"Ndilibe Nanu Ntchito" Lelo Michael Usi Nde Watokotela Abale Ku Chipani Cha UTM

  Рет қаралды 12,573

Malawi Extra

Malawi Extra

Күн бұрын

Пікірлер: 147
@tingamasi106
@tingamasi106 18 күн бұрын
May the living God hu knows everything make you face what skc faced!
@BERNARDSIKWESE
@BERNARDSIKWESE 18 күн бұрын
Nsanje to. Karonga, ife a ku Chitipa sitikupanga nawo
@AnotdManganda
@AnotdManganda 18 күн бұрын
Kavuwevuwe uyu watumidwa
@ShakiraJackson-x8w
@ShakiraJackson-x8w 18 күн бұрын
Kodi nsonkhano wu ndi wa chitukuko kapena wa zipani
@LucksonChipofya
@LucksonChipofya 18 күн бұрын
Galu iyiyi uwona iweyo usi sumamukonda chilima ndiwe chigawenga yudasi
@JeremiahThaulofromMalawi
@JeremiahThaulofromMalawi 18 күн бұрын
Kuyankhula za madala mphuno.sananebepo za imfa ya chilima moyimira UTM ngati mtsogoreri mutipezatu A Usi ndale zikasintha..Ndiosokoneza uyu
@CaphusJailosi
@CaphusJailosi 18 күн бұрын
Koma Dr Usi ndikatundu 😂😂😂
@JackMvura
@JackMvura 18 күн бұрын
Usi Ali ngati Jacob Zuma PANO pa Joni ameneyu akulizani kumene apite usi chipani chimenecho chidzawina mosakaika Mark my prophecy analakwitsa chipani ndi kaliat ndi njawala kukula mtima apa MCP ilowanso kachikena akaliat fungo Latha anjawala watsala ndi mwano palibe akununkha nawonso kabambe ndiwa DPP we don't count on him he can't go forward with UTM on a profile it's okay we don't care
@JaphetSakala-u5j
@JaphetSakala-u5j 18 күн бұрын
Timaziwa ife usi mumaganiza kuti UTM ithela ku conversation. MuyilililaUTM
@tayambapodramagroup
@tayambapodramagroup 18 күн бұрын
Aaaaaa inu zoona chipani tinagulitsa kwa kabambe wafika liti mu chipan kuti anthu over 90 % akamusankhe than ma die hard eni ake?
@TaulayeDesmond-e9v
@TaulayeDesmond-e9v 18 күн бұрын
Unapha nawo chilima iwe mfiti
@MatrechBotomani-l9t
@MatrechBotomani-l9t 17 күн бұрын
Manganya apite ku disciplinary hearing sizingatheke chifukwa mpando wakhalirao ndi wachifumu basi nkhani ndiimeneyo basitu
@happychimtedza3873
@happychimtedza3873 18 күн бұрын
Koma anthu mukumwaza money
@Harryblack-g5i
@Harryblack-g5i 18 күн бұрын
Iye sangafusidwe ndi osatsata malamulo
@MalizeniOliviaBridan
@MalizeniOliviaBridan 18 күн бұрын
Chipani chakazi okhaokha
@MackenzieChoka
@MackenzieChoka 17 күн бұрын
Odya zake alibe milandu at it's best
@MolesBrown
@MolesBrown 18 күн бұрын
Mudzingolimbana ndi zachilima amzanu akutha ntunda inu muli pachilima pomwepo sizikuthandizani uyutu sakugawa maswiti ayi dzichedwani ndichilimayo poti kuti musiye zachilima mwina simungawine
@tingamasi106
@tingamasi106 18 күн бұрын
Akutha mtunda akupita kuti? Ali mchipani? Akukakamira utm coz akudziwa kuti ndi lebel yowinira. Atha pompano
@jamesstambuli200
@jamesstambuli200 18 күн бұрын
Kusokonezatu uku. Awawa azipanga za MCP
@tayambapodramagroup
@tayambapodramagroup 18 күн бұрын
Zopanda umboni
@jomochirwa
@jomochirwa 18 күн бұрын
A usi ndiwochenjela kwambiri 'kabambe sangamake kwa usi
@zayedmitawa8345
@zayedmitawa8345 18 күн бұрын
Kuchenjera kuli pati apapa. Iyeyo akulimbana ndi anthu mmalo mokonza chipani Cha UTM chomwe akuti adayamba ndi Chilima.
@fernandomonjeza8355
@fernandomonjeza8355 18 күн бұрын
Kufuna kusokoneza Chipani uku. Dr Usi akulakwitsa. Adakangonena kuti ndi a MCP.
@zayedmitawa8345
@zayedmitawa8345 18 күн бұрын
Nankhumwa wa UTM Uyu Mutuletseni mchipani basi constitutionally ya chipani.
@EdwardPatel-f1g
@EdwardPatel-f1g 18 күн бұрын
Manganya is so greasy and he's a betrayer he didn't love chilima genuinely
@tayambapodramagroup
@tayambapodramagroup 18 күн бұрын
How sure are you
@JustinKondowe
@JustinKondowe 18 күн бұрын
Yundasi ndiwe usi unangulinsa SkC ,nipo uzinkhala nimanyazi pochura dzina la mulungu .
@KarongaKaronga
@KarongaKaronga 18 күн бұрын
It's u who didn't follow d utm's rules,why u didn't pay the fees for d convention why ? instead u went on trip
@patricksinyala1345
@patricksinyala1345 18 күн бұрын
UTM Inayenela kumutengela Usi ku court ndipo amuchose mchipani. Usi ndi SATANA munthu oipa kwambiri
@tayambapodramagroup
@tayambapodramagroup 18 күн бұрын
Waipa pati
@tayambapodramagroup
@tayambapodramagroup 18 күн бұрын
Kodi zipanizi mumangotsatila kapena mumadziwa zimene zuchitika? Usi walakwa chan? Anthu sanatsate malamulo ndie mukati usi apite ku court
@HopesonLyman
@HopesonLyman 18 күн бұрын
​@@tayambapodramagroupIweyo tanena malamulo omwe anaphwanyidwa pa convetion imene ija
@HopesonLyman
@HopesonLyman 18 күн бұрын
​@@tayambapodramagroupIweyo tanena malamulo omwe anaphwanyidwa pa convetion imene ija
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 18 күн бұрын
Only my future president so far: two more Denis and kamangila simbi njanji nkhwazi za Malawi
@CharlesWitness-vp6dw
@CharlesWitness-vp6dw 18 күн бұрын
Pepani Mr Ussih mwati dzakutchipinda samaulula dza chipani kapena kuti mabvuto Ali Ku chipani cha UTM ndi A inu nonse mupite kuti mukakambiraneko kuti dzithe khonzani chipani chanu cha UTM
@AlickSaid-i1n
@AlickSaid-i1n 18 күн бұрын
Manganya asasokoneze UTM ngati amadziwa malamulo asiye zimene akuchita
@OmmyKunerisi
@OmmyKunerisi 18 күн бұрын
Kunena zoona akuluwa umuthu mulibe komaso ameneyu zikuchita kuoneselatu kuti akuziwapo kathu zaifa ya chilima mwinaso ndiiye adayambisa chifwambachija koma uyuyu aaa sali ku UTM ayi ndi wa tambala ndithu atuluke ndigalu kwabas
@Dinalamakanjira
@Dinalamakanjira 17 күн бұрын
Anthu omwe akumutsata ndi a MCP uyu ndiyemwe akudziwapo kathu pa ngozi ija
@MebleKalitsilo
@MebleKalitsilo 18 күн бұрын
Mai ali a director district koma anasiya kupita ku mcp kaya pano ali chipani chanji anthu akuba agofuna chakudya
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 18 күн бұрын
Manganya ndi DPP bola manganya MCP ndemanyaka enieni
@RafickKassim
@RafickKassim 18 күн бұрын
Iwe chitsilu ukuyakhula zopanda zeru. MCP ikukutumayo ikupwetekesa
@LuciusScott-h7b
@LuciusScott-h7b 18 күн бұрын
Malamulo achani Mesa iye amakana ndiwaukape
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera 18 күн бұрын
Kabwira ananena mu Church kuti mukatole Chakwela, kodi mawu amenwwo anakamba pa ground lamupira?.
@jameshuwanzulu
@jameshuwanzulu 18 күн бұрын
Iweyo usi ndiye kape chifukwa amzakowo sanakuyankhule pa msonkhano anakulembera kalata iwe osalembaso kalata bwanji
@KenaniFoster-q8t
@KenaniFoster-q8t 18 күн бұрын
Koma yah wina agwa ndi bp
@KennieMtseka
@KennieMtseka 18 күн бұрын
Tsono iwe Manga ukuti suchita zinthu zosathata malamulo,msonkhano ukupangitsawo simisonkho yamalawi imeneyo,koma iwe Manga zoona....
@alexsumani6823
@alexsumani6823 18 күн бұрын
KODI UYUYU ANKANENA KUTI AMADZIWA KUPEMPHA,SO FAR WAPEMPHA CHANI , APART FROM KUNYAMULA MATUMBA
@KarongaKaronga
@KarongaKaronga 18 күн бұрын
Ndipo Mr Kabambe iwe usi,sukupuma nawo bwino,ndipo sunatu utsakuka mmimba adah
@LazarusMpinganjira
@LazarusMpinganjira 18 күн бұрын
Akatero utm yamwa utsi wachamba mpungwepungwe after mpungwepungwe
@PraiseMwenegamba-p1p
@PraiseMwenegamba-p1p 17 күн бұрын
Ndi chifukwa ungoyenda ndi nthiko opanda mapoto
@MfuneExwalu
@MfuneExwalu 18 күн бұрын
Kod kumalawi uku nde kwalowa manyaka , ndi amanganya omwe , eeee Malawi yatha ndithu
@NdemboBrothersAdam
@NdemboBrothersAdam 18 күн бұрын
Wise man wanji akuzisusa yekha akuti salimbana nawo kenako nkumafunsa ndalama za pamaliro? Ngati sakulilira UTM bwanji akukamba za wena komanso akuyenda ndi akanganya atawaveka zomwezo?
@jameshuwanzulu
@jameshuwanzulu 18 күн бұрын
Opoyila awa
@CatherineMunthali-r1f
@CatherineMunthali-r1f 18 күн бұрын
Tazingodyani misonkho ya a Malawiyo munali ndani kupanda UTM inu muziti we we we pano
@Dalsonchimlomo
@Dalsonchimlomo 18 күн бұрын
Zakut UTM zisakukhudze Yudas udzingoganizira kut 2025 uzikatan tikakutulutsan 2025 September uno?
@MercyTasherah
@MercyTasherah 18 күн бұрын
Munthu woipa uyu bwanji
@MisheckAselo
@MisheckAselo 18 күн бұрын
Kodi namalira amamufunsa ndalama zachipepeso eeee koma, RIP Mr president chilima 😭😭😭😭
@Harryblack-g5i
@Harryblack-g5i 18 күн бұрын
😅
@GetiverMbewe
@GetiverMbewe 18 күн бұрын
Mmeteni mabvuzi ameneyo akuyesa kuti alimasewela atikufelanji
@DanNzima
@DanNzima 18 күн бұрын
Akusokoneza utm manganya
@tayambapodramagroup
@tayambapodramagroup 18 күн бұрын
Umboni?
@matherochanza6821
@matherochanza6821 18 күн бұрын
Kunyenga konseko osapanga anthu ako bwanji?
@HarlodLemwe
@HarlodLemwe 18 күн бұрын
paja chilungamo chimawawatu madelagates onse aja anali DPp
@CharlesWitness-vp6dw
@CharlesWitness-vp6dw 18 күн бұрын
Kodi Anthu mukuwafunza kuti kodi mwalembetsa adzikabvotera Inu Auzzi kudzera utm kapena MCP kapena mwayambitsa chipani china chanu tiudzeni A Malawi tidziwe?
@CatherineMunthali-r1f
@CatherineMunthali-r1f 18 күн бұрын
Nde kumapita kovota nkukavotela iweyo ? Nde voting yaphweka eti
@victorkachepa3515
@victorkachepa3515 18 күн бұрын
Madness at its best.
@CatherineMunthali-r1f
@CatherineMunthali-r1f 18 күн бұрын
Iwe osawalipila bwanji anthuwo ,makaka a weniwake ukutani nawo
@MakupeWekha
@MakupeWekha 18 күн бұрын
Kodi UTM osamuchotsa bwanji
@FundoGama-c9y
@FundoGama-c9y 18 күн бұрын
Komaso chimanga akunenacho sichaboma ayi ndi Chamabungwe alibe manyazi usi koma boma ili ndipo tayaluka zikolose lapasi 😢😢😢
@henryphiri6100
@henryphiri6100 18 күн бұрын
Dziko liti lapansi limene munaona vice president akugawa chimanga. Kungoonetseratu kuti alibe nzeru zokhala mma office ndikugwira ntchito zotukula Malawi. Bwanji anu ake amabungwe osagawa chimangacho
@HajieMtenje
@HajieMtenje 18 күн бұрын
Zaziiiiii !!!!
@HopesonLyman
@HopesonLyman 18 күн бұрын
Anthu kumangoombera mmanja zili zomse koma abale kusadziwa mkufa komwe ndithu. Inu malamulo amanena kuti ntchito za VP zimakhala zotumidwa ndi President lero manganya akukana anthu mkumaombera mmanja zopusazo. Ngati kumkuyu amalephera kufotokoza mpaka lero ndalama zomwe zinaonongedwa pa maliro amene aja ndiye uyu akufuna kutiuza chiyani mmalo moyambira kumtunda komwe kuli iyeyo
@GeoffreyGondwe-pk6sy
@GeoffreyGondwe-pk6sy 18 күн бұрын
Akuĺu awa amandibowa kwabasi
@PempheroEnoch
@PempheroEnoch 18 күн бұрын
Poverty is a disease
@ShakiraJackson-x8w
@ShakiraJackson-x8w 18 күн бұрын
Osadabwa nsonkhano wonsewo azimayi okha okha angofuna kalero siyani kusokonedza inu ndale si drama
@tingamasi106
@tingamasi106 18 күн бұрын
Musanagunse za 60million mufunse kaye za imfa ya chilima achitsiru inu
@alexsumani6823
@alexsumani6823 18 күн бұрын
Akulu awawa UTM 4:54 ikuwanyengelera kwambiri tisanamizanepo apapa
@AnotdManganda
@AnotdManganda 18 күн бұрын
Ndiwe kachiboliboli kumene
@Molsonabdul
@Molsonabdul 18 күн бұрын
Mai ine bundle yanga ndainongera pa mbudzi yamunthuyi
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 18 күн бұрын
Kod bwanji mukulimbana ndi utm usi mulibe nzelu abambo inu masiku akuthelani komaso ubwino wake simungayambitse utm Ina ayi utm ilipo ndi akabambe ndi anjawala
@TaulayeDesmond-e9v
@TaulayeDesmond-e9v 18 күн бұрын
Zisiru ndi anthu akumusatawo
@gloriaKasambala
@gloriaKasambala 18 күн бұрын
Uyutu azaliza mcp Chifukwa target yake ili pa Tonse Alliance Muti phee mumuwona
@AlexKasowamphete
@AlexKasowamphete 18 күн бұрын
Iwetu misala yakoyi ukusokoneza nayo anthu ...uzikumbukira what ma Sikono told you
@GetiverMbewe
@GetiverMbewe 18 күн бұрын
Mapemphelo anuwa mutitseketselabvula muzingopangazanuzoosasewela ndi mulungu ayi
@MimiKwelepeta
@MimiKwelepeta 18 күн бұрын
Ausi moto moto
@MikeMwanyula
@MikeMwanyula 18 күн бұрын
Siyani zovala za utm pezani ausi
@ChanceJeregn
@ChanceJeregn 18 күн бұрын
Chekecheke thwa uyu adzagwa chagada si kale mu lekeni
@ShamsHaroon-g6o
@ShamsHaroon-g6o 18 күн бұрын
Yudas at his best
@jameshuwanzulu
@jameshuwanzulu 18 күн бұрын
ife tinali ku tikuferanji ku mudi😂😂😂😂😂😂
@AlexChilombo-x2m
@AlexChilombo-x2m 18 күн бұрын
Koma akulu awa Ali ndi vuto koma osangopanga chipani chake bwanji
@ModesterNjikho
@ModesterNjikho 18 күн бұрын
Mcp forward
@EdwardAbu-s7s
@EdwardAbu-s7s 16 күн бұрын
Ziliko
@TwoTwoMhone
@TwoTwoMhone 18 күн бұрын
Mbudzi iyi
@ShakiraJackson-x8w
@ShakiraJackson-x8w 18 күн бұрын
Awatu akuzinamidza kuti 2025 azawina chifukwa akunyamura timatumba ta chimachinga ngati chimangacho chikuchokera tumba mwake
@SamukLungu
@SamukLungu 18 күн бұрын
Asowachochita usi akutumikadi ndi chakwela u t m ikapusa azangoyitengera kubwalo lamulandu nthawi yakamupeni Bola amuchoserethu usi
@francischikaya3146
@francischikaya3146 18 күн бұрын
Uku ndiye timati kulakwitsa zinthu. Izi sindale koma chisokonezo.
@GetiverMbewe
@GetiverMbewe 18 күн бұрын
Galu iwe tangotseka kukamwakwakoko kukununkha
@PreciousKachingwe-t7j
@PreciousKachingwe-t7j 18 күн бұрын
Mwatumidwa kapena mukupanga drama
@eliasmpita3916
@eliasmpita3916 18 күн бұрын
Osanyozera utsogoleri
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera 18 күн бұрын
Wudindo wogawa chimanga ndiwanduna osati President or Vice President.
@tayambapodramagroup
@tayambapodramagroup 18 күн бұрын
Analemba pati ngat chakudy wapeza ndie akqpelek ekha
@ChristopherManase-s1f
@ChristopherManase-s1f 18 күн бұрын
Kkkkk uyu asasula utm ndithu. Kkkkkk
@OnceMwawembe-x7c
@OnceMwawembe-x7c 18 күн бұрын
Tikufelanjitu iyi
@clementchipinga9848
@clementchipinga9848 18 күн бұрын
Usi you are wasting the Malawians money, next year uzisaza.
@tannexmsukwa1918
@tannexmsukwa1918 18 күн бұрын
Wa MCP iwe
@madalitsosymon-r1b
@madalitsosymon-r1b 18 күн бұрын
usi watsara pang'ono kupenga brief me
@sylvesteralfred8355
@sylvesteralfred8355 18 күн бұрын
Anthunso tilibe nanu ntchito
@innocentkalako7814
@innocentkalako7814 18 күн бұрын
koma ibrahim troure ndi dolo kwabasi osati manyaka wa
@AfunikaMafotetsa
@AfunikaMafotetsa 18 күн бұрын
Usi akupanga zopusa ndipo 2025 adzaone malaulo ndi iyeyo ndithu
@StainMajawa
@StainMajawa 18 күн бұрын
Pa infa ya chilima otsayakhulapo kanthu mmmmmm munthu oipa iwe kwabasi
@tayambapodramagroup
@tayambapodramagroup 18 күн бұрын
Usi is the wise person. Utm yapanga zpoila kusasata malamulo pa convention agulitsa chipani kwa kabambe amene wabwera dxana zoonekeratu kuti anapanga bribe ma delegates
@andrewmaluwa2713
@andrewmaluwa2713 18 күн бұрын
Uyu dyera anaona kuti ngati sakhala ndi chakwela ndekuti u VP saumva kukoma, akadakhala wa mzeru akadaona momwe Chilima adamutozela a MCP, mpaka July 2022 Chilima adayankhulapo, iyeyu samaona?
@tayambapodramagroup
@tayambapodramagroup 18 күн бұрын
@andrewmaluwa2713 zimene apanga a utm ku convention mugwirizana nazo? Was it fair?
@LinlyMathewe
@LinlyMathewe 18 күн бұрын
Zaziii anamulesa nda comvention umbuli basi
@lacksonkim9622
@lacksonkim9622 18 күн бұрын
​@@LinlyMathewe eti mbuzi imeneyi inathawa yokha lero azibowa anthu
@KarongaKaronga
@KarongaKaronga 18 күн бұрын
I can see Usi ur always crying for the utm's presidential seat, unfortunately ur not suitable
@rashidadan2533
@rashidadan2533 18 күн бұрын
Mcp ikufunanso kupeleka msembe ina , ndiye pajatu amakhala vice president .
@MarkMasangwa
@MarkMasangwa 18 күн бұрын
😂😂😂😂
@MisheckAselo
@MisheckAselo 18 күн бұрын
Agogo anga adiuza kuti mbuzi itakondwa kwambiri ndiye kuti amalonda ayandikira
@ShakiraJackson-x8w
@ShakiraJackson-x8w 18 күн бұрын
Mbuzi ikakondwa malonda ali pafupi
@HajieMtenje
@HajieMtenje 18 күн бұрын
A. MCP amenewo kkkkk
GWEDE GWEDE | 16 JANUARY 2025
31:11
Malawi News Update
Рет қаралды 2,2 М.
黑天使只对C罗有感觉#short #angel #clown
00:39
Super Beauty team
Рет қаралды 36 МЛН
Quilt Challenge, No Skills, Just Luck#Funnyfamily #Partygames #Funny
00:32
Family Games Media
Рет қаралды 55 МЛН
TIMVETSE | 16 JANUARY 2025
1:00:04
Malawi News Update
Рет қаралды 2,8 М.
Michael Usi - Akanaziwa sakananena izi
5:36
Malawi Top Talent
Рет қаралды 63 М.
黑天使只对C罗有感觉#short #angel #clown
00:39
Super Beauty team
Рет қаралды 36 МЛН