Ana akumuzi njale sakuyidziwa mix poor management kachimizi....you need a driver and always be cautious which vehicle you travelling in to the shows...ngati kagalimoto kanu nka baby its to hire something mechanically reliable....kanuko muzikwela ku mowa
@user-wl9vh6rc5z13 күн бұрын
Better life.
@Biath-m4b13 күн бұрын
God is good
@user-gx3xc9lk8x13 күн бұрын
Eeiishh bola palibe wavulala thank you God
@ayishaslaju635713 күн бұрын
Mmm koma malawi
@actuarialscience228312 күн бұрын
MCP ndi ufiti ndipo imapha. Chenjerani nayo.
@adamu128713 күн бұрын
Mulungu alimbali yanu mafuno abwino
@BrianMaganga13 күн бұрын
Ambuye zikomo
@user-oc9vl9xz8e13 күн бұрын
Zosakhala bwino komano tithokoze kuti mulibwino galimoto mutha kugulanso ina koma moyo nzosatheka alemekezeke Mulungu..