ZOMWE APANGA A NANKHUMWA-ZA MKATI MWACHIPANI CHOMWE AYAMBITSA

  Рет қаралды 19,950

HOT 265

HOT 265

20 күн бұрын

Пікірлер: 108
@Harlod5566
@Harlod5566 18 күн бұрын
Basitu Navitcha uja wamasuka. Moreeeee fireeeeee! APM voting yaaaaaaanga😋😋😋👍
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 18 күн бұрын
Ngati umalephela kutsutsu ku parliament ungakhale otsogoleli otani iwe muthu opanda chilungamo ngati iweyo panopa tikufuna m, tsogoleli oopa mulungu osati asatana ngati inuyo iyaa mwatitola eti
@user-yh3dw6qu7z
@user-yh3dw6qu7z 18 күн бұрын
Osokoneza uyu,ali ngati chilima,anthu woononga dziko.mozambique.
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 18 күн бұрын
DPP pachiongolero basi wina afune asafune basi❤❤❤❤❤
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 18 күн бұрын
APM my vote❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-bf9mj9yb1v
@user-bf9mj9yb1v 18 күн бұрын
APM my vote
@PeterJanuary-lu3hc
@PeterJanuary-lu3hc 18 күн бұрын
Nakhumwa ndiosokoneza kwambili ndipo cholinga chawo ndichokapanga alliance ndi MCP kmbe sangazamphule kanthu,DPP more fire 🔥
@FatimaKazembe-ot1os
@FatimaKazembe-ot1os 17 күн бұрын
Mmm
@user-ez1kc7zp9m
@user-ez1kc7zp9m 18 күн бұрын
Nankhumwa,chilima, Chakwera,mapwala anu.DPP APM my vote
@user-is5dl7np9g
@user-is5dl7np9g 18 күн бұрын
Another Chichewa name for the eagle is mvundula madzi Ngati simukudziwa
@user-kd8ce8iw1k
@user-kd8ce8iw1k 18 күн бұрын
😂 palibe zomuvotela mwana wachepa
@gesinasutherland9241
@gesinasutherland9241 15 күн бұрын
A broz anga a Cemeon Phiri ulemu wanu..More fire A Nankhumwa..
@PatrickNamakhoma-zm6kq
@PatrickNamakhoma-zm6kq 18 күн бұрын
adakali ndi mkhwizi ndi DPP. why choose a name similar to DPP and the colour too. akufuna kusokoneza DPP
@InnoChabwerah
@InnoChabwerah 18 күн бұрын
Apm My Vote ❤
@isaaczidana2914
@isaaczidana2914 18 күн бұрын
Nankhumwa angamuvotere ndani? Kavuwe_vuwe
@AustinChiyembekezo-cx4mz
@AustinChiyembekezo-cx4mz 18 күн бұрын
Papah!! mwapoilatu apa😂😂😂
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 18 күн бұрын
Gulukunyinda uyu galu wangwanayo
@NoelMajawa-wi3vv
@NoelMajawa-wi3vv 18 күн бұрын
Wacita bwino kuyambisa cipani thawi yofinyana ncipani inatha Cilima akamudelela koma atayamba anagwedeza dziko
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 16 күн бұрын
Atupele,nankhumwa,joice Banda,ndi peter onsewo azikagawana ma vote kumwera chakwera basi kuyenda mwantendere mpaka 2030 wooo
@user-cy7gd1go6y
@user-cy7gd1go6y 18 күн бұрын
Nankhumwa mutu wake suukugwira wa balalika 😂😂
@JafferTiles-hp4mu
@JafferTiles-hp4mu 18 күн бұрын
😂😂😂
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 18 күн бұрын
Dpp❤❤❤❤❤
@LuteSynos
@LuteSynos 16 күн бұрын
Marawi waphweka. 😢😢😢😢
@josephchitsulo5882
@josephchitsulo5882 18 күн бұрын
Apa ndiye waziulula yekha kuti ndi chiomba nkhanga, chimunthu choipa mtima, chodanisa, choombanisa anthu, chamoyo oipa
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v 16 күн бұрын
Zose izi ndikusowa zeru
@jamesgama5489
@jamesgama5489 18 күн бұрын
Akafunse NDA ya brown mpinganjira big muyende bho Inu ndi chiwomba nkhangadi
@user-ud9wl8yg1t
@user-ud9wl8yg1t 18 күн бұрын
Mumachedwa kuti kadeti wa mcp tiyeni tiwonane pa ground
@user-bi6pb5gc8t
@user-bi6pb5gc8t 18 күн бұрын
Nankhumwa zomwe wapanga apazi ñdichimodzimodzi kukasekula babashopu yometa mavuzu ankhumba
@PeterFly-mv2nq
@PeterFly-mv2nq 17 күн бұрын
Vote yanga kwa ADAD DPP more fire❤
@user-st6bt5vv9c
@user-st6bt5vv9c 18 күн бұрын
Basi nankhumwa watha palibe achita nsanje Basi mboleche sangawine malo moti akanagwirizane niazake
@JafferTiles-hp4mu
@JafferTiles-hp4mu 18 күн бұрын
Kutha kwa a Nankhumwa😂😂😂😂
@user-yf5vq3dl5u
@user-yf5vq3dl5u 17 күн бұрын
Kungokula muthu opanda zeru mbuzi ya muthu
@mussamapira801
@mussamapira801 18 күн бұрын
Chakuba ichi chinakumwa amakhala ngati wa DPP koma ali wa mcp ali ngati chiompha nkhanga chomwecho chimangonyosola nyama kumangotaya osanya kungophera njilu wachabe 😢😢😢😢
@user-is5dl7np9g
@user-is5dl7np9g 18 күн бұрын
Nankhumwa sangatsogolere dziko la Malawi akudzinyenga chabe
@user-jn2oc3cn3q
@user-jn2oc3cn3q 18 күн бұрын
Kungofuna kuononga nthawi awa Sangakhare president wa Dziko wachulutsa bodza ndikudzikonda yekha
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 18 күн бұрын
DPP bomaaaaaa iloooooooo❤❤❤❤❤
@ahmedmsume1489
@ahmedmsume1489 17 күн бұрын
Logo ngati security company 😂😂😂😂😂
@user-pl2lj6mh1z
@user-pl2lj6mh1z 18 күн бұрын
Ine gulu uyu amandibowa bwanji
@AbuOsman-ts6ef
@AbuOsman-ts6ef 18 күн бұрын
Mukumana ndi Chala inu
@user-pl2lj6mh1z
@user-pl2lj6mh1z 18 күн бұрын
Anakhumwa galu kwabas
@user-xu2ui5em3i
@user-xu2ui5em3i 14 күн бұрын
Amp my vote
@user-oj2jr6kf9c
@user-oj2jr6kf9c 18 күн бұрын
Iwe ife ndiye tinapita kale kwa Peter ukunama
@user-lz5tl7gn4v
@user-lz5tl7gn4v 14 күн бұрын
Aaaa zopusa eti ngati ulendo simukatsegula Manda ku mudzi ndi mwayi
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 18 күн бұрын
Aaaa mutayeni uyoo
@ManzuzoMbawa
@ManzuzoMbawa 17 күн бұрын
Dpp❤❤
@Johnybegood260
@Johnybegood260 18 күн бұрын
wachamba uyu anguvotere ndani?
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 16 күн бұрын
Nankhumwa my vote
@user-rc3ze2oi7u
@user-rc3ze2oi7u 18 күн бұрын
Kkkkkkk nakhumwa kumvesa chisaoni
@user-qb1ef1xw5d
@user-qb1ef1xw5d 18 күн бұрын
Wachita bwino kuyambitsa chipani chake nankhumwa limenelo ndiye tsogolo
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 18 күн бұрын
Kuyambisa chipani chako wachita bwino koma zomwe mwaonesa akulu kosusa tilibe chikhulupiliro painu munkangopanga zamimba yanu osati zaanthu ife president wathu ndi bon kalindo waanthu amphawi.
@MosesNyasulu-lq9sf
@MosesNyasulu-lq9sf 18 күн бұрын
Eggle chimbalame yowopya anthu tose tizadibwa
@FosterChilumba
@FosterChilumba 16 күн бұрын
Angozitu mcp undercover zimatheka bwanji anthu anzeru zawo kugulitsa ufulu wao chifukwa cha ndalama a Yudasi we see u throw
@gabrielben-vj2eb
@gabrielben-vj2eb 18 күн бұрын
hahahahahahaha...koma dzikoli.....kaaya!
@ElliotOrban-th3qn
@ElliotOrban-th3qn 18 күн бұрын
Koma kummwera anthu akuvutikaa kukakomzesa ma ID and akubwezedwaa so malamulo alibe ntcito
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 18 күн бұрын
Nankhumwa ayende bwino, kanauluka kanatera.. Anatopetsa kwambiri...
@JafferTiles-hp4mu
@JafferTiles-hp4mu 18 күн бұрын
Nankhumwa akutsatira mapazi a Brown mpinganjira
@trynessmsowoya4187
@trynessmsowoya4187 18 күн бұрын
Ziliko ku Malawi eee 😅😅😅
@JuliusSikanawawe
@JuliusSikanawawe 18 күн бұрын
Ndizo mphavu aliyense alindifulu kuyambitss chipani Ngati akukhala mopatikizika
@hopembendela
@hopembendela 18 күн бұрын
Galu iwe ukapange ndi akubanja ako dza choomba nkhanga zakozo mbudzi
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 18 күн бұрын
DPP my vote Nankhumwa kagwere
@NijoWanjah
@NijoWanjah 17 күн бұрын
Chitselekwete ichi chomvetsa chison APM woyeeeeeee 1:23
@SullyBartsony
@SullyBartsony 18 күн бұрын
Apa ndiye mwatiojeza mpaka kungwetsa passport ayi zikomo achakwera
@user-vl8uw8mc3u
@user-vl8uw8mc3u 18 күн бұрын
Anapiye angapulumuke koma 😂😂😂😂😂.Rip nankhumwa
@user-cp8rz3qs8l
@user-cp8rz3qs8l 18 күн бұрын
😂😂😂😂 komadi sadya ose
@NijoWanjah
@NijoWanjah 17 күн бұрын
Chiselekwete chamunthu ichi compensation chison DPP ,APM woyeeeeeeeeeeeeeee
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 18 күн бұрын
MUKAMATI msogoleli WA CHIPANI chotsutsa Boma.chipani chake chiti
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 17 күн бұрын
Wachita bwino poti watiuza kale kuti ndi eagle chiomba 😂😂😂😂😂 anankhumwa mukuchepa 😂😂😂😂😂
@JustfiedProperties
@JustfiedProperties 17 күн бұрын
Apm my vote
@FatimaUlanda
@FatimaUlanda 13 күн бұрын
Mumthu osokoneza ngati iyeyu mkumayambitsa chipani kuti zimveke bwanji ? Adad sanalakwitse kumutulutsa ku DPP
@AndrewBwanali
@AndrewBwanali 18 күн бұрын
Munthu walephela kusutsa monga iye wa opposition leader mcp kudusa moyela sangakwanise kulamula boma
@user-uf4db7im7d
@user-uf4db7im7d 18 күн бұрын
Or atakhala ndi chizindikiro chofanana ngati dpd sangasokoneze a Malawi, anthu adzaona pomwe pali chimanga osati mbalame wagwa naye ameneyo! APM motoooooo Navicha more fire in Parliament
@BenBotolo
@BenBotolo 16 күн бұрын
Forming personal parties is not a solution to our development please avoid forming family parties
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 18 күн бұрын
Hot 265 we love you
@hot265.
@hot265. 18 күн бұрын
Zikomo Kwambiri bwana🙏🙏
@user-yf5vq3dl5u
@user-yf5vq3dl5u 17 күн бұрын
Wayambisa chipani koma palibe chomwe akuziwa mbuzi ya muthu imeneyi
@zondanitzulumusicfly.5202
@zondanitzulumusicfly.5202 17 күн бұрын
Chiomba nkhanga too much eating beware Malawi kkkj
@ThoccoBondo-mx7vt
@ThoccoBondo-mx7vt 18 күн бұрын
Nankhumwa manyaka😅😅😅😅
@alexsumani6823
@alexsumani6823 17 күн бұрын
Pano timveno akhothi ati chani uyu ndiye wayamba chipani chake ,tikungokuonanitu
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 17 күн бұрын
zitsiru za anthu nakhumwa nkhope mutu ngati phwala
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 16 күн бұрын
Kaya zanu izo zivotani muzivutika Nokha ine kuno ku joni niripheee nikudya chicken deyire
@Emmanuelngona8751
@Emmanuelngona8751 18 күн бұрын
Chilima president and nankhumwa vice president.
@wangachindeya8577
@wangachindeya8577 18 күн бұрын
😅 President wanji opanda ma looks
@mathewssiliya574
@mathewssiliya574 15 күн бұрын
tikakumana kuseu komweo
@KELVINIDENESS
@KELVINIDENESS 17 күн бұрын
mmm koma agalu awa amatiyesa agalu
@LandiranJubeck
@LandiranJubeck 17 күн бұрын
PDP security forces
@EstherPeter-cf1vf
@EstherPeter-cf1vf 17 күн бұрын
Zogwilizanatu izi ndi a mcp akufuna aisokoneze dpp akufuna anthu adzabalalike povota cholinga asadzaipeze 50 1 pasana pawo sizintheka zimenezo
@user-xm3zl5cg6x
@user-xm3zl5cg6x 17 күн бұрын
Izi ndi zipan zakuba sorry Malawi samalan ndithu
@user-qj3db4lu7c
@user-qj3db4lu7c 18 күн бұрын
Kusowa zochita osamakangotsegula Ku Manda bwanji
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 17 күн бұрын
a mec inu ndiinunso zitsiru
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 18 күн бұрын
Nankhumwa yomweyo kuli wawawa zili bwino zipani zose anachita kuyambisa adpp analibe ndi mp yemwe inu pitilini ndi ufulu wanu
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b 18 күн бұрын
Anakhumwawotu Kaya awonesa zichani zake zimenezo iyeo sangakhaleso president ngakhale patavuta motani ndi mp akuluzaso ameneo 😂
@user-hu6fd8yi7x
@user-hu6fd8yi7x 16 күн бұрын
Sangawine😅
@rashidadan2533
@rashidadan2533 18 күн бұрын
He is not 2 late , but he is weak , even he was a leader of opposition he done nothing Zipani zonse ndizadyela , inshort
@EmercianahKasiku-en6hl
@EmercianahKasiku-en6hl 18 күн бұрын
More fire Dr Namnkhumwa dziko likufuna atsogoleri achinyamata opanda matha kunena za kumtima kwawo this is our next president mufune musafune Dr chilima Dr Namnkhumwa Enock chihana,Atupele muluzi dziko lokomera tonse more 🔥
@ManzuzoMbawa
@ManzuzoMbawa 17 күн бұрын
Hot 265 umakwana
@user-pj7hn2ky5j
@user-pj7hn2ky5j 18 күн бұрын
😂😂😂 50+1 ukuwona ngt masewera kkkk😅
@FatimaKazembe-ot1os
@FatimaKazembe-ot1os 17 күн бұрын
DPP Boma 2025😂😂😂 nakhumwa ndi gawo
@user-be3is8rc4r
@user-be3is8rc4r 18 күн бұрын
Zopanda mchere nakhumwa angakhale president 😂
@gabrielben-vj2eb
@gabrielben-vj2eb 18 күн бұрын
Eti-eti-eti???
@CyprianoSandalamu
@CyprianoSandalamu 18 күн бұрын
Nakhumwa yemweyo 2025 more fire
@EmercianahKasiku-en6hl
@EmercianahKasiku-en6hl 18 күн бұрын
Zamchere nde zija akumakodzedwa asakudziwa adad ali pa msonkhano zija 85 yrs old Gogo kumamulimbikira kit alamulebe Anthu aulesi inu imilani inuyo lija Gogo lakula mwauponda mumafuna muzizasolora muti adadiwo akugona nfi ukalamba 😅😅😅😅 Eagle waona kale sigwira dpp kutha ngati makatani 😢
@mkhulukinyata5198
@mkhulukinyata5198 15 күн бұрын
Mbuzi ya mano pansi Nan'khumwa..Zaka 4 ukungololera kuti boma lizizunza a Malawi bola iwe ukumatsidwa zammanja , Ndiyeno do you think kuti ndindani yemwe angakhulupilire iwe.. Musapusitse an'thu apa , Amalawi akutulukirani mapulani anu wonse ,Iwe Galu Nankhumwa pamodzi Gwape Frank Tumpale Mwenefumbo", Nonsenu ndinu a MCP up to now, Achayini akenu mukuti kuchalira kuyisokonedza Dpp mu 2025 election .. Mmm mwawuponda .Amalawi 2025 akukasamutsa Mbava zonse zomwe zili ku State House , Ndipo tikukayikako APM ..Even muzabele nkulengezanso kuti Chakwera wawina" Koma Amalawi sadzalora inu kuti muwazunzenso ×2 .Apono ndiye tidzagendanano zogendana basi
@alexsumani6823
@alexsumani6823 17 күн бұрын
Watha uyu basi
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 18 күн бұрын
Nankhumwa chifukwa amayenda ndi mcp zeru walibe chifukwa dpd ndi dpp mukuona pali kusiyana then blue kala chimozimozi ndi dpp.chipanicho abwereso kukapanga bwino bwanji nankhumwa akulimbana ndi dpp
@lazaruschitsamba8394
@lazaruschitsamba8394 18 күн бұрын
koma Malawi muntu wa 80 years akapanga chiyani
@duncainjimmy
@duncainjimmy 18 күн бұрын
Ndie omwe sanafike Kuma 80 wa akuchita chani after kulumikizana zipani 9 komabe zakanika kufikira zomwe wa 80 yo anazifikira 😂. Mulungu akutiphunzitsa kulemekeza achikulire ,adadziwa kuti wachikulire amakhala ndimaganizo okhwima ndichifukwanso afikira zaka 80
@IdrisssJabu
@IdrisssJabu 17 күн бұрын
APM my vote
@ChrisEnos-to5uv
@ChrisEnos-to5uv 17 күн бұрын
APM my vote
Aitya Mukotsanjera. Dare ra Chief Mutasa # Karanganda TV
47:30
Karanganda Tv (Waiyepo ere ?)
Рет қаралды 5 М.
Assista na íntegra o Balanço Geral  15/05/2024
MIRAMAR
Рет қаралды 929
Каха с волосами
01:00
К-Media
Рет қаралды 6 МЛН
How to open a can? 🤪 lifehack
00:25
Mr.Clabik - Friends
Рет қаралды 13 МЛН
Don’t take steroids ! 🙏🙏
00:16
Tibo InShape
Рет қаралды 26 МЛН
Let's all try it too‼︎#magic#tenge
00:26
Nonomen ノノメン
Рет қаралды 45 МЛН
KO NHAI PASTOR || Rufu ndiro runotitora kuti tienda kumusha here? ||
8:10
Mandara Seventh Day Adventist Church
Рет қаралды 13
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 13 М.
Kodi A Nankhumwa Akulowela Kuti - Richard Mphepo
26:50
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 43 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
NSOKHANO WA UDF KU BLANTYRE 🙌🙌🙌🙌
14:30
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
MUNTHU WALANKHULA UYU...BON KALINDO, NANKHUMWA NDI A MTAMBO!!! ZOOPSA TAMVANI
20:10
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 17 М.
ESPECIAL CONGRESSO DA RENAMO  |15|05|2024
TV Sucessomoz
Рет қаралды 2,4 М.
Каха с волосами
01:00
К-Media
Рет қаралды 6 МЛН