leader of opposition in parliament
@RaphaelWinford-t7u
@RaphaelWinford-t7u 6 күн бұрын
We need people like you Mr......
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke 5 күн бұрын
Suleiman ndi katundu I like him 🔥🔥
@ChrispinJohnson-py5ie
@ChrispinJohnson-py5ie 5 күн бұрын
sameer suleman ur so genius
@AbdullahFyson-l3j
@AbdullahFyson-l3j 5 күн бұрын
Our next president 🎉inshaallah
@RosinaPatel
@RosinaPatel 5 күн бұрын
insha'Allah
@Mosa-b6g
@Mosa-b6g 5 күн бұрын
We proud of you ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@REXCHARLESKAJAWO
@REXCHARLESKAJAWO 5 күн бұрын
Sulemani ndiwe katundu MCP sikupumira bwino imakuwona kuopysa heavy 😂😂❤
@NicolasKamunga-rv9vr
@NicolasKamunga-rv9vr 5 күн бұрын
Big up Mr Sulleman
@YusufMoyo
@YusufMoyo 5 күн бұрын
Is a big yes for me he must be a rider of opposition ❤❤❤❤❤
@AliNjets
@AliNjets 5 күн бұрын
Katundu bamboo inshaallah next presedent
@ZamundaSambani
@ZamundaSambani 6 күн бұрын
Deserves to be a leader of opposition in the house
@SuleimanRabsonMkhunga
@SuleimanRabsonMkhunga 5 күн бұрын
Makwana brother suleiman
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 4 күн бұрын
Big man ulemu wanu mcp walephela
@OmarManjawira-up3ns
@OmarManjawira-up3ns 5 күн бұрын
Sameer your such a strong man ,,, we trust you in parliament cos you don't allow zopusa
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 5 күн бұрын
Koma mr suleman amayimirila amalawi.the best mp ever in parliament.
@HappyEyeglasses-sq1el
@HappyEyeglasses-sq1el 5 күн бұрын
Munthu wamkulu kwambiri you always stand for the truth boma chiseko chawapana
@MadandoChannel
@MadandoChannel 5 күн бұрын
True here same suleiman sakunama
@munyenyembe
@munyenyembe 5 күн бұрын
Dziko lino likufunikira anthu anzeru ngati Sameer Suleman osati anthu amamina mmutu ngati chimwendo komanso zikhale kamajekete 😂😂😂😂😂
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 5 күн бұрын
Good leader indeed
@ArnoldMatewere
@ArnoldMatewere 4 күн бұрын
Mulankhula chilungamo
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 5 күн бұрын
Ku parliament honestly speaking sikuli bwino
@EDGARMPIKAMEZO
@EDGARMPIKAMEZO 6 күн бұрын
Muli chikondi cha dziko chenicheni mwa Suleman 💪🏾💪🏾💪🏾 apa ndiye a boma ang'alulidwa 🤣🤣🤣 akulephera kudzuka pa mpando kabudula waphwathuka pokhalira 🤣🤣🤣🤣 Kabambe, Suleman, Mtumbuka, Kambala, Njawala, Freddokis, Mahata, Kamangira, Chizuma, Nyaronje Ndi McBride Nkhalamba. 🔥🔥🔥 Timu iyiyi Malawi litha kukhala dziko lokoma. Apule alipowa khansala ku Kasiya zingakome 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼❤️❤️❤️❤️❤️🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@EnockKampondeni
@EnockKampondeni 5 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 ndiwe ghalu kwabasi
@Dellingsmunthali
@Dellingsmunthali 5 күн бұрын
Inu ndichoseni umburi pa zsmbia pompa amapanga fertilizer??
@AlumakioChingalu
@AlumakioChingalu 5 күн бұрын
😂😂Awa mwano basi
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 5 күн бұрын
Chilungamo nthawi zonse chimakhala mwano❤❤
@ENOKMAKONDI
@ENOKMAKONDI 5 күн бұрын
Brian Banda nde ukamati zachitika kuti iwe sukuziwa 😂😂😂😂😂😂
@Oskie265
@Oskie265 5 күн бұрын
Kodi MP pano amalandira ndalama zingati?....Yankho: Ayi koma Chenje Chimasalapo 600K..Ngati akulephera kuyankha mwa Straight funso ngati ili Nzosakaikitsa kuti Zambiri akutiuza ndi Boza lokha lokha...Andale onse ndiadyera komanso Boza.
@emmanuelmasamba352
@emmanuelmasamba352 5 күн бұрын
I am surprised too. Munthu aliyense sangayiwale salary yake kuti amalandira ndalama zingati.
@youngchax
@youngchax 5 күн бұрын
Sitikuziwa kt inu mumagwila tchito kutiko Ngt palichinthu chomwe amabisa anthu nd salary ngt mumagwila tchito ukuziwa zmenezo unless you are a jobless
@youngchax
@youngchax 5 күн бұрын
​@@emmanuelmasamba352salary timabisa akulu Olo Brian yo atamufusa kt amalandila salary zingat sanganene
@HumphreyKasowanjete
@HumphreyKasowanjete 5 күн бұрын
Great son of Malawi
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 5 күн бұрын
2030 our next president is suleman
@youmad9087
@youmad9087 4 күн бұрын
Better now than that granny
@SamuelKhumbiwa
@SamuelKhumbiwa 5 күн бұрын
Inenso ndikugwilizana ndi anzanga kt Suleman akadakhala mtsogoleri otsutsa kuyambila kale lomwelija boma Ili sikanapanga manyaka akupangawa.from now mukafuna kusankha strong leader muzisakha ngt amenewa.
@DaudiHAllie-kk1en
@DaudiHAllie-kk1en 4 күн бұрын
Running a country is a serious business are words that altered by the former president Bakili Muluzi by the way
@EmmanuelMbuluma
@EmmanuelMbuluma 5 күн бұрын
I was thinking kut ma mps amalandila ma millions koma aaaa nawoso akufanana ndima civil servant ma salary
@billybanda7280
@billybanda7280 4 күн бұрын
I think suileman ndi malemu SKC ali ndi thinking capacity yofanana, anthu awawa akanagwila ntchito limodzi dziko lathu likanasintha ndithu!!!
@EmmanuelSambani
@EmmanuelSambani 5 күн бұрын
Sameer Suleman ndi Namacheni wathu kulambula nseu after all kukwezedwa galimoto.
@EmmanuelDanitsa
@EmmanuelDanitsa 5 күн бұрын
Mafuso anakuvtani lero Mr Brian Banda
@ZamundaSambani
@ZamundaSambani 6 күн бұрын
Deserves to b a leader of opposition
@JohnChingamba
@JohnChingamba 5 күн бұрын
❤❤
@EsnartTione
@EsnartTione 5 күн бұрын
Mr Suleiman umakwana,zonse ukunena ndizoona zokha zokha speaker amafunika wa chipani chosutsa
@jezalakaphuka7325
@jezalakaphuka7325 5 күн бұрын
Makina
@GraceChenda-q2g
@GraceChenda-q2g 5 күн бұрын
Mulungu akutetezeni a Suleman,,musakumane ndi za SKC
@cosmaspaindana1325
@cosmaspaindana1325 4 күн бұрын
100%
@joempesi
@joempesi 4 күн бұрын
Peter munthalika akamazapuma pa u president iweyo tizakusankha kukhala president. Ndiwe mfana oganiza booo
@JustinChimera
@JustinChimera 5 күн бұрын
Sulaiman ✊
@RajabAssan
@RajabAssan 4 күн бұрын
Umakwana sameer
@mzeewandembonyirongo2972
@mzeewandembonyirongo2972 5 күн бұрын
Kutsara kuchokera kudzinga bwana MP😢
@RosinaPatel
@RosinaPatel 5 күн бұрын
Pangolin .amalankgula chilungamo thats y MCP amadana naye..paja safuna anthu kudzudzula ngati suleman .Ntanyiwa ..Bakili tv ndi ena onse..bde MCP imeneyi
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 5 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@ChifundoGalusa
@ChifundoGalusa 6 күн бұрын
Pangolin wanthu uyu palibeso.. Koma enanu mukapanga zibwana, Namiyango Banana, Nazareth ward mubesa ndalama.
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 5 күн бұрын
Uyu ndikatundu uyu, ndipachimake MCP kumuda mu parliament,Chimatolera information ngati bakili Muluzi TV.
@JoshuaJuwawo
@JoshuaJuwawo 6 күн бұрын
Leader of opposition
@DelubyMarko
@DelubyMarko 4 күн бұрын
Awawa ndadolo hvy
@veronicamalisero2671
@veronicamalisero2671 5 күн бұрын
Ndipo U speaker wa parliament umafunika Munthu adzichita kulembela based on qualifications , bwezi akupanga apply ngat ntchito izi zosankhidwa chifukwa cha kuchipani sizinganukhe kathu ,mwana samaukila kholo lakeyi chomcho speaker can't go against chipani chake.tikanasintha koma Malawi tikuchita nalo manyazi dziko lathu lomwe
@EnockSankhylani
@EnockSankhylani 5 күн бұрын
Ndipo president angauthedi
@GeorgeChikwesele-k2v
@GeorgeChikwesele-k2v 5 күн бұрын
Nice
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 5 күн бұрын
Our Pangorine
@RaphaelWinford-t7u
@RaphaelWinford-t7u 6 күн бұрын
Iwe manganya mkumati boma ndi lomweri kapolo wamunthu iweeeeee..... Zanu zili pabwino koma anthu akuvutika kwambiri kumidziku mbuzi za atsogoreli.......😊😊😊
@EdoLiwonde-w2h
@EdoLiwonde-w2h 5 күн бұрын
iweyo Nd Suleman Nd mamu wantanda ukuoneka kt Uli ndimasophenya a utsogoleri iwe ndkaporo
@EnockSankhylani
@EnockSankhylani 5 күн бұрын
Or atakhala preasdent
@emmanuelnyirenda3289
@emmanuelnyirenda3289 5 күн бұрын
Samkapanga zosezi ali mbali yolamulira bwanji?
@NedMoses-nc7ev
@NedMoses-nc7ev 5 күн бұрын
Why choosing sleeping people as the leader of opposition??
@NeezeahKumbanga
@NeezeahKumbanga 5 күн бұрын
Km yemwe atenge mpando chaka chamawa eeeeeeee mh ayi mulungu achitepo kanth coz poyambira kukonza zinth kuzavuta poyambira pake anthu awoononga awaaa
@Dellingsmunthali
@Dellingsmunthali 5 күн бұрын
Chomwe chimadabwisa abwana suremani vuto mkabwera muboma nyasi zose mkunenazi m'mazitengaso kodi choncho mavuto angathe mziko??
@NicolasKamunga-rv9vr
@NicolasKamunga-rv9vr 5 күн бұрын
Chikangawa chakwela ( C C) asegura mimba mwa mpezeze. Ipase moto mr Suleiman
@madaloadine
@madaloadine 6 күн бұрын
🙌
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 4 күн бұрын
5kg mbeu ya chimanga yafika pa 55 000 kuno kumzimba eswazini, ndagula ine ma 5kg atatu, zithu sizilibwino mdziko muno.
@TganGawan
@TganGawan 5 күн бұрын
Chamba ndichothandiza
@patrickchapitapita1446
@patrickchapitapita1446 5 күн бұрын
Ukakhala ku opposition umawoneka wa mzeru…
@giftbanda4518
@giftbanda4518 5 күн бұрын
What has happened to Brian Banda.
@franciscomwangonde617
@franciscomwangonde617 4 күн бұрын
Kwa ine,ndi osokoneka mutu
@martinkasamba1576
@martinkasamba1576 6 күн бұрын
Layivi waya
@Chikwawa
@Chikwawa 5 күн бұрын
Vote yathu tinampatsa kanyimbi.
@WysonChilonga
@WysonChilonga 5 күн бұрын
😂😂😂😂
@EnockKampondeni
@EnockKampondeni 5 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@GeorgeNkhata-x1o
@GeorgeNkhata-x1o 5 күн бұрын
Uyu koma ndiamene akanamsankha kukhala reader of options
@johnfikilini.88
@johnfikilini.88 5 күн бұрын
tikadzankhala ndi ma mp ambiri oti alibe katangale adziyakhula mopanda mantha ngati sameer suleman........
@JohnmjigoMalinda
@JohnmjigoMalinda 5 күн бұрын
Umakwana Suleman osaopa osafooka chakwera alibe mzeru
@NumeriKuleti
@NumeriKuleti 5 күн бұрын
Zikomo kwambiri a Suleman taku nyadirani
@GeorgeTembo-v6i
@GeorgeTembo-v6i 6 күн бұрын
Machine amenewo
@andersonmulenga7735
@andersonmulenga7735 6 күн бұрын
Malawi needs a reset button..we are fucked
@abgi.doctor.august
@abgi.doctor.august 5 күн бұрын
My vote is DPP 2025
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 5 күн бұрын
Suleman mulungu adzikusogolelani kwambili amalawi ali kumbali yanu
@RaphaelWinford-t7u
@RaphaelWinford-t7u 6 күн бұрын
Chakwela ndi boma lake mmmmm mbuzi zawanthu agalu awa.....uli ndi tsoka iwe kuthawa ku church 😢😢😢😢.... zoonadi khwapatari kuti wachuma akarowe muwufumu wa MULUNGU kuthamangila zakudziko satana iwe chakwela.....😊
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 5 күн бұрын
Boma likufuna kupanga business pa nkhani ya mafuta, chomwe akufuna ndi kuba basi
@PatrickJunior-f8f
@PatrickJunior-f8f 6 күн бұрын
Anthu amena amawa angathandize ziko chakwera ndi satana wenwen ndi nduna zake Garu
@Chikwawa
@Chikwawa 5 күн бұрын
Uyu chikangawayu anatenga mpando by mistake ya ife, galu woipiratu.
@PatrickMusyani
@PatrickMusyani 6 күн бұрын
Suleman mmmmm ndikatundu
@Yungjoe786
@Yungjoe786 5 күн бұрын
We need to default this Paliament things are totally bad
小路飞和小丑也太帅了#家庭#搞笑 #funny #小丑 #cosplay
00:13
家庭搞笑日记
Рет қаралды 17 МЛН
Каха и дочка
00:28
К-Media
Рет қаралды 2,2 МЛН
Deadpool family by Tsuriki Show
00:12
Tsuriki Show
Рет қаралды 7 МЛН
SIHLE LONZI SPEAKS ON EFF CLOSING DOWN
4:43
THE CREATIVE PASSPORT
Рет қаралды 117
EXCLUSIVE 7 NOVEMBER, 2024 PT 1
40:40
Times 360 Malawi
Рет қаралды 6 М.
USAUVER S10E06 - USAMFUNSE NDIMFUNSA
19:14
Piksy TV
Рет қаралды 59 М.
Izindaba zesiZulu @13H00 l 13 December 2024
24:35
SABC Izindaba
Рет қаралды 17 М.
HOT CURRENT MALAWI | 8 DECEMBER 2024
1:08:08
Malawi News Update
Рет қаралды 15 М.
小路飞和小丑也太帅了#家庭#搞笑 #funny #小丑 #cosplay
00:13
家庭搞笑日记
Рет қаралды 17 МЛН