Akatula udindo chakwerayo, azibale ake onse azachotsedwe ntchto. Galu watitopetsa
@user-oc9vl9xz8e6 күн бұрын
Asilikali a ku Malawi ndi ogona tulo zitsilu zimalimbana ndi anthu wamba usayelekeze kuvala kabudula wa makaka ndiye amaonesa mphamvu zawo ati wavala unform yawo mbudzi
@UsenLashid6 күн бұрын
Komaso Mr ntanyiwa musalore Kuti anthu 8 amene agwidwawo asatuluke Ayi kufikila chakwela atule pansi udindo komaso dziko la South Africa asawapange rilizi Ayi kufikila lamampho atamuzenga mulandu chakwela
@WatsonNtchito5 күн бұрын
Mademo akayambire kumamfumu hotel komweko tiyeni tonse tikasokhane popo pa mfumu hotel ku ma room achulidwawo osaopa
@FrynessMoyo-to2du6 күн бұрын
Koma chakwera wandikwana one day ndi kupedza people they call gringo
@user-ht7vs3dp2u7 күн бұрын
Ntanyiwa iweyo ndi number one radio yako timainyadira kom athu athawa ziko lili rawo kom kumeneko moto kuti buuuuu mumtimamo angokhuta mphuma lokhalokha km mulimba Ntanyiwa woyeee
@PeterMphanzaКүн бұрын
Nice job comred mwana wa amama kuno ku Zambia
@BitonFred4 күн бұрын
Anthu akumalawi umbuli, anachotsa peter, ati wabwino chakwera, pano akufuna peter yemwe uja, mmalawi wanzeru sakuyenera kupeleka vote ku president yemwe analephera kale, votelani atsopano osati apeter muthalika
@Hassankazembe-d3o6 күн бұрын
May God bless you comrade Ntanyiwa
@HalisonSolomon6 күн бұрын
Ankolo ku malawi kulibe a silikali akanakhala kuti alipo zikuchita galu ameneyo mukumuti chokwerayu atamukhazika kale pansi, koma nawo asankha kugwirantchito ndi chipani ayiwala makamulo awo ndi mbuzi za silikali za manu pansi ndi mbuyao chakwerayo tionana chaka cha mawa onse amene akupha ndi chakwera tikhaulitsa boma ili lapita olo ataopseza motani zosatheka
@EllenPhiri-xt8pt6 күн бұрын
Kuti muone ku mcp kuli anthu osaoneka bwino okhaokha pamaso ndionyasa ndi mtima momwe
@MikeMerecah6 күн бұрын
Ma activists athu musakhare chete kunoko akumangidwa mwachisisi mudziwe zimenezi, anthu osatchuka panopa Ali ku area 30 guyz,
@blacksonpeshes50576 күн бұрын
kom mukutivetsa kukoma ndikapanda kuva uthenga kuchokela kwainu sindipuma bwino kod mudarikuti mosemunja
@MathpeterLemon-ls1ns7 күн бұрын
Pano malawi ndi North Korea 😭😭😭
@AugustineIshmael5 күн бұрын
Zachamba basi dikilani 2025 vote yanu ndiye nuclear power osati zabibi zanuzi
Chitsilu chichakwela ndi family yake yonse ambuye tichotseleni munthuyi😊
@user-gj4li2gc8o6 күн бұрын
Nde inu mukuganiza kut olo patabwera peteryo zinthu zingasinthe foundation ya Malawi kuvuta konseko ndi chipani Cha udf olo mutatani Malawi sazasintha
@UsenLashid6 күн бұрын
Kodi inu apolice ndi asilikali ntchito yanu ndi chiyani kumalawiko? Kodi mukuyang'anila zika Zanu zikuphedwa Kodi inu ndinu apolice opanda ntchito pamodzi ndi iwe wa mkulu wa asilikali utule Pasi udindo coz your usiless man dammit asilikali inu achilungamo menyani nkhondo please
@user-gj4li2gc8o6 күн бұрын
Ukanakhala kut mwina ukutiwuza munthu wozamuvotera koma nawenso ukumpangila peter kampen choti uziwe peter nayenso atatitopesa kale sitikunfunanso
Asilikali Aku malawi ndi asilikadzi.west Africa asilikali sakunyengelela kulanda boma
@ThokohPrescotKalonga7 күн бұрын
Malawian kuwopa too much that’s why amakonda kulepheresa mademo so don’t tell us ngati muziwona zoti sizingatheke zochita mademo! Aaa why amakonda kulepheresa mademo
@PartsonMdeza5 күн бұрын
nkhanga zaonaaa
@BrunoChakukuma5 күн бұрын
Ntanyiwa woyeeeee
@NisharChibisa7 күн бұрын
Mumakwana
@user-td6qe4gr6w6 күн бұрын
Chopweteka kwambiri ndi choti ndalama za nkhani nkhani zikuthela kulipira anthu a kunja amene zomwe akuchita mudziko lathu phindu lake opindula ndi ochepa
@GospelSoldiers-sr7np6 күн бұрын
Ndipo kwambili eni dziko kumangosaukirabe
@AjibuTwalibu6 күн бұрын
Umakwana ya mtanyiwa tili nawenawe my brother
@GraceZumazuma7 күн бұрын
Koma Malawi walowa chibwana chakwera anapita ku sukulu koma?pano akusekedwa ndi anthu akunja omwe