A NANKHUMWA NDI AMARY NAVITCHA KU PARLIAMENT-APWETEKANA. ANANKHUMWA ZAWAVUTA🙌🙌

  Рет қаралды 29,852

HOT 265

HOT 265

Ай бұрын

Пікірлер: 93
@VioletTchuwa
@VioletTchuwa Ай бұрын
Nzimayi wanzelu Mary Navitcha❤
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
God bless navichar ❤❤
@user-cb2cv9fz7m
@user-cb2cv9fz7m Ай бұрын
Mommy osataya mtima akunama namkhumwa ndipo musamuope inu ndi boma ndipo tilinanu
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e Ай бұрын
Mulungu ndiwadzatheka bwanji akalindo mulungu azikutetezani
@VINCENTRHINO-mn6wm
@VINCENTRHINO-mn6wm Ай бұрын
Mwana akamauzilidwa mayeso namakhala number 1 khholo lopusa limasangalala Koma Kholo lanzeru limadananazo mau awa ndikutanthauza Kuti pamene aboma akuikira kumbuyo zomwe anankhumwa amayankhula zoti ndizosathandiza Malawi abomawo sadziwa Koma zomwe amayankhula mai navicha ngakhale aboma amadananazo Koma ndizomwe amalawife tikudusamo ndipo abomawo chanzeru akanapanga kunali kuwapanga sapoti mayiwa coz ziringati kuuzira mayeso zomwe boma limayenera kumapangira amalawi
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
God bless born kalindo ❤❤❤❤
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x Ай бұрын
Nankhumwa nkhope ngat dololooooo
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h Ай бұрын
Brave woman keep it up mama Navicha
@user-yf3st5yb1n
@user-yf3st5yb1n Ай бұрын
Born kalindo alakwa chani?mfuti anamuwona nayo 2021 koma mlandu ukayimbidwe lero zakhala bwanji?palowa ndale apa.
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 Ай бұрын
Mary navitcha go a head good words
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Mai Navitcha woyeeeeeeeeee ❤❤❤❤❤❤
@user-cb2cv9fz7m
@user-cb2cv9fz7m Ай бұрын
Bon kalindo umatha ndipodi musatope tilinanu be strong God is with u
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k Ай бұрын
Our pangolin, may God protect you.
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h Ай бұрын
The DCC May the lord be with you
@user-kr1kg5hy9l
@user-kr1kg5hy9l Ай бұрын
Go gooooo Navitcha.
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv Ай бұрын
Mungokuwa zaziii uku Golide wathu mukubesa ndi azungu
@KalebeSamson-bd5jw
@KalebeSamson-bd5jw Ай бұрын
Nankhumwayu ndiosokonezeka kwambiri,
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v Ай бұрын
Aphungu aboma ndiwosokoneza nanga bwanji siakuwachosa munyumba umo akakhala wosusa mukuti atuluke Fuso ndilakuti kodi umozi ulipo?
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Nankhumwa kwake kwatha sure 😂😂😂😂
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv Ай бұрын
Aphungu akewo aaaa zosaphunzira nkomwe Koma mmatsatira mmene anzanu akupangila mmaiko ena ? Mungogwilisidwa ntchito ndi atsamunda zitsirunizeni , mmaso mulimbu ndi kutuwa ndiwukapolo watsamunda Koma simukudziwa Kuti muli muwukapolo kamba kawumbuli zoti anakusinthilani design yawukapolo simudziwa mbuzi Za wanthu , ndinu omvesa chisoni ,zoona Malawi angakhale N0: 7 kumayiko oyendabwino Kodi mufuna kutukwanitsa azimanu bwanji zawuchitsiru.
@user-im4tc9qi4j
@user-im4tc9qi4j Ай бұрын
2021 mpaka lero zongolowa ndale chifukwa choti anatuluka mumgwirizano waboma koma akanakhala kuti sanatukemo mu tonse iyi sikatuluka
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
God protect our president bon kalindo munthu wosarakwa angomufunira zifukwa anthu opanda manyazi awa safuna chilungamo
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 Ай бұрын
😅😅😅😅 people you joke a lot
@issahkagansamussah
@issahkagansamussah Ай бұрын
Ndiyeno bwanji apungu abomao nsanawatulutse pamene akupanga pokosolo nyumbai nsiili bwino mbali yina
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk Ай бұрын
May the good Lord protect our president, president for the poor, the only true and trusted freedom fighter remaining on the ground, the Dddddd!!!!! Cccccc!!!!!!
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k Ай бұрын
Chitsiru si Bon kalindo, koma chitsiru ndi iwe, mulungu akukanthe mfiti iwe.
@BonfaceBanda-nh7cq
@BonfaceBanda-nh7cq Ай бұрын
Ngt kuli anthu omwe akuseweresa ndarama za boma ndi abungu omwe ali Ku nyumba ya malamulo
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete Ай бұрын
The DC may God protect you 😢😢
@pmbdepot431
@pmbdepot431 Ай бұрын
Zautsiru mulunguso chigawenga chimfutichi nyani iwe ndinu mumapha malubino demeti
@BonfaceBanda-nh7cq
@BonfaceBanda-nh7cq Ай бұрын
Nyeranitu muziona ndarama mukudyazo mutipeza kuno kumudzi, muzaziona mmalo momakambilana zithu zopindulila dziko mukungosewera muziona dikilani
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
Navitcha yemweyoooo!
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi Ай бұрын
Mcp must go out
@isaaczidana2914
@isaaczidana2914 Ай бұрын
Boni Kalindo, A mbuye azikhala Mbali yanu nthawi zonse
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
Auzen agalu amenewa aphungu akumalawi ndi mbuzi za anthu
@paulmakaula4937
@paulmakaula4937 Ай бұрын
Mumumvetse Nankhumwa ngati mmadziwa democracy
@languitoneelias9972
@languitoneelias9972 Ай бұрын
Ndale zimasaukitsa ukazitengela msuzi onse umatha
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi Ай бұрын
Mcp never win
@Uncle_B265
@Uncle_B265 Ай бұрын
Chilungamoo chimadwdwaa
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Zaziphasozo andunawo ndiye angolankhula koma ndizopanda sogolo
@hackwellkagolo6614
@hackwellkagolo6614 Ай бұрын
Ha ha ha koma MRB mavuto enieni, asokoneza zithu koma akamayankhula ngati finye, kuzipopa kwambiri koma anthu akukwanisa kuhaka system ya Malawi zachisoni kwambiri
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Eeeee bon kalindo ndi mwana oopsa kwambiri eeeee mabulubuzana kunyumwa ndi dc
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf Ай бұрын
Nankhumwa ndi chitsiru cha munthu muzimuwona nkhopeyo ngati chiswa bumbu
@ApocheC.
@ApocheC. Ай бұрын
😂😂😂😂
@GenialaChalera
@GenialaChalera Ай бұрын
Kalindo akutumidwa ndi dpp
@user-sb4om5pw2h
@user-sb4om5pw2h Ай бұрын
Ku Malawi nkokoma kwambir 😂😂
@user-gk6bf7xe9g
@user-gk6bf7xe9g Ай бұрын
😱
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Zikhare Ng'oma akunamizaso amalawi kachi keni mbamva zopanda manyazi izi
@KalebeSamson-bd5jw
@KalebeSamson-bd5jw Ай бұрын
Amalawi akufunakwabwino tiyeni tithandizane tupemphelera Dzikolathuli kuti likhareko labatandi mtendere.
@AmusedDimSum-hd5yp
@AmusedDimSum-hd5yp Ай бұрын
kodi Kanda bongoman alipo
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz Ай бұрын
za ziiiii nthawi yonseyi anali kuti ankaleka nkhaniyo kuitulutsa bwanjiii ndale iziiiiii koma samukwanitsatu ameneyo ndi mwana oopsyaaa kwambiriiii
@languitoneelias9972
@languitoneelias9972 Ай бұрын
Amapanga makani kudalira mfuti yopanda makalata
@user-vu9rt8gj3o
@user-vu9rt8gj3o Ай бұрын
Nakhumwa galu
@samalanimacdonald9373
@samalanimacdonald9373 Ай бұрын
Ma card athu mpaka 3years yosatulukabe
@TelezaMilimbo
@TelezaMilimbo Ай бұрын
Komatu boma ili ndilotopetsa zeedi akulimbana ndimunthu woti sanawabele amalawi pomwe ambiri a m'bomamo ndi mbava zothelatu
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
Ambuye mutetedzereni president waanthu osauka bon kalindo mutetedzereni kt atululike mndi amene amatiimilira
@MmikeeMateyo-kj2pn
@MmikeeMateyo-kj2pn Ай бұрын
Chitsilu galu kalindo iweyo ukumanamiza athu kuti iweyo ndi President wa athu osauka ukuwapangila chiyani athuwo iweyo koma udziti ndiwe ntolakhani wakhulu ungakhale Presidenti iweyo
@macmsiska2937
@macmsiska2937 Ай бұрын
Zopusa a Malawi
@user-lt3xl7cv5n
@user-lt3xl7cv5n Ай бұрын
Mcp bomaaaaaa
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Ай бұрын
Ine ndikudabwa mumalo moti aphungu aboma azikhala ndiulemo kunyumba iyi koma ndi amene akuyambisa phokoso. Chimene ndimaziwa ine wosusa ndi amene mwina azipanga phokoso. Kusonyeza aphungu a mcp ali ngati mowa wamasesi
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w Ай бұрын
Bon kalindo atuluka Monday pa 08 April inshallah
@ExcitedCornflowers-nw9oc
@ExcitedCornflowers-nw9oc Ай бұрын
Olemekezekaaaa?akhangwaraoooo kkkkkk
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y Ай бұрын
Lazalo ndi anthu ake mwatikwana kwambiri anthu okanika
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h Ай бұрын
Mbuzi za aphungu
@RafickAmiduh
@RafickAmiduh Ай бұрын
MCP ikupumila mphati ndi Bon kalindo ndiyeno sakudziwa Kuti angatani Kuti athane naye
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl Ай бұрын
Bone kalindo anarakwanji nangasi anapitisayekha futiyo a police akwathu yikanakhara mbudzi tikana sinthisa ku zidko Lina pamozi ndi chakwera
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw Ай бұрын
kkkkkkk.koma boma ili fertilizer mpaka April nde akathira mbatatesi chani
@henryphiri6100
@henryphiri6100 Ай бұрын
Mulibe utsogoleri mwa Nankhumwa
@JamesSpondo
@JamesSpondo Ай бұрын
😢
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Ай бұрын
Zovuta kwambiri
@hackwellkagolo6614
@hackwellkagolo6614 Ай бұрын
Zachibwana basi, Moti aphungu awawa amene akutisogolera? Ayi ndithu. Vutoso otsogolera ku wa ku parliament sulibwino or pang'ono. Ma bwalo amilandu mbolaso sindikukuziwa kuti ndi mbali iti imene tinganene kuti ulibwino
@issahkagansamussah
@issahkagansamussah Ай бұрын
Amc ili ndi nankhumwa.
@user-im4tc9qi4j
@user-im4tc9qi4j Ай бұрын
Koma apolice or kumumanga uyuyu pali phindu?
@BrightMpaha
@BrightMpaha Ай бұрын
Koma chonde amalawi Tien aliyense adzuke coz tikuvutika ndiife osat andale,,,inafe timat simudya ndale koma apapa ndikofunika kulifera dziko lathu chifukwa atsogoleri tili nawowa sakuganizila ife ndipo ndikudabwa amipinga simukupangitsa mbindikiro bwanji kuti Mulungu awakathe onsewa bwa? Mwangoti ziiii,,ku HRDC ilikutko ndi ma dem?mwangoti zii,,MDF ilikut mukuona athu anu akuzuzuka muli zii Mesa mumalimbira kuteteza dziko lanu?lero munthu modzi akukupusitsan pokupatsa ndalama,,anthu kumahaka system inu muli momuno muli ziii,,ma lawyer anthu plus tsogoleri wa nyumba ya malamulo Mulungu akukathen anthu oipa koma musangalaliretu ku mwamba kulibe chanu ndipo panopa ndili mkati mopepherera inuyo kuti akuonetsen za Yobu koma osat mukhalenso ndi moyo
@GanMapira
@GanMapira Ай бұрын
Kkkk
@mosesmkolimbo
@mosesmkolimbo Ай бұрын
za zii
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
😂😂😂😂Thumba la fertilizer kulipira January mpakana April fertilizer asanatengedwe😂😂😂😂😂😂😂 my Malawi 😂😂😂
@user-vr5jn8sz5r
@user-vr5jn8sz5r Ай бұрын
Timakunyadilani
@serakillo8668
@serakillo8668 Ай бұрын
Za njalazo munamvotera kongeresi
@mabvutochimkondenji910
@mabvutochimkondenji910 Ай бұрын
chikosa boni karind mmalo mit azithandiza anthu chakudya
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 Ай бұрын
Nankhumwa ndi mfiti ya munthu.
@EdwinMabviko
@EdwinMabviko Ай бұрын
Wamangidwa ndi Kalindo ndiye Nankhunwa wakhala bwanjiso fiti?
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 Ай бұрын
@@EdwinMabviko Ndi amene akupangitsa kuti Tonse Alliance izipanga zinthu zosakhala bwino kwa a Malawi,, sadziwa kutsutsa ku Parliament bola akulandila ma allowance ake.
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Munvere Kaye kuti akuti chani
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 Ай бұрын
@@inessmsiyambiri8517 Ndamveratu and he said no comment which means he doesn't know what to say as a leader of Opposition.
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Ай бұрын
A akwiya coz a speaker anena kuti ayambe kulankhula Navicha🔥
@user-qp9bn5ed5n
@user-qp9bn5ed5n Ай бұрын
Koma abare tiyeni tikondane kuti agaruwa achoke
@issahkagansamussah
@issahkagansamussah Ай бұрын
Pankhani iyi ya akalindoyi ikutuluka chifukwa choti nsali modzi wa tonse allance then chifukwanso choti amadana naye komano mulungu alowelerepo ndithu
@user-yh3dw6qu7z
@user-yh3dw6qu7z Ай бұрын
Mcp akunya naye bon kalindo.nankhumwa ndi nkhumba zedi
@MmikeeMateyo-kj2pn
@MmikeeMateyo-kj2pn Ай бұрын
Chitsilu galu kalindo iweyo ukumanamiza athu kuti iweyo ndi President wa athu osauka ukuwapangila chiyani athuwo iweyo koma udziti ndiwe ntolakhani wakhulu ungakhale Presidenti iweyo
@user-yf3st5yb1n
@user-yf3st5yb1n Ай бұрын
Galu chisilu iwe ukambanji?
маленький брат прыгает в бассейн
00:15
GL Show Russian
Рет қаралды 3,8 МЛН
路飞关冰箱怎么关不上#海贼王 #路飞
00:12
路飞与唐舞桐
Рет қаралды 3,8 МЛН
蜘蛛侠这操作也太坏了吧#蜘蛛侠#超人#超凡蜘蛛
00:47
超凡蜘蛛
Рет қаралды 48 МЛН
Каха с волосами
01:00
К-Media
Рет қаралды 6 МЛН
2024-05-14_NEWSHOUR0514
30:02
tbnewswatch
Рет қаралды 208
INE NDI BON KALINDO MWANA OWOPYA KWAMBIRI/13 May 2024
14:14
BILLY KAUNDA'S STORY
27:39
THAT GUY
Рет қаралды 40 М.
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
Chilima vs The Rest - Samuel Lwara
25:47
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 6 М.
NSOKHANO WA UDF KU BLANTYRE 🙌🙌🙌🙌
14:30
HOT 265
Рет қаралды 15 М.
маленький брат прыгает в бассейн
00:15
GL Show Russian
Рет қаралды 3,8 МЛН