BON KALINDO LERO PA 9 SEPT WATI DZIKO LAFIKA POKUDYA CHITEZE ILI NJALA YOTI SINACHITIKEPO KALE LONSE

  Рет қаралды 20,429

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер
@CHRISTOPHERCHINYONGONYA
@CHRISTOPHERCHINYONGONYA Ай бұрын
Malawi ndichifukwa chani tikungolekela idzidzi 😢😢😢 tiyeni tipange umodzi ndikumuchotsa chakwela pampando mothandizana ndi a President anthu Born Kalindo
@OsmanGanda-bz3mp
@OsmanGanda-bz3mp Ай бұрын
Amwene Bon kalindo Inu ndikatundu 7:02 musazafe muzangosowa Mumatiimilira sure ❤
@TrizaDzimbiri
@TrizaDzimbiri Ай бұрын
Amene amanena kuti chakwera adzawinaso ma vote next year ndi munthu okuti anabadwa kwa ng'azi
@JummahNelson
@JummahNelson Ай бұрын
Dc💯💯💯💯
@BlessingsKamwendo-z9g
@BlessingsKamwendo-z9g Ай бұрын
Iiiiiiiii ndipo zoopsya a president anthu a DC
@MosesDicostar
@MosesDicostar Ай бұрын
Khani yasoya pieces yo ndy manja mwako kalindo 👏👏👏👏👏
@chibezagoma3892
@chibezagoma3892 Ай бұрын
Bon kalindoooo
@FanizoKawindula
@FanizoKawindula Ай бұрын
Musiyeni Asimei amutukwane david
@WysonAdamu
@WysonAdamu Ай бұрын
Koditu akulu akulu chimene chikufunika ndichakuti chakwela achoke ndiye Pali mbudzi Zina ndiye dzikuyikila kumbuyo ndienaso Pali agalu ena ndipamene akukuwa mbalimu abedze Kuti Abele zisankho unu muganize njalayo tikufa nayo pano ndiye adzawineso ndiye tose tidza mwalila pembo Langa ndiili abungwe la oyendesa dzisankho chonde mukupemphani chonde musazapange mistek mudzalowesa nkhondo ine ndangonena
@InnocentNitamanMilanzi
@InnocentNitamanMilanzi Ай бұрын
Koma abale ambuye mutithandize mwezi unowu anthu kumadya chiteze inenso chibadwileni sindinazionepo
@FrancisMakuluni
@FrancisMakuluni Ай бұрын
The DC🔥🔥🔥🔥
@Paul-q2p
@Paul-q2p Ай бұрын
Vuto ndiloti amene akapanga mademo nthawi ija ndi chakwela tsopano Ali ndi chakwela ndiye Paline oyambitsaso mademo pokha pokho onse atuluke mcp
@GeniusChilumpha-t3t
@GeniusChilumpha-t3t Ай бұрын
Ya mary chilima yokhayo ikokeni bwana DC
@MariaGatoma
@MariaGatoma Ай бұрын
Komaso abale bwanji osamuchosa,,,kodi akuopsya,?kodi kumbukilani kuti iye anachita mademo ndikulowa boma kodi zikukanika pati,,,athandizeni anthu chakwela achoke,,kuyakhula mwayakhula mokwanila sakuva ndipo sazavaso,,,,chisoni alibe ,,,achoke
@MoosaSame
@MoosaSame Ай бұрын
More fire Booooon kalindoooo ❤❤❤❤❤🎉🎉🎉
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm Ай бұрын
Mcp ikudalira mphamvu za kumidima pa chisankho cha 2025 .
@KayceeMw-t2f
@KayceeMw-t2f Ай бұрын
Iweo for silute umakwana
@GegeJazola
@GegeJazola Ай бұрын
The dc palibeso
@BvutoOsman
@BvutoOsman Ай бұрын
Kenako muziti kalindo mutu wake sumagwila mitu yanu yogwilayo bwanji simumalankhula
@ussimasi2458
@ussimasi2458 Ай бұрын
koma chakwela ndeayi mmmm 😢
@JacquereenPereira
@JacquereenPereira Ай бұрын
Zoonad sitinavedi kuti chitedze chimadyedwa koma kuyabwa osati kudya Mene chiyabwila chitedze sindi kudziwa kuti akuchithyola bwanji president ango khalila kuyenda kokodya Magar khanu khono ku China Athu akudya chitedze nde nkumauza kuti adziyakha kwachaa zazii
@MthusaniKingstonMpofu
@MthusaniKingstonMpofu Ай бұрын
The Dcc
@BlessingsKamwendo-z9g
@BlessingsKamwendo-z9g Ай бұрын
Nenani a kalindo, soya pieces dzina lake lina ndi mwandidzidzimusa kkkkk ndiwo zachangu
@DavidKanyemba-n2s
@DavidKanyemba-n2s Ай бұрын
Kufuna kulemera Ku MCP miyezi yatsalayi dyera ma MP anthu
@SostinMatchado-z2o
@SostinMatchado-z2o Ай бұрын
Komatu chakwera kuyankhula ndiye ukuyankhulidwa koma mmutu mwakomo umaganiza bwanji ukakhala ndili inetu nditazisiya izi sikuti mupusa ayi zisiyeni nkhwiyo wathu ukafika pachipumi tibwera Komwe Uliko tidzakubilibinye galu iwe wandikwana bwanji
@ussimasi2458
@ussimasi2458 Ай бұрын
omuthandizila sakumuuuza zabwino
@WhiteRichard-cw2fo
@WhiteRichard-cw2fo Ай бұрын
Chakwela alibe zelu olo pamg' ono
@CathleenMsaya
@CathleenMsaya Ай бұрын
DC chikangawa ndi mbava
@JuliusKamoto
@JuliusKamoto Ай бұрын
Msilikali wathu
@allankapito5821
@allankapito5821 Ай бұрын
Akuti a opposition muli vyende
@PEDROCHIBADE
@PEDROCHIBADE Ай бұрын
Muwawuze agalu amenewa paka kumadya chiteze mwenzi uno mulungu atithandize
@MillieMalakam
@MillieMalakam Ай бұрын
Chakwela ndi nduna xake ndimbuziso kwambili
@JesterChikuni
@JesterChikuni Ай бұрын
Ndipo ndaona atsogoleri adziko akulephera km uyuyu uyu waonjeza ndipo ndi tsiku la munthu,ndipo pa ma report la Ndege akati Ndege inali yoonongeka?Kani imangoyamba kuuluka ndegeyo asanaioneone?tidziyionaona wheel barrow youenda pansi kmnso yoti itachita ngozi singaphe munthu kulibwanji chinthu chotenga anthu mkomwemkomwe Ndege youenda mlengalenga isachitidwe kauniuni kt ili bwino kt ingauluke
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza Ай бұрын
Zonsezo ndiwutsogoleri umene ulipo panowu anthu awutora kwambiri a business akungopanga chilichonse chomwe angafune
@happychavula4469
@happychavula4469 Ай бұрын
Kkkkkk chiteze mazi 9 mmmmmmm
@SmithBlessco-v8t
@SmithBlessco-v8t Ай бұрын
Kupusa mazungulila Malawi yose inu mutu ngati ng'azi mwayamba kuyankhula zaziii
@FestonMalunga
@FestonMalunga Ай бұрын
Mwana woyipa kwambiri ndizovuta kwambiri
@ClaraThemuka
@ClaraThemuka Ай бұрын
Ndipo tikuvutika
@MadalitsoMononga
@MadalitsoMononga Ай бұрын
amwe mumatha inuyo
@MalizeniOliviaBridan
@MalizeniOliviaBridan Ай бұрын
Kabambe atenge udindoo tivomela
@MervinKandoje
@MervinKandoje Ай бұрын
Mpaka tafika polilira soya pieces 😂
@JeremiahKapundu-j1p
@JeremiahKapundu-j1p Ай бұрын
Zoonad
@PercyRoos
@PercyRoos Ай бұрын
Katundu pangolin 😂
@RobertNyaude
@RobertNyaude Ай бұрын
😢
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 Ай бұрын
The DC mwana woyipa kwambiri
@Chikwawa
@Chikwawa Ай бұрын
Bon inuyo munatilakwitsa kuti tivotere zomwe zili panozi. Onani anthu akudya chitedze.
@BressingsMahele
@BressingsMahele Ай бұрын
Zamphamvu
@bensonjamu4038
@bensonjamu4038 Ай бұрын
Dangerous child
@CorneliusSande
@CorneliusSande Ай бұрын
Yambani ndinu kuthandiza zaboma zimakhala zochedwa .
Это было очень близко...
00:10
Аришнев
Рет қаралды 7 МЛН
Fake watermelon by Secret Vlog
00:16
Secret Vlog
Рет қаралды 37 МЛН
When u fight over the armrest
00:41
Adam W
Рет қаралды 8 МЛН
Это было очень близко...
00:10
Аришнев
Рет қаралды 7 МЛН