APULE LERO ZATANI KUYANKHULA CHONCHI

  Рет қаралды 17,289

HOT 265

HOT 265

29 күн бұрын

Пікірлер: 166
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 27 күн бұрын
Kkkkkkk I think some thing is wrong with Chakwera,,,he doesn't know what he is doing.Iye ndiye wachipwirikiti heavy
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 26 күн бұрын
Khope iyi siya u president ayi koma nyawu
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 27 күн бұрын
Mbuzi nkhumba nyani like u sukutha kuyendesa Boma
@jonathankwangulero4450
@jonathankwangulero4450 27 күн бұрын
Simply put Chakwera is in Competent. He has destroyed Malawi. Sad to say, APM was better when himself was average. It just shows how doomed Malawi is. CHAKWERA mmmmmmhu - speechless
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 26 күн бұрын
Mutu wa, bwanawa unanyada ndithu Muthu osamva chison ngat njoka
@ChristopherBaluti
@ChristopherBaluti 27 күн бұрын
🎉iweo ndamene sumatha ntchiko galu weni weni
@user-fi2by2ui9o
@user-fi2by2ui9o 27 күн бұрын
Zikuchita kuwonetseratu kuti anthu ambiri omwe akupereka ma coment apapa ndi otsutsa, komanso kutsutsa kwake kwa ubulutuu
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve 27 күн бұрын
Wambula kusambila ndiwetu anthu akugwira ntchito monyinyilika
@user-qn2nu4xs9i
@user-qn2nu4xs9i 27 күн бұрын
So what did you do in four year???
@user-oh5vs1gl4n
@user-oh5vs1gl4n 27 күн бұрын
bola madala apm ❤❤❤ idzi ndie mbwelera za anthu
@user-qq1uj7ct6n
@user-qq1uj7ct6n 26 күн бұрын
Munthu wopanda mfundo ngat uyu sindidamuwonepo ndithu. Chilichonse kuchita kulembeleledwa Eishiii za manyazi
@bisweckchimphamba8497
@bisweckchimphamba8497 27 күн бұрын
4years kumanangokamba zambuyo .inu mwapangapo chiyani pa 4yrs imeneyi apart from kuba,inu ndiye mulibe mfundo
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 26 күн бұрын
Ai kuwalembera 😄! President omvesa chisoni ngati uyu nziko muno sakufunika ife ngati anthu ozindikilako mziko muno tikufuna president oti akayankhula za nzelu ngati izi azichitaso chimozimozi pa ground osati mmene umachitila iwe chakwela kdi wa ziwa liti zimenezi iweyo amalawi sukuwaziwa iwe , wachedwa oloso utapasidwa mpata sungakwanise za kuvuta.
@user-ud3vp9zb7f
@user-ud3vp9zb7f 24 күн бұрын
Good gvt all the time
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 27 күн бұрын
Adpp kukwana mwawononga dziko mkamatukwana ndiye kuti mkuziwa kuyankhula anthu osapephela nkuona dpp ndichipani zikwanje mwaonjezeso dppchipani chotukwana mulungu akuwoneni wotukwanu
@abdulrafiquekalembo469
@abdulrafiquekalembo469 27 күн бұрын
Mudapeza zitaonongeke bwanji,popeza zinthu zinali bwino nthawi imeneyo,zinthu zinali zotchipa.Iwe galu Chakwera ndi amene waononga zonse zimene zimayenda bwino nthawi ya DPP
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 27 күн бұрын
Ngati kuli munthu waononga zinthu ndi Chakwera
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 27 күн бұрын
Iyeso akufunika kuwongoledwaka
@goodvisionmedia2023
@goodvisionmedia2023 27 күн бұрын
Aaaaa mbuzi yamunthu iwe nde pomwe anasiyila a DPP ndi pano sukuwona kusiyana pano tili Pati iwe ulibe umunthu ineyo ndichewa tinakuvotela iweyo koma palibe ndinabesa vote yanga 4 year osasitha or kuti adpp anawonoga 4 year is far bro
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 27 күн бұрын
Mwasimikiza nokha apule kuti nduna zanu ndizaku church kwanu komaso ndi achibale anu aphungu wose akukuonani kuti inu abwana ndinu ogona mwanena nokha apule kuti anthu sakukuopani Mulungu akusekani kumaso ndi speech mwayankhulayo. Bwana ndinu antchito ndi amene munalemna nokha😂😂😂😂😂😂😂
@jeanbotomani9081
@jeanbotomani9081 27 күн бұрын
Anagwetsa economy ndi ndani tikuonanitu
@AustinMbike
@AustinMbike 23 күн бұрын
Munthu uyu ndiye president weniweni wa masophenya akukhazikhitsa zinthu zikuluzikulu zokha zokha, zana lomweli amayakhula za Agriculture, Tourism and minining zomwe sizinamvekepo mu mbili ya zaka 35 zathazo, more fire Mr president akufunika anthu omulimbikitsa. Otsutsawa tili nawo mpaka imfa kumasutsa ndi zabwino zomwe.
@francistsutsu4811
@francistsutsu4811 27 күн бұрын
palinso za bola, apm angatipangire chiani cha nzeru atabwereranso ndi mmene alirimo? Amalawi tiyeni timovereze kusitha maganizidwe athu
@macrinenduna1024
@macrinenduna1024 26 күн бұрын
Kuvomereza zichani? Kodi uyu akamatinamiza kuti Malawi/ ulamuliro wake wakomana climate changes, ku S.A, Moz., Zambia bwanji? Kuitenga wogodomala ife? Tayendani muwone mmene maiko ena moyo wukuyendera. Salary ya aphunzitsi apa Nyasaland ikufanana ndi ya mlonda wa muno Mocambique ukasintha meticas to kwacha. Ndiye nkumavomereza zopusazo. Chakwera komanso mlangizi wake kaya amakhala pansi to verify first a speech to be addressed to a nation as such, a shame.
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 27 күн бұрын
Koma galu chakwela kumangopitiliza kwanamiza anthu zamanyi bas
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 27 күн бұрын
Ndiye kuti wa uletsi ndi mwini chakwela yemweyo😂😂😂😂😂galu yomweyo
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 27 күн бұрын
Fact
@Slyvia-uu3wc
@Slyvia-uu3wc 26 күн бұрын
Kodi amatidyetsa thawi yonseyi anali chakwera patumbo pa make ndithu
@yasitafuphiri-nw2he
@yasitafuphiri-nw2he 27 күн бұрын
Chakwera is changing malawi government amicably, by 2030 things will be in right channel 😊
@user-ee6be5kl5o
@user-ee6be5kl5o 27 күн бұрын
Pulezidenti uyu zoonadi alive nzeru poyankhula angochooka aneneyu ndipo alibe manyazi tulani udindo mwalephera basi osamangodya ndalama Zathu Za misonkho ayi palibe chimene ukuchitila anthu a mmmalawi
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 27 күн бұрын
President anati,kwa anthu oputsafe,azatsitha, Malawi pa two years lero, history ingochulukilabe.kuba,kwachuluka Burkina Faso yatenga boma,lawo,ife tilikale.lero, Burkina Faso yatsitha kupotsa, malawi.mr president chilungamo chikuwasoeekela,manyazi bwa?mutu mphwiiii munamizile,ogwila ntchito?
@IsmailBrighton-gm4tl
@IsmailBrighton-gm4tl 27 күн бұрын
Lkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ayayaaaaaaaaa
@gminsuranceassesors6611
@gminsuranceassesors6611 26 күн бұрын
Munthu woyambirira kuti akaphunzisidwe ku sukulu imeneyi ndi Chakwerayi akathale limodzi ndi Zamba wakeyo. Anthu omwe akubweresa chipwirikiti ku Boma ndi ma bulutu amenewa.
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w 27 күн бұрын
Komatu munthu amene walemba speech imeneyi Ali pandale zomwe chakwera sakudziwa apa chakwera akuzidzudzira yekha kkkkkkkkk walemba speech imeneyi I salute
@FrankDimaria-oy9zu
@FrankDimaria-oy9zu 27 күн бұрын
😊achakwela pepani anthu ambili osatha ntchito mudawalemba nokha apatu sikuonetsa kti wapatsogolo saziwa ntchito uyutu ndiye chakwera ntchito yomwe ife tinakutuma yakubvuta usanamizile ena wachedwa 😅😅😅😅😅
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 27 күн бұрын
😂😂😂😂..koma amalawi timanamizidwa ndithu eeeich nkuluyu waonoga dziko kwambiri
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d 27 күн бұрын
Chakwera ulibe zelu iweyo ndi garu bola garu ankhoza kukhala ndizeru
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 27 күн бұрын
Mmmmm ngati ndimutukwanetu mbudzi imeneyi anthu lero akulephera kugura sopo chifukwa chaiwe kukweza mtengo chilichose iwe bwantasa zed
@gloriambale2277
@gloriambale2277 27 күн бұрын
Chakwera ndiwe khuluku oyambilira bas uziti khuluku wachani apa .....tamangodya ndramazo 2025 ndipafupi apa
@user-rl5zq1qr4d
@user-rl5zq1qr4d 27 күн бұрын
akuwombera mmanjawo ndi aganyu omwe sakudziwa chimene akuwombera mmanja awayimika kusogolo kuti alamati lyololo lololo zizimveka 😂😂😂😂😂😂😂 mminyo mwanu mabvuzi atali kupitilira mboliwo
@kubengovender6996
@kubengovender6996 27 күн бұрын
Sharp big!!
@user-mv1ho9pp7o
@user-mv1ho9pp7o 26 күн бұрын
Ndiwe opusa kwambiri nthawi ya Peter sitimagona ndi njara koma uyu analowa boma kut adzaphe anthu ndi njara nthawi ya Peter chimanga chimapeza paliponse paja mumkati tikupita ku kenani uku ndi kukenani kepana tili ku guputo chakwera ndiwe galu ulibe fundo
@GreevinMugowa-tk9bp
@GreevinMugowa-tk9bp 27 күн бұрын
Satha kulankhula uyu,, Ndipo saziwa chomwe akutanthauza
@user-ku5fs6lv4n
@user-ku5fs6lv4n 27 күн бұрын
Nanga zukhala bwanjiso apa? munthu kumadziwa vuto lako koma osakonza.mmmm ai ndithu
@user-vq7rs7zj2r
@user-vq7rs7zj2r 27 күн бұрын
Chakwera nduna zako zikukunamiza kwambiri trust me
@jomochirwa
@jomochirwa 27 күн бұрын
Mwalankhula mochedwa kaya apule ,azanu amuluzi adanena izi pa masiku woyambilila atangolowa m'boma kuti mcp idatenga kena kalikonse.
@user-ig7dv8rp7r
@user-ig7dv8rp7r 27 күн бұрын
Mbuzi ya muthu saziwa ntchito ya president
@user-kj7hr2jf1l
@user-kj7hr2jf1l 27 күн бұрын
Chakwera bwanji asatura pasi udindo wakurepherani
@ClintonMpiyama
@ClintonMpiyama 25 күн бұрын
Kkkkkkk nkhaniyi sikumveka bwino
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 27 күн бұрын
Apa tilikubundurwa palibe chanzelu apa 😂
@jamusnamwino-br2iz
@jamusnamwino-br2iz 27 күн бұрын
kkkkkkk koma gayz uyudi ndilazalo waumbawi kkkkkkk
@user-cp7hu6xu8h
@user-cp7hu6xu8h 26 күн бұрын
Mbuzi yamunthu Kodi timagula bwanji katundu munthawi ya DPP soap Suga chimanga komaso frtereza inuyo Dola mwapanga chain ziko muno achakwera tioneseni zomwe mwapanga
@MikeMalinga-xx8ys
@MikeMalinga-xx8ys 27 күн бұрын
Zomwe akuyankhula sizikumveka ndimamvela kuyankhula kwa Peter munthalika.. zonse zomwe akuyankhula ndimveka zokomela amalawife
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 27 күн бұрын
Wotukwananu chakunkhuzani ndichiyani akuyankhula zaanthhu wogwira ntchito mboma ulangizi ndiye inu mkutukwana chani adpp satana wazaza mkamwa mwanu mopanda manyazi zisilu
@tasmania527
@tasmania527 27 күн бұрын
Asiyeni akhalira kutukwana mpaka zaka 50 wo. Anthu amenewa anazolowera chisawawa ali mboma.
@CyprianoSandalamu
@CyprianoSandalamu 27 күн бұрын
Anthu mutukwana chakwera mavuto onsewa adabwera ndi iyeyu?panzaka 26 , munthu angathane ndi mavuto azaka zonsezi munthu walamula zaka 4,bodza limenero, mavuto awapezadi ndipondi zoona,Inu adpp kukadakhala kuti president peter amayendetsa bwino boma likadakupumukani?
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 27 күн бұрын
Ndengat anapeza zinthu zitaonongeka iye sakukhoza bwanji Bulutu
@MphatsogiftJerejr
@MphatsogiftJerejr 27 күн бұрын
Imagine kumanena izi lero after 4 years za ziii
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 27 күн бұрын
Kod anayamba kumwa mowa eti😂😂😂😂😂
@JafaliAjusa-zg2xi
@JafaliAjusa-zg2xi 27 күн бұрын
Awa ndiye ndi manyi kwambili
@LawrenceDickens-jk3zx
@LawrenceDickens-jk3zx 27 күн бұрын
Palibepo chanzelu apaaaaa😢😢
@YamikaniBwanalichisale
@YamikaniBwanalichisale 12 күн бұрын
Mesa inu mudabwera kudzakonza zoonongekazo
@IsaacBlazio-je4tf
@IsaacBlazio-je4tf 27 күн бұрын
Koma ndie kuwerengadi😂😂😂😂
@JamesMalango
@JamesMalango 27 күн бұрын
President uyu ndy madzi amphale eni eni
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d 27 күн бұрын
Chakwera patsolele ose takhala nao kuno kumalawi palibe waba ndalama kuposa iweyo ndi ana ako pankholo pamako wamva galu iweyo eti
@user-yk3wc9ei5g
@user-yk3wc9ei5g 27 күн бұрын
Ukanakhala wanzeru sukanawerenga zimenezi wakulem berayo akunena iweyo.
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 27 күн бұрын
Kodi iwe chakwera ukurakhura fundo zopanda zeru iweyo ukuona.kuti anthu akufa ninjara bwanji osasisa mitengo ya sugar nikatundu wina wambiri omwe unakwera mitengo anthu.akumizi akuvutika iweyo ungorakhura zako zamutu siyira peter ayendese boma osati iweyo poto poto miyendo apa umaona ngati u president niophweka wapha anthu ambiri iweyo chakwera ndiwe sataniki iwe ni bushiri bolani bushiri osati iweyo chakwera mapazi ako ndithu
@mailosyasin3110
@mailosyasin3110 27 күн бұрын
Koma adpp mmmm mukuonjeza kutukwana bwanji mudikile 2025 kusiyana ndikumangonyoza inde tikudziwa kuti chakwela zikumuvuta pena koma mmm mwanyanya tele tsoka ndilo 2025 Muzakalepheranso kuwina muzangosamukatu kkkkk
@user-vl8uw8mc3u
@user-vl8uw8mc3u 18 күн бұрын
Vomelezani mwalephela basi mupuma posachedwa muzidikila milandu yotibela ndalama zathu
@user-if3ny3wm3j
@user-if3ny3wm3j 26 күн бұрын
Koma azinu mmmmm mulindivuto kwinakulikose bwana koma kuchoka uko milomo mbuuuuu iyeo akukakhua kunyumba kwake imwe mavuto thoooooo koma muli zooooona abwana ndiye amuna anumukawachula kuti ndani Koma mumavesa chisoni ndinthu
@CapherineKatemangu-ml9yq
@CapherineKatemangu-ml9yq 27 күн бұрын
Kodi zinsiru za azimayi zikuombera manjazi zili ndinzeru koma
@jameschidafumbwa1039
@jameschidafumbwa1039 26 күн бұрын
😂😂😂😂 this guy is sick, osapita kunja, iweyo ndiye oyamba kupita chipwilikiti chipose pa menepo?
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 27 күн бұрын
pansana pa mako iwe chakwera😊
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 27 күн бұрын
😢😢koma unkapemphera zoona iwe chakwera?
@user-fp5qn5ci2v
@user-fp5qn5ci2v 27 күн бұрын
Owoo? Pano nde anthuwo akutha kugwira ntchito? Koma musamaapezese anthu choyankhula
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias 27 күн бұрын
Nde mwati akuwelenga mbwelera zi?? ++😂😂😂
@DIRECTORJARVMACK
@DIRECTORJARVMACK 16 күн бұрын
Ndiye umalonjezelanji zonse zija?
@JohnMasauko
@JohnMasauko 26 күн бұрын
Zomomela nokha munthu agwira bwanji ntchito molimbika tea asanamwe ndi sugar mmene akuduliramu komaso mmene zinthu zakwelera mitengomu za ziii
@user-li8kh7sx2x
@user-li8kh7sx2x 27 күн бұрын
Chakwera or kupanda kupanga campaign iwe udzawina social media isakuphwanyitse mutu braz ndi ya temporary 2025 chakera Moto kuti buuu!
@user-it7xg7sc3w
@user-it7xg7sc3w 27 күн бұрын
Satha
@user-cy7gd1go6y
@user-cy7gd1go6y 26 күн бұрын
Kape iwe ndigalu kwabasi
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 27 күн бұрын
Awa asatikwanepo school yanji iyeso akufunika school chifukwa ndiokanika
@StiveKantiki
@StiveKantiki 27 күн бұрын
Ndiye bwanji sunkasiya kuchiyambi kt akhoze anaonongawo mbuzi yamunthu tizamanga banja lako lonse uzaona
@lestermaide-yy4xy
@lestermaide-yy4xy 27 күн бұрын
Very fantastic and helful
@marryphili5419
@marryphili5419 27 күн бұрын
Chisilu iwe mbuzi Garu pamene wumalowa mu boma kwacha inali yakugwa mesa iwe amene wunagwesa kwacha Kuti wuziba bwino ndarama mbamva iwe vuto sufuna kuvomereza Kuti zakukanika
@chizandaesau4611
@chizandaesau4611 27 күн бұрын
Amwene chisanipo nkhopeyanu tipange concentrate massage
@user-yi4bs3cd7w
@user-yi4bs3cd7w 27 күн бұрын
Mbuzi mbuzi
@user-hl3vl9nt1b
@user-hl3vl9nt1b 26 күн бұрын
M'mene mukugonelamo ndizowonadi
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 27 күн бұрын
Nthawi yako yatha Chakwera 2025 ukapitilize ubusa
@TsalaniponDan
@TsalaniponDan 27 күн бұрын
My president
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x 27 күн бұрын
Mbuzi ya Mano kunsi umatengeranji boma loonongekq nkhope ngat choseterq anyan😊
@AmaduJuma
@AmaduJuma 27 күн бұрын
Gwape uyu,mbunzi yopanda mzeru,kakalima achakwera
@user-rn5ff7fn9c
@user-rn5ff7fn9c 27 күн бұрын
Nde iweo sukusakaza?
@user-yk3wc9ei5g
@user-yk3wc9ei5g 27 күн бұрын
Uyambe wapitalu School yo iweyo Chakwera
@owenmoses9434
@owenmoses9434 27 күн бұрын
Kkkk akuwelengaet analemba chimwendo 😂😮😮😮 koma uyu guys??
@user-vp8mr5ot7q
@user-vp8mr5ot7q 27 күн бұрын
Chauta amutenga uyu before election mungoti pheee! Sangangamzumze mtundu wa anthu
@UmaliDaili-nd6uu
@UmaliDaili-nd6uu 24 күн бұрын
Galu wamuthu choka apa iwe ukuona ngati athu ali mtulu tikumana 2025 kukachipinda
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 27 күн бұрын
Ladzalo ulibe nzeru ulufuna unene kuti mcp ndi omwe akutha ntchito mbusa opanda nzeru dziko lakukanika
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 26 күн бұрын
Something is wrong with our president
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 17 күн бұрын
Mose adafunsa Mulungu chifukwa chomwe adzalangire anthu ena ndipo.Mulungu adamuuza kut apite kut madimba komwe kumalimidwa tirigu.Atafika adspeza kut anthu akugwra ntchito zosiyana siyana .Ena amakolora ndipo ena amaotcha zotsalira zake.Mose (AS) atabwelera Mulungu adamuuza kut anthu aja amaotcha nphwepwa chimodz modxinso alipo ena anaoneka ngt anthu koma nd mphwepwa za dziko lapansi ..choncho musakhale odabwa.dziwani kut kukhala ndichuma sikuopa Mulungu chifukwa Mulungu anamadalitsa amene wamufuna ....km anthu anakuuzan za MCP km kusanva.kodi Mbuzi inabereke bakha? Tiyeni munavotera nokha tiyeni nazon
@GogomphatsoSinosi
@GogomphatsoSinosi 26 күн бұрын
Iwe ndi GALU kwabasi
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 27 күн бұрын
Kodi mukuziwa kut panopa peter afika pa saizi yozikhonzera yekha chifukwa chokalamba anazikhonzera ku mangochi
@user-qi8xe7qh1e
@user-qi8xe7qh1e 27 күн бұрын
Achakwela mukamanena kuti munapeza m'boma mu anthu osaziwa ntchito mukufuna kutha ndauza chani osaziwa ntchito kapena osaziwa kuba ndalama zaboma
@user-gq1lj6nc8h
@user-gq1lj6nc8h 27 күн бұрын
Tazingadyani misokhoyo bas iyyaa
@user-xe9el5qk9h
@user-xe9el5qk9h 22 күн бұрын
Kape
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 27 күн бұрын
Chiboma chokwelera ichi DPP inatha kale pitala mukungochedwa pitalayo a dzavotela chakwera nudziwa ine saona chifukwa chokalamba DPP sadzaiona
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 27 күн бұрын
Uyu munthu akufuna anthu azimunyozaeti zimene opangazi
@macrinenduna1024
@macrinenduna1024 26 күн бұрын
Mbuzi ya munthu
Tikuferanji 11 May 2024
25:11
Edson Gunsalu
Рет қаралды 12 М.
I MADE A CARDBOARD SWING!#asmr
00:40
HAYATAKU はやたく
Рет қаралды 30 МЛН
ISSEI funny story😂😂😂Strange World | Magic Lips💋
00:36
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 116 МЛН
路飞关冰箱怎么关不上#海贼王 #路飞
00:12
路飞与唐舞桐
Рет қаралды 3,8 МЛН
Skeffa Chimoto Apresident new Audio Official
8:35
Yathu Music Official
Рет қаралды 72 М.
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
NSOKHANO WA UDF KU BLANTYRE 🙌🙌🙌🙌
14:30
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
Cruise 5 with Prophet Habakkuk Stanford Sinyangwe
1:06:02
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 83 М.
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
A MARY NAVICHA ATHA MAU KU INTERVIEW 🙌🙌🙌🙌🙌
23:51
NKHANI ZALERO-TSOGOLO LA TONSE ALLIANCE LIKUYENDERA PATIPO?
17:17