BON KALINDO 11 JULY 2024 KUNG’ALURA PA THURSDAY

  Рет қаралды 28,704

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

22 күн бұрын

Пікірлер: 223
@VungaQueen
@VungaQueen 20 күн бұрын
Apa nde chakwela akutitola kwambiri mulungu mumve kulilira kwa amalawife mupaka kugilitsa mutchenga uli wachilengendwe ayi zikomo magamuro anu chakwera adutsa muyetso mitsozi yanthu kuvutika kwanthu dzikhare pa panja lanu achakwera 🥲🥲 inu aboni kalindo keep it up kutiuza anthu opepelawa 🔥🔥🔥🔥
@FRAVIOKUNSANJA
@FRAVIOKUNSANJA 19 күн бұрын
Koma boma ili lafika posauzana n'chenga umene akulesa wayamba kuvuula lero ameneyu galu kwabasi chakwera atimaliza tonse
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk 19 күн бұрын
Powerful talking from our beloved president, president for the poor always there for poor Malawian citizens the Dddddd Cccccc!!!!, proud of you always. May the good Lord continue to guide and protect you always 🔥🔥🔥🔥
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana 20 күн бұрын
Akuti apolice adzisilira mpunga WA Ana school koma ADC inuyo ndi wa wani long live a kalindo anya manyi achakwera achitsiru amenewo , nde bwino akalindo ineso maganizo amenewo nariwo kuti athu asavotere chauzika akalindo inuyo inuyo ambuye akudaritseni ife kwakwataine sitikupanga nawo zopusazo tikulira ife ku Ntcheu😢😢😢 koma God knows chakwera adzafa imfa yowawa
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg 20 күн бұрын
😂😂😂😂😂 DC ndiyakatundu zoona
@user-hk3hg1to4e
@user-hk3hg1to4e 19 күн бұрын
Anatiloza ndi malemu chilima aise pomuchita follow achinyamata ife😢😢
@StevieChikaonda
@StevieChikaonda 19 күн бұрын
Uku nde kung'alulatu 10,000% ayi zikomo ndithu💪💪💪💪💪💪💪
@FisherAction
@FisherAction 20 күн бұрын
Big mulungu akudaliseni ndipo pitirizani kutiombola kuwachosa amalawi mw agaluwa a mcp
@EllenPhiri-xt8pt
@EllenPhiri-xt8pt 19 күн бұрын
God bless you Mr DC you always stand for the poor this government of chakwala is useless ever
@GoodsonDiwadiwa
@GoodsonDiwadiwa 19 күн бұрын
The Dc Bon Kalindo anthileni fire anthu osowa umunthuwa osanyengelera ayi
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 20 күн бұрын
This two much guyz..koma kuli Mulungu amatha kumuchitsa munthu pa mpando ndikuthamangitsa kukamusiya ku ntchire..koma mmawelenga baibulo????? Inalipo mfumu ina imachita zimenezi koma ngati simusamala Mr president ndi nduna zanu mupalanura mkwiyo wa Yehova....take my note
@EmmanuelMpalagule
@EmmanuelMpalagule 19 күн бұрын
Mr kalindo u are a hero, the opposition the very week, the opposition is in deep slumber,
@vitumbikokamanga5869
@vitumbikokamanga5869 20 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤go deeper mr kalindo you are the best ❤❤❤❤❤❤
@raytavares2256
@raytavares2256 19 күн бұрын
Mr president the DC we love you and greetings from North London UK
@GamaGama-z8p
@GamaGama-z8p 19 күн бұрын
Tell dem the dccccc!!! Never stop fighting for the poor innocent people we vote for purposes Mr born we are on ur side
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 20 күн бұрын
Kalindo we are failing to thank you but only God will thank you
@DeliaKaduya
@DeliaKaduya 19 күн бұрын
Koma Mulungu ngati kunali kufuna kwanu kuti munthu uyu awulawe u president ayi pafikapa ife anthu anu timveni kulira kwathu 😢, Ife anthu akumuzi kuti tigule sopo timadalira kuvuwula mchenga omwewo kuti tichape, onani pomwe zinthu zafikapa Yehova, ingobwerani muzaweruzepo dziko lanuli Ambuye
@RidwanAdam-nq6lz
@RidwanAdam-nq6lz 20 күн бұрын
Booooon kalindooooo 🔥🔥
@user-or7ng3fj8f
@user-or7ng3fj8f 19 күн бұрын
Mr Bonnnnnnnnnnn kalindo DC big up kodi bwanji osayambisa madem bwanji kumalawiko galu ameneyo ife kuno atikwana kwambiri ndithu tiye nazo Mr bonnnnnn kalindo the DC
@GRACIOUSKENAN
@GRACIOUSKENAN 19 күн бұрын
Timanva nanu kukoma nsaname🎉🎉 ndipo mau anu amatitothoza ifeo,ndiposo pa mpando wa upresident inuo mwafika kale bwana,zolembalemba zangosala tsiku loyikika bas
@kelvinmphande3754
@kelvinmphande3754 20 күн бұрын
It's the sikusinja Gwenembe song for me
@HawardStainly
@HawardStainly 19 күн бұрын
Akubwila fodya wamagogo wakuzino uja,(maganga).
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 20 күн бұрын
The DC 🔥🔥💕 Chakwera atule pansi udindo..., Palibe zoti asintheso ai.., tikumunyengelela uyuh.. _
@limbanimtitima9170
@limbanimtitima9170 19 күн бұрын
Kung'alula big man,ife Angoni kuntcheu ndife oganiza kkkkk😂
@chimwemwemasamba2880
@chimwemwemasamba2880 19 күн бұрын
Allowance ya manebbtatenga koma ndiyochepa kobasi....polingalira ndi mmene zinthu zakweleramu
@gwatandingo9502
@gwatandingo9502 19 күн бұрын
Muli bwino koma Anthu Ena sakukhulupilira inuyo boss munatitenga kutisiya ku sewo inuyo munapita kunja nokha mukadya ndalama zatha lero mwabwera 😂😂😂😂😂😂
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 19 күн бұрын
Our president more fire 🔥 Booooon kalindoooo 🔥 🙌
@MartinsKhumalo
@MartinsKhumalo 20 күн бұрын
❤❤❤ ndimakunyadilani 👏👏
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 20 күн бұрын
The dc our poor president in Malawi
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju 19 күн бұрын
Make mbuuu mwana mbuuuuu long live the DC
@pacharokoloviko1694
@pacharokoloviko1694 15 күн бұрын
😂😂😂😂 ati kufuna kumangidwa!! Komadi ndiwe DC
@JabesAlfaiate-t4v
@JabesAlfaiate-t4v 20 күн бұрын
A kalindo tiyankhulileni ife tili nanu mcp ndi yoipadi ifeyo a malawi amenetili kuno ku Mozambique tili o khuzika ndi zomwe likuchita boma la a chakwela , ku vuula mchenga mpaka laicence zinachitikako kuti ? Keep it up a kalindo.
@AudettaYohanie-fl3oc
@AudettaYohanie-fl3oc 20 күн бұрын
Aaaah koma izizi ndiye chakwera wationjedza zedi ,koma chifukwa chani kweni kweni?
@user-wu4tl2yn9e
@user-wu4tl2yn9e 19 күн бұрын
Khaaaaaa wafika the DC
@loycemmadi9303
@loycemmadi9303 19 күн бұрын
And it's the song for me😂😂😂😂Winiko Ayi ndithu
@MosesKalenge
@MosesKalenge 20 күн бұрын
ULEMU WANU MR, THE DC..... BON KALINDO 💪✊✊✊📡🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@mbewemisoyaanenenji1908
@mbewemisoyaanenenji1908 19 күн бұрын
Boooon Kalindo , Pangolin mwana womvuta kwambiri
@PempheroKasimongwa
@PempheroKasimongwa 19 күн бұрын
Kalindo 🎉🎉 iweyo ndi 1,,,ku Egypt kuja timadya kwabasi ❤❤
@JaxyKumwenda
@JaxyKumwenda 19 күн бұрын
Tikufuna mademo bwana osamunyengerera Chakwera
@gwatandingo9502
@gwatandingo9502 19 күн бұрын
Koma mpaka chenga mmmm mawonjeza
@user-ko1lk3br4r
@user-ko1lk3br4r 20 күн бұрын
Mafuta ayamba kuchoka ku Mozambique kukafika ku area 50 ku Lilongwe kudzela pa njanje ai zikomo
@user-lp8wj3vq4x
@user-lp8wj3vq4x 19 күн бұрын
Ife dzuro timadikira mademo, agalu amenewa atitopesa
@OwamiSimeon
@OwamiSimeon 19 күн бұрын
Born kalindo more 🔥
@LuundoJohnkabage
@LuundoJohnkabage 20 күн бұрын
😅😂ayi ziliko mpaka boma kugulitsa ntchenga😂😂😂😂
@MarkinaJohn
@MarkinaJohn 19 күн бұрын
Kkkkkkk koma DC kkkkk gwenembe
@BatsonKadzuwa-tl3rp
@BatsonKadzuwa-tl3rp 19 күн бұрын
Zoonadi mboni ndineyo nditachita ngoz ku Queens ndinalipira kut andithandize
@HannockMesiwni
@HannockMesiwni 19 күн бұрын
Njira ya ld pokavota sitikavota nkhondo ichitike ichitike
@MariamJaffali
@MariamJaffali 20 күн бұрын
The DC boooooon kalindoooooooo
@KnowledgecGodwin-xo4pw
@KnowledgecGodwin-xo4pw 19 күн бұрын
Chakwera nkongo wamako ,mboli Yako ,machende ako ,alipwisi alitongo.
@MouriceChimkondo
@MouriceChimkondo 19 күн бұрын
Kkkkkk
@RashidSaid-lk6bb
@RashidSaid-lk6bb 19 күн бұрын
Uchitsilu ndiye umeneo Sizidachitikepo
@annamazingashaibuh6276
@annamazingashaibuh6276 19 күн бұрын
Kkkkk koma ndipo akavoteraa nda amawooo hiyaa mau Mr Bon
@IvieMwabile
@IvieMwabile 19 күн бұрын
Akufuna kutimpha agalu amenewa.go deeper
@JohnAsendi
@JohnAsendi 19 күн бұрын
Kkkk Boma amalawi kutifinya tiwona zinthu shop chaine chasala ndi maepute katoni okhaokha ndatawira kunnjenga ndiyemukulesa mukufuna kundipha chani mukandiphera kuzenje komweko 😮😮😮😮
@annamazingashaibuh6276
@annamazingashaibuh6276 19 күн бұрын
Uyu ndi nyoooo kwa nyooo ulemu wanu aaaa mchenga athu anayambira kale za mchenga athu amadyera momo abale eishh sambi
@RashidSaid-lk6bb
@RashidSaid-lk6bb 19 күн бұрын
MCP ikufuna kuzabela ma vote chifukwa sizidachitikepo ku voter without ID ngakhale kuno ku South Africa
@RafickRaj
@RafickRaj 19 күн бұрын
Mmatha madhala madhala inu mungoyimila koma zikhala bwino
@LovelyJapaneseMaples-xc2bc
@LovelyJapaneseMaples-xc2bc 19 күн бұрын
Kuswakuswa big osaopa😊
@user-kw7wr4kq9w
@user-kw7wr4kq9w 19 күн бұрын
We only need solutions not only kulalika
@OmegaNjati
@OmegaNjati 19 күн бұрын
Ambuye nditengeni
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q 19 күн бұрын
Mafumu aku ntcheu mtima wawo ukuwawa alibe dyera ndi mafumu odziwa kulira moyo wa munthu sizocheza
@MouriceChimkondo
@MouriceChimkondo 19 күн бұрын
Following boss
@duncainjimmy
@duncainjimmy 19 күн бұрын
Mulungu adalenda dothi osati Chakwera ai
@OsmanBakali-s5x
@OsmanBakali-s5x 20 күн бұрын
Where are we going to make our hustle now😭😭😭 mpakana nchenga omweu tkatenge chilolezo? 🔥🔥🔥🔥🔥
@babranzima8120
@babranzima8120 19 күн бұрын
Ndizisilu zaathu zathu ananyerapo chenga iyewo chakwera
@user-gd6zb2bv8f
@user-gd6zb2bv8f 18 күн бұрын
Koma funso nkumati kuti, Kodi Chakwela ndi Zikhale wacheyo, samachita manyazi konse akamamva izi? kapena umunthu wanu unatha?? The DC tell them shit
@densonchiwaya8439
@densonchiwaya8439 19 күн бұрын
Mau awaa sikalindoo
@ChondezVick
@ChondezVick 19 күн бұрын
The DC himself 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@happychimwemwe-1805
@happychimwemwe-1805 19 күн бұрын
Umakwana booooon kalindo
@user-qc7qg4cy6k
@user-qc7qg4cy6k 19 күн бұрын
Totally agree the dc
@dinahmunthali5324
@dinahmunthali5324 19 күн бұрын
Ine nyimbo ndi zomwe zimandi waza koophya ati Sikusinja ndi Gwenembe amkaimba agogo awake DC popita ku Mzuzu akudutsa mu chikangawa 😂😂😂😂😂 DC makina 😂😂
@LinoMatchado
@LinoMatchado 19 күн бұрын
Iyayi na ya mchenga yokhayo boma likunena zoona chifukwa mchenga is in the group of minerals and any mineral is a government property which is minored through the government permission. Everywhere in the world illegal mining is prohibited citizens are allowed to collect sand ndi wilibala basi not with a thipa truck then you have to go face the law which is in the constitution every country.
@JamesKambale-s2c
@JamesKambale-s2c 19 күн бұрын
Koditu uku mcp kwangokula mbuzi za anthu
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 20 күн бұрын
The Dc bon kalindo good Messnge
@texonkautera
@texonkautera 19 күн бұрын
Anthu amene amabweresa Mbatata Ku nsika wa Limbe Ku chokers Ku Mulanje akuzunzidwa kwambiri akafika kuti asise a Police akuchosa misonkho akuti alakwa akalipire. K20 Pamene anthu akupangira mavuto mafuta anadula Palibe chomwe akupindula
@user-hb1ll8lj3v
@user-hb1ll8lj3v 19 күн бұрын
Gwenembe ND sikisinje yemweyo 😂😂😂😂
@MynessChirwa
@MynessChirwa 19 күн бұрын
😂😂😂 book la gwenembe kodi kkk
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q 19 күн бұрын
Ndipo zoonadi chonsecho sanapangile anthuwo chochita
@LoveBanda-sw1nu
@LoveBanda-sw1nu 19 күн бұрын
😅😅😅😅kumalawi mkokoma ndithu bwanawa akutiposa zochita
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 19 күн бұрын
Ng'alula DC
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju 19 күн бұрын
Sikusinja ndi Gwenembe😅😅😅😅😅😅😅 Nyengo yokhadxula kukhazula
@SimonMtonga-kf5ht
@SimonMtonga-kf5ht 19 күн бұрын
Born kalindo more fire
@jameskamanga628
@jameskamanga628 18 күн бұрын
Koma mkulu uyu kkkkkkkk sikusinja sikusinja kkk
@loycemmadi9303
@loycemmadi9303 19 күн бұрын
Mr kalindo munafika aaaah kukanapezeka ambiri ngati inu bwezi dzikoli titaona zina aaaah
@TutuAlfred-y2l
@TutuAlfred-y2l 19 күн бұрын
😂😂😂😂😂. Zosatheka sizidzatheka nanga chenga ndichani uyo wasala pang'no kt amfe ameneyo chisilu chamunthuyo muuze ambere Ku muloza border kuno aone kt angatile ife kuvuula chenga.
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 19 күн бұрын
Osakhala presdent bwanji abon kalindo Tayambitsani chipani cha amphawi
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg 20 күн бұрын
😂😂😂😂 azingomwadi ambuye mtengeni 😂😂😂😂😂
@user-wu8kp7ui5j
@user-wu8kp7ui5j 19 күн бұрын
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥
@LonnieGrem
@LonnieGrem 20 күн бұрын
🙌🙌🙌ay zikomo
@user-nn4bf1kw9h
@user-nn4bf1kw9h 19 күн бұрын
Ing'alureni 🔥🔥
@azunguauskay4903
@azunguauskay4903 19 күн бұрын
😂😂 Akalindo nyimboyo ndayikonda
@user-no2mx4go8p
@user-no2mx4go8p 19 күн бұрын
Mpakana licence 😂😂😂😂😂🙌🙌🙌🙌 zili kumalawi nzatose akatenge licence ndi driver 😂😂😂😂
@Sugerman-tw4do
@Sugerman-tw4do 18 күн бұрын
Big Bos DC mumakwa
@ChikumbutsoTsalangu
@ChikumbutsoTsalangu 20 күн бұрын
Ati pedza madzi mu tikuvula chenga tikhapanamo
@MarthaJafali
@MarthaJafali 20 күн бұрын
Sure
@WitnessPhiri-zr9uf
@WitnessPhiri-zr9uf 19 күн бұрын
Aborn kalindo nde mumatiziwisa nkhani zambili mumatiyimilira koma or mukuyankhula anthuwa palibe chomwe akuva bwanji kuti kupangike mademo poti apo akuwona ngati tikusangalala ndi ulamuliro wawoo kukufunika ma demo kuti Ave ngati mumene anapangila azathu ku Kenya lizaini sangapange popanda ma demo 😢
@stanfordnsona
@stanfordnsona 19 күн бұрын
Kalindo umatitsekula maso
@mlimolubanda6348
@mlimolubanda6348 19 күн бұрын
The DC .....
@samuelgambatula2415
@samuelgambatula2415 19 күн бұрын
Tiyambe mademo.... Ulemu wathapo apa
@user-fq4kv8dj4t
@user-fq4kv8dj4t 19 күн бұрын
Zoona aliyense akavote opanda cha unzika basi nanga izizo nchilungamo
@Vascomw
@Vascomw 19 күн бұрын
Ndipo live eeee a police eeee akuwo jeza
@user-sv5yi9gt4u
@user-sv5yi9gt4u 20 күн бұрын
Zoona Born Kalindo auzeni ife tikuvutika kwambirii pa msewu kuno ku Kasungu chamama
@ZainuluNsalule
@ZainuluNsalule 19 күн бұрын
Good
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 20 күн бұрын
Koma m,chenga wa mulungu abale koma chakwela ambuye mutengeni watituza mokwanila mulungu mulangeni galu ameneu
A Michael Usi Inu Si A UTM - Lyton Mangochi
23:13
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 9 М.
Каха заблудился в горах
00:57
К-Media
Рет қаралды 7 МЛН
DAD LEFT HIS OLD SOCKS ON THE COUCH…😱😂
00:24
JULI_PROETO
Рет қаралды 16 МЛН
Я обещал подарить ему самокат!
01:00
Vlad Samokatchik
Рет қаралды 6 МЛН
Assista na íntegra o Interacção Matinal 31/07/2024
Portal FM | Fala Moçambique
Рет қаралды 249
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BON KALINDO
59:52
Zodiak Malawi
Рет қаралды 48 М.
ZOMWE ZIKUCHITIKA KUMALAWI
44:29
Jimmy
Рет қаралды 4,3 М.
Ine Ndimalimbana Ndi Area 30 - Bon Kalindo
15:49
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 12 М.
Каха заблудился в горах
00:57
К-Media
Рет қаралды 7 МЛН