Ine ndikafuna kunyamuka sindingapite ku Israel kulibwino ndipete zikolina because kupita muzina la boma zilowa kundale
@tisuhmakhwah708521 күн бұрын
Zomveka bwnobwino kut ulendo palibe for now.😂😂 Nkhani zaku malawi ukamazimvela ma tv/radio akunja zimakhala zosiyana kuno nduna boma la malawi likunama too much 😂😂😂
@NumbDee21 күн бұрын
i went ku Israel last of last year osati za tchito i went for tourism was detained for 4days.(anthu opanda chisoni) ndinabwera opanda katundu it took 15days after kukavuta kuma office awo airline.kuti atumize suitcase yanga. But i thank God .Am in Europe now .8months tsopano after kundikana