NKHANI ZALERO-TSOGOLO LA TONSE ALLIANCE LIKUYENDERA PATIPO?

  Рет қаралды 21,292

HOT 265

HOT 265

28 күн бұрын

Пікірлер: 33
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 26 күн бұрын
Mbuzi za anthu, akanaletsa chakwera ndi chilima okuba enieni.
@user-ub9vb3qh4p
@user-ub9vb3qh4p 25 күн бұрын
Iwe uzichosapo chinkhope chakocho ndi zimaso Zako zazikuluzo tikufuna tiziona nkhanizo bwino
@kubengovender6996
@kubengovender6996 26 күн бұрын
Big up brother man!!
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 26 күн бұрын
Mgwirizano wa tonse adangotilakwila kuchotsa boma la DPP, anthu amasangalala kusiyana ndi mavuto ali panopa.
@user-fl7br3dw4h
@user-fl7br3dw4h 26 күн бұрын
Chisilu chophunzila bwino Chief justice uyu mbudzi nayoso yokuba chakwela ndye kachisilu ndi mbamva izake chilima anthu okuba awa palibe azawavotele
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 25 күн бұрын
America yaretsa olakwika .I think aphonya
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 26 күн бұрын
Bwanji Amalora mbudzi Chakwera kulowa dziko la America pamene iyeyo ndye mwini wakubayo
@SymonNamalomba-sh3fu
@SymonNamalomba-sh3fu 26 күн бұрын
Useless wicked Chief Justice
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 24 күн бұрын
Asiya mbava zenizeni
@GeoffreyShariff
@GeoffreyShariff 25 күн бұрын
Ulemu kumpando muyetsesa kutifukulira khani
@PetersonMvahekhe
@PetersonMvahekhe 18 күн бұрын
Wosamatinamiza abale
@MathewsMANDUTU-lh6oo
@MathewsMANDUTU-lh6oo 25 күн бұрын
Kkkkkkkkkkkk Koma uwu ndi umboni kuti boma la chakwera lazadza ndi m'bava,,,, ndye ena mukamakakila kuti chakwera ukuyendetsa dziko bwino uyu ndi amene ali patsogolo Kuba ndalama amalawi.
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr 26 күн бұрын
Kodi zoti ukamaika nkhani usamaikepo nkhope yakoyo sizimveka kapena mwano? Kunena zoona umabowetsa program yi and kumangolankhula mwachidule mitu yankhaniyo. Aford munaitha kupatuka nsanga, Nanu a Utm pangani zomwezo changu. Mcp sitikuifunanso next year
@clivendecha8554
@clivendecha8554 26 күн бұрын
if you really wna people to support your channel, you should remove your chinkhope when u playing the upcoming video.... just do intro then leave the news playing without your face on screen but you can always show up and comment after the news.
@rashidadan2533
@rashidadan2533 26 күн бұрын
Remaining chakwela and, saulos Chilima ,
@ThokiseWiriyam-ws1ec
@ThokiseWiriyam-ws1ec 25 күн бұрын
Mbava zokhazokha
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z 26 күн бұрын
NO PANI NO GAIN NGAT AMELICA IKUFUN KULESA ANTHU INDAKAYABA KULESA ACHAKWEL NDI ACHILIM
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 26 күн бұрын
Akukondera apa achina mkaka akuyendera ma galimoto odula asattar chilungamo apa chasowa..
@user-xo2hi3vu8k
@user-xo2hi3vu8k 26 күн бұрын
Tachioneni maso chili phenipheni ngt chiziri plz mukubowesa khope yanu isamaoneke
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 26 күн бұрын
Mbava chakwera ukutumikira iwe ndiapananja lako gonthi foseki
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 26 күн бұрын
Chilungamo apo chasowa achina mkaka nanga awsiyilanji?? Ma galimoto akuyendera, a a akangotenga onse omwe Ali pa list paja aaaa
@ChimwemweMagombobanda
@ChimwemweMagombobanda 26 күн бұрын
Chitukuko chilichonse angoti ku Lilongwe basi ,,mavoti muzatengeso komko
@MarthaMalopa-kw9xw
@MarthaMalopa-kw9xw 26 күн бұрын
Koma Malawi Judiciary ndi nyatwa! Kkkkkkk hahahaha
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 26 күн бұрын
Chakwela mbava chilima boma 2025
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 26 күн бұрын
Ife tikuona kuchedwa kuzavotera dpp
@user-sb8hi8vc9w
@user-sb8hi8vc9w 25 күн бұрын
Ika Manda mapaz Anu athu achinyengo inu muzaziona tiyen nazo
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z 26 күн бұрын
NO PAIN NO GAIN WHAT ABOUT CKWEL AD CHILIM CHINYENGO AMELICA BWANJ IKUSIYA CHAKWEL NDI CHILIM
@DylesMtenje
@DylesMtenje 26 күн бұрын
Olo tivote mawa mcp paulendo
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 26 күн бұрын
Asova a tonsewo
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v 25 күн бұрын
Malawi akuvuti pano chifukwa cha anthu wozenga milandu
@JamesMalango
@JamesMalango 26 күн бұрын
Enawo awasiya pati?
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 26 күн бұрын
Thanks
@ConeriasPhiri
@ConeriasPhiri 26 күн бұрын
Kumavotera chocho
SHE WANTED CHIPS, BUT SHE GOT CARROTS 🤣🥕
00:19
OKUNJATA
Рет қаралды 4,2 МЛН
Did you find it?! 🤔✨✍️ #funnyart
00:11
Artistomg
Рет қаралды 15 МЛН
Эта Мама Испортила Гендер-Пати 😂
00:40
Глеб Рандалайнен
Рет қаралды 9 МЛН
Маленькая и средняя фанта
00:56
Multi DO Smile Russian
Рет қаралды 2,5 МЛН
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
Kodi Mulandu Wa Chilima Ndekuti Watha?   Bon Kalindo
12:51
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 41 М.
Skeffa Chimoto Apresident new Audio Official
8:35
Yathu Music Official
Рет қаралды 72 М.
A Boma akufuna kumugula Kalindo kuti asiye kuzudzula boma
15:10
CRUISE 5 WITH LILIAN ESTELLA PATEL PART 1
52:10
Zodiak Malawi
Рет қаралды 16 М.
A Lyton Mangochi Awawuze A Malawi Chilungamo - Bon Kalindo
13:46
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 21 М.
SHE WANTED CHIPS, BUT SHE GOT CARROTS 🤣🥕
00:19
OKUNJATA
Рет қаралды 4,2 МЛН