HON MOSES KUNKUYU PA HOT CURRENT 🔥🔥🔥

  Рет қаралды 14,819

HOT 265

HOT 265

Ай бұрын

Пікірлер: 70
@user-hy6gc6ld9w
@user-hy6gc6ld9w 29 күн бұрын
Muziziwatu kuti amalawi ife tikukuwonani inu andevu zamwai mumayamba mwachita meeting kumbariko musanabwere pa podium ndinu anthu oipa mwagawana ndalama ndipo umboni ulipo sife anthu opusa kma muzayankha zimenezi
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Ndalama munakapereka kwansundwe
@malawigeneralguide1646
@malawigeneralguide1646 29 күн бұрын
Iwenso takuona kwambiri....uzingosiya nkhaniyo basi nanga pamenepo ukutanipo😏
@DONGOSOLODAVIE
@DONGOSOLODAVIE 28 күн бұрын
Uzingotipatsilapo program yo bas koma zomazionetsa PA screen pa ineyo zimandinyansa kwambiri timafuna tidziwaona anthuwo kumaso chifukwa bodza limaonekera mmaso adatero akuluakulu tikudziwa kut Chanel yi ndiyako komano usamaziikepo pamenepo please we need large pictures
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 29 күн бұрын
Hot current yabowa bwanji
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Abale DPP inachoka m'boma zaka zapitazo takambani zomwe ziri pa ground onani ku MCP isiyeni DPP
@mizekidokotala9801
@mizekidokotala9801 29 күн бұрын
❤u
@user-wq9lp7sv9r
@user-wq9lp7sv9r 28 күн бұрын
This is great hot current worthy listening and sharing
@PraiseBwanali-xq8kn
@PraiseBwanali-xq8kn 19 күн бұрын
Whenever you're ukuwonetsa program iweyo uzisunthapo uziyika program yokhayo I think zizibeba bro
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 29 күн бұрын
Dpp timamwa tea tsikunditsiku kuno kumalawi lelo surga Ali pa 4000 timwaso tea agaluinu
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Kunkuyu anatuma bod gud wawo nkukapha alani witika chifukwa Cha nkadzi
@ZelinaKisswell
@ZelinaKisswell Ай бұрын
Inu tamaikan full screen yazomwe zikuchitika nanga inu mukutanipo APA tiziwaona anthuo bhobh aaaa mwatani Kodi
@user-yx5ck5oi8j
@user-yx5ck5oi8j 29 күн бұрын
Ndipo aaaaa
@moniesphiri7852
@moniesphiri7852 29 күн бұрын
If he show full screen it is going to be copyright... KZbin will strack his channel... Because it's not his original content
@ZelinaKisswell
@ZelinaKisswell 29 күн бұрын
That's not the reason ask him why he put himself on their n he will give you parallel answer to what you r saying
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Ай бұрын
Kuyankhula kopanda nzeru anduna awa amadzithiramo kwambiri... Mumkati nyasi zinali mbuyomu what do you mean??? Ukusiya zanuzo nyasizo
@PeterPhiri-nd6op
@PeterPhiri-nd6op 29 күн бұрын
Zonyasa zilipo zopano oseti a dpp mukulephela kuyakhula za nyasi zanuzi zisilu inu
@user-le3lr6jn7g
@user-le3lr6jn7g Ай бұрын
Kunkuyu ndi munthu owononga kwambiri
@JosephKuyeli-rc9on
@JosephKuyeli-rc9on 24 күн бұрын
Bwanji osamulanda katundu wake mesa akamatenga ngongole amayenela kukhala ndima Securities... Mukambaxi ndizabodza bwana
@timothyphiri1704
@timothyphiri1704 Ай бұрын
We love what you are doing hot 265. It would be nice if you only appear in the videos if you are commenting. Thank you.
@LucyHopeson
@LucyHopeson 27 күн бұрын
I don't think kuti munthu wandale angavomeleze cholakwika chomwe chipani chawo chikuchita
@henryphiri6100
@henryphiri6100 29 күн бұрын
Mmalo motiuza kuti mutsekulira ma company anyuwani mukutiuza za nziii zogulitsa zitumbuwa
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d 29 күн бұрын
Nkuyu tamadyani ndalama zokuba zoooo ndi chakwela wakoyooo
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d 29 күн бұрын
Komaso ife amalawi ngati ulendo uno tikuka votela MCP ndiye kuti ndife zisiro
@henryhenry6632
@henryhenry6632 29 күн бұрын
Chitsilu ndiwe, pathako pako
@user-cb2cv9fz7m
@user-cb2cv9fz7m 29 күн бұрын
Mbava za chakwera izi yiyaaa kungondithera data basi,kuba kuba nkhaza ndipo mukuchikatu muberetu
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 29 күн бұрын
Kodi kukhulukilana ngongoleyo Chifukwa chani?ifensotu timaifuna ngongoleyo. Kodi ifenso titadzapeza ngongoleyo mudzatikhululukila?
@ChanceKachoka
@ChanceKachoka 29 күн бұрын
Program ya neef ndi ulendo wa kampeni. Malawi tisagone tulo. Anthuwa amasamala Za Mimba zawo.
@GodsonLindan-hn4kp
@GodsonLindan-hn4kp 29 күн бұрын
Mr kunkuyu mulungu akulangani, mmanja mwanu muli magazi.Munapha Allan witika chifukwa cha hule . lero mukunena zozungulira mutu komaso chakwera angokuyang'anani mugwera limodz mu 2025.
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 29 күн бұрын
Kumkuyu kodi umadzitenha kt ndani munulo 0panda mfundo ukati nyansi zomwe zinalimo mbuyomu iwe ndi ladzalo ndi anzako okuba mbomamu simukudziwa kt mwaposa zipani zonse anzanutu amaba koma ife akumudzi osadziwa koma inu iiiiiiii mwaonjedza
@user-uv7yq1fx4r
@user-uv7yq1fx4r Ай бұрын
Akunama akulandila okhaokha a mcp
@ChangeChambo
@ChangeChambo 28 күн бұрын
Nduna zaku bagamoyo ndinu manyaka enieni, RIP Allan witika
@patassonelucaszovuta3431
@patassonelucaszovuta3431 29 күн бұрын
Kodi ngongole zimenezo zilibe malamulo eti nanga mpakana nduna kunkuyu kumatenganao
@malawigeneralguide1646
@malawigeneralguide1646 29 күн бұрын
Palibe chanzeru nduna yakambapo pa funso loti chidawapangisa nchani kukhululukila ngongole 😢😏
@user-uv1vu6ub5o
@user-uv1vu6ub5o 29 күн бұрын
Kumkuyu palibe cha nzeru chomwe unganene mmaja mwako muli magazi unapha witika iwe, muthu watsoka iwe, kuda ndi mtima omwe
@Inno-brave
@Inno-brave 28 күн бұрын
Anyamata a Hot current miti yawo simagwira ntchito bwino coz amangopanga criticize komano they have either solution to that or even suggestions
@user-zn5uf6lq7p
@user-zn5uf6lq7p 26 күн бұрын
Akutitu ndiabusa nso amenewo kma Mtambwiri ndithu😂
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t Ай бұрын
Kukuyu ndi nduna yamatama ndiye ngat nife ikuyenda bwino chakwera akupempha ndalama ya chimanga njala yalowa bwanji
@dorcasmwale6328
@dorcasmwale6328 Ай бұрын
Kodi neef ndi ya amphawi kapena ndiyowonjezela kwa ameneyo Ali nazo kale?
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 29 күн бұрын
Za Allan Witika 😢😢😢😢
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj Ай бұрын
Samanyi bassi pharediyo mwakuta
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Kunkuyu kunyasa mawu nkhati nkhumba yaimuna
@dorcasmwale6328
@dorcasmwale6328 Ай бұрын
koma mwano umenewu sakudziwa kuti akunyoza mabwano awo omwe akupanga zopusaso
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Ай бұрын
Kunkuyu ndiwe garu bas ukati unyase nkhope
@user-eo6zi1kd3q
@user-eo6zi1kd3q Ай бұрын
Akutanipo appaa kkkk zaziii
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 28 күн бұрын
Compain imeneyo agalu amenewo.
@user-gx8or3yz9u
@user-gx8or3yz9u 19 күн бұрын
Kodi munthuyu mumalimbana naye chani ?musiyeni ndimene anazikomzela inu dzimverani nkhaniyo basi
@user-ul5hh3cz8z
@user-ul5hh3cz8z Ай бұрын
Mosses ndimbuze tonde wonukha ndichikamwe chake 😂😂 lazalo amanja zapasi Malawi muyembekeze zimenezo surga akupita Ku Zim
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 29 күн бұрын
Zautsilu osamakamba za 58billion yapita ku state house
@user-nx7yz4qo8f
@user-nx7yz4qo8f 29 күн бұрын
Kambani zanu not Dpp ,
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Danzi lakunkuyu nkhati posetera pamphaka
@JameMirward-vm4dm
@JameMirward-vm4dm Ай бұрын
You lose more comments just because of putting your face,,
@user-cb2cv9fz7m
@user-cb2cv9fz7m 29 күн бұрын
Wakupha uyu adapha Allan,kumkuyu ndi galu otheratu
@chikubauleni
@chikubauleni 27 күн бұрын
do you have umboni
@user-ub9on7oj7l
@user-ub9on7oj7l 29 күн бұрын
Kama grasi iwe kunkuyu. Panyapako wamva nkhope mulamba owamba
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Kunkuyu kunyasa nkhope nkhati galimoto ya police
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 29 күн бұрын
Munthu nduna ya Boma akukatenga ndalama ku Neef.Komatu dzindalama alinazo.koma akumana anthu oti atha kuthandizika pama Business awo.Hiii kudzikundikila chuma.
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 25 күн бұрын
Galu hiwee na bagamoyo wanu chakwela
@user-uv7yq1fx4r
@user-uv7yq1fx4r Ай бұрын
Olo inuso mupanga chimozimozi
@ChrisNtanga-do5hk
@ChrisNtanga-do5hk 29 күн бұрын
Koma pamalawi mmmmmh kut upeze ngongole ya neef ukuyenera uvale makaka achipan
@user-lt9xb8sq1r
@user-lt9xb8sq1r 29 күн бұрын
Zachamba basi
@user-po4bk7fw2w
@user-po4bk7fw2w 29 күн бұрын
A Pankuku mudzikula,stop zomakamba za dpp, tizikamba zaler. It's now 4 years d dpp isali muboma mavutowa apezeka munthawi ya mcp
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Iweyo kunkuyu uyankhe funsolo likumveka usaname kuti silikumveka
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 29 күн бұрын
Iwe kumkuyu machendako galu
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Musanamizire andale ena mumawaponderedza andale ena mumakhalamo nokha
@MphatsoLuka-gn3lr
@MphatsoLuka-gn3lr Ай бұрын
Kondi bomali dilatundu umodzi
@simonpaul6567
@simonpaul6567 Ай бұрын
Moses kunkuyu galu wa munthu uyu
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Ай бұрын
Kodi kunkuyu ukamati mbuyomu munali nyasi ukutanthauza chani? Popeza boma lanuli ndilimene lazaza ndi nyasi instead of clearing the lable you are creating alot of lables.
Andrew Azzopardi on RTK103 | 11 ta' Mejju 2024
2:56:43
Newsbook Malta
Рет қаралды 4,7 М.
Dziko Layipa - Andrew Masuako Banda
25:38
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 7 М.
Glow Stick Secret (part 2) 😱 #shorts
00:33
Mr DegrEE
Рет қаралды 32 МЛН
CRUISE 5 WITH MOSES KUNKUYU KALONGASHAWA - 05 February 2023
53:53
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 15 М.
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
TIMES EXCLUSIVE WITH ALFRED GANGATA - 10 AUGUST 2019
39:26
Times 360 Malawi
Рет қаралды 10 М.
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
CRUISE 5 WITH ISAAC JOMO OSMAN
1:11:28
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 54 М.
TIMES EXCLUSIVE WITH MIKE CHITENJE - 27 JULY 2019
46:42
Times 360 Malawi
Рет қаралды 13 М.
INE NDI BON KALINDO MWANA OWOPYA KWAMBIRI/13 May 2024
14:14