I don't think that the government has to review everything to the public
@TONYJUSTIN-cx7yt Жыл бұрын
Iweyo ase the best of the best history in malawi 🇲🇼 👌
@onester4946 Жыл бұрын
This journalist is genius. Umafufuza aise. Big up. I like how you use deep knowledge to research news. Chakwera is killing refugees.
@bernadakim6544 Жыл бұрын
Kod ndinu muli ndi ka KZbin Channel kanu kopepela mumakatcha bakili muluzi 🤣🤣🤣, zot kutali pass out week yatha ya ma cadet simumaziwa? Zot kunafika ma general from different countries like Zambia, Rwanda, eswantin, Mozambique,Kenya, Tanzania pamwambowo chifukwa ena mwa omwewa amapanga pass out are from those countries simukuziwa iyayi? Page iyiyi yazaza NDI ma bulutu.. very foolish, stupid and ignorant.. ka school kaja pena pake kamathandiza
@devlinebhema2729 Жыл бұрын
@@bernadakim6544 bulutu nd iwe aise palibe akukukukamamiza kut uzinvela
@thomassimbaya197 Жыл бұрын
Watching from Zambia muchinga province God bless you,you are the best,
@ancientnkhata1137 Жыл бұрын
This journalist is very great.
@EmmanuelThom2-xf6ij Жыл бұрын
More thanx bro 4 keeping us updated
@yasinkamwendo-jf7sc Жыл бұрын
Big up brother King 🤴 of history ❤❤❤
@MamaEmma-h3iАй бұрын
I like his narrations. He is good.
@honourablesc97tv Жыл бұрын
One of the best Channel🔥🔥🔥🙏🙏😍
@successngoma Жыл бұрын
Malawi 🇲🇼 God help us
@argentchilanga3246 Жыл бұрын
Zikachitika timvera Kwa inu big man give us more zomwe zikuchitika mziko lathu from South Africa
@matamandonkhoma8163 Жыл бұрын
You stand for Us Boss
@chitimbethegreat-pc1bp Жыл бұрын
Chakwera ndi mzake chilima have change Malawi to den of robbers
@davenchimadzi6529 Жыл бұрын
Asazakunamizeni chakwela sanali m'busa wa mulungu. Awawa ndmaplan omwe akupanga kukhomzekela zisankho gyz tisamale kufa anthu kuno😭😭😭😭
@ManuelMalunga-fl3vq Жыл бұрын
Yaaaaah oooooh!! Point iyi zedi thanks brother Wanga 😢😢
@WilliamChopika-d1z Жыл бұрын
Inuyo munadalitsika boss much respect, izizi nde zikufunikila mu dziko lathu lino
@andersonmaster8055 Жыл бұрын
Best chanel than ever
@misianguisheraufi4803 Жыл бұрын
This is nice narration, evidence based journalist
@mateyudyton4739 Жыл бұрын
Good work brother keep on informing us
@mathiasmajamanda5797 Жыл бұрын
This is great and well explained
@wilsonsawasawa3794 Жыл бұрын
You are the best! Big up
@rashidstamburi2705 Жыл бұрын
Big up 💪🏻
@ahmedmsume1489 Жыл бұрын
Koma ase iweyu u can rule Malawi coz u know history alot
@ManuelMalunga-fl3vq Жыл бұрын
Ndipo zedi brother ndidolo uyu zed
@farookousmane715 Жыл бұрын
King of history!
@drbanda6105 Жыл бұрын
Bbe up♥️♥️♥️
@chekiamaabdul5083 Жыл бұрын
Asilikali a Malawi ndiye kuti ntchito Samatha??? Mpaka kuwabweletsela asilikali adziko lina aaaaaa shame
@martinkhozombah Жыл бұрын
Keep up the good work boss
@JeanMarieNsengiyumva-qu9vm Жыл бұрын
😭😭😭😭😭yoooooohhh Mulungu Tetezelani ana akoo
@titomethiwa4213 Жыл бұрын
Ndimakunyadilani big man koma ndimafuna ndifunse zikuwoneka kuti kangame ndimuthu oipa kwambiri koma sangakusakeni inuyo chifukwa ndimuthu oipa
@ManuelMalunga-fl3vq Жыл бұрын
Amakhala Kuti iyeyonso Ali well safeguarded by his people boss
@johnchavula3282 Жыл бұрын
Thanks but please do Hosni Mubarak
@innocentissah2636 Жыл бұрын
Chakwera khala serious osaononge dziko la Malawi ndi nkhondo, ona ku DRC nkhondo yemwe amalimbikitsa ndi Kagame yemweyonso,kulira kulowetsa zigawenga m'dziko zoona, watitopetsa ndiwe munthu osaganiza.
Chakwela ndichitsiru kwambili angalole bwanji asilikale alowe mu mziko ngat muli khondo , Nundwe naye angokhala ngat alibe mutu zautsilu kwabwas nkondo yili ku ukraine not ku malawi
@daviemafunga Жыл бұрын
Munabadwa masiku okwanira brother mumakwana heavy
@promisemakawa1556 Жыл бұрын
Atsogoleri aku Malawi ndi zitsiru
@justicenyirenda2049 Жыл бұрын
Timva zinthu🙌
@levisondaka6392 Жыл бұрын
This is true story I remember well my friend from Rwanda who were taken to that country they were killed by this guy's truly you can feel bad what I Saw that time please work up Malawi
@Ntatesibusisombata Жыл бұрын
As malawian citizens I will never allowed this nonsense to happen m"boma liyenela kuwasiya anthuwa tizikhalanawo mwantendele ngatimene timakhaliramu osamati kumazuka ndikumasawusa mitima yaanthu osalakwa
Koma chakwerayu ndi buzi yamunthu akulolawesa zigawenga ziko zoo a
@kuziririzaisabatosiitegeko7088 Жыл бұрын
Kagame anayambitsa nkondo mu drc,njira zimene anazera mukulowa drc ndizimene ukuzera kuyambitsa nkondo ku Malawi!
@marthankhoma1063 Жыл бұрын
Akuyanjana ndi anthu oipa kufuna kusokoneza bziko la Malawi
@maxgulani1391 Жыл бұрын
Chakwera ndi Mbuzi yamunthu ameneyi angobwerera Ku church basi
@pastonmoda-pk4uj Жыл бұрын
Koma mulungu akuwaona sangasanglale muthu akuvutika chocho
@ibrahimatibu8784 Жыл бұрын
Malawi kwathu bass ndi mbili yakale palibe chabwino misonzi yokha kumangotuluka
@NeoMaphango Жыл бұрын
😢Yo
@ShinglaiAli-be3ynАй бұрын
🔥🔥
@nyararaishumba9288 Жыл бұрын
Chakwera walandilapo ndalama pamenepo afuna aphese Anthu bas
@ManuelMalunga-fl3vq Жыл бұрын
Kwambiri zedi iye wadyapo miyoyo yathu ikupululuka😢
@AlexKaunda-ir6rz Жыл бұрын
😂😂😂 Apolice akumalawi mavuto awanthu
@lewisbonongwe8518 Жыл бұрын
Malawi lero Ali pa mpeni vuto ili Matsatatsata Amalawi lero ndi izi Ntchito Qne million zija ma Mega farm aja Kudya katatu kuja ndikumeneku amalawi kususuka lero ndi nkhondo iyo
@henrymunthali1280 Жыл бұрын
Kkkkkkk pot ndi akuda akanakhala ogalukila achizungu mukana khala chete
@molicieeosama8877 Жыл бұрын
Kagame He going mad naw
@AlickNyirongo-cp1dn Жыл бұрын
chakwela sure bt niphala la munthu angalowese asilikali a ku ruward sure
@yampanyamulenda9377 Жыл бұрын
Whaooww 😲😲 I can't believe that in Malawi you have such brilliant journalist 🤔🤔 Tell them, teach them 😂😂😂 Many people don't know exactly what we be the consequences of the presence of this rwandeses on the Malawi land
@jacquesnsabiyaremye3166 Жыл бұрын
Apapa zayambika, Chakwela akusewela ndi team((Rwandan Solders) imene sakiyidziwa. Anthuwa amalora kupeleka ndalama iliyonse cholinga aketse mwazi(Blood) basi. Mukaitsatila bwino nkhani mupeza kuti boma la Malawi lalandira ndalama za nkhani nkhani cholinga Ma Refugees asowe mtendele basi. Si izi Zayayambika ku Chileka ndi madela ena ndi ena.
@Rafiki-pk7hw Жыл бұрын
Chakwala ndikamukonsa koma mmmm ndaona kuti ndi manyi amuthu
Mcp yosogozedwa ndi Apuledenti a mpingo shame .alola bwanji zimenezi 😢
@georgekalichero7829 Жыл бұрын
Mmmmm kagame ndiwachabe
@mansonchinkhuzi Жыл бұрын
Zikhale asabwerere mmbuyo kufikila awavachoke basi akakhale ku chitipa pakati padziko ayi ati takana amalawi amasomphenya
@rosseshaibu1576 Жыл бұрын
❤❤❤
@oscarkachale9234 Жыл бұрын
Live them
@nashoniclifford172 Жыл бұрын
Wait Malawi idzazindikira bwino patsogolo
@frankmajawa528 Жыл бұрын
Km iziz sizabwino these ppo came here bcoz they wanted peace and they hav sweat alot fo them to get wat ever they hav now penapake ndbwino kumaganiza kut ndtakhala ine ndkupangidwa zimenezo ndnganve bwanj, God must be the only helper
@emmanuellemson2683 Жыл бұрын
Mamvuto osewa akudza kamba ka gulu lomenyera ma ufulu nd omwe anakankhira dziko la malawi ku gahena pofuna kuti chakwera ankhale mtsogoleri wadziko la malawi.
@GraceBeza-d7o Жыл бұрын
Chakwera akuononga nziko 😢😢
@gladysbonongwe1038 Жыл бұрын
Kobasi
@rickiez Жыл бұрын
Im afraid to comment......Zikhale Ng'oma ndimunthu wabwino.
@HestingsBellow Жыл бұрын
Crying for my mother Malawi
@andrewmafungah2350 Жыл бұрын
za iwe ndimayimika manja, ndiwe katakwe wodziwa kufufudza nkhani 👏👏👏🙏.