This UTM is the future.. Ife zama comedy sitikupanganawo... 🔥🔥🔥
@IBRAHIMCHIPASULA5 ай бұрын
I salute you hon. Kaliat
@mollymasangano4735 ай бұрын
I have enjoyed the video koma mumadula mau ena ,YEAh wayaka moto kuti buu,Mayi Kaliyati wosaaa.
@AngozoMalunga5 ай бұрын
I loved this utm so much
@BrightZionga5 ай бұрын
I love this UTM not yamanganya keep it up guys ❤❤❤
@don.swankymib41145 ай бұрын
Ya Usi ndi yama strategy osati kumangolongolola
@CharlesPhiri-ds1rk5 ай бұрын
Me I don't belong to any party...but I really hurt Malawian politics.....ndale zomangonyozana....be the best example with American politics together in one plartfoam...wina kutsitsa fundo wina kutsitsa fundo...anthu ndikumadziwa chotu adzachite...km mmmmmmm my country shame😢😢😢😢😢
@ShillahLawrence5 ай бұрын
IAM still UTM ,bcoz UTM is our Moto ,and it is the only party in MW
@MiddayDeleza5 ай бұрын
Kkkkk kkkk more fire hounarable Kaliat
@SueWahna5 ай бұрын
Kwen ndi katundu 😅😅😅
@BrightZionga5 ай бұрын
Kkkkkk usi akuti watuluka amati ndatuluka😂😂😂zakeyu sangaone patali
@PollyLysonLutepo5 ай бұрын
The best way kwa Usi. Ndikumuchotsa m'chipanimo. Pangani zomwe anapanga Peter pomuchotsa Nankhumwa yemwe anali m'thira kuwili. Usi afuna kugulitsa anthu a UTM ku mcp. Asanakwanilise zofuna zake m'chotseni.
@SueWahna5 ай бұрын
Another mfana oganiza bhoo 😅😅😅😅
@MathewKalinkhu5 ай бұрын
Koma tipemphe kuti alliance yikalepobe ndi AFORD, UDF ndi DPP.
@LeviChakwira5 ай бұрын
Mulimbikise achinyamata kuti akalembetse ndikuvota. That's the way to go
@aminkums5155 ай бұрын
Akweni enough to fit chilima shoes
@MakhiMakhi-w6t5 ай бұрын
A UTM yankhulani fundo Za chitukuko not everyday nkhani ya chilima or muyankhule kwambiri chilima sangadzuke muzimu wake rest in peace
@ChembeWaimba5 ай бұрын
UTM back to DPP kumpoto palibe chomwe mungaphulepo mwauponda mufunse zomwe anawona Chakufwa Chihana, ku Mpoto sasaturara zopusa