ZIMAFUSO ZOTULUTSA MISONZI KUCHOKERA KWA BRIAN BANDA-🤔🤔13 April 2024

  Рет қаралды 51,714

HOT 265

HOT 265

Ай бұрын

Пікірлер: 195
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 Ай бұрын
Ndili ndi pempho Kwa ayini channel itchi zingatheke your photo isamakhalepo muziseye video isewele full screen please chifukwa zomaonela half ayi ndithu sizabwino we link your channel but when you end up put your face in the TV it's good please my brother and you always poster the good things and we are happy for that's If it's need to show your face I mean like your on video I understand but something like this leave the TV play it self we thought your face my apology
@user-nx9zx6fv4i
@user-nx9zx6fv4i 29 күн бұрын
Channel Ichi ndichabwino Koma kachithuzi Kanu pakonapo mzichotsa mwachitsanzo muluzi TV samayika nkhope ndipempho
@OwenWalter-nz7uo
@OwenWalter-nz7uo Ай бұрын
Bro tamachosani nkhope yanuyo sizikumaoneka bwino plz siyani vidio ichite play payokha plz plz
@basheeribrahim1050
@basheeribrahim1050 25 күн бұрын
How about you create your own channel bwana
@user-jb5yb9wq3y
@user-jb5yb9wq3y Ай бұрын
APM my vote
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Ай бұрын
APM my vot❤
@user-uv7yq1fx4r
@user-uv7yq1fx4r Ай бұрын
Inu mukufuna kuti muzamalize dzikoli 2025 vomelezani kuti mwalephela kazipitani mukapume mwatilephela
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Dpp woyeeee ❤❤❤❤❤❤❤❤
@Betty-fe9ql
@Betty-fe9ql Ай бұрын
Zoyambana ayitu 😂😂 pitani Ku Paige house uko
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
@@Betty-fe9ql 😃😃😃😃Nanga akufuna azitinamiza ifeyo kutiona Ngati oputsa??? Akhaula ifee ozawina tikuudziwa Kale president wathu ndi Peter Munthalika basi, president osasankha odziwa mavuto amphawife
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 29 күн бұрын
​@@user-uc1pd1tc2x😂😂😂😂😂
@EphronJames
@EphronJames 24 күн бұрын
,
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 Ай бұрын
MCP just forget Malawian the won't vote you trust me
@PatrickMariko
@PatrickMariko Ай бұрын
Munabwera kudzaononga Malawi osati kuthandiza anthu akumudzi mcp
@user-mv1ho9pp7o
@user-mv1ho9pp7o Ай бұрын
MCE chaka cha mawa paulendo okalima 😂😂😂
@martiusgeorge6514
@martiusgeorge6514 Ай бұрын
Kodi chinkhope chakocho umachiikiranji?
@OFG-th3st
@OFG-th3st 8 күн бұрын
Nkhope yakoyo bwa aaaaa chimidzi😩😩💔💔🙌
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Ай бұрын
Gwape weniweni
@josephkaunda1755
@josephkaunda1755 Ай бұрын
Following and listening Mr Banda
@michaellowole1088
@michaellowole1088 Ай бұрын
Munthu wakulu Brian banda ❤
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d Ай бұрын
Ndiwe mbuzi anthu akuvutika iweyo ukunena zogula magalimoto pamene anthu akufa ndinjala pankholo pako
@RobbertKenson
@RobbertKenson Ай бұрын
Mukufuna ku gulira azitsogoleri magalimoto tilindi ana mmamizi amene akulephera kupitilinza maphunziro awo chifukwa chosowa nthandizo ra ndalama and tili ndi amphawi oti Oro fertilizer wa pukoni sakwanisa kugura otsathandiza anthu amenewo bwanji mulibe mfundo Achaima Banda
@user-tn5eq9fp2z
@user-tn5eq9fp2z 29 күн бұрын
Akuti ma fortune 😂😂😂 ndalama za boma zipite basi
@NumbDee
@NumbDee 28 күн бұрын
APM My vote
@edenngoma8214
@edenngoma8214 27 күн бұрын
Chayima Banda is very intelligent man and you deserve to be Secretary General
@Alomwe
@Alomwe Ай бұрын
Muululana. Ndalama zilimo muchipanimu . Zikuchokera kuti?
@user-vx5vk5ss6k
@user-vx5vk5ss6k 19 күн бұрын
Mbava iziiii
@FosterChakanga
@FosterChakanga Ай бұрын
Kodi ndiwe wa MCP iweyo.Ndikunena mwini wa channel iwe.Yes or No can be a better answer
@innocentmanyera1861
@innocentmanyera1861 28 күн бұрын
ukadziwa ufuna utani
@FosterChakanga
@FosterChakanga 27 күн бұрын
@@innocentmanyera1861 ndikufunsa mwiniwake
@FefieTenisha-du7ge
@FefieTenisha-du7ge 24 күн бұрын
Empty manifesto that won't take ordinary Malawians anywhere.. The hopeful SG is just focusing on party members especially those bearing seats of power.. Flashing money,cars etc to office bearers won't take Malawians anywhere... I wonder what Western education does to our minds!!!
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Ай бұрын
Kodi iwe Chaima Banda, magalimoto ukufuna kugulira anthu a chipaniwo ndalama zake uzizitenga kut nanga ziziwapindulira chani amalawi omwe akuvutika ndi njala mdziko muno, iweyo Chaima Banda unamva kut, kut njala amaipangira campaign????
@innocentmanyera1861
@innocentmanyera1861 28 күн бұрын
cedetish colours fwetseki
@user-iu7gr2hj1j
@user-iu7gr2hj1j Ай бұрын
Vuto la MCP imakonda chipani osati a Malawi
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 Ай бұрын
Naye akuyakhula Ngati chakwela 😂😂
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv Ай бұрын
😂😂😂 musaiwaletu paja ndi chief advisor a chakwela
@georgengwira3152
@georgengwira3152 19 күн бұрын
Nyawu izi 😂
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x Ай бұрын
Tinamva kale zonsezi DC anafotokoza kale kut kwabwela magalimoto ndalama zathu zomwe mukutibelazi palibe chachilendo tinamva zonse ndi Bon kalindooooooo Dangerous child
@falayichitsotso5371
@falayichitsotso5371 21 күн бұрын
😂😂 MCP kuyakhulatu uku Kodi ndalama muzigawa chonchozo mpaka magalimoto chifukwa chofuna kuvoteledwa iweyo ukupeleka ndalamayo ukazawina sindiye business yofuna zako Kuti zibwerere pobwerera Kwa zimenezo amalawi ndikumavutika MCP ilibe sogolo
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m Ай бұрын
Mbwelela zoyankhula za ziiii
@noahtsamdoka1172
@noahtsamdoka1172 Ай бұрын
Zinangowona kuchitika kuika pampando zidzetezi or ine school mulibe ndikutha kuonanso mchere mulibe umu tinabetsa ndithu my word is park & go 2025 na chikho ichi chitipitikire ndilo khumbo langa 😏😩😫😵
@JafaliAjusa-zg2xi
@JafaliAjusa-zg2xi Ай бұрын
Bwerlesani ma galimoto anthu azifa ndi njala anthu oipa Inu
@samsonhavenoyayshonga2609
@samsonhavenoyayshonga2609 Ай бұрын
Kkkkkkk Koma Ku MCP akusowa ndi chonena kukhala ngati akuzitsusa okha,akudziwa kuti ndiolephera
@user-hq6dq7zr1e
@user-hq6dq7zr1e Ай бұрын
Zopusa zopanda mzelu,apm my vote
@IsaacBlazio-je4tf
@IsaacBlazio-je4tf Ай бұрын
Akuluwa ngaboza akuyankhulitsa zaboza zeni zeni
@victorauwana7258
@victorauwana7258 Ай бұрын
Anthu amaziwiatu kuti mcp yaba zambili ..
@lucksongondwe8266
@lucksongondwe8266 25 күн бұрын
Maboza everywhere. Agula magalimoto ndilama zokuba m'boma. Alibe mfundo m'dalayu
@MadalitsoGama
@MadalitsoGama Ай бұрын
Ndiambweleratu oBanda wa, oti n'cha? Akawinila ku?
@JameMirward-vm4dm
@JameMirward-vm4dm Ай бұрын
Iwe nkhope yako simafna kuionapo pambali pa video 📷
@PiusChawinga
@PiusChawinga Ай бұрын
Best of luck
@happymumba2261
@happymumba2261 Ай бұрын
Zaziii zokhazokha anthu akuvutika ndi njala
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
Mcp ikutha 2025😂😂😅😅 Apm is my vote ❤❤❤❤❤
@user-gd2kl1fx1q
@user-gd2kl1fx1q Ай бұрын
Chipan ichi mbava zambiri ndi dpp paubale tionana 2025 muziona sure ndpo muzakanda
@innocentkandulu2825
@innocentkandulu2825 Ай бұрын
ndalama zilimuchipani osati ku boma. Kuoneselatu kuti ndichipani chokuba chaba ndalama boma
@user-yi4oc4xz4v
@user-yi4oc4xz4v Ай бұрын
Dziwanthu idzi mulibe utsogoleri ,mwaba zambiri ayi zikomo zambiri
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 3 күн бұрын
MCP ichoke zoona koma ku voterani DPP nde sibdingachite mistake yotero😂😂😂
@robertchitsulo8006
@robertchitsulo8006 Ай бұрын
Akulu awa aaaa ndioyakhula kwambiri mkaka uja ndiwabwino zingomvuta aribe Matama . Mwa awa mulibe usogoleri sure koma kuyakhulalitsa
@emmanuelchavula7144
@emmanuelchavula7144 Ай бұрын
Fundo zosamveka zoti sizingatukule dziko personal interest 😢 aaaaaa SKC my vote these people must respect that guy otherwise fundo ambiri mwaiwo they cannot convince Malawians to vote for mcp no way
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 Ай бұрын
Bodza la mbale wawo ndende ndilimene akunenaapali
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq Ай бұрын
Kodi mcp ikufuna chani kumalawi poti alephela kale ndiye akupangatso ndale akufuna kumalidzilatu dzikolo ifetu sitikuwafuna sugar paka 4000 y iwe chakwela ulekeletu kupanga kapeni galu
@raytavares2256
@raytavares2256 Ай бұрын
What about buying aeroplanes for Malawi than just buying cars while people are struggling with money and food including medicines in all government hospitals.
@chipiliromalola6380
@chipiliromalola6380 29 күн бұрын
APM MY VOTE 💙
@user-lj3jb6hf9f
@user-lj3jb6hf9f Ай бұрын
Kkkkk koma shaaa
@mcdonaldchikoti9422
@mcdonaldchikoti9422 Ай бұрын
I am afraid that this manifesto is too sweet, it doesn't have sound sources of such income to support all the activities. In such way, depending on grants and well wishes is not sustainable for viability of such activities and growth of the MCP😢😢
@misheckmkandawire3340
@misheckmkandawire3340 Ай бұрын
Chaima Banda our president 2030
@LuteSynos
@LuteSynos Ай бұрын
😢😢
@owenmoses9434
@owenmoses9434 Ай бұрын
Kkkk muja achitira mwana ukampeza akusakula ndiwo mumphika😮😮😮 manjenje with asingle question from Brian Banda😂😂 mpaka kusintha nkhani kuyamba zakuyela ku mtolangani😅
@williamdaka79
@williamdaka79 26 күн бұрын
Palibe fundo yeniyeni apo ndalama zichoka kuti? Ndiadyera amenewo kugula ma galimoto ndikuthandidza a malawi?
@user-oh5vs1gl4n
@user-oh5vs1gl4n Ай бұрын
awa akupita chaka cha mawachi Adadi ndikatundu awina ndithu
@user-kr1kg5hy9l
@user-kr1kg5hy9l Ай бұрын
Ana awa sangamake.
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 Ай бұрын
😢 zaziiiii!, I was thinking kuti muli ndima better policies for the Nation.😮old tired brain full of nonsense.
@TroubleKatsala-jp2li
@TroubleKatsala-jp2li Ай бұрын
Kodi mukuwakalipila anthuwao? 😅😅
@user-tn2qg1vs9j
@user-tn2qg1vs9j Ай бұрын
Iwe WA MCP mmalo mokamba zachinga muno mmalawi chaka chino chavuta muli busy ndi magalimoto ndiwe galu kwabas
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh 29 күн бұрын
Chake ochakwera akulephera kuendetsa dziko cz ma alagizi ake nao ndi olepheranso
@user-xm4pb5sq5v
@user-xm4pb5sq5v 26 күн бұрын
Kodi ndale za maiko akwa nzathu zimakhalanso chonchi???uli ndi kutukula dziko kapena chipani?
@malickjeofly7843
@malickjeofly7843 Ай бұрын
Kodi anthu amene anangobadwa ndi bodza bas😊
@BostonGwazani-hl3bg
@BostonGwazani-hl3bg 27 күн бұрын
Ine ndine area chairman koma sindingakhale ndifundo zofoka ngati izi,uyu sangakhale SG.
@user-dn3gp6yi4y
@user-dn3gp6yi4y 12 күн бұрын
Za pa usilu bs malo mokamba mavuto omwe akukumana awanthu ku mamidzi ndalama mukukambazo anthu amudzi sapezeko kalikotse chipani Cha matama ichi😂
@Boi_sheed97Boi_sheed97-cj7og
@Boi_sheed97Boi_sheed97-cj7og 25 күн бұрын
Mfundo zowauza ana .. M'malo molimbikisa ulimi ali busy kamba zansalu ndiye quantem kkkk kkkk malawians need to change mindset
@user-qx3dd7xt9c
@user-qx3dd7xt9c Ай бұрын
Wait the end not malubwa lubwa wa
@jedoforsure2842
@jedoforsure2842 28 күн бұрын
Chakwela mpaka 2030
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Ай бұрын
Mukuvera bwino abambo awa akuti kunamizana ku chipani cha mcp ndikochuluka kwambiri ndichifukwa amanamiza mutundu wamalawi. Akuti agula magalimoto komaso kupereka ndalama. Ndalama zo akunena misokho yamalawi ndi akuba. Bwanji ngati ali ndindalama bwanji kugula mankhwala kuzupatala or chitukuko koma akuti agulila anthu magalimoto pali zeru pamenepo mukaona amalawi. Munthu wakulo koma zeru alibe.mcp musamupase mupando ameneyo.
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv Ай бұрын
29:31 Awa achaima ngati ali a chief advisor a president achakwera mmmmm mmh ndipanja penipeni ndekani zikuvuta kumpandoku mulibekanthu umu mbambadi, achakwera nde mumaphunzira ndimayankhulidwe omwe ? Awa ndi cheif advisor nanga kuli apambuyo pa awa alibwanji sidovu lenileni vuto lotenga anthu opanda upangili maphunzilo ndilimeneli ,sungatenge munthu alibe upangili wa u mananger nkuzamuyi mu office popeza ndimbalewanu ayi chichukwa ameneyi nde supplier wa anthu ali pansi pake ndengati iye mmutu mwake mulibekathu ndekuti onse alipansiwa akhala opanda supply mapeto Ake kampani sipanga ndalama nde ndi izi , simungatenge banjalanu lonse kugwila ntchito m'boma including ndi ana Anu omwe , Kodi pakakhala zosayenda bwino angazuzule ndindani kapena angaletse ndindani , eeeee mwatambalalatu pawudindowu Ngati simuzachoka akulu 9:31
@DalitsoTanganyika-gw9qi
@DalitsoTanganyika-gw9qi Ай бұрын
Akulu awa sangamuuze President za nzeru
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv Ай бұрын
@@DalitsoTanganyika-gw9qi 😀😀 palibe chanzeru chomwe chingatuluke umu mbambadi
@LysonPagone
@LysonPagone Ай бұрын
Life is like a ball
@yasitafuphiri-nw2he
@yasitafuphiri-nw2he 29 күн бұрын
Briana uli khweeee !!! 😢😢😢
@SalomeSimtowe
@SalomeSimtowe 23 күн бұрын
APM 🎉
@user-tn5eq9fp2z
@user-tn5eq9fp2z 29 күн бұрын
or manyazi alibe akuyankhulamo 😂😂😂
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem Ай бұрын
Zadziiiii Magilimoto kma anthu auvutika mmidzimu nyani iwe
@user-cy7gd1go6y
@user-cy7gd1go6y 29 күн бұрын
Apm❤❤
@amaghana1999
@amaghana1999 9 күн бұрын
Sakudwaka koma akuluwa? 😂
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 29 күн бұрын
Awuladi mussah Ken msonda here is your messages 🤣🤣🤣🤣
@LuteSynos
@LuteSynos Ай бұрын
Achitsilu awaaa
@ChangeChambo
@ChangeChambo Ай бұрын
Bodza ngati chakwela moyenda chinyau agalu inu mwatikwana
@user-oj2jr6kf9c
@user-oj2jr6kf9c Ай бұрын
Kape uyu
@user-dv6rt6vb6e
@user-dv6rt6vb6e 23 күн бұрын
Mmalo mokwanisa malonjezo apa mufuna muzilemeleze nokha ndi ma fortuner
@violetnkhoma8535
@violetnkhoma8535 Ай бұрын
Mpaka ndege? 😅
@becksibrahim8404
@becksibrahim8404 29 күн бұрын
Maka ya ma vetaran ili bwino akukakamira ma udindo chifkwa sanapase chochita ngat veteran
@user-vx5vk5ss6k
@user-vx5vk5ss6k 19 күн бұрын
That’s bullshit speach your still young my friend you don’t know what’s pples fill like
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Ай бұрын
😂😂😂😂 mkulu uyu ndi mbudzi yen yen zoti ukambeko za fertilizer atchipe ai koma ukunena za fortuner yoyendera Ukat chimutu mbaaa
@MustafaKadango
@MustafaKadango Ай бұрын
APM may Vot
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw Ай бұрын
Ya maveteyo ndi mbambande Baba chaima
@enockdaisi1306
@enockdaisi1306 11 күн бұрын
Kkkk kubwelaa Fortuna. These pipo are not for development
@NumbDee
@NumbDee 28 күн бұрын
Mwayakhula mwachangu
@MnenulaSamuel
@MnenulaSamuel Ай бұрын
Mphwala lake ameneyo
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 29 күн бұрын
Civil War yayambika
@EdwardBarnaba
@EdwardBarnaba Ай бұрын
Sizikundipatsa chilimbikitso fundo zao just kungoyakhula basi ndie zomwe amadziwa a MCP
@StellaPukutani
@StellaPukutani 22 күн бұрын
Mmmmmmm
@MarciaNetonMagulinho-dq3fi
@MarciaNetonMagulinho-dq3fi Ай бұрын
Zolankhura zokhazokha zawuchitsilu bas molomot muzithandza anthu ndalamazo koma ee azikhulukira mulungu ndzopusa ukuyankhulazo
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Ай бұрын
Palibe cha nzeru apa any way DPP MY VOTE
@user-tn2qg1vs9j
@user-tn2qg1vs9j Ай бұрын
Iwe WA MCP Kuda kuli biiii galu nyama yako iwe kapeniyo ife ayi
@ShafineLouis
@ShafineLouis Ай бұрын
Athu inu bodza simudzasiya chakwera osanalowe kukhala president anatilonjeza zambili koma pano anatiyiwala nde bodza lekani
6 às 9 |EDIÇÃO DE QUARTA-FEIRA |15|05|2024
TV Sucessomoz
Рет қаралды 181
Uma Ki Super Power To Dekho 😂
00:15
Uma Bai
Рет қаралды 36 МЛН
Она Постояла За Себя! ❤️
00:25
Глеб Рандалайнен
Рет қаралды 4,6 МЛН
[Vowel]물고기는 물에서 살아야 해🐟🤣Fish have to live in the water #funny
00:53
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
NSOKHANO WA UDF KU BLANTYRE 🙌🙌🙌🙌
14:30
HOT 265
Рет қаралды 15 М.
Izeki ndi Jakobo-Njinga
16:46
sosola761
Рет қаралды 719 М.
Tikuferanji 6 April 2024
25:19
Edson Gunsalu
Рет қаралды 31 М.
Zomwe Wayankhura Patricia Kaliati Zadabwitsa Anthu
26:21
Hanifa Mw
Рет қаралды 24 М.
A MARY NAVICHA ATHA MAU KU INTERVIEW 🙌🙌🙌🙌🙌
23:51