ZIDALI LERO KU BLANTYRE LIMBE🤔🤔

  Рет қаралды 19,094

HOT 265

HOT 265

Ай бұрын

Пікірлер: 138
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v Ай бұрын
Ku Malawi tilebe president zowona
@user-ql7ik4mw6p
@user-ql7ik4mw6p Ай бұрын
Anamenya.a.DPP.bwanji.ku.lilongwe.aja.bwanji.zimunagwile.si.ulamulilo.wayinu.achakwela.ndinu.achibwana.kwabasi
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 Ай бұрын
Iweso ndi amene wazuza kwambiri a Malawi Mulungu akuone kwambiri
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba Ай бұрын
Kodi ameneyu akuone mubukhu galuyo mfundo zake angosakaniza zosamveka zonkhazonkha,pot amalawi ndiopusa angoombela manja zilizose
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Athu a dpp aja bwanji sunagwile ifetu usatione kupusa wamva tatopa nawetu chakwela, wachibwana mudziko muno Mesa ndiwe
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
Ladzalo ulibe fundo kkkkk pamene ukufuba unene kt chani
@BlessingsBukucha
@BlessingsBukucha Ай бұрын
Ngati zakuwawa upite ku Zambia ife zikuenda momuno simunati mulila zenizeni agaluinu mbava
@sayidimisessa
@sayidimisessa Ай бұрын
Aaaaa achakwera zimene ayankhula , ndimomwe likuyendera zikoli sizikugwirizana nkutalitali, from south Africa
@hassanrasheed1379
@hassanrasheed1379 Ай бұрын
Koma President chakwera aaa awa nde fundo alibe Bwelera zokha zokha.
@sungananigondwe2807
@sungananigondwe2807 Ай бұрын
Koma mbuzi iyi yimapepelesa anthu 😂😂
@enockbanda4530
@enockbanda4530 Ай бұрын
Malamulo adziko LA Malawi 🇲🇼 amaphinja osawuka olemera kundende sakhara koma okupa nkhuku ndi Ena osaukawo. My Malawi my pain but is one day we gonna see
@user-jb5yb9wq3y
@user-jb5yb9wq3y Ай бұрын
Apolice 6000 enao ndi anyamata a youth osati Apolice, tikumana pa ground
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 Ай бұрын
Koma achitetezo chilipo dzikomo?
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Ай бұрын
Kodi Chakwera uli ndi umunthu koma, milomo ya mtundu wanji yosatopa ndi bodza, sikuchulukatu kwa a police komwe kumabweretsa chilungamo m'dziko koma one's commitment.
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 Ай бұрын
He is the worst president Malawi has ever had you must go it's a matter of time
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td Ай бұрын
Sanje sipindula wakutokosa umaphabawo zibale athu alubino muyambilaso akachoka not in his time forget
@yassinnandera5634
@yassinnandera5634 Ай бұрын
😅
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz Ай бұрын
Aaaaaàaaaa mbudzi iyi
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju Ай бұрын
Sugar akupezeka ku zimbabwe wa mlw akutuluka bwanji sugar apolice alipo ....lamulo lake liti
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Kkkkkk koma chakwela iwe aaaaa anakhonza kunama
@noahtsamdoka1172
@noahtsamdoka1172 Ай бұрын
Manyaka enieni
@IsaacKulongwe-ol5mx
@IsaacKulongwe-ol5mx Ай бұрын
MUFUNE MUSAFUNE CHAKWERA 2025 BOMA .GOGO WANU UJA OPANDA MANO UJA AKAGWERE UKO!!!!!! CHAKWERA ❤❤❤❤
@user-tw7jx8tf1u
@user-tw7jx8tf1u Ай бұрын
Iwe a gogo ako alipo ngat peter choka
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d Ай бұрын
Chakwera ndi galu ulibe ndi fundo bola nkhumba Ndi iwe
@davidjames9711
@davidjames9711 Ай бұрын
Mfundo za adah awawa zero pa 10
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s Ай бұрын
Iwe wa 265 usamaika za chakwera wati kwana uyu
@user-bf1sz6pu1n
@user-bf1sz6pu1n Ай бұрын
Kodi aphunzitsi alimo angati mziko muno? Ndiokwanila?
@VictorAmos-my8ne
@VictorAmos-my8ne Ай бұрын
Akulu amenewa ndiopa zedi, akutisakazila dziko ,
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d Ай бұрын
Komotso amene akuombela manja nawo alibe dzero akukupasani chani chakwera kuba ndichimene akuziwa
@user-bs5yp3un1m
@user-bs5yp3un1m Ай бұрын
Akurakhura ngat aribetu mabwara
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc Ай бұрын
Mpaka utagonati. aaaaa uyu wakwa,chiozadi ndithu.
@leveltrapper4322
@leveltrapper4322 Ай бұрын
Paja amangobwebweta2 😂😂😂😂 kd Malawi akulamulira ndi UTI kd
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r Ай бұрын
Zoona mbuzi yamuthu kkk
@user-hq6dq7zr1e
@user-hq6dq7zr1e Ай бұрын
Aaaaa apa nde kayano 😅
@TadalaJuwao
@TadalaJuwao Ай бұрын
Tiziopa uniform kuti azitichitira nkhadza?
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 Ай бұрын
He is a president by Speech not by action
@carlossadimba595
@carlossadimba595 Ай бұрын
Lamulo likhale la mphamvu kuposa ndale .....koma andale ndi omwe mumaononga police I was watching Mp from mangochi who instructed office of police to transfer police officer that was abuse of power by the member of parliament ....
@FrancisChibwana
@FrancisChibwana Ай бұрын
😮 😮😮😅😅 mbwelera km izi
@zephasibanda4462
@zephasibanda4462 Ай бұрын
Akulu amenewa zoyankhulazo akuchita kuonera likasa komabe akudodoma kuwerenga kwakebwanji mwina naowonso satha chichewa ngati kamuzu
@mchipengule
@mchipengule Ай бұрын
Sasia Kodi mukuti President walakwa chiyani? Inu anthu a Dpp Mulungu sangakudalitseni AYI ndipo mwai wanu olowa m'boma palibe. Nkhuku ua njohu siyiswa. Ifedo a Dpp munatitopetsa kwambiri. Kumbukilani maliro akatuluka munyumba sabwrlera.
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q Ай бұрын
Ayi president uyu niwa sataniki kwake nikupha paribe chazeru anganenepo ayi
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 Ай бұрын
Ena uniform ikuwakhwepa nde aopedwa bwanji 😂😂😂😂 zopepela galu iwe.. Uphele basi.
@sandimizeka3199
@sandimizeka3199 Ай бұрын
Amenei nchisilu
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Ай бұрын
Ma comments mukalandila, muzimuonesa chakwelayo aziwelenga ekha , In Africa , this kind of president we call him ldiot , Bcose all members of MCP who're under case of corruption are free .
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias Ай бұрын
😂😂😂😂
@henryhenry5369
@henryhenry5369 Ай бұрын
Ku Mpoto ndi MCP who ever say he's DPP go to hell and we make sure MCP win every vote . I hate APM and the DPP plus Namalomba. You 2 guys don't come to Mpoto ndipo muzawona nyekwe
@chiswamemo2186
@chiswamemo2186 Ай бұрын
Or wapolice yo yekha akuchita kuti mbwelera zake iziii 😂🙌
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias Ай бұрын
A youth amenewo ukufuna azitichitira nkhanza tikamamuzuzula
@user-is5dl7np9g
@user-is5dl7np9g Ай бұрын
Mumanga Liti malawi watsopano poti muli pa ulendo pano lamulo liribe mphavu chili ndi mphavu ndi chipani kagwere uko chakwera mbuzi
@user-fs1qo2yd9y
@user-fs1qo2yd9y Ай бұрын
Kod amamulembela ndindani uyu kkkk
@user-uv1vu6ub5o
@user-uv1vu6ub5o 28 күн бұрын
Kuyakhula ndikosavuta eish
@HanishaissahKagansa
@HanishaissahKagansa Ай бұрын
Awanso ndiye ayi
@kelvindickson
@kelvindickson Ай бұрын
Kodi kumakhalanso Amayi achipani koma amawapasa nsalu za Malawi police eti
@IsaacKulongwe-ol5mx
@IsaacKulongwe-ol5mx Ай бұрын
U can point a finger at someone forgetting that 4 fingers are pointing at u
@user-cb2cv9fz7m
@user-cb2cv9fz7m Ай бұрын
Apolice ake mbava Zo zaziii, wakuba iwe nthawi yako yatha ndipo ulibenso mfundo apa nde bolanso bon kalindo Ali ndi mfundo, mbuzi ya munthu chakwera
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Kodi iweyo ndeukukwanilitsa malamulowo, bwanji mumangolakhula koma osachita
@FOSTERLUPIYA-zc1xv
@FOSTERLUPIYA-zc1xv Ай бұрын
Kunyoza mtsogoleri wa dziko ndi tsoka pa maso pa Mulungu.Ndipo sizabwino kutero .
@user-mq5vs4hn6o
@user-mq5vs4hn6o Ай бұрын
Machende ako
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j Ай бұрын
Ntchito ya umbava ndi uchigawenga ndiyo u police choncho apo waonjezela zigawenga za MCP mu chisankho cha 2025,,,,,, Wa satanic we ungalephere kulimbadi mtima, siuja umkati mkalephela kuwina ndikhetsa mwazi! Lero ukungochititsa ngozi ponseponse ,kod ngongole udatenga cash mu 2020 ija kut udzabweze magazi ija kod siudamalizebe?
@jamesgama5489
@jamesgama5489 Ай бұрын
Iziwopedwa unform yong'ambika akumavala yoperepesekayi makamaka ku PMF 😢😢😢
@TadalaJuwao
@TadalaJuwao Ай бұрын
Achinyamata amene akumavala t shirt ya MCP akumalandira ma 7000 msonkhano ukatha
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m Ай бұрын
Mulibe mfundo zomveka mungobweleza bweleza
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Ай бұрын
Km chimene akuyankhula iyeyu akuchidziwa ?uyuyu ndi bulutu la munthu
@user-mk7fh5ml8s
@user-mk7fh5ml8s Ай бұрын
Apapo ndavomeleza kuti ku Malawi tilibe President ndizoonadi.
@henryhenry5369
@henryhenry5369 Ай бұрын
Chakwera is the best DPP wait for Jesus to come. And you have an aggry APM . And amatipatsa manyazi ku UN
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg Ай бұрын
Uyu sakudziwa chomwe akuyskhula satana wamaliza malawi
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 Ай бұрын
Lakukanikani Boma kuyendetsa
@arafatMtyala-bo8ev
@arafatMtyala-bo8ev Ай бұрын
Zaziiiiiii akulu awaso zoyakhula zawo
@ClementMinyanga
@ClementMinyanga Ай бұрын
Mbuz yenyen iyi
@IsaacKulongwe-ol5mx
@IsaacKulongwe-ol5mx Ай бұрын
Mufuna chakwera azibweretsa thumba la ufa pakhomo panu .Chitani manyazi anthu kummwera kuzolowera zolandira za ulere
@StevenFombe
@StevenFombe Ай бұрын
Sebia at its best
@AbuOsman-ts6ef
@AbuOsman-ts6ef Ай бұрын
Akulakhula ngati akudwala
@BatsonKadzuwa-tl3rp
@BatsonKadzuwa-tl3rp Ай бұрын
A kuluwa ndi achitsilu
@user-bs5yp3un1m
@user-bs5yp3un1m Ай бұрын
uzawanyadra rit popedxa thawiyako yatha
@user-iw6cz5ft2l
@user-iw6cz5ft2l Ай бұрын
Anzawo akupondedwa kumangochi uko
@hassammaulana4529
@hassammaulana4529 Ай бұрын
Za ziiiii
@afrozwayson7482
@afrozwayson7482 Ай бұрын
Enawo si apolice ndi ayufi
@feehasaidid.r.d
@feehasaidid.r.d Ай бұрын
President wasabola owawa kwambiri Mulungu akuoneni posachedwapa iwe
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem Ай бұрын
Zadziiiii
@StevenFombe
@StevenFombe Ай бұрын
Don't cheat us don't push to them akakhala pa mnkhate sapheka
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq Ай бұрын
Iwe takamba dzoveka apolice woakugwila Natchito yamanda winiko machenako nda police akowo
@louisgolden
@louisgolden Ай бұрын
Uyi ndi satana basi Mutu wakeso
@duncainjimmy
@duncainjimmy Ай бұрын
Komano nthawi imene kwachuluka apolisiyi ndiyomwenso kwavuta ndi corruption
@user-rd4ft9nd8t
@user-rd4ft9nd8t Ай бұрын
Akadakhala kuti akugwira bwino ntchito nanga aja anamenya anthu kulilongwe kuja apolisi kunalibe? Ok
@StevenFombe
@StevenFombe Ай бұрын
Our money
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t Ай бұрын
A police omanga avutika okhaokha
@AmaChidzinga
@AmaChidzinga Ай бұрын
Koma dpp munatikwana kaletu paja
@user-zw8ns7bk7s
@user-zw8ns7bk7s Ай бұрын
Ma passport ndiomwe tikufuna osakhala zopusa ukulubwa apawa pa nkholo pa amako iwe
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Kodi mesa Satana wakulu ndiwe kuliso Satana wina kuposa iwe
@james-zd2nz
@james-zd2nz Ай бұрын
lwe galu kwambiri
@starneckkulemero7548
@starneckkulemero7548 Ай бұрын
Anthu ena amatha kupeza mwayi ngakhale Ali chitsiru.
@user-yg9em7qq2v
@user-yg9em7qq2v Ай бұрын
Ndimbuzi uyu
@user-ok7xz1qr3k
@user-ok7xz1qr3k Ай бұрын
Apapa watinamiza kuti maulamulilo onse anapeza anapeza apolice13000 aa ndikusowa mfundo
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Anzawo audasi sakondwela or tikhala zabwino bwanji satanai wazaza mmitimamo
@joicemumba3608
@joicemumba3608 Ай бұрын
Ukutipangila waka viwawa Nauzereza wako
@user-kl1vk1gx2q
@user-kl1vk1gx2q Ай бұрын
Alibe chokamba mbuz chakwera panya pako
@petertukula1649
@petertukula1649 Ай бұрын
🙄
@OrtonKabbichi
@OrtonKabbichi Ай бұрын
Useless leader, no mutu
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q Ай бұрын
Zaziiiiiii
@FrancisDinala
@FrancisDinala Ай бұрын
Iwe ndi galu kobas
@francischingwalu
@francischingwalu Ай бұрын
Iwe chakwela utule pasi undindo tatopa nawe tidzabwela kumeneko iwe ukachoka
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Zoona apulu mkunena zoona
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r Ай бұрын
Mbuzi yamuthu
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Ай бұрын
Chisiru cha munthu!!!!!
@IsaacKulongwe-ol5mx
@IsaacKulongwe-ol5mx Ай бұрын
One of the best leaders on the land of Africa
@FosterChakanga
@FosterChakanga Ай бұрын
Kodi hot265 ndi ya mcp kani?😢😢😢ikumangotipatsa ma speech a chakwela bwanji?
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 13 М.
одни дома // EVA mash @TweetvilleCartoon
01:00
EVA mash
Рет қаралды 6 МЛН
DNA Tinashe Mugabe Padare Rachief Mutasa
15:49
TICHKACH MTV
Рет қаралды 21 М.
Anthu omwe ali ndi kuthekera kozawina u President Chaka cha mawa
11:27
Mai Mutsvangwa finally speaks
6:54
Rory Studios News
Рет қаралды 72 М.
Skeffa Chimoto Apresident new Audio Official
8:35
Yathu Music Official
Рет қаралды 73 М.
ESPECIAL CONGRESSO DA RENAMO  |15|05|2024
TV Sucessomoz
Рет қаралды 1,6 М.
Professor Peter Mutharika Speech Mjamba Rally (19 December 2021)
19:34
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 19 М.
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 17 М.