NKHANI ZALERO - ANTHU AZUZULA BOMA LA ACHAKWERA POIKILA KUMBUYO ISRAEL

  Рет қаралды 9,990

HOT 265

HOT 265

Ай бұрын

Пікірлер: 77
@MartinChiumia-ge9xi
@MartinChiumia-ge9xi Ай бұрын
Israel is blessed, being against Israel is a curse according to the holy book.
@user-tn2qg1vs9j
@user-tn2qg1vs9j Ай бұрын
Iwe tipaseni zokudza a Boni Kalindo pls guys bwanji mwangoti dzzzz
@MisheckAselo
@MisheckAselo Ай бұрын
Ochakwera ndinu ochitsiru zedi
@user-bi5lg8mg9y
@user-bi5lg8mg9y Ай бұрын
Chakwera z devi leader in malawi💔
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv Ай бұрын
Dziko la Malawi ndi dziko lomvesa chiso kwambiri , Poyamba dzikoli linalamulidwa ndi munthu obwera kamudzu ndipo kamudzu analibe chikondi ndi dzikoli popesa sikunali kwawo ndipo amasakaza ndi Kuba Chuma chaboma mosaopa chiuta, komanso anawonanga ndikuphwasula maubale amayiko onse Muno mu Africa , Chifukwa kamudzu anali pambuyo ndi atsamunda nkumathandiza kupha anthu akuda ofanana kungu , mwa Ichi maubale ndi maiko anzathu Muno mu Africa , Anasokonekera , lelo munthu Ngati Malawi kutuluka kunja Kwa dziko la Malawi umachita manyaz ndi Mantha Kuti uzitchule Kuti ndine mmalawi , aliyense amene anatuluka kunja Kwa dziko la Malawi zimenezi akudzidziwa, Ndikulimba ntima kuzitchula Kuti ndine Malawi Ngati Uli kunja Kwa dziko lino 1 sulemekezeka, umaoneka Ngati ndiwe munthu wa pansi kwambiri, ndipo mMalawi sangapeze chilollezo chogwira ntchito mmaiko xhofanana ndi maiko ena onse Muno mu Africa , Izi zili chontcho kamba ka mbiliyathu sitikhala nawo muwumodzi mmayiko amuno mu Africa , mMalawi ndiwodedwa dziko lililonse kamba Koti dzikoli likulamulidwa ndi anthu opanda nzeru amangolamulidwa ndi atsamunda, pomwe anzathu akutuluka mulamulilo wa atsamunda Ife mpamene tikulowa more , Ndipo ntsogoleli uyu chakwela waliononga dziko moyipa ndipo Ngati akalowe Ku paradise I think palibe amene akalowe Ku gahena, Koma dziwani Kuti moyo Uno ndimasewela chabe ndipo simukhala ndimoyo mpaka 500years mufa posachedwapa ndipo mukayankha pamaso pa Chiuta pazomwe muchitazi mbambadi yinu muzakhala mmamvuto akulu 17:09
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Mbuli zokhazokha zandale ndikuchita zipembezo zokupha amasapota aluya
@patricksinyala1345
@patricksinyala1345 Ай бұрын
Msiyeni Malawi akhale malawi
@mafukenimasangwi5487
@mafukenimasangwi5487 Ай бұрын
Chakwela yo ndima ganizo ake osati a a Malawi ayi anati funsa enafe
@user-xe5lb4uf3n
@user-xe5lb4uf3n Ай бұрын
Waiwala kt kuli a Malawi kumeneko km Chakwera alibe chikondi ndi anthu omwe akuwatsogolera . Zodandaulisa nkumati ndi Mbusa.
@ivychithyoka1551
@ivychithyoka1551 Ай бұрын
Zosadabwisa !!!!!
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 Ай бұрын
Sakuziwa chomwe akupanga akuluwa
@Fridaymwase
@Fridaymwase Ай бұрын
Choyamba mudziwe chakwera anayamba ubusa akudziwa mulungu chomwe anapanga Ndi mtundu anachita bwino kusayankha po
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
​@@Fridaymwase😂😂😂😂😂Tabwelezanso wanenazo pls😂😂😂
@kennedybanda
@kennedybanda Ай бұрын
daudi siya kuyankhula zopepera wamva
@user-lw4hw9ce4w
@user-lw4hw9ce4w Ай бұрын
Ngati pope Francis akuzuzula Israel ndiye wina azikati god bless Israel the promised land zaukape basi
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf Ай бұрын
chakwera ndi chitdiru chamunthu satana mapwalsake
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Iweyo ndi mbuli maiko ambiri amaikonda Israel akuphedwa Hamasaki ikuphesa anthu a ma Palestinian anaiputa dala Israel zolakwa za
@user-qq4ks5mf2s
@user-qq4ks5mf2s Ай бұрын
Amalawi tiyeni tichite partnership ndi Russia. Zengelezu analinda kwaukwau
@user-rk3gq7gd8f
@user-rk3gq7gd8f Ай бұрын
Amewa ndiye mawu tiyeni Tidwell Russia
@MathewsMANDUTU-lh6oo
@MathewsMANDUTU-lh6oo Ай бұрын
Mmmmmmhhhh Ine ndye chakwera wandithesa nzeru,, munthuyu ndi okonda dollar heavy kuteroko wazitapa kwao kwa ayudako zili thumbammm.
@user-sc4mb4if5p
@user-sc4mb4if5p Ай бұрын
Chakwera amaganiza kuti akapha ma Palestine onse ndiye kuti athana ndi chi Islam mpaka ndi aku Malawi omwe komwe kuri kuganiza mozondoka
@malvinhusted6245
@malvinhusted6245 Ай бұрын
Achakwera ndachitsirutu
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 Ай бұрын
Kodi inu zoti Chakwera ndi chitsilu simukhulupilirabe
@user-vh1pf9kv8v
@user-vh1pf9kv8v Ай бұрын
Kaya amaganizaabwanji kaya
@MartherWard-fr9ue
@MartherWard-fr9ue Ай бұрын
OAAI
@georgejim51
@georgejim51 Ай бұрын
Kodi tidzimvera iwe kapena zodiac udzisaka khani zako
@IsaacKulongwe-ol5mx
@IsaacKulongwe-ol5mx Ай бұрын
I support Israel and IDF .God bless the people of the promised Land.
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w Ай бұрын
You don't even know your Bible
@patricksinyala1345
@patricksinyala1345 Ай бұрын
I love the Bible the only true word of God, not zinazi zoti atumiki Ake anali amisala osagwila Mitu satana kuwaonekela Iwo kymayesa Mulungu kkkkkkk Koma muhammadi😂 Gahena is waiting for you shameful feck prophet that never even spoke to God himself.
@user-sc4mb4if5p
@user-sc4mb4if5p Ай бұрын
Mcp government always takes place on wrong direction . We saw this on mcp of Kamuzu Banda to day with Chakwera
@user-vh1pf9kv8v
@user-vh1pf9kv8v Ай бұрын
Amalawii tikapuma kumwamba
@user-sc4mb4if5p
@user-sc4mb4if5p Ай бұрын
Chakwera akufuna kukwaniritsa Malemba ma majority ya israel ndi a Yuda yomwe chakwera anaphunzitsidwa kuti ndi mtundu wa Yesu yemwe ari Mulungu wa Chakwela ndi mcp pomwe ma Palestine majority yawo ndi ma Arabic omwe ndi akhristu ndi Aslam zomwe chakwera samadziwa koma amayesa kuti akupha chi Islam zomwe kuli kusowa mzelu
@user-qi8xe7qh1e
@user-qi8xe7qh1e Ай бұрын
Amalawi zayambika nsembe asataniki achuluka kuphatikizanso chakwela ndiwa sataniki ndipo ngozizo sizonati muziona zochuluka ngati akuikila kumbuyo izilayeli
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Chakwera 😂😂😂😂😂😂😂😂 mfiti nthakati yachabechabe tipha ndi mwala soon wait n c
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Ай бұрын
Free!! Free!! Palestine 🇵🇸
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp Ай бұрын
Chakwela amagwilzana ndiifa Komanso kukhapana iye mtima mbee
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Chimodzimodzi inuyo mumangophana mukumbukire anthu anafa pawulamuliro wanu
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Ku mpoto kunaeomberedwa anthu ambiri mchifukwa salufunanso Dpp inawapha abale wawo atola nkhani akukanika kuyanlhulapo kuwopa ndikukondera
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Sakufunanso dpp anawapha osalakwa
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi Ай бұрын
Achakwera ndi wasatanic Netanyahu ndi wa satanic Ndikukhulupilira kuti Mulungu atimvera chisoni kuti dziko lathu la Malawi kuti aka kakhale koyamba ndi komaliza kukhala ndi chitsiru chonyasa ndi choipa ngati a lazaro chakwera chitsiru choipitsitsa mdziko la Malawi.
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Palibe zimenezo a christu sangasapote hamasi gulu lazigawenga
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Ай бұрын
Puppet weniweni
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w Ай бұрын
Chakwera ndi wa satanic
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Nanga osaizuzula hamasi zomwe inakaputa mwadala Isreal
@mphatsomaulidi3424
@mphatsomaulidi3424 Ай бұрын
We support Israel 🇮🇱 🇲🇼 ❤❤❤❤
@user-mx3rw2dt4z
@user-mx3rw2dt4z Ай бұрын
Km president waganiza bwanji kuikira kumbuyo Israel
@user-vh1pf9kv8v
@user-vh1pf9kv8v Ай бұрын
Ndalama imayakhula
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w Ай бұрын
Chakwera ndi wamagadzi
@johnkambala692
@johnkambala692 Ай бұрын
Kusavota sikutanthauza Kuti kukhala kumbuyo kwa israel ai.
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Ndindani anayambisa nkhondo ku Israel atolankhani muzifunse kaye kuti Israel inayambisa nkhondo chifukwa chani?
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh Ай бұрын
Inu achigao chapakari mwamuona president wanu?timakuuzani kut ndiachitsiru mumakana
@malawigeneralguide1646
@malawigeneralguide1646 Ай бұрын
Pappet government 😢
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete Ай бұрын
Is not a surprise mcp ndichotcho imasapota athuoyipa kamuzu amachitachimozimozi ndichifukwa South Africans they don't like us here kamuzu analiso kumbali ya azungu amapha ma south Africans
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem Ай бұрын
Uja zaunyau znamulowa ndepaja mmati ndi m'busa
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Iweyo mtundu wako ndiye mbuli zokhazokha bolanso nyawuyo imangiovina koma mbuzi zolimbana ndi chakwera
@user-ym6xu3xt2i
@user-ym6xu3xt2i Ай бұрын
Achoke alibe umunthu achakwera 25 25 no vote for mcp
@afritouch4660
@afritouch4660 Ай бұрын
We support Israel 1000%.. Agalu asilamu inu kagwereni uku..!! Munakamuyamba nokha mu Yuda..!! Akumalizeni basi..!!
@issahkagansamussah
@issahkagansamussah Ай бұрын
Ndaachisilu Inu simukuziwa zomwe ukulankhula chifukwa choti alandila kanphoto kuchoka ku isrle ndiye paka kuopa kulankhulapo chilangamo
@afritouch4660
@afritouch4660 Ай бұрын
@@NkambusyeYusufu-eq5hy aku komoleni kumene afisi M’dima inu.. Mumakonda nkhondo kenaka muzirira.. Akusasureni kumene inu asilamu okudya nkhumba
@afritouch4660
@afritouch4660 Ай бұрын
@@issahkagansamussah asilamu ndi zigawenga zogwiririra azimayi aku Israel osalakwa.. aku meteni kumene.. Aluta konti nuwa..!! Tia silamu ta fake takuno ku Malawi.. Ti amidyomba 😂
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w Ай бұрын
Mukulankhulatu ngati munachita kubadwa mwa munthutu
@user-sc4mb4if5p
@user-sc4mb4if5p Ай бұрын
Father like son Kamuzu of Mcp was doing the same thing with the apartheid government of South Africa. Kamuzu wa mcp amathandiza azungu kuzunza ndi kupha anthu a kuda a ku South Africa Mozambique zimbabwe ndi wena otero. Izi si za chilendo kuwona mcp of Chakwera supporting the Israel akudutsa momwe amkadutsa kale kungoti kwinaku akuchita manyazi kupha poyela kamba ka democracy
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Nanga a stambuli matafali anapha ndi kamuzu mwana wa ku pole anapha ndi chakwera Anthu aku mzuzu amademo anaphedwa ndi chakwera
@user-rl3ku3yo6o
@user-rl3ku3yo6o Ай бұрын
ubwino wake kumalawi kunalowa usatana
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf Ай бұрын
chakwera delivery ndikumwalila anthu pa ngozi
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Dziko lililonse anthu amafa pangozi posachedwapa Bus ku south africa yapha anthu onse a bus kupulumuka mwana modzi
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 Ай бұрын
Kodi kuli Dziko la Gaza🤣??? I don’t like the Presidency of Chakwera BUT if there is one thing that Chakwera has done is to stand with Israel. Mawu a Mulungu amanenetsa in black and white that whoever curses Israel will be cursed and whoever blesses Israel will be blessed. So Chakwera is 100% correct and right. 🇮🇱🇮🇱🇮🇱🇮🇱
@user-ky2fs3zr8y
@user-ky2fs3zr8y Ай бұрын
Nkhondo inabwera bwanji ku Gaza osamangosonya chala Israel, Hamas bwanji inakayamba ntopola ku Israel ,kayiyatsa kp yr mouth shut .
@Innocentkafa-dq9gf
@Innocentkafa-dq9gf Ай бұрын
Inetu langa ndi funso chabe, Kodi Hamasi pomwe inkakaishosha muja simkaganizira za ma consequences ake? Ukaishosha limba
@user-vd6gu7tv5u
@user-vd6gu7tv5u Ай бұрын
Mkhondo sinayambile pamenepaja, zisaten bwino bwino mudziwa chilungamo.
@Innocentkafa-dq9gf
@Innocentkafa-dq9gf Ай бұрын
Ndiye inayambila pati? Kunali Nkhondo before 7th October last year? Or unali mkwiyo wakale kale ndiye amafunabe pobwezera? Abwana ndife a Malawi, anthu akuda ndithu. Ndiye ndi umalawi wanthuu timati mphechepeche mwa Njovu sapitamo kawili, Malawi tiyeni tizituluke akambilane zithe 😂😂😂
@user-sc4mb4if5p
@user-sc4mb4if5p Ай бұрын
Innocents kumafufuza kaye usanalankhule kuwopa kukhala mgulu la anthu otembeleledwa usakudziwa
@Chiso2019
@Chiso2019 Ай бұрын
A hrdc mukhale chete...dziikilani kumbuyo mesa mumaikila kumbuyo inuyo....pero chibanzi chantha?
@Chiso2019
@Chiso2019 Ай бұрын
Lero chibanzi chantha????
@user-kl1vk1gx2q
@user-kl1vk1gx2q Ай бұрын
Chakwera akugulitsa malawi km MH yokha ayi tigawana dziko lamalawi chifukwa mbuli chakwera mutu mwake mwanzaxa mamina
I PEELED OFF THE CARDBOARD WATERMELON!#asmr
00:56
HAYATAKU はやたく
Рет қаралды 26 МЛН
Don’t take steroids ! 🙏🙏
00:16
Tibo InShape
Рет қаралды 25 МЛН
原来小女孩在求救#海贼王  #路飞
00:32
路飞与唐舞桐
Рет қаралды 65 МЛН
GADGETS VS HACKS || Random Useful Tools For your child #hacks #gadgets
00:35
MAI JANE ANSAH (TIPPEX) part TWO-02
53:34
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 11 М.
Tikuferanji 05 May 2024
25:27
Edson Gunsalu
Рет қаралды 7 М.
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
NSOKHANO WA UDF KU BLANTYRE 🙌🙌🙌🙌
14:30
HOT 265
Рет қаралды 15 М.
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
Mangochi-Nyama ya Nkhumba scandal
20:46
Enock Bwanali
Рет қаралды 38 М.
The Court Of Malawi
24:32
Jimmy Chimera
Рет қаралды 36 М.
Tikuferanji 11 May 2024
25:11
Edson Gunsalu
Рет қаралды 12 М.
I PEELED OFF THE CARDBOARD WATERMELON!#asmr
00:56
HAYATAKU はやたく
Рет қаралды 26 МЛН