A KEN NSONDA WALAVULA MAU KUSERIKU 🙌🙌🙌🤔🤔🤔

  Рет қаралды 8,719

HOT 265

HOT 265

23 күн бұрын

Пікірлер: 100
@Abdul-xk8dq
@Abdul-xk8dq 21 күн бұрын
Nkhope kungakhala ngati mtembo
@GogomphatsoSinosi
@GogomphatsoSinosi 21 күн бұрын
Ken msonda pa ntumbo Pako wanvaaaa
@JamesMannuel
@JamesMannuel 21 күн бұрын
Pepani abambowa amalandila mankhwala a arv mutu adzunguza mutu
@StiveKantiki
@StiveKantiki 21 күн бұрын
Mcp ikuti yatenga prayer kunena ansonda 😂😂 munthu oti kwawo olo ukhasala sanamusankhepo ndikumati prayer kkkkkk
@KhwipsFilm5050production
@KhwipsFilm5050production 19 күн бұрын
Matenda amukwana uyu
@ophlexmkondowe8107
@ophlexmkondowe8107 20 күн бұрын
MCP popanda alliance singawine mukuzinamiza
@LucianoKanyemba
@LucianoKanyemba 21 күн бұрын
Auze zoona Msonda come 2025 Kuli chigumula
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 21 күн бұрын
Inetu ndikamava kuti amsonda ndimaona ngati ndi munthu osadziwa kuti ndi Skelton anafa kale ndi mkona mmutu mwake mulibe nzeru koma skeleton uyu asatinyanse mcp singawine
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 21 күн бұрын
Zigulisani gondolosi yemweyo ndale ikakukanikan
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 21 күн бұрын
Ofayifa iweyo ukufuna kuswa mphale dzathu iweyo
@KennethKadawati-jc1el
@KennethKadawati-jc1el 21 күн бұрын
Nkhope ngati Bikiton wa zambia
@frankchavula3594
@frankchavula3594 19 күн бұрын
iwe ndiwe huge pa ndale Ken
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 21 күн бұрын
Mutu unasokonekera awa
@user-lf6qf2tw5o
@user-lf6qf2tw5o 21 күн бұрын
Mmaiwala amene adakuikan pa mpando zoonadi fulu amanyera omutola
@user-tb9wn1hb3m
@user-tb9wn1hb3m 21 күн бұрын
Komaso asonda afotokoze bwino mmene chipani ya mcp chimabeledwa zisakho zapitazo chifukwa iwowo anali alamula ndiye atiuze mmene amabela
@WilfredMathews-yl6ij
@WilfredMathews-yl6ij 21 күн бұрын
Aaaaaaa ken nsonda chijacket chachikulucho wanva idiotic , mbuzi
@user-yk1hw8kd5l
@user-yk1hw8kd5l 20 күн бұрын
Ansonda timakuziwan kut ndinu amaluzi 😂😂😂😂
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 21 күн бұрын
Kungozinyozesa ulere jkkkkk
@user-jz6lc4kq3b
@user-jz6lc4kq3b 21 күн бұрын
Choka iwe nkhape nanga mzukwa
@CharlesMpaso
@CharlesMpaso 21 күн бұрын
Chonde amalawi uyu muzingomumvesa ali ndi vuto lodwala dwala moti mutu wake sukugwira ayi 🤞
@KennethsaibaNgwali
@KennethsaibaNgwali 18 күн бұрын
MCP yatha inunso mwatha pa ndale,tsoka nyanja ndi mtunda poti oyipawo atsikila konko
@TomChikumbutso-uw9li
@TomChikumbutso-uw9li 21 күн бұрын
Mbuzi yamunthu iyi
@frankbanda7333
@frankbanda7333 21 күн бұрын
Iyi ndi galu mwayiona makutu ake awa akukula kuposa mutu wake nchifukwa nzeru alibe galu uyu
@jamesgama5489
@jamesgama5489 21 күн бұрын
Choka iwe usatinyase apa shatapu
@NabilKazembe
@NabilKazembe 12 күн бұрын
ineso ndikumweleza kuti patumbo pako wava nanyongo wamako
@user-oj5ym5uy7s
@user-oj5ym5uy7s 20 күн бұрын
Msonda ndiwe galu opanda ntchito, lakuchulukira ndi dyera
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 21 күн бұрын
Nkalamba yopandazeru asonda Malo mot muzilapilat mukupita kumwalila kukakamimila zipani bass
@kanjibamumba4963
@kanjibamumba4963 21 күн бұрын
This oid Man is something he don't know what is doing hule wa zipani mukulu uyu😮😮😮😂😂😂
@user-wi9pe2hz7e
@user-wi9pe2hz7e 16 күн бұрын
Kod alliance mwaithesa?
@HedgensChisale
@HedgensChisale 21 күн бұрын
Sonda machende ako wava
@EmercianahKasiku-en6hl
@EmercianahKasiku-en6hl 20 күн бұрын
Wandale wa nzeru Ken Nsonda kaya amudwala aliyese amadwala komaso kulibe wa muyaya and kulowa or kutuluka chipani ndi ufulu mu democracy Iwo amadzudzula pomwe pasakuyenda bwino eg Peter munthalika wakula komaso ananena ekha kuti saima nde Iwo kupita ku camp Ina sunali mulandu koma matha a Pitala mumuopa Namkhumwa paja iye saluza masankho that madala saziwa ndale za multiparty
@user-hd6xc5ud2b
@user-hd6xc5ud2b 21 күн бұрын
Ndiwe chule ndithu😅
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 21 күн бұрын
Koma muleme uyu kaje chimutu
@user-xv5pr3ji6w
@user-xv5pr3ji6w 21 күн бұрын
Kkkkk kutenga maliro kunyumba kwa mzako kukalirira kunyumba kwako ,.. mcp yatola maliro iyiii kkk
@chimwemwekankhuni7162
@chimwemwekankhuni7162 21 күн бұрын
Hahahahahahahahahahaha
@user-tl1jq2gc5b
@user-tl1jq2gc5b 19 күн бұрын
Atitu aika zipangizo mu ma tower kut azabere zisakho mogwirizana ndi a MEC ndi a ma phone akutero kalindo uyu awinadi
@user-pb1yr1jx5g
@user-pb1yr1jx5g 21 күн бұрын
Aaaaaa kudwalako inu muziyenda PP DPP UDF ACHISILU INU
@user-rc3ze2oi7u
@user-rc3ze2oi7u 21 күн бұрын
😂😂😂😂 bodza nsonda
@Johnybegood260
@Johnybegood260 21 күн бұрын
Mongo wakondwa awa tango apasani away kanga chepe akapume SI zoona ayi
@SinyoroMoyo
@SinyoroMoyo 21 күн бұрын
Mbuzi zadyerazi zilipo zambiri kuli msondayi,kuli uladi musa,kuli adausi mbuzi zeni zeni
@UseniMailosi
@UseniMailosi 21 күн бұрын
Andale amatawila kumene sikubereka alemele adalawo
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk 21 күн бұрын
Manyaka enieni
@HenryKeyala
@HenryKeyala 21 күн бұрын
Akudwala uyu muzimuona khosilo
@user-hb9sm9hn9g
@user-hb9sm9hn9g 21 күн бұрын
Mtolankhani uyu akucheza ndi tseka mkudyere
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 21 күн бұрын
Mkulu osusuka uyu watha ma plan
@AndersonInnocent
@AndersonInnocent 21 күн бұрын
Makutu nonga Nyakalemwalemwa galu Nsonda anthu akutchelenga na njala iwe na Chakwela ndinu oipa kwambili
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 21 күн бұрын
Kmtu mankhwala aja siachibwanadi eti😂
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 21 күн бұрын
Kuzimu ? Amsondo musamasewele ndimulungu😂😂😂😂
@user-gk6bf7xe9g
@user-gk6bf7xe9g 21 күн бұрын
😱😱😱
@SteveShaya
@SteveShaya 21 күн бұрын
Kungozitukwanitsapo apa malume😂😂😂
@JafferTiles-hp4mu
@JafferTiles-hp4mu 21 күн бұрын
Msonda ndi munthu woti alibe tsogolo la ndale sadziwa chomwe amafuna mundale, nawo a timveni mwasowa munthu womupanga interview kkkkkkk munthu ndi ukhansala sanakhalepo
@trinitylupapa3535
@trinitylupapa3535 21 күн бұрын
A msonda tangodya naomi misonkho yahtu tikudziwa simungagwire ntchito kwina kulikonse
@SymonNamalomba-sh3fu
@SymonNamalomba-sh3fu 21 күн бұрын
Tate wafuko la mayi ako
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e 21 күн бұрын
Manyazi akugwireni madala, mudzawina poti munaponya kale mavoti
@HedgensChisale
@HedgensChisale 21 күн бұрын
Chisiru galu wa munthu iwe
@user-ti8ds7iq8z
@user-ti8ds7iq8z 21 күн бұрын
Keni Msonda ndiwamisala
@user-cw9is2lm2x
@user-cw9is2lm2x 21 күн бұрын
Kkkk asonda ovesa chison
@user-lz5tl7gn4v
@user-lz5tl7gn4v 21 күн бұрын
Takaoneni kusongoka ngati swala 😂zima jacket over size kamunthu kopanda manyazi
@user-nj3gn5xq2s
@user-nj3gn5xq2s 21 күн бұрын
Mbuzi iyi
@user-lw9su5om5z
@user-lw9su5om5z 21 күн бұрын
Nsonda kutuwa mmutu ngat udalowa mu dengu laufa mwana opanda nzeru iwe 😅😅😅
@stellakaluluma8241
@stellakaluluma8241 21 күн бұрын
A Monday Chamba chikukupwetekani, siyani kusuta chifukwa siku Lina muzaoezeka mutavula
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 21 күн бұрын
Aken msonda ndiabodza ndiadyera chifukwa ari makutu oima kuoneserat kunama kwawo.
@mussahkachere2332
@mussahkachere2332 21 күн бұрын
Uyutu akusaka Saka pofela uyu
@user-ir8md7uq1j
@user-ir8md7uq1j 21 күн бұрын
Kkkkkkk koma sonda mukupenga misara chakwer sangawine
@mamulemathekga
@mamulemathekga 21 күн бұрын
Inendikulu mbilaapa dzangawine achakwera 2025
@StiveKantiki
@StiveKantiki 21 күн бұрын
Nsonda chipani chosiliza kulowa ndichimenecho kungoyelekeza kupita kwina uzaswedwa size kukana
@SinyoroMoyo
@SinyoroMoyo 21 күн бұрын
Koma yah 😂😂😂
@francis12fombe54
@francis12fombe54 21 күн бұрын
Kkkkkkk😂😂
@maxwellchifupa1538
@maxwellchifupa1538 21 күн бұрын
Osangoyamba ulimi bwanji, munthu kumakalamba ndi bodza mmalo molapa, vuto ndi ndalama
@yusufsadic2930
@yusufsadic2930 21 күн бұрын
Awa ndi Anthu omwe akumasokonez anthu yaw Chifukw chongochotsedw ku dpp lelo akt chakwer diwabwino
@ThomasMunyolowa
@ThomasMunyolowa 21 күн бұрын
Pita ku chipatala galu iwe
@user-nj3gn5xq2s
@user-nj3gn5xq2s 21 күн бұрын
Ndachitsiru awa
@Uncle_B265
@Uncle_B265 21 күн бұрын
Watan iwe Kodi ukuona ngati ngati ukudya tonse tikudyaaa
@Abdul-xk8dq
@Abdul-xk8dq 21 күн бұрын
Ansonda mumatelo ndani sakuziwani muzathawanso
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 21 күн бұрын
Kkkkk zamanyazi tazingobani nthawi yanu muzayaluka 2025 mavoti ndi athu osati akubanja kwanu ansondo inu mulibe manyazi sogolo lanu ndi zaka zanu zatha muzimvele chisoni
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 21 күн бұрын
Anthu ena ndiwomvesa chisoni kwambili,azavotere chakwera ndi ana akotu
@DanielnachanzaBanda
@DanielnachanzaBanda 21 күн бұрын
Koma akuluwa ndi omvesa chisoni komanso mayazi palibe.
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 21 күн бұрын
Opepera uyu mcp singawine
@GREGORYAUSTENNYONDO
@GREGORYAUSTENNYONDO 21 күн бұрын
Za🎉phavu
@josephchitsulo5882
@josephchitsulo5882 21 күн бұрын
Kodi simukumuona maonekedwe achewo? Akufa uyu pompano, sakudziwa chomwe akulankhula
@LuciusLungu
@LuciusLungu 21 күн бұрын
Ken iwe mtumbuka mnyane, tumatama bwafuke waka. Koma abale ndiye masuta durban poison chambacho. 😂😂😂
@godfreysingini1508
@godfreysingini1508 21 күн бұрын
A msonda kkkkk ukatelo ulipa ganyu
@AustinChiyembekezo-cx4mz
@AustinChiyembekezo-cx4mz 21 күн бұрын
😂
@user-uv1vu6ub5o
@user-uv1vu6ub5o 21 күн бұрын
Dyera iyaaaa kukana kulera zidzukulu uko, kumangoti uko mwalowera opanda chochita ngt Jacob maphang'ombe kk
@user-ul5hh3cz8z
@user-ul5hh3cz8z 21 күн бұрын
😂 madala wa zikuvuta ndichani kupanga Zina siyilani anyamata muli busy kuononga ziko .nanuso atolankhani palibe chimney mumafusa zopanda zeru. Afuseni kothandiza amalawi
@user-ob1wx4gf2h
@user-ob1wx4gf2h 21 күн бұрын
Dyela lizakuphani inu😅😅
@Slyvia-uu3wc
@Slyvia-uu3wc 21 күн бұрын
Polakhula muzinganiza kuti,,,anthu anavotera tonse aliyasi otsati MCP yokha ,,,akuluwa ndalama ziwapha
@MkandawileLloyd
@MkandawileLloyd 21 күн бұрын
Mesa amakutumani mbuzi yamuthu iwe
@senaherbo3714
@senaherbo3714 21 күн бұрын
A political beach.....
@user-ub9on7oj7l
@user-ub9on7oj7l 21 күн бұрын
Kodi akeni nsonda itakhala nyama ingakhale nyama yanji????
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 21 күн бұрын
Itakhala nyama ikhala nyama yagalu
@user-ub9on7oj7l
@user-ub9on7oj7l 21 күн бұрын
@@user-hm9nc7lz6e kapena kanyimbi
@victorauwana7258
@victorauwana7258 21 күн бұрын
Hahaha 😂.. vote is our key
@KennethKadawati-jc1el
@KennethKadawati-jc1el 21 күн бұрын
Kkkkkkkkkk tazingowabela okuba anzakowo unangosala chingwe pa mtengo mbuzi inachokamo mwaiwe kapolo weniweni
@coastersRob
@coastersRob 21 күн бұрын
Kodi udakalibe ndi moyo eti koma ndiye wathatu kakhosi kali njoooo
@robertchitsulo8006
@robertchitsulo8006 21 күн бұрын
Ine sindilowa ku chipani kkkkkk ndimafusa midzimu yanga kkkkkk malawi kuri zithu kkkkkk
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 21 күн бұрын
Umufuse chilima akuza za MCP, 2025 out.Ubwino wake iwenso Nsonda ukugula nawo sugar 3500, stupid.
@SinyoroMoyo
@SinyoroMoyo 21 күн бұрын
Amuonetsa nyekhwe achina mkaka kumeneko
@robertchitsulo8006
@robertchitsulo8006 21 күн бұрын
Muthu ineee Pamwai nachoka koma ndafika pa chisomo . Ine pheeeee pa boma peni peni pa zipaso .
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
Balloon Pop Racing Is INTENSE!!!
01:00
A4
Рет қаралды 15 МЛН
The magical amulet of the cross! #clown #小丑 #shorts
00:54
好人小丑
Рет қаралды 20 МЛН
NSOKHANO WA UDF KU BLANTYRE 🙌🙌🙌🙌
14:30
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
Kodi Mulandu Wa Chilima Ndekuti Watha?   Bon Kalindo
12:51
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 41 М.
Tikuferanji 20 April 2024
28:08
Edson Gunsalu
Рет қаралды 30 М.
Cruise 5 with Prophet Habakkuk Stanford Sinyangwe
1:06:02
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 83 М.
MUNTHU WALANKHULA UYU...BON KALINDO, NANKHUMWA NDI A MTAMBO!!! ZOOPSA TAMVANI
20:10
国盟虽败犹荣?|阿耀闲聊政治
9:28
阿耀闲聊政治 Ah Yau Talks Politics
Рет қаралды 76 М.
Balloon Pop Racing Is INTENSE!!!
01:00
A4
Рет қаралды 15 МЛН