DR CHAKWELA ADAZUZULA DZIKO LA AMERICA MU CHICHEWA CHIFUKWA CHANI? HOT CURRENT 🔥🔥

  Рет қаралды 9,945

HOT 265

HOT 265

25 күн бұрын

Пікірлер: 79
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 23 күн бұрын
Ndili kumbuyo kwa America. America inapereka mpaka mokwanira kuti tifufudzane tokha koma tarephera. mpaka 4 years kuli ziii nde mumati atani
@robertzambia8697
@robertzambia8697 23 күн бұрын
Malawi amaombela Maja zili zose akulakhula anyamatawasoo apa zozizila
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 22 күн бұрын
Eh eh mpaka 4 years akufufuzabe?
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 23 күн бұрын
Penapake anyamata inu analysis imakuvutani mukuzikolakola kwambiri, ma court athu sakugwira ntchito yawo bwino.Muzikumbukira mlandu wa chisankho anaupasa masiku ndipo zinatheka, milandu ya anthu enawa ikukanika pati kuipasa nthawi????
@tshidikepadisa3148
@tshidikepadisa3148 22 күн бұрын
imavutadu milandu imeneyo ndi yaliti ma court akumachedwesa dala ku gamula cholinga ayizizilise milanduyo ithele malele munayambila muja wa chilima uku weluzidwa bwanji enawo kuli ziiii
@andreabanda7838
@andreabanda7838 23 күн бұрын
But for how should we wait for the courts in legal perspectives. Are the judges really working in this country specifically on these matters that USA has complained. Indeed our justice system is too slow.
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 22 күн бұрын
Ma Americans ndi owopsya aiona kale nkhaniyo ,ife tikhoza kunena kuti afulumila yes. Koma nkutheka mamulumuzana amene apanga Mack -wa awafufuza kale mwa okha moti ma Americans akuziwa chimene akunena ndithu, moti amene apeleka kalatai kuwafusa akhoza kupeleka umboni ndithu.
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 22 күн бұрын
Ndie ma guys kumeneko tisaziikile ku mbuyo system yathu ya ka fukufuku pa nkhani ya katangale ndi zina za mbili si zilibwino ku boma-ku moti kungopemba Mulungu azalowerelepo potipasa anthu owoopa Mulungu bsi
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 22 күн бұрын
Komadi inu anyamata kumeneko ku fufuza nkhani ena apa akuti mpaka 4 years akufufuza mulandu , kodi amakhala aku fufuza golide chan ai it's to much ku malawi kuno that's why ma Americans angokuuzani ma wise bsi iya
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 22 күн бұрын
Yes it is more than necessary. He has More power to tell them the truth about America behavior
@Cee-H-Cee
@Cee-H-Cee 23 күн бұрын
First to watch
@DaimonJulio-ce8mq
@DaimonJulio-ce8mq 23 күн бұрын
Congratulations live from Johannesburg
@abdulsalammkwepu3321
@abdulsalammkwepu3321 20 күн бұрын
Vuto ndima court athu they are very very slow when comes to passing judgement, even the issue of leader of opposition is still hanging there. Don't blame america
@francismungu7749
@francismungu7749 22 күн бұрын
MCP anagula ma court, police mdf . Zonse ndani sakuziwa kumalawi kulibe justice and democracy. Mcp anaphwanya zonse koma simadolo la 40 lizakwana
@MatSecurity-gq3hr
@MatSecurity-gq3hr 22 күн бұрын
Dziko Ndi Anthu Ake❤
@paulmakaula4937
@paulmakaula4937 23 күн бұрын
Anyamata athu a Times timantha tayamba kuwapeza, their paymasters ayika timinga😢😢
@hackwellkagolo6614
@hackwellkagolo6614 22 күн бұрын
Chakwera he did mistake kuyankhula pagulu la anthu. Amereka sunayime pachulu but they wrote a letter and to respond anayenelaso alembe kalata. Poyankha mkalata anayenela afufuze bwino ngati President chifukwa vuto ndi lakuti mulandu omwewo wina akuyendela kukhoti pamene ena anangochosedwa m'maudindo awo pamenepo pali kukondela. ACB mwayipha zikugwira tchito yawo ngati momwe inayambila ndiye amereka yakhalangati yalowa m'malo mwa ACB and sinanene kuti amangidwe ayi nkhani ndiyoti anthuwo asazapiteso ku America ndiye inu musanyasidwe kapena kukamila ngati ku Americako ndikwanu. Tiyeni tizidya nandolo kuMalawi komkuno basi.
@PatrickHennry
@PatrickHennry 22 күн бұрын
Amawauzatu anthu adziko lawo ndipo dziko lanthu timayankhula chichewa ndiye adachita bwino. Wamkulu akamalakwitsa osangokunkhala chete ayi nayeso azidzudzudzulidwa azidziwaso mavuto awo
@Moses51
@Moses51 22 күн бұрын
All world 🌎 there are know that Malawi there too much crampions
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 23 күн бұрын
Chakwela ndi mbuzi
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 22 күн бұрын
For how long that's why governments of America take actions
@user-oe1lg4xo7w
@user-oe1lg4xo7w 22 күн бұрын
Anyamata atatuinu mmmm pamutupanu palibe nzeru mwadziwika kuti ndinu Ayumi a mcp inunso ndi mbava akufufuzene kumeneko
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 22 күн бұрын
President sadalakwitse tikati bwanji amalankhula chichewa bwanji samalankhula English zangowonetselatu kuti atolankhani enanso ndi mbiri zenizeni . Chakwera amawuza amalawi a president samawuza america . America adalemba kalata choteronso Boma liyankhanso kudzeranso mu kalata office ndi office .
@apostledavismsosa
@apostledavismsosa 17 күн бұрын
I dont see any mistake in the lstter wrote with American embacy. Chifukwa Malawi imangoyimbanyimbo pa nkhani ya katangale.Aliyense akakhala pa mpando nkhani ndi kubsa basi. Zimakhala zowawa ngat watumiza thandizo kwa munthu yemwe wafuna kuti lika mufikire kenaka ukamve kuti thandizolo wadya ndiyemwe unamutumayo Makawi ikuonjeza a Merica sikulakwa.
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 22 күн бұрын
Milungu ya MCP ili m'makhothi ndipo akhothi ndiomwe akuwononga dzikoli zikukhala bwanji milandu nkumatha zaka 4
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 23 күн бұрын
Chakwela ndimbuzi kwabas ozungulila mutu kwabas
@Moses51
@Moses51 22 күн бұрын
Akafuna kuyanihula chakwela ndawinzose amayangula chidzungu why him he did speak in chitchewa why
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 22 күн бұрын
ACB yake itiso nanu mesa ili limoz ndi achakwerawo kodi komaso sikugwila tchito iliyonse. Nanunso muli limoz ndi MCP kapena
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 23 күн бұрын
Amawopa kuti America imumvela zoyankhula zake
@chisosera
@chisosera 21 күн бұрын
It is shameful to use power or riches to oppress the poor. American embassy should have contacted Malawi government on the issue if they had a concern. Malawi is sovereign country and is very right to remind America of our independence. Speaking in Chichewa is not wrong, it is also the pride of local language, every other country leader in most Europe and rest of the world speak in there language. Well done Malawi. Mindset change!
@HaroonSaidi-jv3ek
@HaroonSaidi-jv3ek 20 күн бұрын
What about Uladi mussa why u didn't say that?
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 22 күн бұрын
Chakwera moto we want such of African leaders who no fear America
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 23 күн бұрын
Mbava zokhazokha boma la malawi
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 21 күн бұрын
Times pano inadya chi bazi aaa zinasiya kukoma
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 22 күн бұрын
He has rights to speak into his mother's language
@georgejere2922
@georgejere2922 22 күн бұрын
Akuopa kuti angamve kkkkkkkkkk😅😅😅😅😅😅
@HaroonSaidi-jv3ek
@HaroonSaidi-jv3ek 20 күн бұрын
KKKKKKK mmmmm lero ?
@henryhenry6632
@henryhenry6632 22 күн бұрын
Ma cadet
@chisosera
@chisosera 21 күн бұрын
Behaviour without respect
@danielmsowoya9107
@danielmsowoya9107 19 күн бұрын
Kaya chizungu Kaya Chichewa komabe wachita bwino kunena chilungamo. Asamatitole azunguwa
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 22 күн бұрын
Thank a lot Chakwera to shut America,
@charitymhone9983
@charitymhone9983 22 күн бұрын
Mmmm nanu inu chakwera angapange shout down America who is chakwera, wasiyilanji kuyankhula mchizungu kt America imve, galu ya munthu... Mumangoombera mmanja ndizopanda pale, zaziiii
@user-hd7wq2yc6m
@user-hd7wq2yc6m 22 күн бұрын
America popanga chiganizo chimenechi choletsa anthu 4 a merica inawona kale kuti boma la Malawi pamozi ndi ma court athu alibe chilungamo pa nkhani yimeneyi anthu 4 amenewa akuchitidwa sheiled ndi boma lathu boma la malawi ndilakuba kwambiri this government is worst than any government we had since mart party democracy, so a Merica is not wrong to burn these 4 people not to travel to their countty a Merica is our big partainer interms of development so a Merica is well montering us on how governmet is using their funds inuso awounder Msiska simumayha kumasilira bwino nkhani mumakhotesera daladala kaya boma lanuli linakudyetsani kamba ku kamwa kwanuko, mlandu mpaka 4 years ma court akutani? Kuzengerezera dala, ACB ilikoso kino ku Malawi? a Merica should contnue to burn those who have been left out including himself chakwera pa anthu onse aja anatchulidwa chilima yekha kuimbidwa mlandu? Onse aja amatchulidwa 79 alikuti? This government is worst than any governmet we had since mart party government from 1994 useless government
@AbuOsman-ts6ef
@AbuOsman-ts6ef 22 күн бұрын
Mantha awo
@hakimbaiton
@hakimbaiton 22 күн бұрын
2:20
@MikeKachiwala-ln5vp
@MikeKachiwala-ln5vp 22 күн бұрын
You guys you must know that Malawi is dying slowly because of corruption.
@jamesgama5489
@jamesgama5489 22 күн бұрын
Akudelera ma Court ake ati! Mbala zokhazokha ziri kuma Court athuwa
@ChicoBanda-kq7py
@ChicoBanda-kq7py 22 күн бұрын
Ndikumbuyo kwa America lolani mulungu akuseguleni maso chakwela asanakunamizeni zomwe akuyskhula pachilima atanena küt akunkhuzidwa zakatangale anamuyimisa ntchito chifukwa chanji ? Kumbukilani osamuyikile kumbuyo chakwela
@user-tg4mf5rm3d
@user-tg4mf5rm3d 22 күн бұрын
Apurewo amadana nadxo chifukwa akamaba ndalamaso amakasunga kwa mericako nde ngati akwa usa kuti asapite nde kuti bas ndalama amabadzo zakatenga
@musorosikoti-sd2xk
@musorosikoti-sd2xk 23 күн бұрын
useless program!
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 22 күн бұрын
Komanso nanunsotu zikuwonesa kuti muli limozi, ma court ake ati omwe sakugwila tchitowo😡😡
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 23 күн бұрын
Chakwera ndi mphemvu. chitsiru chachikuru mmalawi.
@nditumenichagunda4192
@nditumenichagunda4192 21 күн бұрын
Chizungu ngati cha ana
@user-ul5hh3cz8z
@user-ul5hh3cz8z 22 күн бұрын
😂 chakwela he is Nephilim indeed I feel very sorry for the malawians.les just put in hand of God to have a good leader.
@user-oe1lg4xo7w
@user-oe1lg4xo7w 22 күн бұрын
Anyamata inu simukuthanso kulankhula chizungu mukayambenso school yakwacha 😂😂😂 America yalasa nyani chende .
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 22 күн бұрын
America ilange zen zen kumene nawoso awawa lero adyesedwa mabazi zoyakhula zao lero szkumvekaso
@alexmkolongo3089
@alexmkolongo3089 22 күн бұрын
Mpaka zaka 5 nkhani yomwei
@IsaacKamwendo-bb7xz
@IsaacKamwendo-bb7xz 13 күн бұрын
Chakwela ndi mbuzi yamunthu ndithu
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 22 күн бұрын
Chakwera ayenera ku phepesa ku zidko la America asanamukanizeso iyeyo vuto lakusauka ndirimenero
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 22 күн бұрын
Dziko la america lipepese osati president wa Malawi apepese .
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 22 күн бұрын
America needs to be taken as a God. .their not God of Malawi
@charitymhone9983
@charitymhone9983 22 күн бұрын
America is a superpower if you don't know bro, she is rulling the whole world.... Chakwera ndi mbwewa ya munthu
@Moses51
@Moses51 22 күн бұрын
Chakwela amayenda mali😅😅😅
@user-td1ll5ge6n
@user-td1ll5ge6n 22 күн бұрын
Kubaso kumakhala kulemekezana zaziiii mwanyabe mbuzi inu mwayaluka
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l 22 күн бұрын
Chakwela ndiopepela
@ChristopherBaluti
@ChristopherBaluti 23 күн бұрын
Ati udolo mwini wake wakeo
@AmujeMwamad
@AmujeMwamad 23 күн бұрын
😂 kma zinthu zake
@georgemponda
@georgemponda 22 күн бұрын
Koma anakayankha nchizungu ndi nchichewa momwe. I remember how Bingu responded to Americans interms of Malawi economy. Chakwera knows himself he's a puppet, he can't even stand and show his anger over America.
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 22 күн бұрын
Pamene paja amalidziwitsa dziko lamalawi lo mwe iye ndi president . America idatulutsa chikalata nawonso boma awayankha kudzeranso mukalata
@georgemponda
@georgemponda 22 күн бұрын
Koma nanga mnchikalatamo Kunkuyu anayankha ngati momwe apresident-yo adayankhulila... chakwera wawonetsa nkwiyo wanchifinyira kufuna kutseka mmaso amalawi😂😂😂😂
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 22 күн бұрын
I am behind Chakwera America must focus on their matter not Malawi... We are tired of you America to treat you as God. Shut up
@HaroonSaidi-jv3ek
@HaroonSaidi-jv3ek 20 күн бұрын
Then u shouldn't receive their money they ar talking about their money what u get from them
@user-ud3vp9zb7f
@user-ud3vp9zb7f 23 күн бұрын
Aaa zaziii inu mumafuna aziyankhura chizungu pamene amauuza amalawi anzake # anachita bwino kuyankhula chichewa
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 22 күн бұрын
You don't know nothing AAA Malawi yo imadalila America
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
ОДИН ДОМА #shorts
00:34
Паша Осадчий
Рет қаралды 6 МЛН
Зу-зу Күлпәш. Көрінбейтін адам. (4-бөлім)
54:41
YouTube's Biggest Mistake..
00:34
Stokes Twins
Рет қаралды 64 МЛН
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
History of Africa from the 16th to the 20th Century
3:39:03
Jabzy
Рет қаралды 7 МЛН
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
Misomali Ya Six Inches Yothana Ndi Zipani Zotsutsa - Bon Kalindo
17:18
Times Exclusive featuring Thomson Mpinganjira - 3 February 2024
1:07:40
Times 360 Malawi
Рет қаралды 146 М.
NSOKHANO WA UDF KU BLANTYRE 🙌🙌🙌🙌
14:30
HOT 265
Рет қаралды 15 М.
CRUISE 5 WITH LILIAN ESTELLA PATEL PART 1
52:10
Zodiak Malawi
Рет қаралды 16 М.
A MARY NAVICHA ATHA MAU KU INTERVIEW 🙌🙌🙌🙌🙌
23:51
Kodi Mulandu Wa Chilima Ndekuti Watha?   Bon Kalindo
12:51
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 41 М.
ОДИН ДОМА #shorts
00:34
Паша Осадчий
Рет қаралды 6 МЛН