KWAGWANJI? LERO KWACHEMASO🔥🔥🔥🤔🤔🤔 MALAWI SAZATHEKADI. 22 April 2024

  Рет қаралды 14,062

HOT 265

HOT 265

24 күн бұрын

Пікірлер: 84
@user-te3ps3kf2t
@user-te3ps3kf2t 23 күн бұрын
America ayenela kulankhula chifukwa ndi ayini ake a ndalama ,it's painful kumaona kuti akutumiza Thandie wina mkumaika mthumba make Malo mothandizila anthu Osauka
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 23 күн бұрын
Kumangoti ma court, ma court ake ati??? America sinalakwise coz too much delays ma court anthu especially milandu yeni yeni osati za born kalindo anthuwa onse ngakuba chakweraso ndiye mbudzi yeni yeni.
@rashidadan2533
@rashidadan2533 23 күн бұрын
MALAWl has destroyed because of Chakwela and his cabinet and his family , I will Happy to see this Crue are arrested , big criminals in MALAWl , We don't have court of justice here in MALAWl because all of them are under corruption of this particular government of MCP
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 23 күн бұрын
Chilungamo chili poyela apa abale palibe zozungulila zungulila apa ,milandu paka ifike 2025 kuma vote 🗳 chigamulo chizakhala liri?
@patassonelucaszovuta3431
@patassonelucaszovuta3431 23 күн бұрын
Kodi olo inuyo a kunkuyu mungalole kuti munthu amene ali ndi mbili yakuba adzibwela kunyumba kwanu kumadzacheza ndizachidziwikile kuti munthu wakuba sitimulola kubwela kunyumba kwathu
@DylesMtenje
@DylesMtenje 23 күн бұрын
Chakwela kunkuyu chimwendo mkaka mukuzitenga ngat Madolo muli agalu enene fwesek
@sweeneykamwendo6251
@sweeneykamwendo6251 23 күн бұрын
Pulezidenti omvetsa chisoni ndipo alibe manyazi
@masoyaonamunkhondya9074
@masoyaonamunkhondya9074 21 күн бұрын
Zoti a Malawi adziwe nzoti milandu ku Malawi kuno ndi a ife osauka chifukwa siyimatenga nthawi kutha Ku ma court koma zandare pa nkhaniyi ayi. President wanthu afulumira ovutika tinkhara ifeyo common people. Chonde iwo a pepese
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 23 күн бұрын
Yes zoona zikanateladi kumbali,,koma chakwela inamukhudza khani ija, chifukwa mu athu akatangalewo chakwela alimo,chifukwa walupha malile kuesa kuzibisa koma ziululika zayamba kale man chakwela
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 23 күн бұрын
President chakwera sadaganize polankhula kunyoza America, akukhala ngati akugwirizana ndi kuba.
@JIMMYWATHONJE
@JIMMYWATHONJE 23 күн бұрын
Chakwela the fool of the foolest
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 23 күн бұрын
Ma jaji athu palibe ilipo alimumbuyo ma boma lachakwela akupanga business ndichakwela ,,mukhani zakatangale
@happymumba2261
@happymumba2261 23 күн бұрын
Pamafunika kt milandu yonse imene ili mmakhoti izengedwe chaka chino chisanathe coz kuzengereza kuzenga milandu ndichifukwa chake maiko ataya chikhulupirilo ndimmene tukuchitira
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 23 күн бұрын
President akuziwapo kanthu, ndithu. And kufufuza mpaka ati 4 years akufufuzabe , aaaaaah koma amene anatilozayo ndi emweyo tili ndi vuto la muwubongo makamaka akuluakulu ku ntundaku zosaenda . Ma mericans-wa ndie kuti anafufuza kale pa okha why inu mukuchedwa pa zifukwa zoti nonse ndi akuba ndie ndi zovuta kuti akuba okhaokha sangayalusane. Ndie angoona kuti anthuwa ndi amozi asatipusise tingowauza zochita bsi eyetu.
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 23 күн бұрын
chakwera ndi chitsiru zamukwana ban imeneyi chifukwa iye ndimbavanso yayikulunso
@user-ul5hh3cz8z
@user-ul5hh3cz8z 23 күн бұрын
Çhakwela ATI tiyipasemoto yakuba 😂 okalozedwa suununkha chithandizo muchipeza Kuti. AAAAAA chimozesi kukuyu 😂😂😂 mbuziyi yatisausa
@user-mp5sd7yb7l
@user-mp5sd7yb7l 23 күн бұрын
Plezident waunsilu ameneyu
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 23 күн бұрын
Umphawii sizinthu ayi antthu amakutukwana chifukwa chaumphawi apule ali ngati kholo tele amalawi akutukwana apule chifukwa chowayimila
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 23 күн бұрын
Chakwera kodi wadziwa liti kuti America ndiyokuba ndiwe galu kwambiri usazapitenso kumeneko
@user-ev4or2kg4z
@user-ev4or2kg4z 23 күн бұрын
Mvuto a chakwela iwonso ndi mbava ndi chifukwa achita zimenezi
@robertchitsulo8006
@robertchitsulo8006 23 күн бұрын
Akulu process in low yake itiyo ? Ma count athu amachedwese milandu dala ?
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 23 күн бұрын
Milandu ili mokoti ,, tsono mosemuja mukoti igemulidwa liti kodi kufufuza kwake kotani
@user-ee6be5kl5o
@user-ee6be5kl5o 23 күн бұрын
Mbava zokha zokha mwaonjeza kwambiri bomalimeneli ndi LA anthu okuba kwambiri zikubisana chifukwa onse ndi ambava kulibwino achoke anthu amenewa sakuthandiza mzika za amalawi
@chipilirokalison1334
@chipilirokalison1334 23 күн бұрын
Aba zambiri ayamba kukula mtama a Malawi kkkkkkkk tiziona.
@ChangeChambo
@ChangeChambo 22 күн бұрын
Mbuzi ya president chakwela moyenda chinyau watikwana
@esthermalixani2244
@esthermalixani2244 23 күн бұрын
America sinarakwuse coz america ikutivera chison ife amarawi coz khani ikakhara ku court imachedw kt aweruze mpaka zaka zambili
@Dorah-zl9uf
@Dorah-zl9uf 23 күн бұрын
God job America 😂😂😂
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 23 күн бұрын
Nkhaniyo kukhotiko mpaka 4years akudikira chiyani sadalakwitse boma la America
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 23 күн бұрын
Makhothi kulibe, Acb kulibe asamaname apapa ma Judge nda Mcp aweruza bwanji milandu🙌🙌
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 23 күн бұрын
Chakwela ndiwolakwa
@GiftMshani
@GiftMshani 22 күн бұрын
In malawi we need a crismatic leader not a trained leader
@DylesMtenje
@DylesMtenje 23 күн бұрын
Mbava chakwela
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 22 күн бұрын
Achakwera akuopa awa kuti kwatsala tchire ndikomwe kupita moto. Akudziwa kuti nayenso akachoka pampando milandu yake ikazayamba iyeyu ndi ana ake adzaletsedwanso kulowa ku America poti ndikumene amakabitsa ndalama akuwabela amalawi.
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 22 күн бұрын
Iiii kunkuyu ngati sudziwatu iweyo mkaka , zikhale , Richard ndiamene mukuononga dziko lathu dziwa lero
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 23 күн бұрын
Bayana ndi wa mcp
@MustaphaMvula
@MustaphaMvula 23 күн бұрын
Muziponya nkhani zimene zachitika.kumene osati zakale Big
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 23 күн бұрын
Chilungamo chili poelatu tisamachedwe ndikufunsana mafunso apa, chakwela walakhula zambili chifukwa waona kuti luphanga likupita kwaiye because iyeyo ali mugulu la athu 4 ayimikidwa kutuluka ku America, chakwela alimo America yangopanga manyazi kwambili
@marryphili5419
@marryphili5419 22 күн бұрын
President wopanda manyazi ndipo mwayaluka Kuba mupaka ku dziko la eni ake mwalengeska Malawi
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 23 күн бұрын
Chakwela ulibe nzelu nonse ndi mbava zokhazokha
@PiliraniDenesi
@PiliraniDenesi 23 күн бұрын
Musadabwe nazo akudziwa zochita America kalipo kalipo
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 22 күн бұрын
Maloya ake mbavazo mese amachedwesa mulandu daladala kumaonangat amalawi ndiopusa
@anthonymhango9924
@anthonymhango9924 23 күн бұрын
Chakwera mutu wake sugwila ntchito 😂😂😂😂mutsogoleri opoira Anthu akubvutika kwambiri no vote for 2025😂😂😂😂😂
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 22 күн бұрын
Uyu ndiye manyi eneene
@mussamapira801
@mussamapira801 23 күн бұрын
Sindikuziwa kuti anthu Andale mumayanlhula mozungulira bwanji koma nkhaniyo mukuyiona kuti ikupita apo a president akuopa kuti nkhaniyo ndiyawo
@ChristopherBaluti
@ChristopherBaluti 23 күн бұрын
Kodi Vuto ndilakut zinthu zi ndizagulu chifukwa zinakhala za anthu watha BweZi nda police omwe akut america yachita bwino kutelo
@user-xz7mo8zy8f
@user-xz7mo8zy8f 23 күн бұрын
Manyumba mwanga onse oganilizidwa zakuba asalowe. Yatero America. Simple
@user-ce5gf4im1m
@user-ce5gf4im1m 23 күн бұрын
🤔
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w 23 күн бұрын
Wosawuka alibe mawu ,mukanakumana Kaye NDI anzanu wotsutsa boma akupatseni mayankhidwe
@patiencetebulo
@patiencetebulo 23 күн бұрын
Chakwela nd I mbuzi ya president
@marypatriciamakuru226
@marypatriciamakuru226 23 күн бұрын
Mbava zokha okha izi mkuona zikuberekana iyaaa. Timakhalira kukapempha konko,. Sitikidzera mpoto ophika nsima
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 23 күн бұрын
Chakwera ndi chitsilu amaleka kuyakhula chizungu chakwa America bwanji
@user-og8qm5qx8f
@user-og8qm5qx8f 23 күн бұрын
Zozungulira ayi tangoyankhani mafunso komanso palibepo mbalume pamenepo ndi Street thing answer the question pls
@paulmakaula4937
@paulmakaula4937 22 күн бұрын
America has followed its laws as quoted, the bsn is applied in America not Malawi...in Malawi they're free and relaxed BUT not America, they don't entertain those issues
@petertaulo8014
@petertaulo8014 23 күн бұрын
America yachita bwano kutelo
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 22 күн бұрын
Ndeakuti ma Court anthu akumalawi amatha kugwira ntchito kuposa America????😂😂😂 Koma Chakwera guys i think wapenga
@kubengovender6996
@kubengovender6996 23 күн бұрын
Alibe mphatso yawu president!!
@petertaulo8014
@petertaulo8014 23 күн бұрын
Kumkuyu garu wa munthu.
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w 22 күн бұрын
Dziko la malawi limadalu
@johnjoachim3820
@johnjoachim3820 23 күн бұрын
Support criminal adha awa and wina akamati amuvotela😮
@DylesMtenje
@DylesMtenje 23 күн бұрын
Chakwela is efeliaa
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 22 күн бұрын
Galu waluma mbuyache kkkkkk wapenga chakwera
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 22 күн бұрын
Kodi wakuba alindiufulu zopusa
@user-zl8fl7yp8q
@user-zl8fl7yp8q 21 күн бұрын
Makhotiso mukumapanga chinyengo mukudziwa kit anatigura chakwera
@DylesMtenje
@DylesMtenje 23 күн бұрын
Chakwela ndi. Wakuba. Amange bas mboni ndine
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 23 күн бұрын
Makhothi ake ati,???? Ku Malawi kulibe mathoti anapangidwa Captured ndi mcp ngati injunction ya nankhumwa kutha years nde milandu zinazi anga kambe.. Tinawombera mfiti mmanja...
@jonathanmalanda7742
@jonathanmalanda7742 23 күн бұрын
Amalawi ku opa America dziko lopanda yankho pa lokha
@bensonmughandira
@bensonmughandira 23 күн бұрын
😂Galu wankota sakandira pachabe.les wait and see. wait
@user-yk3wc9ei5g
@user-yk3wc9ei5g 22 күн бұрын
Chakwera is corrupt,thats why he is defending those people.
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w 22 күн бұрын
Kodi nkhaniyo kumakothiko idapita liti? Koma mukungopondereza chifukwa mukudziwa kuti munaba limodzi .america isiye kaye kuthandiza Malawi kwa 10 month kaye tione kuti mulipanga solve bwanji dziko lamalawi
@user-oe1lg4xo7w
@user-oe1lg4xo7w 23 күн бұрын
Ukamamubwezera mawu munthu okuzuzula zimangowoneseratu kuti ukuvomereza kulakwakwako . Kunena zowona boma lachakwera ndirazimbava ndipo makhoti onse Akulamuliridwa ndi chakwera ndi chipanichake cha mcp. Akunkuyunso sangalankhule chirungamo chifukwanayenso ndibamva.
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 22 күн бұрын
Kodi kumkuyu mmutu mwake mulimzeru?
@alexmkolongo3089
@alexmkolongo3089 23 күн бұрын
Sizikugwilizana watsala iwe
@chipanganofackison5185
@chipanganofackison5185 22 күн бұрын
Guys ma American siwofunika kumawasekelera eya zowona amapereka mathandizo Koma amakhara ndicholinga mudzikomo pamapeto adzakupusitseni then atenge zofunazo mosavuta and we need to know dziko lirilose limene mulimikangano ma American akango yamba kulowelerapo mapeto ake dziko limalowa nkhondo mcholinga azidzapangamo ma businesses azida zankhondo president wa Malawi akadapanda kulankhulapo mukadatiso ndiwogona kwambiri
@user-hx6ly3cl8m
@user-hx6ly3cl8m 23 күн бұрын
Makhot anthu akugwila ntchito ndi emusip
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 23 күн бұрын
kumkuyunso ali limodzi muwumbsva
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w 22 күн бұрын
Dziko la Malawi limadalira kuphepmpha ku america komweko ndiye americawo awone zochita basi
@user-zl8fl7yp8q
@user-zl8fl7yp8q 21 күн бұрын
Musavutike ndi kuganizaso chakwera ndi mbava.akanakhara wanzeru akanat America yandithandiza athuwa ndimbavadi
@user-uv7yq1fx4r
@user-uv7yq1fx4r 23 күн бұрын
Makondela inu koma akanakhala azipani zina bwezi mutamanga kalekale
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 23 күн бұрын
American tsinalakwe chakwelalayo ndiye wakuba kwambili mbava dzokhadzokha sitikumu funa pamozi ndi kunkuyu achoke dpp boma 2025 tatopa komaso joice banda usiletu kunamidza athu komaso athu muchenjele Joyce anaba ndalama ya ndege anayda yekha ndiye chenjelani mudza wona mavuto ngati womwewa komasotu Joyce banda alinali ku mcp motelo idzi akupanga dala akupanga akufuna kuti dpp isawine ku mwela akufuna dpp ndi pp pakati akudziwakale kuti mcp ndiyo winawina kale chonde amalawi musapange mistake kawili Joyce ndiwo tsokonedza my name is Patrick form South Africa
@violetnkhoma8535
@violetnkhoma8535 23 күн бұрын
Koma abaalee 😂
@user-zg9se4rw6v
@user-zg9se4rw6v 23 күн бұрын
Eee achita bwino pule akwiya
@CyprianoSandalamu
@CyprianoSandalamu 23 күн бұрын
America sadalakwitse ,manyumba mwathu,tikaona kuti mwana wathu akuba,amasalidwa ndi abale amakolo Ake kuti asabwere kunyumba kwathu, chifukwa Cha mbiri yakuba,ndiye dziko Lili ndi anthu akuba ndye ma mericans asekere zupusazo?
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 22 күн бұрын
You are not honest Mr President, kutha mau chifukwa aletsa mbava kulowa dziko lawo?? Mr President mukanakhala wina mukanauza a ma court athu azifulumiza milandu osat mpaka 4yrs milandu isanathe. Munthu womvesa chisoni Chakwera.
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 22 күн бұрын
Akuzengeleza kuzenga milandu chifukwa chani
I MADE A CARDBOARD SWING!#asmr
00:40
HAYATAKU はやたく
Рет қаралды 30 МЛН
HOT CURRENT 🔥 🔥 🔥 12 May 2024
25:53
HOT 265
Рет қаралды 14 М.
ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌
22:25
HOT 265
Рет қаралды 18 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
54 calls made to accused No.3 the day Meyiwa was killed
4:14
Newzroom Afrika
Рет қаралды 1,4 М.
Kodi Mulandu Wa Chilima Ndekuti Watha?   Bon Kalindo
12:51
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 41 М.
HOT CURRENT - 28 JULY 2019
55:18
Times 360 Malawi
Рет қаралды 10 М.