Izi mukunama Boma la Nankhono Lili Bali iti yadziko la Malawi.Mwazi wa chilima ukukuzuzani mupenga tikuonelani.Bakili tv Komaso Limpopo FM ilipo ikutiuza zonse.Mokulemekezani bwana mukunama kwambiri.
@augustMag5 күн бұрын
Mmmmmhu ndiye nkhani mutu wake ndi chani?
@PatienceMphuche5 күн бұрын
Kkkkk koma anthu atopatu
@user-uc1pd1tc2x5 күн бұрын
Pls ndiphwanyiredi Chakwerayo ndi Zikhale Ng'omayo Komanso Kunkuyu pls pls
@user-rg4du4vu9r5 күн бұрын
Kkkkkkkkk km wina akango khuta bonya wake uko basi wapeka zakezo nkumaza rankhura apa km zina zot usagura kunvesera kumat awa akuchita kunveka kt nyumba mwawo ufa muribetu awa kkklkkkkk nazoni guys 😂😂😂